Тёмный
No video :(

Uladi Mussa at MCP, Kumachenjera pa town 

Malawi Page
Подписаться 77 тыс.
Просмотров 53 тыс.
50% 1

Uladi Mussa facing Lazarus Chakwera, joins MCP from Prison.
A Uladi Mussa alengeza kuti tsopano alowa chipani cha Malawi Congress Party (MCP). A Mussa alengeza izi lero ku Salima pamsonkhano wa chitukuko omwe mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera akonza. A Mussa ndi m'modzi mwa anthu omwe adachotsedwa mu chipani cha Democratic Progressive Party masiku apitawa.
SUBSCRIBE

Опубликовано:

 

28 янв 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 226   
@juniormaononga99
@juniormaononga99 6 месяцев назад
Uladi Mussa honestly had no point.😂😂😂
@user-yf8ek2hp3e
@user-yf8ek2hp3e 4 месяца назад
In politics we no longer need anthu afundo we need anthu olongolora simple
@CharlesMateya
@CharlesMateya 6 месяцев назад
Ife sitikugwedezeka APM woyeeeeee❤❤❤
@user-qw4qp5bf8m
@user-qw4qp5bf8m 6 месяцев назад
Mbava yapitaso kumene kuli mbava zimzake😅😅😅😅
@ErickIssah
@ErickIssah 6 месяцев назад
😂😂😂,
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 5 месяцев назад
Ndipo kwambiri
@user-yg9rs7tp2x
@user-yg9rs7tp2x 6 месяцев назад
choka ndiwe galu kwabasi
@MusaManati-ho4zf
@MusaManati-ho4zf 6 месяцев назад
Oipa sasowa ,,,, mwina ndi oipa kaya😢
@chizzzandazzzi6693
@chizzzandazzzi6693 6 месяцев назад
DPP woyeeeeeeeeeee!!!!
@khanilapozo-fj5tq
@khanilapozo-fj5tq 6 месяцев назад
Tikhoza kukometsera ndi lilime kuti Mcp is the party of the people koma dzuchita kuwonetseratu kuti mood ya anthu ikuyankhula zina.Mcp sikuchita za anthu pa ground
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 6 месяцев назад
Munatha auladi mussa😂😂😂😂😂😂😂
@user-vw4vc9xd5z
@user-vw4vc9xd5z 6 месяцев назад
president okuba mbuzi wamunthu nonse amene mwachoka dzipani zina kupita kumeneko zakuti zamanu nonse anthu akumpha malawi inu anthu oyipa kwambili 😊😊
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 6 месяцев назад
Kkkkkkkk zachisoni kwambiri auladi mussa
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 6 месяцев назад
Kuteloko ena akusatila koma anthu akumalawi muli mumavuto kumangokuvinitsani basi hhhhh ayi zikomo
@AubreyThipa-zc6vs
@AubreyThipa-zc6vs 6 месяцев назад
Uladi mafuta anatha kalekale mu Tank😂😂😂😂😂😂
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 5 месяцев назад
Bye bye Ulad musa
@levisonmoyo1306
@levisonmoyo1306 6 месяцев назад
Malawian politics makes me sick 🤢 every
@majiyabon247
@majiyabon247 5 месяцев назад
Big up boss 💐💖
@FOSTERLUPIYA-zc1xv
@FOSTERLUPIYA-zc1xv 6 месяцев назад
Mamuna uyu .kuganiza booo
@user-vw4vc9xd5z
@user-vw4vc9xd5z 6 месяцев назад
amalawi ndizisiru kwambili munthu oti zimukumufuna nkumapita ku sonkhano kwake
@ErickIssah
@ErickIssah 6 месяцев назад
Amalawife ndizitsilu kwambili timangombela mmanja zilizonse,ndi chifukwa tikungosaukabe mpakampaka😢😢😢
@RashidLwandle
@RashidLwandle 6 месяцев назад
Apm my vote osat agalu inu
@usherkays4379
@usherkays4379 6 месяцев назад
Shaaa uyudi ndi chenji golo umbava basi uwu shameless man
@user-xd4ip3nd1v
@user-xd4ip3nd1v 6 месяцев назад
Chakwera my vote
@user-hm4iq4lz5v
@user-hm4iq4lz5v 6 месяцев назад
Welcome Mr
@MaxwellChiwaya-tv7kn
@MaxwellChiwaya-tv7kn 6 месяцев назад
The fall down of Mwenemutape kingdom
@EliahLetulo
@EliahLetulo 6 месяцев назад
Hule wa zipani uyuyu ndikape ife ndia adad APM ❤
@GiftSalijeni
@GiftSalijeni 6 месяцев назад
APM is the best ...we are subtracting adyelen km next year tikukayakhula pa mavote ...
