Тёмный

Chipani cha UTM chalengeza kuti chatuluka mu mgwirizano wa Tonse Alliance 

Makosana
Подписаться 67 тыс.
Просмотров 87 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 246   
@kelvinchola739
@kelvinchola739 23 дня назад
Mmmm a Malawi chonde tengani Maiwa ngati mtsogoleli wa dziko la Malawi, ali ndi mphatso yaikulu Kambili. Kuchokela ku Zambia 🇿🇲
@julietbanda5203
@julietbanda5203 23 дня назад
Zakhala bwino kutuluka mumgwirizano, congrants utm and dpp my votes
@user-dp9uy6qt7x
@user-dp9uy6qt7x 22 дня назад
Hh😊i
@FazackKambwiri-he8xe
@FazackKambwiri-he8xe 23 дня назад
A UTM mwachita bwino kutuluka alliance yanu mmmm inali yakupha
@spargomw
@spargomw 23 дня назад
Ng'ona zizidyana zokhazokha tsopana😂😂😂😂😂😂 Ngat ali Chauta yemwe wakuuzan kut mutuluke, tingoti Alemekezeke Yehova coz ku Tonse mukadatha Psitiiiiiiiii. Atsaleko Manga yekha ku Tonse'ko😂😂😂😂😂
@ElizabethMajiga
@ElizabethMajiga 23 дня назад
Mwafita bwino ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@BlessingsmadalitsoShumba
@BlessingsmadalitsoShumba 23 дня назад
😂😂😂😅 wakwanika bale
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 23 дня назад
Apa nde aonetsa kuti ndie mafanadi oganiza BHO😅😅😅😅😅
@MervinChipembere
@MervinChipembere 23 дня назад
💥
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 23 дня назад
Mwachita zimene mwini wake wa chipani SKC akadachita akanakhala kuti alipobe Ambuye akudalitseni utm senior leaders
@JamesKadango-qs3ej
@JamesKadango-qs3ej 23 дня назад
Congratulations faz for SKC
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 23 дня назад
mwachedwa nazo zinthu anthu inu. munawonerera muvi kuti ukuloweni m'maso ndipo lero ndizi chipani ichi sogolo kweni kweni silikuoneka
@willardkajalika-m8g
@willardkajalika-m8g 23 дня назад
I'm just saying all the best mwachita bwino ndithu akhaleko okha akanganyawo
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 23 дня назад
Job well done 😅😅😅😂😂😂😂atsaleko adzidyana okha okha yomweyo mr Chikangawa 😅😅😅😂😂😂
@DonexMajiga-su9yv
@DonexMajiga-su9yv 23 дня назад
Dpp my vote😂😂
@Dean-De-Matrex1
@Dean-De-Matrex1 24 дня назад
Zikomo UTM pothetha mgwilidzano umeneo ndi anthu akuphawa
@BlessingsmadalitsoShumba
@BlessingsmadalitsoShumba 23 дня назад
Perfect breaking news 🎉🎉 i love it keep up ❤ utm
@CharlesChipwere
@CharlesChipwere 23 дня назад
Mai kaliyati mwachita bwino kutuluka allance ndizomwe ndimadilira zikomo ndamva bwino kuchoka Kwa mavaphire sianthu away taonani mmene ikungwera kwacha sangakwanitse kuyendetsa boma
@SothinieKanjuchi
@SothinieKanjuchi 23 дня назад
UTM for life ❤
@GertrudeMakumba
@GertrudeMakumba 23 дня назад
Zosangalatsa kwambiri changa chikunkhala chisoni mmmmm imfa imandiwawa
@joejoman4541
@joejoman4541 23 дня назад
❤nw i can able to go home n start support our country
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 23 дня назад
Ken msonda azalowera kuti ngati MCP yaluza 2025?
