Тёмный

USAUVER S07E10 KUTHAMANGA THAMANGA 

Piksy TV
Подписаться 59 тыс.
Просмотров 93 тыс.
50% 1

Kuthamangathamanga.. Mafizo?

Развлечения

Опубликовано:

 

23 фев 2023

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 294   
@tiyamikeemmanuelkabanga4105
Komatu chozemba chinakumana ndi chokwawa. Mtebe anytime aziona ndithu
@tazmeenmdals9904
@tazmeenmdals9904 Год назад
I love the new guy😂😂😂 ati iwe ndi ndan nayenso iwe ndi ndan😂😂🙌🙌🙌 ziwoneka mnyumba imeneyi
@cynthiachibwana6109
@cynthiachibwana6109 Год назад
Ati mai wangwirooo kkkk mtopola new guy mnyumba umu kayaaa
@gracekachali4505
@gracekachali4505 Год назад
Is mayi wagwiroo for Mee kugofikila kuyakha mwano ati iwe ndi nda😂😂😂😂😂
@josephymakwete7085
@josephymakwete7085 Год назад
Koma adha new alibho hvy
@andrewchiusiwa3487
@andrewchiusiwa3487 Месяц назад
​@@gracekachali4505 it was prophetic to Jetu's song. Apo akanangoyankhilatu kuti "ine ndi Jetu"😂😂
@tonychimphepo9402
@tonychimphepo9402 Год назад
Big up guys mukuyitha..... Koma nthawi nde mukutibera2 aaah! Atleast ka 45min chabwino
@janicevangelder2119
@janicevangelder2119 Год назад
Looking forward to the next episode. I CANT WAIT
@joreendallas8102
@joreendallas8102 Год назад
My first time watching this, and I'm already addicted 🔥😍
@elidadailesi1324
@elidadailesi1324 Год назад
Usaver is addictive my friend😘🤣🤣
@joreendallas8102
@joreendallas8102 Год назад
I can't bet, yes eeh
@tazmeenmdals9904
@tazmeenmdals9904 Год назад
Komanso Edo you amakwanitsa heavy 😂😂😂 he does it more naturally and effortlessly
@milibanda8841
@milibanda8841 Год назад
Always you take me to anoder levels you guys Mumatiimiliraa🤞🤘🖐
@dicebophani4074
@dicebophani4074 Год назад
Have been waiting for so long......#bestInMalawi
@tasneemkuipa5761
@tasneemkuipa5761 Год назад
Mwandisiyila mmalele guys😢 Koma it's giving 🔥keep it up guys 👌 Please add the time if possible Much love mumantha🥂
@FLORIDAMAIGWA-mk7je
@FLORIDAMAIGWA-mk7je Год назад
Komatu sangie ndi pisky mumandiwaza hvy please taponyani mwachangu next yo mpaka tizigona ndi njira zoona
@bensonpaul6866
@bensonpaul6866 Год назад
Massive guys... The Series is getting hotter day by day🔥🔥
@khadijahbwanali362
@khadijahbwanali362 Год назад
This is really good work..
@hopesonnanguwo1444
@hopesonnanguwo1444 Год назад
Inu mukachimwa muzilapa kwa ine ineso ndizilapa kwa inu ndikachimwa🤣🤣🤣
@isaacjackson2555
@isaacjackson2555 Год назад
Kkkk akut pamenepo!!!! Wailowa bho ase...welcome kwangozo
@ellenchambwinja-vn3dl
@ellenchambwinja-vn3dl Год назад
Welcome back mamie iiiiii koma mpakan iwe ndan aaaaa komatu
@BlenacAnimations
@BlenacAnimations Год назад
Guys, inuyo ndi one. I like this show boss
@amoscollerahgondwe1551
@amoscollerahgondwe1551 Год назад
Gani is like "yeselo imadziwikatu"🤣🤣🤣🤣🤣
@elizachatchuka2805
@elizachatchuka2805 Год назад
Ati abusa amakonda kuyenda mothamanga😂😂😂great work guys
@prekam265
@prekam265 Год назад
