First things first.....sangie wafunsa a 5years Aja ndi inu??😂😂 Bwanji simunamuyakhe...komanso angozo chidhindo chanu chili kuti uncle amwana......😂😂🙌🙌🙌 Also pakati is the real deal amwene...it's the way he was calling the wetaaaaa!!!! for me evidence mmanja.....mmakwana guys