@user-ql8nf2vb8s
@user-ql8nf2vb8s 23 дня назад
Very good very good very
@InnocentBanda-u8y
@InnocentBanda-u8y 23 дня назад
Nde ndiwe mtsogoleli nkumawopa kukumana ndi anthu omwe ukuwasogolera pali zabwino pamenepa ndiyankheniko
@alexgweje8610
@alexgweje8610 22 дня назад
Mwachedwa inu mukadapanga izi nthawi imene Chilima adakali ndi moyo anthu amkakuuzani kuti mutuluke Alliance koma kusamva inu bwelerani ku Dpp basi
@NoxyNyika
@NoxyNyika 23 дня назад
OLO MUTATULUKA ZILI NKANTHU😂😂😂 MOTO WAMAPESI SULIMBA
@Chifundokapondodza-f6d
@Chifundokapondodza-f6d 23 дня назад
Mwapanga zanthengo wapatari kwambiri
@user-wq9ex2sf3b
@user-wq9ex2sf3b 23 дня назад
UTM for life from Zambia 🇿🇲
@GracePendame
@GracePendame 23 дня назад
Yomweyo apapa ndiye ziribwino
@user-zr7wk4oq2x
@user-zr7wk4oq2x 24 дня назад
We're a little bit happy now 🙏
@henryphiri6100
@henryphiri6100 23 дня назад
Kaliati ndinu a experience ku ndale musalore Manganya kukupusitsani.ndiwazitsutso
@emmaculatemenzeiwa
@emmaculatemenzeiwa 22 дня назад
It's not too late it's a united movement ❤
@HarrisonMponela
@HarrisonMponela 23 дня назад
That's a brilliant idea
@Vaps-king
@Vaps-king 23 дня назад
I can feel the pain inside her speech 😢
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 23 дня назад
Lululuuuuuuuuiuuuuu mwachita bwino kwasiya atombolomboyo a MCP aziphana okha okha. Very soon freedom is coming tomorrow mwachita bwino kutuluka . Lero ndigona bwino iiiiii infa ya Dr Chilima aaaayosaiwalika😭😭😭😭
@misheckjanuary1696
@misheckjanuary1696 24 дня назад
Zathapo 🤗
@MphatsoSteven-r8n
@MphatsoSteven-r8n 23 дня назад
Mwachita bwino kutulukamo mutonse mai Patricia kaliat mwalankhula bwino kwambili🎉👏👏👏👏
@ThomasMwandila-tn7cf
@ThomasMwandila-tn7cf 23 дня назад
Mama mwayankhura nthaks
@SydneySibande-z6k
@SydneySibande-z6k 23 дня назад
Very wise Leaders of UTM and all members, Leave crodiles alone to eat themselves,RIP Baba Saulos Chilima
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 23 дня назад
SKC forever in our hearts ❤❤❤❤❤❤
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 23 дня назад
Kaliati morefire mai inuyo MULUNGU adzikudalitsani ine utm my vote
@HassanIssaAbdulKarim
@HassanIssaAbdulKarim 23 дня назад
Strong woman . Courageous. Fearless. Few we have .
@user-nz9ty3ih1v
@user-nz9ty3ih1v 23 дня назад
kkkk kuteloko apa paseweredwa game kungoti apange gwilizano ndi DPP UDF ndi a FOD
@HaroonAlibarara
@HaroonAlibarara 22 дня назад
Zili bwino ndinthu utm oyeee🎉🎉🎉🎉
@Inayake
@Inayake 23 дня назад
Manganya ndi wa MCP, he is not a genuine member of UTM, Hon. Kaliati I salute you!!
@HakeemJossam
@HakeemJossam 23 дня назад
look sharp 🎉
@FredrickKachingwe
@FredrickKachingwe 23 дня назад
Utm motto ku buuuu
@FrankSpison-o7o
@FrankSpison-o7o 23 дня назад
Zikomo kwambili ndipo yehovah satitaya ife ayi anamalirs🎉
@FatsanTobiyas
@FatsanTobiyas 23 дня назад
Ngati ifa yakwamulungu alemekezeke ngati ndiabusa chakwela mulungu adzaziona ngati falawo safelapo
@SphiweSendaluzi
@SphiweSendaluzi 23 дня назад
UTM standing for us youths too Tikavote guys❤
@HastingsMaclondonmuhoko
@HastingsMaclondonmuhoko 20 дней назад
Good decision
@tiyowoyechiparton2785
@tiyowoyechiparton2785 23 дня назад
Muphese ma lawyer pano 😂😂😂
@TroubleMuthala
@TroubleMuthala 23 дня назад
That's nice 👍
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 23 дня назад
I like it 👍
@JeanyMdedza
@JeanyMdedza 23 дня назад
Good idea
@HopefulCoralReef-tx4vx
@HopefulCoralReef-tx4vx 23 дня назад
Achita bwino ndithu potuluka chipani cha MCP or blood part
@EagerChicken-qj6xu
@EagerChicken-qj6xu 23 дня назад
Komabe ndikukhulupilira kuti mwini wake sakadakhalanso ndi maganizo obwelelanso ku chipani cha dpp. Kuli aford udf konso ndi zipani zina. Think twice .f,
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 23 дня назад
Zoona nkhani ikumveka bwino ndithu palibe chifukwa chibwelera ku DPP
@ClifordMumba-f1i
@ClifordMumba-f1i 23 дня назад
Nice potuluka mugwirizano
@Littlefair7
@Littlefair7 23 дня назад
Chipani chikufunika mtsogoleri ochangamuka ngati SKC, akweni mukukwanira pa udindo upresident.