Gani my all time favorite 😂😂
@twarichissah4222
@twarichissah4222 Год назад
Hahahahahaha ndafwa ndatha 😂😂😂😂😂😂 koma guy’s more fire 🔥 mmakwanila inuyo
@mboneramsimuko7583
@mboneramsimuko7583 Год назад
Eddoh amandiwaza 🔥🔥🔥 koma alendo waapeza Patricia siwamasewera 🤣🤣🤣🤣🤣
@andrewchiusiwa3487
@andrewchiusiwa3487 Месяц назад
10:53 Paja m'busa ananena kuti ndi 'Davide ndi Uliya', nde here we go. Albert sanalakwitse kuima😂 akonzekere
@fredoalfred8909
@fredoalfred8909 Год назад
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥you guys keep pushing mwayaka
@linahmoses2356
@linahmoses2356 Год назад
Ilove the new guy kkkkkk ati iwe ndi NDA🤣
@MsSerahMw
@MsSerahMw Год назад
Koma a edho😂😂😂ati muoneka kuti mulizakatu😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@markboazdaire6747
@markboazdaire6747 Год назад
Mr white ndebvu nde akuthawatu kkkkk mkubhebhesa guyz🔥🔥🔥🔥
@Toxincj
@Toxincj 2 месяца назад
Km episode iyiyi is the best
@erickondowe8781
@erickondowe8781 Год назад
This is good well made
@constantinechimodzichiwaul6907
nde ati spiritual father
@joseblessmasauko7450
@joseblessmasauko7450 Год назад
I love u guys continue kutipasa staff yabho
@tisunganemaonga3502
@tisunganemaonga3502 Год назад
Mwabwera guys🔥🔥
@chikondiphiri7077
@chikondiphiri7077 Год назад
😂😂😂😂😂Abusaaaaaaa , cant wait for another episode
@chifundobryanmanyamba4837
@chifundobryanmanyamba4837 Год назад
Lol
@daviekasusu9015
@daviekasusu9015 Год назад
Keep the fire 🔥🔥🔥 burning guys ☺️
@ivyfrankie-jf2eq
@ivyfrankie-jf2eq Год назад
Ntebe ATI madam sakupeza bwino😂😂😂😂🙌
@chiccopartrice7378
@chiccopartrice7378 Год назад
Akut anthu ndifeyo asaaaaa😅😅😅 Mtebe nae kudzangoiyonela patali eeeeeish 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@reubenchiumia-tr2jt
@reubenchiumia-tr2jt Год назад
🔥🔥🔥🔥 koma ka usauver tshirt kali bhobho kwambiri, nde mwati mteba a ulula machimo kkk
@mercygarnet5955
@mercygarnet5955 Год назад
It's "anthu ndifeo" for me😂😂🔥
@nyasavoicebox
@nyasavoicebox Год назад
🤣
@arthurntchito
@arthurntchito Год назад
Kma tu pamene atapezekere mtebe pachema 😂🙌
@AlliUsuman-mj1mr
@AlliUsuman-mj1mr Год назад
Akt kukadakhala kopanda azimayi kusamba njeeeeeeee😂😂😂😂
@simdoo1025
@simdoo1025 Год назад
Ganizani eee kkkk umakwanitsa aise kkkkkkkkk ati ndimakhala Kwa Sister wanga awa ndamuna awo kkk
@mayamikohamison-ox2iy
@mayamikohamison-ox2iy Год назад
Ganizan ndi bigy amandiwaza
@margaretmpando6793
@margaretmpando6793 Год назад
Mukuoneka kuti muli zaka tu 🤣😂😅🤣 a Edo kuyankhula kwabwanji ukuku kkkkk
@MirrieMw
@MirrieMw Год назад
Mukazachimvetsa chibale simuzadabwa 😂😂 kkk Ati mumuuze kwabwera anthu akumuyang'ana kkk komatu guyz mukuthatu kenanso mwachangu
@khadijailiyasa5315
@khadijailiyasa5315 Год назад
Komatu abusa akungo thamanga thamanga 🤣🤣😂 ukamalakwa umangozithawatu wekha 🤗
@sothinchipeta6098
@sothinchipeta6098 Год назад
Mowa nd mowa, cholinga nchimoz kkkkkkkk man gani samasewera
@yamikanigross1455
