Тёмный

KU MPOTO KWACHITIKA ZINTHU ZOKHUDZA PRESIDENT NDIPO PHALOMBE BOYS IKUZUKUTA MOZAMA 

Malawi Trends TV
Подписаться 50 тыс.
Просмотров 46 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

29 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 111   
@Dalitsombewe-f9l
@Dalitsombewe-f9l 2 месяца назад
Pitiriza Phalombe boy.that's true and 100%
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 2 месяца назад
Kulibe asirikari ndi nduna yachitetezo ku malawi. I wish minister wa chitetezo adakamakhala msirikari
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 2 месяца назад
Thats true....the minister not fit all for such position with no security skills at all
@wistonkamatenda
@wistonkamatenda 2 месяца назад
Zill good ndi malae❤❤❤❤❤❤
@MonijaKataika
@MonijaKataika 2 месяца назад
💯 mwana mulomwe mwamulapulamotu...😭 Uyu atenge u VP now till 2025. APM my vote.
@CatherineDesire
@CatherineDesire 2 месяца назад
Kulibe chimene MC P ikudziwa koma kupha kokha basi100 percent perfect palibeso owapotsa
@MonicaBvumbwe
@MonicaBvumbwe 2 месяца назад
Asilikali akumalawi amafasa kwambiri kuiwala kt. TChito yawo ndikuteteza ndikuyang'anila ziko lino kma amangoyang'anila zithu zikuwonongeka😢
@CatherineDesire
@CatherineDesire 2 месяца назад
Sikufatsa Koma kumbwambwana komaso manthongo mu brain
@CatherineDesire
@CatherineDesire 2 месяца назад
😒😔anangokomokeranji anakangopitilatu ka anakaferatu👹👿😈akanakamuona Chilima
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 месяца назад
Ben longwe ochinda Mwana wake chimwendo Banda mphuno Ngati tomato
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂😂😂
@Itemsworld
@Itemsworld 2 месяца назад
May God help Malawi, tears of the sun over Malawi
@LinessPelete
@LinessPelete 2 месяца назад
Keep it up
@FrankKaufa
@FrankKaufa 2 месяца назад
Amen m'bale
@sthoramexjrsa902
@sthoramexjrsa902 2 месяца назад
Your big man 💪💪💪
@lyiemax
@lyiemax 2 месяца назад
Powerful speech
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 2 месяца назад
Ben longwe machende ake tikamudzimitsa ife meneyo siyeni ndalama alandiradzo akadyera kumanda ndipo 2025 ku wina or wosa wina basi sitizalora kuti atiramule ife
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 месяца назад
Good man❤ Zoona
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 2 месяца назад
Asilikali anthu saziwa ntchito yawo chomwe amadziwa ndi kulondera ku state house basi. Ma guard bolanso a G4 amadziwa chochita koma MDF panja peni peni.
@MussaNgoma-r2k
@MussaNgoma-r2k 2 месяца назад
He was not foreverdeath😊 will be there for ever
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 месяца назад
Koma zooona anthu ena ukalowa mmbalacks mpakana ukapha Anthu, aaaaa zooona asilikali mwatidabwitsadi . Asilikali alibe chipani koma apapa ndiye yai sipali bwino
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 2 месяца назад
Asirikari onse ndi a MCP
@LovenessMagombo-t3c
@LovenessMagombo-t3c 2 месяца назад
Zoopsatu, ngati achiwembu akulowa kuzida komweko mpaka kupha munthu, mmmmm
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 2 месяца назад
2025 saafika ? 😂😂😂😂 Poti okupha ndi lupanga amati adzafanso ndi lupanga
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 месяца назад
Mwayankhula bwino braz zaonjeza kwambiri.
