Тёмный

Anthu anamusika Waxy K, zifukwa 5 zimene zinapangitsa, 

Sam Malvitha
Подписаться 79 тыс.
Просмотров 81 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

16 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 130   
@paulmkhumba1517
@paulmkhumba1517 Год назад
Mwanayi kudzimvamo ndikulimbana ndi gwamba ndipamene ndinamusika mwalasa
@GradysbandaGradysbanda
@GradysbandaGradysbanda Год назад
Wamuunikira bwino ngati wali wakumva akungoyenela kumvetsetsa bas
@cadohjabu5565
@cadohjabu5565 Год назад
bodza Munthu wina sangatsitse talent ya wina Sound ndi game imatembenukq
@mercy8426
@mercy8426 11 дней назад
Iwe waxy sanathe anayimba nyimbo ndi Mazombwe kids ahhh koma iwe hedex zakambi basi
@StuartGundas
@StuartGundas 2 месяца назад
aaaaaa sanathe dekhan mudzamuona kukangana nd momwe ulili moyo brasa
@evansjailos504
@evansjailos504 10 месяцев назад
komano kwa mwanayu sadzatha, choti mudziwe ndichakuti ukatchuka pa moyo wako pamapezeka zithu ziwili (1) moyo kuchoka (2) kukhara ndi moyo. ndeno anthu ena omwe amamuda' amamuda pa zifukwa zawo, komano kwa ine ndi akubanja kwanthu timamukonda kwambili mphaka relo komaso mphakana adzafe.
@MosesMbeya
@MosesMbeya 5 месяцев назад
Wakufa lelo sakufa mawa sikut adatha ayi mwan uyu alipo kom iye
@PreciousStephano
@PreciousStephano 8 месяцев назад
Young King Waxy Kay ndi katundu omanga ndimawaya ndipo sazatha
@TomHardy-b4x
@TomHardy-b4x Год назад
Mmmmmmmm. Zaboza zimenezo sanathe wangopuma kaye kuimba
@user-ev5yf6pc7c
@user-ev5yf6pc7c Год назад
Sanathe ayi waxy azakhalabe waxy basi msanje Malawi anabadwa opanda Kathu NDE Ngati amayimba NDI daliso WA mulungu basi komaso azakhala akuimba kod inuyo bro mulindi mbiliyanji mumangonenatu zaena Zanu bwanji
@user-ri8dw1ob7d
@user-ri8dw1ob7d 3 месяца назад
Ameneyi asiye basi osanyengerere aaah sahh
@shakirahissah5381
@shakirahissah5381 Год назад
Mowa Chamba ndikuzimva
@YamikaniMasauli
@YamikaniMasauli Год назад
Nyimbo zake zinabwela pakamoz nde kunali kovuta anthu kusunga mmaganizo
@mimhossan8886
@mimhossan8886 Год назад
Kodi kumeneku kukhomelera misomali kuti anthu amene amamukonda Waxy asmukonde, aziti iyeyo anatha. Koma anthu sitifunilanadi zabwino
@MavutoTheu-fj4yw
@MavutoTheu-fj4yw Год назад
Inuyo zot waxy kay anatha simziwa 😂
@KarenBregger
@KarenBregger 8 дней назад
Koma Malawi Zanu atsapite phasokolo basic wata a lipo akhanzatha adzata munzaona mwava chisilu iwe
@KarenBregger
@KarenBregger 8 дней назад
is twoo much saje
@MichaelMedi
@MichaelMedi Год назад
Zili bho
@laurankhana9833
@laurankhana9833 Год назад
Kukhomelerana amalawi sangapite pa tsogolo ana ambiri woyimbawa amabwelera tingoti kalipo kalipo alipo ena amabweza azawo sangapite chitsogolo aaaaa
@noahtsamdoka1172
@noahtsamdoka1172 Год назад
amwene sindikugwilizana Nanu or kutsutsana Nanu but watch the comments find votes yourself ndipamene udziwile Atha or ayi 🤣🤣🤣
@esaunyirenda3428
@esaunyirenda3428 Год назад
akulimbana ndi goat
@juliusmataya4685
@juliusmataya4685 Год назад
Ndimaona ngati sumayimira mbali koma ayi mbola, insubsbribe done.
@sammalvitha
@sammalvitha Год назад
104 subscribed while watching this video 3 unsubscribed while watching this video Ma negative comments ambili than ma positive comments I just wanted to share..