@yamikanigross1455 Год назад
Abusa akuthawathawa kkkkkk kmatu akupeza tsku lina
@lennahchanika
@lennahchanika Год назад
Hyphe for me ati umuze kwabwera an2 akumufuna
@sandramhlanga7956
@sandramhlanga7956 Год назад
Continue Mr ngozo
@BlenacAnimations
@BlenacAnimations Год назад
Kodi izithela kuthawa Mtebe yo? Koma tsiku lozakumana lo kkkk
@catrinamulowa1848
@catrinamulowa1848 Год назад
🔥🔥🔥🔥 keep it up guys
@Viewymw
@Viewymw Год назад
Ganizani is a don 🔥
@lazarolucianodomingos800
@lazarolucianodomingos800 Год назад
Kkkk pamenepa zabeba kuti Mtebe wayiwala foni, pakufunika Belita ayimbe foni, koma zikhale kuti Mtebe number ya Belita anaseva kuti phwando lakakowa
@Alhaasibuh24
@Alhaasibuh24 Год назад
First to comment 🙄🙄👊👊👊✌️😍
@mosesmkandawire1057
@mosesmkandawire1057 Год назад
Kkkkk koma muthebe mpaka kuzigwia yekha pakhosi
@MindsetChange144
@MindsetChange144 Год назад
Love you guys
@isenyirenda4483
@isenyirenda4483 Год назад
Ati mayi wangwiro 😃😃😃
@elidamoses1912
@elidamoses1912 Год назад
Pamenepo!!!!....kkkk...more fire guys
@reflopictures
@reflopictures Год назад
Mtebe nde la 40 likumuyandikiratu, am seeing belita akuyimba phone right mu phone ya zibwenzi waisiyayo, mbola braz E11 ikoma heve
@pachaloziba4474
@pachaloziba4474 Год назад
All my favourite people 🥰🥰
@alickkamanga5783
@alickkamanga5783 Год назад
Kamatha kakukoma akaka, waiting for next episode
@mixedbagwithanankhoma476
@mixedbagwithanankhoma476 Год назад
Hahahahaha hahahahaha hahahahaha hahahahaha hahahahaha hahahahaha hahahahaha hahahahaha ati muli zaka komatu
@innocentjuliusnkhoma3235
@innocentjuliusnkhoma3235 Год назад
Ineyo ndufikira ngozo akakumana ndi Namkalizi uja kut zitha bwanji
@ketithawatha3901
@ketithawatha3901 Год назад
I love you guys 🥰keep it up
@ankolonjemw4913
@ankolonjemw4913 Год назад
Keeping good work my brothers and sisters I'm interested for this to join 💥💥💥
@glochiwaula2005
@glochiwaula2005 Год назад
Palipo pomwe akukatumikira hahaha, patipo Ganizani🤣😂
@mphatsodyetsan-sl3nm
@mphatsodyetsan-sl3nm Год назад
Mtebe chokwawa chinakumana ndi chozemba uziona day 1
@tee-qk3ri
@tee-qk3ri Год назад
Its iweo tidzifunsa iweo from hyphen for me
@magretmgawa2992
@magretmgawa2992 Год назад
Ganizani, ati palipo pomwe akukatumikira 😂
@muza8710
@muza8710 Год назад
Edo ndiwa mabodza😂😂... A Member asiya phone Belita asayimbetu..
@penielmakaika8937
@penielmakaika8937 Год назад
My favourite
@moneytalkwithpru
@moneytalkwithpru Год назад
Ati amakhala kwa sister wake angozowo ndi amuna ake a sister yo 😂
@chimwemwenyirenda174
@chimwemwenyirenda174 Год назад
Mumakwana magaye
@ceciliamulewa6311
@ceciliamulewa6311 Год назад
Ati anthu ndifeyo🤣🤣🤣. Ameneyu ativutatu
@patriciaaron2568
@patriciaaron2568 Год назад
Mtebede waiwelenga😂😂😂😂😂
@ruthmhango1811
@ruthmhango1811 Год назад
Ati anthu ndifeyo aaaaaah 😂😂
@duniamkandawire8317
@duniamkandawire8317 Год назад
Hyphen 😂😂 ATI "mumuuze anthu akumufuna" 😂
@lusakoswira9000