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e 2 месяца назад
No matter what chakwela ngwakumpha anampha amiya wamphaso SKC pamozi ndi abaleathu 8
@marryphili5419
@marryphili5419 2 месяца назад
Aziwona achikangawa mizimu ya anthu 9 yiwasaka mupaka yiwakathe amenewo aziwona
@EdwardZuze-r7w
@EdwardZuze-r7w 2 месяца назад
Asilikali a MDF, sakulikonda dziko lawo, they are few solders amene ali ndi umunthu. A silikali, Ulemu wanu ndi mphamvu zanu zili kuti? musakomedwe ndi zosala kuleka kutetedza dziko la
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 месяца назад
Inu mukunena Joyce Banda hule Amina ake mumawaona bwanji anagona kale achimwene😢😢
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 месяца назад
Pitilizani kutiuza alomwe azathue
@ElizabethNkhonjera
@ElizabethNkhonjera 2 месяца назад
#Malawi Difence Force
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 2 месяца назад
Kma asilikali a Malawi anasaduka azilonda a chikangawa naga akuti chasika kapena chakwera aaaaaaaa ine guys ai
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 2 месяца назад
Kodi ife a malawi sitingathe kumupha chakwela yu, kodi ifeyo mene tilili mumalawi muno tikhulephela kumupha chilima yu, ine akundinyasatu chakwela koopysa , abale tiyeni tipange madhemo omupha chakwela asatizuze ife ayi , tatopa jonh longwe yo abwele tionetsane monga ine mwana wapa balaka longwe ndikufuna koopysa kwambili
@Dinalamakanjira
@Dinalamakanjira 2 месяца назад
Nzimu WA Achilima ndi Agadama
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 месяца назад
Musiyeni peter muthalika salimbana ndi chonde mudzatenga tsoka ndithu
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 2 месяца назад
Ulemu wanu big boy umata man
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
iwowo akusangarara kuti anthu akurowa mcp akukafunako ndarama zo zabooka 😂😂
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 2 месяца назад
Apite ameneyo basi sitikumufuna chikangawa iwe watitopetsa ndipo ndikuona kuchedwa pa 8 tinthane nazo ife zimenezi isa
@DevisonHala
@DevisonHala 2 месяца назад
Asilikali amalawi adalowa ndale osati kuteteza dziko chilima amaphedwa iwo amawonera zikuchitika bwanji?
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂 chakwera magazi kuribe kusi kwanyanja ukufunaso ena
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 2 месяца назад
Jyce banda simunthu ameneuja wakhala akupha anthu maulamulilo wako uja pano aliwone ndi ndakwela okupha okha okha
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
yavuta ndindarama asondawo akuyendera ndarama amenewo chisiru chopusa
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 месяца назад
Mulungu atichitile chifundo dziko la Malawi
@charlesmasauko4651
@charlesmasauko4651 2 месяца назад
Asilikali a Malawi ndi Ogona
@LindaNkwazi
@LindaNkwazi 2 месяца назад
Chikangawa muziona
@AshimayeGama
@AshimayeGama 2 месяца назад
Chilima dzofuna bodza osati mcp ayi chilima chilima ndamene anabweletsa mavuto kuno kumalawo kuno ifetikutu dpp moto 2025boma
@EmmanuelNtago
@EmmanuelNtago 2 месяца назад
Anachita kutitengerako yekha chilima ku MCP ndthu aaaa,,,popanda iye sitikanakhara pano tukamba za MCp konse mmm
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
zimastanic izizi zimangokharira magazi
@MphatsoPemba
@MphatsoPemba 2 месяца назад
Kwapula phalombe tsiku Lina tikanyele pakhomo pakwawo
@ritchardchakuma5725
@ritchardchakuma5725 2 месяца назад
Wabwino zose ifekwathu kwatha😭😭😭
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 месяца назад
Asilikani nawonso akudya nawo ndlama za boma akuwopa kuchita po kanthu
@HassanTmasuku
@HassanTmasuku 2 месяца назад
Asilikali opusa awa ntchito kumenya ma civilian asilikali analipo padzana achina chigawa ndi anzawo osati awa
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 2 месяца назад
Pwiyapwiya mumaitha auzeni
@AjibuTwalibu
@AjibuTwalibu 2 месяца назад
Mmm mpakana kukomoka
@IssaLazack-ij1gf
@IssaLazack-ij1gf 2 месяца назад
Koma chona chili mutima mwanumo mukuchiziwa chifukwa chimene mukwyila amenewa ndichani yiwenso ndiwe mfiti mumadya nyama yawanthu ndichikhangawa wanuyo wakhutha yee
@CatherineDesire
@CatherineDesire 2 месяца назад
David anagonjetsa Golliat
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 2 месяца назад
Bola akadafa tigawane chuma a malawi
@CharlesPhiri-ds1rk
@CharlesPhiri-ds1rk 2 месяца назад
Ndye ife tizinva kutukwanako? Ngat mulibe fundo musileni kalindo bwanji?
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
koma tigwirane m'manja ambuye atisogorere
@McfalenGola
@McfalenGola 2 месяца назад
AFA nayenso chikangawa
@wistonkamatenda
@wistonkamatenda 2 месяца назад
Ngoz ndi ngoz basss cilungam akudziwa ndi mulungu
@DevisonHala
@DevisonHala 2 месяца назад
Asilikali amalawi akuphana wokhawokha chifukwa akulandila ndalama kwachakwera
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 2 месяца назад
Nkhani ndiyoona ndalama zabooka ndichifukwa anthu akukhamukilako
@AlfredWalusa
@AlfredWalusa 2 месяца назад
Asilikali tilibe ku malawi
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 2 месяца назад
Ndizodabwitsa kwambiri kuti police ya Malawi, Army yaku Malawi, ati makhothi ndi mabungwe aja amati ndiomilira anthu aja onsewo angoti ziiii koma akulandira ndalama ndima allowance nthawi zonse, pamene anthu osalakwa omwe saadavotere Chakwera ndi anzake akuzunzika kwambiri, zomvetsa chisoni.