@GiftChadika-he7nd
@GiftChadika-he7nd Год назад
Iweyo ukulankhulawe ndwe mbuli yamunthu ...tamusiyen mwana mulungu anamupasa mphaso iweyo ndwe chisilu mbulu yamunthu gwamba wake uti mfiti ija ndpo usalankhure nkhan ya martse usatikumbuse mabala amartse galu iwe ngati ukusowa nkhani khara chisilu wamva
@user-ev5yf6pc7c
@user-ev5yf6pc7c Год назад
Amadya kwawo sanabwerepo kuzakupempha Kuti upase ndalama ayi ineyo waxy sindimaziwa ai and sindikokonda nyimbo ai Koma bro mwandinyatsa heavy start today to read your life and you will see it will help you not busy talking about someone else's no
@edwardyusufu9697
@edwardyusufu9697 Год назад
Mmmmm man mwachedwa kufufuza zakutha kwa waxy K pano akuzitolela kuposa Goat wanu
@patricklikwepa7707
@patricklikwepa7707 Год назад
Sam sunafike polakhula chonchi peleka ulemu kwa ma artist athu Chonde usapangenxo kwawina
@ibratime
@ibratime Год назад
Amwene muyaluka ndi zaziii waxy sanathe ameneyo ndidolo
@thomdickson5437
@thomdickson5437 Год назад
Zoti waxy anatha mukudziwa ndinu. No one is hot 4ver
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 Год назад
Watumidwa ndi nkhono uyu
@AsemahleFutshane-id9wh
@AsemahleFutshane-id9wh Год назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@BizweckMbwindinga
@BizweckMbwindinga Год назад
Akulu kenako ndisiya kukupangani follow chifukwa mulibe zelu
@AlufishaLenard
@AlufishaLenard 5 месяцев назад
Mnwa ndiopusa
@jafalimustafa3822
@jafalimustafa3822 Год назад
waxy ndikaswiri osamatimizapoo apaa
@sibubrightcmasulanphiri3652
Utale boy on the top😅😅😅😅
@michealpostan
@michealpostan Год назад
Waxy anatha athu ena alowemo iya
@GiftChadika-he7nd
@GiftChadika-he7nd Год назад
Waxy mwana wanzelu ndpo amaimba bwno kwambiri ukulankhura nkhan ya gwamba zoonjezera za ufiti bas kagwere uko amalawi njiru musiyen mwana
@COLLINGSSAMSON
@COLLINGSSAMSON Год назад
Bro mukunama inu. Ine mfana uyu ndimamfila hvy . Ndipo amaimba bhoo hvy. Ma artist ambili pano akumatha km mfanayi sazatha bro
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 Год назад
Muuze broo
@GradysbandaGradysbanda
@GradysbandaGradysbanda Год назад
Umakwa
@PreciousSacheuka-fs3iz
@PreciousSacheuka-fs3iz Год назад
Umalengeza zopusa iwe waxy alipobe kungoti alibe moyo wotengeka ndi zadzikozi ngati kale lija
@FrankNkhoma-mz3nb
@FrankNkhoma-mz3nb 5 месяцев назад
Nice
@jamesgift4001
@jamesgift4001 Год назад
😂😂🤣mwangosowa nkhani chabe
@shupikayintuwaluwa-5899
@shupikayintuwaluwa-5899 Год назад
Thus true, I think the best suggestion z wat u hv jst said
@PromiseBrazio-ud7fd
@PromiseBrazio-ud7fd Год назад
Ok
@KhoRomeoBanda
@KhoRomeoBanda Год назад
🎉
@IdrissahChuma
@IdrissahChuma Год назад
Iwe ndiwaboza ase
@Ahyamiechiwanda
@Ahyamiechiwanda Год назад
😂😂😂😂😂😂😂
@jamesjealous-p4v
@jamesjealous-p4v 8 месяцев назад
Kwa inu anatha ife tikanamufila ❤❤❤
@MosesMbeya
@MosesMbeya 5 месяцев назад
Zowona tiyipatsa mo🎤🎤
@AmizohBeya
@AmizohBeya Год назад
Uncle inuyo ndaboza kwambili,,,,waxy kay akumvekabe
@Ishumailimbwana-fs6fu
@Ishumailimbwana-fs6fu Год назад
Wikise ndimwana kwa waxy kay waxy ndifumu
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 Год назад
Iweyo poyamba pamachende akowooo aseee.. Kodi mumawona ngati gwamba wanuyi ndi mulungu.. Iwe uzitha kusyanisa pakati pakuths kuyimba ndi kulemera. Ndee wins akamafuna kukusochelesa uzingoti eya bwana ksphe mayi akoo eya bwana kuopa kusikidwa ndimafans.. Mapwalako iwee
@sammalvitha
@sammalvitha Год назад
Nde wapindula Chan?