@victormsibandemenyu665
@victormsibandemenyu665 6 месяцев назад
Nthawi yapita kuzisankho ndichoncho anthu kukalowa komwe afuna akadye nawo
@AllieK743
@AllieK743 6 месяцев назад
Change goal 🔥
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd 6 месяцев назад
Ameneyi achooooooooooooka!!!!!
@aaronmagombo9805
@aaronmagombo9805 6 месяцев назад
Zaziii basi a Uladi munali kale inu
@KhonzoBlose-wq7zm
@KhonzoBlose-wq7zm 6 месяцев назад
Sindingaononge data yanga ndizopusa ngati izi ,Uladi musu mapwala ako ndi chakwala wakoyo
@CalmAgilityPuppy-mt1mu
@CalmAgilityPuppy-mt1mu 6 месяцев назад
😂😂😂😂
@user-mw8dq4is6k
@user-mw8dq4is6k 6 месяцев назад
Malawian politics nde kayatu🙌🙌🤣🤣
@thesocietynews3181
@thesocietynews3181 6 месяцев назад
APM MY VOTE🎉🎉🎉🎉
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 6 месяцев назад
Ali tiyeni tikadye uku 😂😂😂 ndikuona nkhondo ku malawi
@carlossadimba595
@carlossadimba595 6 месяцев назад
Kkkkkk I wonder with women who date politicians do they truely believe in what they promised for love ????? Sachedwa kutembenuka
@MaxwellChiwaya-tv7kn
@MaxwellChiwaya-tv7kn 6 месяцев назад
APM my vote
@CalmAgilityPuppy-mt1mu
@CalmAgilityPuppy-mt1mu 6 месяцев назад
Ndiwe kavuwevuwe iwe olad musa
@user-xo8ms5wh2s
@user-xo8ms5wh2s 6 месяцев назад
Kkkkkk kumachenjera pa town mavuto alipo
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 6 месяцев назад
Kkkk kokadya ndalama ayi zikomo.
@rodglae6657
@rodglae6657 6 месяцев назад
@ChrissyChibwana
@ChrissyChibwana 3 месяца назад
Adad woyeeeee
@user-px4po1xo3f
@user-px4po1xo3f 6 месяцев назад
😢😢😢😢😢😢
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 6 месяцев назад
Ukatopa ndi uhule umakwatiwa ndi mbava kapena kuti chakwera akufune akudyele chenjera ndi uladi mussa malipiro aku ndendene ndi omwe chipangwi chikasowa chogwila chimagwila sanza
@user-fy9gb8xj6k
@user-fy9gb8xj6k 6 месяцев назад
Mayb simukuona bt see how many hands in the air🤪
@robertrichman9376
@robertrichman9376 6 месяцев назад
Ndale za Malawi zopepela nkaona tingosaukirabe
@christinaibbu4339
@christinaibbu4339 6 месяцев назад
Muziti amalawi infe ndi zisilu
@robertrichman9376
@robertrichman9376 6 месяцев назад
@@christinaibbu4339 ndazipanga include tu, nkaona ndati tingosaukirabe
@christinaibbu4339
@christinaibbu4339 6 месяцев назад
@@robertrichman9376 kkkkkkkkk km
@MosesBanda-ef6fj
@MosesBanda-ef6fj 6 месяцев назад
Kwacha yagwa uladi mussa machende ako ndiwe mbuzi ya munthu a mcp pempho langa ndiloti chonde agalu onse amene alowa chipani chanucho muwa onense kapena muwatsowetse ngati muja munatsowetsera male sidic miya
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 2 месяца назад
Koma ine sindikumvesa ai ndimaganidza kuti utm ndi mcp akupanga zimozi koma ishiiiiii ndare ndizoipa kwambiri
@user-jq1gy5ds9n
@user-jq1gy5ds9n 6 месяцев назад
Boma ilo
@user-gh1yc3mu5r
@user-gh1yc3mu5r 6 месяцев назад
Zako anamusapota ameneu more than you koma anamutaya kungomugwirisa gwirisa ntchito ndi kumulavula so ask yourself mr Uladi Musa who are you? Mudyereni basi poti unali ku prison ulibe kalikose enanuso mungopitila ku MCP chifukwa chauphawi poverty
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 6 месяцев назад
Uladi musawe.ndie ukuyenela kukachindana ndi mai mia nonse makafili
@user-nq5en9mq3f
@user-nq5en9mq3f 6 месяцев назад
Zili bwino
@user-pr7xr2sv7z
@user-pr7xr2sv7z 6 месяцев назад
My vote chakwera progressive
@user-fr9dc7en9b
@user-fr9dc7en9b 6 месяцев назад
I see a cold welcome
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 6 месяцев назад
Uladi munthu, omvetsa chisoni kunali anzanu ankayankhulisanso choncho pano kuli ziiiii muzaziona.