@lusakoswira9000 Год назад
Ati izi ndingochedwa nazo....... Mula mumafikanso kuno ....😂😂😂🤣
@MWENEMUHASSA
@MWENEMUHASSA Год назад
Ati kudalisidwa ndi dazi Wina imviii🤣🤣🤣🤣🤣
@damiankondwani2040
@damiankondwani2040 Год назад
Mowa ndi mowa basi 😂😂😂
@shantelnoah2446
@shantelnoah2446 Год назад
Abusa nao 😂😂😂angoyenda chothamanga😂
@GenWealth728
@GenWealth728 Год назад
Koma a Edo wo nde amakhala ndi mafusotu......
@kumbukanimalunga7575
@kumbukanimalunga7575 Год назад
Patricia wayankhidwatu ukuuu naye thebedee akuchita kuzigwilitsatu Guys mumakomesa angakhale lero gan mwapezeleratu kkkkk
@aishaesmansa6999
@aishaesmansa6999 Год назад
Mmakwana guys❤️❤️❤️
@omegamatanda5541
@omegamatanda5541 Год назад
😂😂😂😂 iweyo ndinda🤣 koma ndafaa
@kingsleynoah6777
@kingsleynoah6777 Год назад
waiting for the next
@charleschilole3166
@charleschilole3166 Год назад
Ati anthu alikuti,anthuwo ndye mesa ndneyo😅😅😅
@innocentbanda9942
@innocentbanda9942 Год назад
Ntebe dziko likuchepa
@paulmapepa9094
@paulmapepa9094 Год назад
hahahahah ati ukazachimvetsa chibale hahaha ganizani
@rawlingsmkomera1924
@rawlingsmkomera1924 Год назад
Awesome
@tamaralongwe9401
@tamaralongwe9401 Год назад
Alendo abwanji? Ntebe kuzipasa ukapolo
@girlmama265
@girlmama265 Год назад
Koma mulendo wa mwanoyo ndingamuswe mbama, mnyumba mwanga mmenemo mopangila zopusazo?
@lusunguhkayira6924
@lusunguhkayira6924 Год назад
Kopezera mpumulo😂😂😂
@chiukepotychuxxyluwingakal1784
Mumatha we need nepman
@kelvinchipole4335
@kelvinchipole4335 Год назад
Inu mukachimwa mudzilapa kwa ine 🤣🤣🤣🤣😂😂😂😂 the opposite is true
@finahukasha1179
@finahukasha1179 Год назад
A ganizani mpaka chizungu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@kelvinchirwa7476
@kelvinchirwa7476 Год назад
kkkkk komatu mlendo uyuyu ndiwamwano
@francescakapakasa1036
@francescakapakasa1036 Год назад
Mwabwera🔥
@Viewymw
@Viewymw Год назад
😂 ati mayi angwilo
@daviembunju5278
@daviembunju5278 Год назад
Keep it up guy's
@tonychimphepo9402
@tonychimphepo9402 Год назад
Koma Man Gani ndi one ..... Munthu ndiwe Wiseman wa abusa chomadabwiranso pagulu kuti abusa Ali ndi mkazi nchani?
@stevengwiranipansi21
@stevengwiranipansi21 Год назад
Ubusa uwu watilaka bas😂😂😂😂
@clivedinala8540
@clivedinala8540 Год назад
Kma nthawi taonjezerani atleast ka 30 to 45 kakumakomatu....
@zairachisolola-ls5qh
@zairachisolola-ls5qh Год назад
Komatu mwandisiya malele 🤣🤣🤣🤣
Далее
USAUVER S07E11 - MUDYA CHA
11:43
Просмотров 100 тыс.
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Просмотров 14 тыс.
ЮТУБ БЛОКИРУЮТ?
02:04
Просмотров 637 тыс.
Китайка Шрек всех Сожрал😂😆
00:20
Musikana Webasa - Part 1
20:01
Просмотров 14 тыс.
Usauver S06 Intro   Matope
4:16
Просмотров 46 тыс.
Usauver S09E09 - Safety Boots
20:30
Просмотров 35 тыс.
USAUVER S07E09   NDIKUFULUMIRA
16:13
Просмотров 66 тыс.
USAUVER S07E05   MTENDE WA MUNTI
11:32
Просмотров 51 тыс.
Usauver S04E10A - Pa Zalewa 11
14:29
Просмотров 65 тыс.