@RobertGoliat-gt2qh
@RobertGoliat-gt2qh 23 дня назад
Bwererani komwe mudachokera congrats UTM
@SuzgoMunthali
@SuzgoMunthali 23 дня назад
Mukatuluka 2023 bwezi chilima alipo Lero Koma Palibe yomwe amaziwazamawa only God knows
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 23 дня назад
Amwene...chilima samamva
@KhamaRaysonYoyora-nj9so
@KhamaRaysonYoyora-nj9so 23 дня назад
Good development
@user-px6tc4in6s
@user-px6tc4in6s 14 дней назад
Mary wachita bwino kuzisiya, ndalama anakamudyera iya
@MAGIEWAJOHN
@MAGIEWAJOHN 20 дней назад
Ai zikomo kwambiri mwachita bwino ndithu ambuye adzikutsogorerani ndithu
@AufiThera
@AufiThera 23 дня назад
Mulungu wayankha the DC 💪 alandile ulem
@andyngola3542
@andyngola3542 23 дня назад
Mcp ikhale yokha, all the best
@florenceharawa519
@florenceharawa519 22 дня назад
UTM Moto kuti🔥🔥🔥
@FrancisBanda-g9v
@FrancisBanda-g9v 21 день назад
Osada nkhawa ninthawi ikubwera 2025 kwakhala minyezi yocepa mai
@MonicaSembo
@MonicaSembo 18 дней назад
SKC made me to join politics
@linahmpl9709
@linahmpl9709 23 дня назад
Mbuzi izi bwanji simukhatuluka chilima alimoyo cause chilima amakhala akunena nde mumadikilira alowe Manda Kaye mwadya unsi
@MosesKalenge
@MosesKalenge 23 дня назад
VERY GOOD KUTURUKA KUMANDAKO MMMMMMMMM🙌🙌🙌🙌🙌😢 R.I.P SKC 😭 😭😭😭😭
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya 23 дня назад
Apa ndiye mwachita bwino, asaleko amagazi okhaokhawo, Chipani choipa chosamva madandaulo awanthu, ntchito kumanga, kupha anthu osalakwa agalu a MCP
@WysonMalack
@WysonMalack 23 дня назад
Mhuuu aaa ine nkhani ya a Chilima omandivetsa chisoni mukayankhura kungotchurapo a Chilima sindipilira Loma kututsa misozi naso manga basi ndipo ndimati adaferanjiii? Mzimu wawo uziusa mu ntendere mpaka kumuvula kohala maliseche mhuuuu Malawi mchiyani?
