Тёмный

A ZIKHALE NG'OMA UKU NDIYE KWATENTHA🙌🙌🙌 TAMVANI MFUNDO ZOMWE ABWELA NAZO 

HOT 265
Подписаться 71 тыс.
Просмотров 39 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

10 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 540   
@UseniMailosi
@UseniMailosi 24 дня назад
Malawi chikangawa party
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o 23 дня назад
😂😂😂
@Allan-bk1
@Allan-bk1 23 дня назад
😂😂😂😂😂
@ackimchindimba9912
@ackimchindimba9912 24 дня назад
Mudyeleni apapa ndalama ziyamba kuphweka bas ndi kampeniyi tiyeni tiwadyele koma tonse ndikudziwa kuti ndife APM
@corretabanda7685
@corretabanda7685 23 дня назад
Nyama za mmanyumba mwanu. God is good and his eyes can see even in the heart of everyone. It will not work in the Name of Jesus
@user-wq3dh1ly2o
@user-wq3dh1ly2o 22 дня назад
Olo patavuta bwanji simungalamulileso dziko la malawi chifukwa munataya chipangano ambuye sangalole kuti mutilamulile anthu akupha inu
@anniedennis7127
@anniedennis7127 24 дня назад
Ng'ona zodya anthu zingalamulire anthu
@JumaGadaff
@JumaGadaff 16 дней назад
Bwana kuvota tidzavota koma dziwani kuti muli ndi mulandu ku chikangawa zikomo mulungu ankhale Nanu amen 🙏🙏🙏🙏
@spargomw
@spargomw 23 дня назад
Zikhale Ng'oma😂😂😂😂 tsitsi muzipesako tisamakugemuleni zonse😂😂
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke 23 дня назад
😂😂😂😂😂
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 23 дня назад
Kukhwima afiti
@nadiahPhiri
@nadiahPhiri 23 дня назад
Umfiti sizinthu
@user-wu4tl2yn9e
@user-wu4tl2yn9e 24 дня назад
Before kuvota aliyense azizakumbuka kuchikangawa
@CatherineDesire
@CatherineDesire 24 дня назад
Eish ndipo 😭😭😭
@MeleckDennis-vg3bv
@MeleckDennis-vg3bv 24 дня назад
Zopusa zokhazokha mfiti za anthu,kwanu kwathapo agalu inu
@BrunoMbewe-xj1yy
@BrunoMbewe-xj1yy 21 день назад
Ndangothokoza kuti mene mumampephelamo mu Mpephero lanu nonse simuna mutchulemo Yesu khristu.Zaoneka kuti inuyo mwazi wayesu simunauziwe mene munagwilira ntchito, pitilizani kugwira ntchito zakumidimazo.
@Sammy-vb1ed
@Sammy-vb1ed 23 дня назад
Mudzina la yesu krist ndikupemphera kut uone zowawawa zikhale
@Gmtmphats124gy
@Gmtmphats124gy 23 дня назад
Akanakhala kuti mulungu amalanga mpompo mpompo akanakuthilan moto pasokhano wanu omweo
@ChristopherKawilam
@ChristopherKawilam 23 дня назад
Ngat boza bro
@giftmaliwa2385
@giftmaliwa2385 24 дня назад
Za make Dzana this new generation
@user-eg8wx8oi5z
@user-eg8wx8oi5z 23 дня назад
Now it makes sense kod nkhumbai Nd mtumbuka eti😂😂
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 23 дня назад
Dzigawenga dzawanthu anthu akupha inuuu ng'ona zomwe mwachita pakupha abale athu asanu ndi anayi aja kuchikangawa dziko lonse lapansi ladziwa choonadi chifukwa ma German aja anenana zonse kuti black box inali ku palace.Ndipo anenaso kuti ndichiwembu chomwe munakonza.Pomwe inu muli pheee kufuna kutiuza bodza, ife tadziwa kale ndipo muyaluka
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 23 дня назад
Mukumbukeni chilima amene munamupha uja azikhale ng.oma ndipo zimu wake ukufinyeni ndipo khalira pomwe
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 24 дня назад
ana asatana awa Mzimu wa chilima ukuvutitsani
@lawrencekauwa8005
@lawrencekauwa8005 22 дня назад
Kkkkkkk,,,, to be a supporter 🙌
@ephraimmbiza9727
@ephraimmbiza9727 21 день назад
Most important thing is that you know yourself that you will not come back in government
@RobertChisenga-ci2mq
@RobertChisenga-ci2mq 23 дня назад
Do you think karonga's ndizitsilu? Poti kukaronga kuliso mbudzi ndizomwe zilikumenekozo
@LindaNkwazi
@LindaNkwazi 20 дней назад
U r still remembering chikangawa
@georgemponda
@georgemponda 24 дня назад
Mbuli izi😂😂😂😂 Zikhalebg'oma nde panja penipeni
@user-sh1rj3ol3t
@user-sh1rj3ol3t 24 дня назад
But tu Laz has failed Malawians way more than APM
@ustintembo
@ustintembo 24 дня назад
Ndipo inu mmm..