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 Год назад
Iweyo panga lako dzina utchuke naweso siya kunyoza amzako mboli yako
@user-vf6ip1xs8i
@user-vf6ip1xs8i 7 месяцев назад
Timakonda mwana mzathu waxy k osat afiti mukunenawo
@umalibakali9033
@umalibakali9033 Год назад
👍👍👍👍👍
@MavutoTheu-fj4yw
@MavutoTheu-fj4yw Год назад
Mnthu ngat anatha nd zovuta kut azukeso mwamphavu chifukwa zimakhala kut anthu ambili alibe chidwi pa iye kutchuka zimagwilizana nd kut anthu ali nd chidwi bwanj pa iwe
@EmmanuelPotani-b1g
@EmmanuelPotani-b1g Год назад
Omwa tea azamwanso waxy sangathe momwe mukuganizilamo😊
@shamsiyyahonline1234
@shamsiyyahonline1234 Год назад
ukungofuna kutchukira pa mwanayi
@OmarBwaila
@OmarBwaila 7 месяцев назад
Mwanayi ndi doro😂
@user-sf7yb4el9i
@user-sf7yb4el9i Год назад
Ndipo zoona
@ganizanichisale1449
@ganizanichisale1449 Год назад
Kkkk
@SHARIFAUSTINSAINET
@SHARIFAUSTINSAINET Год назад
Online
@EmmanuelKatadzukacomedy
@EmmanuelKatadzukacomedy 2 месяца назад
Kunthako kkk
@HadijaAnafi
@HadijaAnafi Год назад
Ukunama big fumukazi😝✌️
@andreabrighten301
@andreabrighten301 Год назад
Mabodza big waxy akuvekabe
@FrankNdeleman-tk9tv
@FrankNdeleman-tk9tv Год назад
Ndiwe wabodza chitsiru
@emmiewaselinah219
@emmiewaselinah219 Год назад
Ulindi mabonyo iwe aaaa waxy ndi dolo
@matthew534
@matthew534 Год назад
Mpangeso story ya gwamba zikomo mmatiziwisa zambiri
@user-sg8ii8fd9c
@user-sg8ii8fd9c 6 месяцев назад
Kkkkkkkk
@user-lo9nu8pq6g
@user-lo9nu8pq6g Год назад
Jealous
@Pungwe123
@Pungwe123 Год назад
Unatha ndiiweyo....uyu sanathe ma haters❌❌❌❌
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 Год назад
Ngwaphwisi uyuu
@peterpaulkatambika4216
@peterpaulkatambika4216 Год назад
eee nzovutatu izi🥱
@EstherDebwe
@EstherDebwe 5 месяцев назад
Ndipo zovutaditu
@LoydKapalamula-ig4un
@LoydKapalamula-ig4un Год назад
Zoonzake zimenezo
@HawaAl-j7m
@HawaAl-j7m Год назад
Linalo ndi sanje😂😂😂
@IdrissahChuma
@IdrissahChuma Год назад
Iweyo ndiwadyela waboza
@HlupekireBanda
@HlupekireBanda Год назад
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉l ko
@IBRAMakalani-zk7wk
@IBRAMakalani-zk7wk 11 месяцев назад
Mungomupangila mwanayo jalasi bc
@essaudollo6394
@essaudollo6394 Год назад
Iwe ndi baka wava
@bartonnjolwa
@bartonnjolwa Год назад
😂kuthoko
@sammalvitha
@sammalvitha Год назад
Mukuganiza kwambili t 😅🤣
@KhimzyMike13
@KhimzyMike13 Год назад
Yaeh izi nde zazi unsubscribe today
@hendsonmaganizoofficial1758
Unsubscribe in peace 🙏🏻ife taphunzirapo kanthu
@ririvilla1423
@ririvilla1423 Год назад
Inenso ndapanga unsubscribe
@franquenassone9993
@franquenassone9993 Год назад
Kusowa nchitotu uku magobo akusowaet
@RaphaelChipime-sb7ol
@RaphaelChipime-sb7ol Год назад
Mulibe mzerutu madolo
@laddinshaibu6932
@laddinshaibu6932 Год назад
You forget something mowa to munch
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 Год назад
And ganja too much
@futuremoyo5714
@futuremoyo5714 Год назад
Mowa Chamba mwana wang'ono that's fuck
@FatimaSaidi-mz8fi
@FatimaSaidi-mz8fi Год назад
Akutumatu iweee osamapanga zako bwanjiiii😂😂😂
@dalitsoulnchengah9538
@dalitsoulnchengah9538 Год назад
Iwe mbole yako wamva
@sammalvitha
@sammalvitha Год назад
Mukukwiya mmalo mwa enat
@SusanCamlon
@SusanCamlon Год назад
Asamajombenso ku sataniki zonsezo ndi chabe
@evasonleston5457
@evasonleston5457 Год назад
kkkk km yah mwatero
@patricknzima3053
@patricknzima3053 Год назад
kikikiki kikikiki
@billybanda2808
@billybanda2808 Год назад
Za dziko Lapansi zonse mzachabe
@daudigodfrey1369
@daudigodfrey1369 Год назад
Time basi chilichose ndithawi
@VeronicashalomPhiri
@VeronicashalomPhiri Год назад
Sanatheretu akuzitolera Kaye😎😅
@IdrissahChuma
@IdrissahChuma Год назад
Iweyo siumaziwa umangolongolola bas
@user-ce6wv7ss3y
@user-ce6wv7ss3y Год назад
Kkkkkkkk😂😂😂 mukunama man waxy Kay ndi machine oplasa
@harryjaymw
@harryjaymw Год назад
Muli kachilungamo 😂😂
@IdrissahChuma
@IdrissahChuma Год назад
Kod iwe unaimbapo ???