@TiyaMtete
@TiyaMtete 6 месяцев назад
Apm my vote
@user-nv7lz7nj2p
@user-nv7lz7nj2p 6 месяцев назад
Boma iloooooo❤❤❤
@user-qe4uz9sq7f
@user-qe4uz9sq7f 6 месяцев назад
😢😢😢😢😢
@rabsonsikelo-pu1qu
@rabsonsikelo-pu1qu 6 месяцев назад
Mmm Kaka sazatheka... koma aa bas kumachenjere
@melodybashiriahmad914
@melodybashiriahmad914 6 месяцев назад
uyutu si Kaka ai. osamasokoneza
@hezekiayelemia
@hezekiayelemia 6 месяцев назад
It's true kuti player wabwino sasowa team
@MosesBanda-ef6fj
@MosesBanda-ef6fj 6 месяцев назад
Osati chipani chimene chinadzuza ndi kupha makola athu ayi zikomo galu uladi mussa kumene uliko machende ako
@yohaneben5452
@yohaneben5452 6 месяцев назад
Izi ndizomwe tikadasauka mpaka pano. Nthawi yanu inatha. Mbanva.
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 6 месяцев назад
Change goal😂 ife APM my vote
@user-nx7ot6vw7k
@user-nx7ot6vw7k 6 месяцев назад
Azawinaso MCP Bakiri adalephera kuthesa chipanichi ndiye Peter angati kkkkk
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 6 месяцев назад
Change goal mbuzi ya munthu, Akuopa kumangidwa amenewa, akagwere uko timadziwa kuti Akusokoneza DPP ndi anthu ake amenewa.
@user-fk2mq7ev3g
@user-fk2mq7ev3g 6 месяцев назад
Koma ichi mmmh 😂😂😂ndi dyera mmmh
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 6 месяцев назад
Pitani muzikanyengedwa kuthako kwakoko
@user-um1un9vh6l
@user-um1un9vh6l 6 месяцев назад
Blinders
@chikondipound5077
@chikondipound5077 6 месяцев назад
Yasaukatu iyi 😢ikufuna ndarama Abusa inu chonde mukhare ni maso auzimu
@user-pz8yb8sy6b
@user-pz8yb8sy6b 6 месяцев назад
Anthu a dyera awa
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 6 месяцев назад
Liberation time...
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 6 месяцев назад
Mbanva kumangozungulira basiii ,,
@DokotalaPhungu-lk4kn
@DokotalaPhungu-lk4kn 6 месяцев назад
Mbava yogulisa ma citizenship kwa obwera iwe. Kape.
@hendkachibowo9672
@hendkachibowo9672 6 месяцев назад
Ine pheee kudikila chilima atuluke ndi yake ija yoti ulendo uno ndi wachakwela winawo chilima
@user-uf4db7im7d
@user-uf4db7im7d 6 месяцев назад
Ulowa wekha ku MCP mbuzi iweeeee
@angelj3771
@angelj3771 6 месяцев назад
They are using junked political animations...this method was an ideal in the years 70's . Nowadays peaple are with open eyes
@user-jr5bo4to2j
@user-jr5bo4to2j 6 месяцев назад
Kkk takulandilani
@RashidLwandle
@RashidLwandle 6 месяцев назад
Mwakumana zitsiru nokhanokha
@christinaibbu4339
@christinaibbu4339 6 месяцев назад
Galu uladi Mussa podyera galu iwe
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 6 месяцев назад
Dyela izakupweteka sure
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n 6 месяцев назад
Munthu akamakhala wonenepa koma wopanda mfundo sizimveka bwino bwanji.... Akut,, a Chakwera kut asakhale zaka 10 alakwa cha? Hahahahah Upulezidenti ukuchita kumukhala uyu. 😂😂😂 Mumbili ya dziko palibeso usogoleli wopepela ngat uwu. Manyaka eni eni.