@peterjoshua2595
@peterjoshua2595 21 день назад
100% sure
@millionsenenje5010
@millionsenenje5010 23 дня назад
Mr Kamuyambeni ndiinu bambo wanga koma pena pake mhhhhhhh
@juntoiman
@juntoiman 23 дня назад
Pathako panu nonse Zikhale Ng'oma pantumbo pako wamva
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 23 дня назад
Uyu sikhale ngoma same like idi ameen
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 24 дня назад
😂😂😂😂 tango mdyelani ndalamazo azakhumudwa ameneyo
@FrancoKaunga-rq2ki
@FrancoKaunga-rq2ki 23 дня назад
Zikhale ngoma nkhope ngati kazizi mfwiti zawanthu! Kwacha kwacha 😂zakale kale. Kasi nkhumeta uli uko zikhale ngoma?
@FrankHaruni
@FrankHaruni 23 дня назад
😂😂😂😂 awande manyiwo😅😅😅😅
@HassanMbalaka-gb5sv
@HassanMbalaka-gb5sv 23 дня назад
Palinyimbo inayake amat paulendooo paulendooo aaaayeee paulendoooo. Awakwao kwantha
@BittonRashid
@BittonRashid 22 дня назад
Aye aye paulendo tulinkwaula tulinkwaula kkkkkkk mfundo
@EphraimNaveya-hz1du
@EphraimNaveya-hz1du 15 дней назад
Za ziiiiiii afiti simungazawine muli ndi magazi kale
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 23 дня назад
Mmmmm izo ndi ng'ona zikuruzikuru zikudyani
@alboxenzambabanda7230
@alboxenzambabanda7230 22 дня назад
Time to see chiterera
@ashikalam8616
@ashikalam8616 24 дня назад
😮 mbuzi za wanthu zonsezi
@MusaKazembe-b1d
@MusaKazembe-b1d 19 дней назад
They are not even ashamed 😮
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 22 дня назад
Dziko linaola...nduna yosapesa😅😅😅😅😅😅
@IssacMateyo
@IssacMateyo 24 дня назад
Amuna mutu wake ometa ngati chiboliwo Muthu osokonezayo zazi
@hopembendela
@hopembendela 23 дня назад
Kkkkkkkkkk manganya mukunva koma ati ndiwe mwana osapola panchombotu udziona
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 23 дня назад
Chikangawa party, okupha Inu muganiza asakudziwa ndani
@kinggasperagain
@kinggasperagain 23 дня назад
Kweni Malawi inasoka ivinthe kuwina waka nbwe chikurya waka ndalama
@PaulMwaona-kh1fj
@PaulMwaona-kh1fj 24 дня назад
Ubwino wake achinyamata alipo ambili kunjaku,apapa pachulukana makolo otamba
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 24 дня назад
Kusawa zoveselatu nanuso, agalu eni eni
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo 23 дня назад
Zikhale Ng'oma muti chani apaa tiyeni uko 😂😂😂
@KhondanKhondan
@KhondanKhondan 24 дня назад
Aaaaaa chisili chamuthu zikhl
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana 20 дней назад
Aaaa dzitsiru dza athu kunamizana kukhwapa kwanu nonse
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 23 дня назад
Mukuzinamiza agalu Inu za kumachende, azimai nonse Nyini zanu zamanu,mugawane nonse phwala limodzi limodzi agalu okupha
@user-yp5cj2xb9y
@user-yp5cj2xb9y 23 дня назад
😂😂😂😂 koma 😂😂
@SphiweMalata
@SphiweMalata 23 дня назад
😂😂😂eeeh koma tikuyenda otopa kale
@PreciousBandah-l2r
@PreciousBandah-l2r 18 дней назад
Makape inu
@Sammy-vb1ed
@Sammy-vb1ed 23 дня назад
Azikhaleo kwaona nkhopeyo ngati muru wamanyi afisi 😂😂😂😂😂😂.