@SbueSbusiso
@SbueSbusiso 23 дня назад
Osaopa tili pambuyo pa utm
@user-fn5pu5zw5t
@user-fn5pu5zw5t 22 дня назад
Osabwelelanso ku DPP please
@HussainKabila
@HussainKabila 23 дня назад
💔💔💔💔🤪🤪🤪🤪😭😭zosangala mwachita bho kwambili osaopa
@B1Chitatata
@B1Chitatata 23 дня назад
Salute UTM osaopa osatopa osafooka
@user-es4jt6ds8m
@user-es4jt6ds8m 23 дня назад
Macheal utsi asapiteso Ku UTM please guys
@Leo-fj6gz
@Leo-fj6gz 23 дня назад
Mwabwela inuyo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💪🏾💪🏾💪🏾🇲🇼
@HopeMakoka
@HopeMakoka 23 дня назад
Atsaleko ekha wazisudzoyo
@BenedictChikaoneka
@BenedictChikaoneka 23 дня назад
Akuluakulu achipani basi omwewo? Tizipani tinati koma guys
@MadalitsoTamayenda-ez5pj
@MadalitsoTamayenda-ez5pj 22 дня назад
😂😂😂😂😂😂 skc woyee 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯💪💪💪💪
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q 19 дней назад
Mwachita bwino manganya simunthu nsiyeni
@user-vf2fo1mb2c
@user-vf2fo1mb2c 23 дня назад
Yebo chomene mwawanthu 😅❤MWN
@julietbanda5203
@julietbanda5203 23 дня назад
Manganya ndiwa mcp,mayi Patricia kaliat congratulations for your speech
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 23 дня назад
Mbbambande UTM awawa asiyeni apange zawo Bon kalindo uja wosadzamuphweketsa Ndikatundu womanga ndi mawaya
@ChikondiBJosaya-pr1zu
@ChikondiBJosaya-pr1zu 22 дня назад
Apa ndiye DPP 2025 wooo
@SamuelAntone-mz6nq
@SamuelAntone-mz6nq 22 дня назад
Tili momo UTM tikavotabe basi kya tikaluza kya tiwina tilimomo ife
@HanunKelekesa
@HanunKelekesa 23 дня назад
Mwachita bwino till limodzi
@TishaSamu-kc4ks
@TishaSamu-kc4ks 23 дня назад
Good decision.
@ElliottBelon
@ElliottBelon 23 дня назад
No alliance nkhan yabwino mai kaliat anthu akupha achoke Malawi siwawo
@TorshKadango
@TorshKadango 23 дня назад
Ndpo zachita bwino kwambli osatopa osaopa osafooka
@webstermbewe8395
@webstermbewe8395 23 дня назад
Yes I wish chilima had done it in July 2022
@MemoryGalaonga
@MemoryGalaonga 21 день назад
Chipani cha utm chachinyata
@Fredoh10
@Fredoh10 23 дня назад
Ndipo maganizo abwino amenewo ndthu, ndiye chomwe akuyenera kupanga achipan cha UTM nchoti agwire ntchito nd a DPP ndipo zinthu zizayenda bwino even awo sazakhalaso nd mphavu
@GibsonLackson-sf6uh
@GibsonLackson-sf6uh 23 дня назад
Good decision sitiopa kmaso kufooka 😳😳😳😳😳😳😳😳😳😳😳😳😳
@SajeFurniture-wj1ue
@SajeFurniture-wj1ue 23 дня назад
Great move
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 23 дня назад
Mwachita bwino mwatulukamo atsale ndi chikangawa waoyo
@BiCyfer-pp8ke
@BiCyfer-pp8ke 22 дня назад
Kkkk km amai awa
@BittonNgwangwa
@BittonNgwangwa 23 дня назад
Mungotenga thomu mpinganjira asogolere chipani tizawina 2025 basi
@janealinanemthunzi2880
@janealinanemthunzi2880 23 дня назад
Koma osabweleraso ku dpp
@GeorgeLipengaphiri
@GeorgeLipengaphiri 23 дня назад
Amai takulandilani inu mwabwela
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 23 дня назад
UTM you have to move manganya
@BwanaGD
@BwanaGD 23 дня назад
Komati inu a UTM kudzinthetsa mwadzi nthetsako mutiphetsa amatitu akamawona inuyo amalimba mtima koma apa eee tikuntha bas
@FrankSaizi-cc4bj
@FrankSaizi-cc4bj 23 дня назад
Well done come out of tonse alliance
@julietbanda5203
@julietbanda5203 23 дня назад
Osaopa osafoka osanjenjemera,tidzafera mbendela yathuyi
Далее
DR JOYCE BANDA KUYANKHULA KOYAMBA MU CHAKA CHINO
16:16
MPHEPO ZINAYI: UTM KUTULUKA MU MGWIRIZANO
59:06
Просмотров 8 тыс.