@Clyne_Phiri_265
@Clyne_Phiri_265 6 месяцев назад
Dyera chabe iyi
@carlossadimba595
@carlossadimba595 6 месяцев назад
Madzi oyenda sadzalila mpunga Peter muthalika he will loose miselably
@ChikondiKatundu-ng7gj
@ChikondiKatundu-ng7gj 6 месяцев назад
Mbuz zanthu izii
@ChristopherLipenga
@ChristopherLipenga 6 месяцев назад
kkkk ati munthu u president ukumuyenera uyu 🤣😂😂 koma ndale ai zikomo
@josiahgarley3824
@josiahgarley3824 6 месяцев назад
Why welcoming such folks. We all know that greedy. Zaumbava basi
@BerthAusten
@BerthAusten 6 месяцев назад
Uladi mussa nyera lidzakumpha ndi umphawi wakowo iweyo ndi chakwela wakoyo masende wanu
@WilfredMathews-yl6ij
@WilfredMathews-yl6ij 6 месяцев назад
Achitsiru Inu kuteroko kutulusidwa kundende kuja idali plan yokhla Ngt akukhululukira kuli kotino ulowe mcp
@chimwemwekankhuni7162
@chimwemwekankhuni7162 6 месяцев назад
Kape uyu dyera basi
@user-qe9if9ju3r
@user-qe9if9ju3r 6 месяцев назад
Mulungu akutiwona kubsala kulbe. Nde a aaaa Mulungu akutisunga ndthu mpaka tikavota 3:07 3:07 3:07
@TimbaTv001
@TimbaTv001 6 месяцев назад
Andale nonse pankolo panu mmafuna kumationa kupusa basa sindingavotele mbalame iliyonse ever
@user-mq2or1lz8h
@user-mq2or1lz8h 6 месяцев назад
Ndiyetu wakumbukila nkhaza zomwe zinaliku mcp ine ngati ndimaziziwa kuti mcp ipanga nkhaza chotere
@user-cu2rp2yj4r
@user-cu2rp2yj4r 6 месяцев назад
Kma iwe mussah ukuona ngt ife a2 tikufuna mu2 udzikhala uprezident kma iweyo ulibe mfundo DPP ikunyenyerani limodzi
@user-ro1mi6yg8m
@user-ro1mi6yg8m 6 месяцев назад
Aulad kuchenjera patauni sikumeneku.
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 6 месяцев назад
Kkkkk anakutulutsa kuti udzalowe Mcp kagwere uko ..
@MisheckAselo
@MisheckAselo 6 месяцев назад
Aaaaa kunada a galu kwabasi
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 6 месяцев назад
Nonse muli pamenepo mikongo ya Manu,kwachera m'manyumba mwanu panyero pa Manu, wanthu akufa Njala iwe Musa ukuti chani panyero pa mako
@georgemmeto9722
@georgemmeto9722 6 месяцев назад
Kkkkkkk
@BenissoneErnesto-eh6zs
@BenissoneErnesto-eh6zs 6 месяцев назад
Dpp oyeeeeee moto kt buuuuuuuuuuuuu
@user-lv4jh2wr1f
@user-lv4jh2wr1f 5 месяцев назад
Opusa ameneyi ofuna kubera anthu.
@happychimwemwe-1805
@happychimwemwe-1805 6 месяцев назад
Alibe ulesi dyela lokhalokha😅
@user-jq1gy5ds9n
@user-jq1gy5ds9n 6 месяцев назад
Team tambala ndi deal osati zanu izo za Peter opanda mano
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 6 месяцев назад
Nzeru ulibe iwe timatsata chili mwa APM osati mano chonnsecho ukugona ndi njala foseke
@tasmania527
@tasmania527 6 месяцев назад
kalime kuti udzidalire wekha kape iwe. Ulira mpaka liti? You think APM Mathanyula adzakupatsa chimanga? wauponda. MCP ndi dilu my friend and DPP ndi chipani cha mtundu umodzi chopanda tsogolo.@@user-qm1qb2jp4s
@ebenezerkamanga6016
@ebenezerkamanga6016 6 месяцев назад
Machende ako iwe
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 6 месяцев назад
@@ebenezerkamanga6016 mbolo wako
@tasmania527
@tasmania527 6 месяцев назад
@@user-qm1qb2jp4s Mwa Pitala muli chani? Mungoti mumasata chipani cha mtundu wanu. Palibe chanzeru Pitala anapanga muulamliro wake, bola malemu mbale wake.
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 6 месяцев назад
Kwacha .kukhara ine nditha kuyankha Yagwa
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 5 месяцев назад
APM bomaaaaaa
@user-xw6xf1gt7p
@user-xw6xf1gt7p 6 месяцев назад
Tilakuwi ndende ndi ooopsya
@brightbwanali2509
@brightbwanali2509 6 месяцев назад
Mbava iyi.
@user-rl3os8ex1w
@user-rl3os8ex1w 6 месяцев назад
Apm woyeeeee
Далее
Викторина от ПАПЫ 🆘 | WICSUR #shorts
00:56
Бмв сгорела , это нормально?
01:01
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH ULADI MUSSA
1:01:29
Просмотров 21 тыс.
THE LAZARUS CHAKWERA DOCUMENTARY
58:51
Просмотров 71 тыс.
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Просмотров 59 тыс.