@user-nu3zg6pr1l
@user-nu3zg6pr1l 23 дня назад
Koma please siku Lina Mulungu wanga nanu mudzayike comment please
@HopeMakoka
@HopeMakoka 23 дня назад
Akabwerstsa ndalamazo landirani guys Koma zodzalamuliranso awa mmmmmm Kumwamba kudzatsika pansi
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v 23 дня назад
Kodi khope zimenezo zikuyakhula apazi pamodzi ndi zikhale ng,oma zamasana kapena zautsiku mmmmm anthu andalama olo kuwezuka
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 23 дня назад
Ndi zausiku mumuone or zikhameyo khope yace ngati chidzukwa
@user-mq2or1lz8h
@user-mq2or1lz8h 23 дня назад
Fundo yogwira mtima njakuti kuti ukhale mtsogoleli pakufunika ukhale nduna ,kupanda izizi ndiyekuti palibe chanzeru so funso nkumati? Tate wanu kuti akhale mtsogoleli anali ndani???😅😅😅😅
@innocentmakande5535
@innocentmakande5535 24 дня назад
Palibe popangira vn Kodi,? Ndimafuna nditukwana live
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov 23 дня назад
Viskulu vinu kwacha ninkhuni mpakana kupemphela pamusonkhano apo naumo wanthu wakutambulila namwe kuzomelezganga kwacha chitima chikukolana kweni in fact Mose imwe mukukondwa na mcp Mavi yinu
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 23 дня назад
My pipo tiyenda bwanji 😢 koma able
@BashiruIbrahima-h6z
@BashiruIbrahima-h6z 23 дня назад
Kodi awa udindo wawo uja akuwuona kuchepa?? I'm feel sorry kwa manganya
@henryphiri6100
@henryphiri6100 23 дня назад
Manganya ndi mbuzi.amuthanso ngati saulos.nzeru za ma Rwanda amenewa nzoipa
@ChilangoNdalama
@ChilangoNdalama 23 дня назад
Suiona vote yanga Chaka chamawa ndangokudyera aise
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 23 дня назад
Adyeren vote ndimumtima bas
@StanleyChirwa-d6b
@StanleyChirwa-d6b 23 дня назад
😂😂😂 koma ndaseka kwacha kapena kwada
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 23 дня назад
Manganya waziwonera wekha kuti iweyo komanso utm sakufunani uziganizile
@BeliLikhola
@BeliLikhola 18 дней назад
muuzeni chilungamo ameneyo, chigawenga ameneyo
@user-mq2or1lz8h
@user-mq2or1lz8h 23 дня назад
😢😢😢😢oooh he has confirmed that this is serious business 😢😢😢rip SKS
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 24 дня назад
Kuika jingo apa mungaluphe akt ai chifukwa njala 😂😂😂
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 23 дня назад
Chikangawa party mbuzi hiziiiii
@amosnyongo6565
@amosnyongo6565 23 дня назад
Pemphero lanu silingafike kumwamba afiti inu
@PartsonMdeza
@PartsonMdeza 22 дня назад
Mmm kmaaa 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@CannyMpehla-d1s
@CannyMpehla-d1s 23 дня назад
koma malawi waoladi ng'omaso ikhale vp kkkkkkkk
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 23 дня назад
Kkkkk boma simuliona 2025
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy 24 дня назад
Zikuchita kuonekeratu poyera kut izi ndi manyaka masewera enieni anthu akulu zimimba nzeru zimapita kutiko kod
@LawrenceNoson
@LawrenceNoson 23 дня назад
Masewela chani😅😅😅
@CatherineDesire
@CatherineDesire 24 дня назад
Bolansoni papa kwacha wakeyo or najere or Uja mbusa uja wa 6 milion wa 😇 uja 🤣🤣🤣🤣sidzinakukhareni simdzakharapo kamuzu mbuzi inu
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 23 дня назад
Mayo mayo chitumbuka sitikunva yankhurani chichewa
@ChimwemweJuwao
@ChimwemweJuwao 18 дней назад
Haha koma ndiye mukungooneka Mano okhatu kuli kuda Kwa athu kumeneko ndye kwati mukufuna u vice Muthu ukafuna kufa umankhotha makutu kaye
@IshumaliMakajunior
@IshumaliMakajunior 23 дня назад
Ndipo lnu mukanadziwa mene tikuvera
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk 24 дня назад
Chikangawa forest
@rexphiri7242
@rexphiri7242 23 дня назад
Makape okha okha 😢
@BrightNyoni-yd4ip
@BrightNyoni-yd4ip 22 дня назад
Gulu iwe usamaseweletsa dzina la yesu nkhumba iwe
@jamesgama5489
@jamesgama5489 23 дня назад
Kwachaaa! Wachani mulibe manyazi eti!!.
