Тёмный
No video :(

APHANA OKHAOKHA A MCP 

TIDZIWE TV
Подписаться 8 тыс.
Просмотров 7 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

26 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 40   
@PraiseBoyce
@PraiseBoyce 7 месяцев назад
Mmmmm koma Chaka chino anthu mumphana ndinthu koma Ubwino wake simukubwerelaso mu boma kwanu kwatha basi
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 7 месяцев назад
Kkkkkkk
@KondwaniMadeya
@KondwaniMadeya 7 месяцев назад
Ubwino wake ndi nokhanokha ng'ona za mmabango muthana ,anthu oipa inu
@Pangolinimw
@Pangolinimw 7 месяцев назад
😂😂😂😂 nepman ananena kut is ng'ona sa mmabango 😂😂😂
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 7 месяцев назад
Tinaziwa ife chimwendo ameneyo mmmm akuyetsa azakhala chomcho mpakana litilo
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 3 месяца назад
Gyz muzinkhala serious pobweresa nkhan izi zitipindurila Chan akupanga nkhola mwawo ine ndimwana wa dad chipan chamangazi ichi
@HadjiMachado
@HadjiMachado Месяц назад
Nokhanokha oipa mwaonana akuonenso iwenso amen
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 7 месяцев назад
Mmmm chimwendo be careful sir yakho likubwela pasongolo
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 7 месяцев назад
Koma munthu uyu ndi woyipa kwambiri eesh💔💔kumuvulaza mzanu chomchi chipani chadzifwamba.
@user-nx9tj5ho2c
@user-nx9tj5ho2c 7 месяцев назад
Devil's on each other's neck 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@andiwochishadreck3753
@andiwochishadreck3753 7 месяцев назад
Ndiye ife titani??????
@gracechiumia7103
@gracechiumia7103 7 месяцев назад
Tiyeni nazo mumphana kumeneko mcp sichipani
@user-zw8ns7bk7s
@user-zw8ns7bk7s 7 месяцев назад
Koma amalawi ndife anthu omvesa chisoni kwambili nsalu zachani anthu kumapitadi kumakalandila nsalu aaaa
@user-vd6gu7tv5u
@user-vd6gu7tv5u 7 месяцев назад
Ine ndikuwona ngati akumenya ndi a Dpp ukulakwisa iwee, pajatu ya mkhaza ndi dpp😂😂😂😂😂
@BladesBullets-pu5uw
@BladesBullets-pu5uw 7 месяцев назад
Ok pakuti ubwino wake mukunena mukuziseka nokha.
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 7 месяцев назад
Munasowatu brother,
@hopembendela
@hopembendela 7 месяцев назад
Dzikachuluka kudzenje mbewa dzimaphana kkkkk nafwa ine
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d 7 месяцев назад
Phanani basi a MCP 😂😂😂😂
@alicehananiya
@alicehananiya 7 месяцев назад
Mu phanadi simunati apo mwangoyamba MCP chioani choipa kwambili chofuna mwadzi wa anthu
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko 13 дней назад
Nokhanokha ngati mukuphana chincho sikuchita kuoneseratu kuti ndinu achipani chokupha iwe chimwendo ukumenyeranji munthu osalakwa? Chimutu ngati !!! Kwinaku ndilakwisa
@ThokozaniMaulana-oi5hz
@ThokozaniMaulana-oi5hz 2 месяца назад
Ndie audio ija mukumati ndiyabidza nkhanza zake zimenezi
@juliusnjerengo2610
@juliusnjerengo2610 7 месяцев назад
Ati sibwino kuti okhaokha kumamenyana koma azimenya adani awo a opposition parties. no wonder a MCP akumapha anthu pazifukwa zozizira, Evil people.
@KimChisola-gm7yw
@KimChisola-gm7yw 7 месяцев назад
Ukungoyene kuzifunsa kuti chipani cha mcp ndi cha mtendere
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l 3 месяца назад
Choyipa ichi chisatana ichi
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 7 месяцев назад
Mmmm zosankhala bwino bro
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 7 месяцев назад
Nonsenu ndinu dzitsiru muku limbana Kuti muziba ndalama za Wanthu,pa nyini pa Manu nonse
@MaxwellMustafa-ec8fc
@MaxwellMustafa-ec8fc 7 месяцев назад
Koma muzayaluka mu 2025 now we are saying next year
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 7 месяцев назад
Akuponda pang'ono ukuyankhulawe muphana
@ConfusedAtv-bs4gc
@ConfusedAtv-bs4gc 7 месяцев назад
Phanani agalu inu mizimu yaanthu osauku ikukulangani simunati agalu inu mutulukako pompano kumeneko mukanatibela misonkho yathu simumatulusapo oudio pano chifukwa Kuti mwtibulifwa mwafuna Kuti aliyense adziwe agaluinu
@user-mc8gk4xv3f
@user-mc8gk4xv3f 7 месяцев назад
Adzayankha angakhale kumenya kokhako
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 7 месяцев назад
mwatsimikiza kuti chipani chanu chakuphano
@user-hl5ii9ns8b
@user-hl5ii9ns8b 7 месяцев назад
Enawa ndiopa basi
@kondwanimunthali7401
@kondwanimunthali7401 7 месяцев назад
Phananani nokha mmene mumaphera anthu
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 7 месяцев назад
Chimwendo Banda ndi chifwamba. Udzayankha.
@joicemartin-ji5zu
@joicemartin-ji5zu 7 месяцев назад
A m mcp okupha zifwamba zokhazokha kkkkkk
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 7 месяцев назад
Momwe mukudyera musatinyase
@user-pe7lo1fe9b
@user-pe7lo1fe9b 7 месяцев назад
Iweyo siumadziwa kuti mcp ndiyakupha
@joemlelemba6572
@joemlelemba6572 7 месяцев назад
Zobvuta anthu awa eish
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 7 месяцев назад
MCP, sichipani cholamulira boma koma kagulu kaupandu mdziko
@ChimwemweMagombobanda
@ChimwemweMagombobanda 7 месяцев назад
A chimwendo musayese zanu xilibwino ayi ukakwela muntengo usaipise pansi chifukwa udusila pomwepo ukamasika
Далее
Report La Chilima Labwela - Ntanyiwa Kufotokoza
31:53
ПАВЕЛ ДУРОВ АРЕСТОВАН
1:45:21
Просмотров 114 тыс.
I Took a LUNCHBAR OFF A Poster 🤯 #shorts
00:17
Просмотров 2,7 млн
12 August 2024
2:38
Просмотров 103
CHIBANGILI CHIKUPANGA ZODABWITSA KU BLANTYRE PART 1
13:53
BON KALINDO LERO PA 27 AUGUST 2024 |
17:02
Просмотров 11 тыс.
PAMENE MULUNGU AKHALA CHETE - Pastor TY Nyirenda
1:09:20
ПАВЕЛ ДУРОВ АРЕСТОВАН
1:45:21
Просмотров 114 тыс.