@thirdgenerationmovies710
@thirdgenerationmovies710 Год назад
Who sent you
@siwedmataya7429
@siwedmataya7429 Год назад
Inu hip hop sikumapngudwa follow ngt kale ase aaaaaa tiuzen amene akupangidwa follow kwambiri artist wa hip hop aaaaaa mwapala
@SamsonNyadani-qc8be
@SamsonNyadani-qc8be Год назад
Iyi nde wapala nao ufuna kuti tikusike kapena. Wayambano kutumidwa eeti! Mkona udamchemerera namadingo kuti atakhala presdent basi ndakusiya wayamba kulandira banzi ndi anthu
@IbbrahTabu
@IbbrahTabu Год назад
waxy kay ndidolo
@HarryKabula-ml4lh
@HarryKabula-ml4lh Год назад
Wandibowa tu apa ase timakutsatilani koma apa pokha mwanama sanje eti
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 Год назад
Sanathe
@NoahKalima
@NoahKalima Год назад
Anthutu akukususani
@emmanuelyamikani1959
@emmanuelyamikani1959 Год назад
Kutaya nthawi nkumalimbana nd mwana 😂😂😂😂😂 dolo nd dolo
@ethelMaduka
@ethelMaduka Год назад
Inenso aka nakatuluka nkobhowa🚮
@charleskalajira380
@charleskalajira380 Год назад
Mukunama man sanathe...
@FatimaSaidi-mz8fi
@FatimaSaidi-mz8fi Год назад
Asamu mukayambuleso 1 musalimbane ndi mwanayuuuu
@mbawabuliyan9704
@mbawabuliyan9704 Год назад
Adatha chani
@BrightNtau-hu6br
@BrightNtau-hu6br Год назад
Ase ingotseka Chanel chakochi wava zaboza ife ai nthangala zakoso
@FrankNdeleman-tk9tv
@FrankNdeleman-tk9tv Год назад
Uyudi nthangala zake
@EllenMkweza
@EllenMkweza Год назад
Koma nde mumakhala ndi nthawitu ine nde ndimmamkondabe waxy k
@sammalvitha
@sammalvitha Год назад
Mai anga amamukondabe mbenjere ndi chibade
@CHRISTOPHERCHAMA-dp7qo
@CHRISTOPHERCHAMA-dp7qo Год назад
You just hate him
@ririvilla1423
@ririvilla1423 Год назад
You are a hater yourself I still like waxy ndipo sanathe
@johnlonelyjere5300
@johnlonelyjere5300 Год назад
Ndinu opepera bro stick to your business
Далее
Mbili komanso chiyambi cha Driemo
10:28
Просмотров 116 тыс.
BON KALINDO LERO PA 17 SEPTEMBER 2024 |
18:22
Просмотров 2,5 тыс.
CHUMA CHOLANDA - Episode 147
10:08
Просмотров 143 тыс.
Oimba omwe ananyozapo Bushiri
13:06
Просмотров 493 тыс.
Kucheza ndi wa Sataniki Mpakana Waziwulula Yekha
20:20
Просмотров 158 тыс.
Oimba omwe anamwalila  ali nkat mojambula nyimbo,
23:52
Просмотров 148 тыс.