@AchinaKellz
@AchinaKellz 21 день назад
Koma achina joza 😂😂
@MisheckAselo
@MisheckAselo 23 дня назад
Ndimamva chisoni ndi anthu apanda nzeru ndikumanamiza anthu, mwaba zakwana azikhale ng'oma 😮
@ANDREWMATITI
@ANDREWMATITI 23 дня назад
Angodyelatu ndalama ameneyo nthawi yamuthela
@rabisonpias5131
@rabisonpias5131 24 дня назад
“Akuti kumabwera ndalama “ ndalama za misonkho yanu zomwe zija ndi zimenezo. M’malao momagura mankhwala mzipatalaa , akungotafuna ndi Ma families awo
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 23 дня назад
Mukamawanamiza anthuwo mumayesa kuti ndi Ana iwowo maso alibe samaganiza ndi alendo mumalawi muno amalawi anasukusula akakupasani mphatso landilani bvoti ili mumtima
@MarriamBakalie
@MarriamBakalie 23 дня назад
Manganya beware upita ngati chilima those r the same people who killed chilima with the same position they r nt happy with u take care
@mchotseniliwonde4182
@mchotseniliwonde4182 21 день назад
Nyama zillkulu zikulu 😂
@PatreckHija
@PatreckHija 24 дня назад
Iwe buzi kwabasi angakuvotele ndani iwe 😂😂😂😂
@alfrededwinmadziataika5869
@alfrededwinmadziataika5869 23 дня назад
Sapesa Adana ndimadzi..😮😮😮😮😮
@ChrissySalimu
@ChrissySalimu 23 дня назад
Wooooooooooooooooooooo
@zondanitzulumusicfly.5202
@zondanitzulumusicfly.5202 23 дня назад
Adziwa kuti babiloni is falling.
@KennedyKanyama-ce8lb
@KennedyKanyama-ce8lb 23 дня назад
Mukutaya nthawi yanu dziko mwalitora eti kkkkkkkkkk
@BlessingsNyirenda-ru7ss
@BlessingsNyirenda-ru7ss 24 дня назад
Anthu awiri zaziii
@alexgweje8610
@alexgweje8610 23 дня назад
Mulibe manyanzi anthu okupha inu 😢
@Felista-m4q
@Felista-m4q 23 дня назад
Simuyiwonanso vot yamalawi😊
@Zamwano
@Zamwano 23 дня назад
Ma suit ake amenewo chingawine ichoo 😅
@user-mq2or1lz8h
@user-mq2or1lz8h 23 дня назад
😢😢😢😢 mpakana kumutchula mulungu nyasi ngati?😢😢😢😢😢😢
@pacharokoloviko1694
@pacharokoloviko1694 21 день назад
Mayankhulidwe ake amenewa anthu aphanako uku
@CharlesMongola-jw7sk
@CharlesMongola-jw7sk 22 дня назад
Pepani mfundo zanu zopusazo musaphenso Manganya,afiti inu
@LekkttarKhembo-or1tx
@LekkttarKhembo-or1tx 20 дней назад
Zitsiru za Malawi zikhale chakwera nonse ndinu osadura ndipo mumanukha kabudula mwanumo mukutinyasa tu
@lame8
@lame8 24 дня назад
Alandila ma 20 pin zikuchita kuonesa. Kuwatengela anthu ku Hotel kobisika angolowobela manja chifukwa cha ndalama😢
@MaxwellMulula-hj3rd
@MaxwellMulula-hj3rd 23 дня назад
😂😂🤣onse kuseka maso kupatula camera mn😅
@TeciaKumpitah
@TeciaKumpitah 23 дня назад
Mnsonkhano osakapangira pa ground bwanji mukuopa chani? Afiti mukacita kuda ngt thako, majekete onyasawo mbuziiiii
@EviChio
@EviChio 23 дня назад
Mungodzinyenga ndichala bas
Далее
Викторина от ПАПЫ 🆘 | WICSUR #shorts
00:56
Викторина от ПАПЫ 🆘 | WICSUR #shorts
00:56