@AlexKamowa-u7m
@AlexKamowa-u7m 2 месяца назад
Kulankhula momveka bwino saowebas
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 месяца назад
Sstana joyce banda even bushiri is involved
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
mutu wataya
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 2 месяца назад
Koma aromwe simugona turo ndiboma koma mukunamatu chakwera satuluka pampando boma la peter laromwe lokhalokha kodi malubino aja munalikupha anali mcp agalu inu zaziii utiwuza chani galu iwe
@CatherineDesire
@CatherineDesire 2 месяца назад
Asilikali akomoka chifufu
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 2 месяца назад
Mbuzi yamunthu iwe saulos wamukonda kamba koti wamwalira ndiboza lako ukhaula udya ulomwe wako womwewo ukhaula ukuwonaso azipani zakozo akuthawaso akulowa mu mcp chifukwa chani ndiye 2025 uzafa ndi bp mulomwe wopanda khalidwe iwe azako aromwe panopa akuzindikira wanakomoka kutiko chakwera ndimaboza akowo mbuzi yamunthu iwe
@OdettaLowrence
@OdettaLowrence 2 месяца назад
Uli mbali iti iweo?
@OdettaLowrence
@OdettaLowrence 2 месяца назад
Usilikali pano walowa ndale , ndalama basi zisilu za asilikali za relo, ndipo ndie akundinyatsa bwino, Malo moti mademo akuchitikawa asilikali bwenzi Ali PA number one kma kuli zillll, Malo moti amuchose alamulire kwa salaku kma ayi, apa Nila manja mphechempheche zisilu
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 2 месяца назад
Apita musiyen
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 2 месяца назад
Vuto nd wamkulu wa asilikali anadya chibanzi that's why mulibe chitetedzo mu dziko lanthu
@mustaf-q4j
@mustaf-q4j 2 месяца назад
Asilikali apasidwa ndalama
@wistonkamatenda
@wistonkamatenda 2 месяца назад
Ukusokosa boma koma mcp
@GetrudDube
@GetrudDube 2 месяца назад
Palibe chinsinsi
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 месяца назад
No point
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂asilikari ake okonda sex
@hagayichiluwe
@hagayichiluwe 2 месяца назад
Kuteloko uganiza kuti alomwe mungalamule dziko chifukwa chambwelela zakozi? Zaziiiiii
@WorriedNdhlovu
@WorriedNdhlovu 2 месяца назад
Kukula konseko madala koma nzelu mukibe
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 месяца назад
Ndiye mwakula zinakukanikani kale . Ukubwera ndi iti madala
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 месяца назад
Chokukhalani ndi ufiti basi a mcp kupanda chilima mwaphayu mukadalamulira ndani .
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 месяца назад
Madala awa ndichocho amaikila kumbuyo MCP asiyeni ikubwela thawi oipa ose azatha phwiti
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 2 месяца назад
Chikangawa team
@IanAllstal
@IanAllstal 2 месяца назад
Mlomwe kuliratu momveka apa Kodi Mukumva bwanji bwana Aliyese akukulozani Zala inu nchifukwa chani muzifuse bwana sure Enaso anazuzulidwa mokwana mapeto ake anapita ganizani bwino
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 месяца назад
PALIBE FUNDO YONVEKA MUTSAWAVUTITSE ATHU KUNVA DZOPANDA MUTU,,, JOYCE BANDA ATANI,,ANAKUUDZA KUTI NDI ASATANIKI NDI NDANI NDEKUTI NAWETSO NDIWE WATSATANIKI.
@IssaLazack-ij1gf
@IssaLazack-ij1gf 2 месяца назад
Mpatumbo Pako Garu wamunthu osaumbaraooo
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 месяца назад
A MALAWI MBUZI ZOSE ZIKULONGOLOLA PA SOCIAL MEDIA NDI ZIMENE KU SUKULU SIZINAPITE,,,KHALAMBA YANU INAWONONGA ZIKO CHAKWELA ALI PA TCHITO CHACHIKULU KUKHOZA ZITHU ZIMENE KHALAMBA YANU INA ONONGA
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 2 месяца назад
Pakuti nawenso ndi m'mene walembera apapa zawonetsa kuti school mwa iweyonso mulibe,kulamulira si school Koma umunthu,a school ndi awa akungobawa
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 2 месяца назад
Chikangawa team 😂😂
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 месяца назад
IWE NDIWE MULOMWE CHICHEWA CHAKO SICHIKUNVEKA NGATI WATUMIDWA NDI PETER MUTHALIKA WAWUPONDA IFE SITIKUFUNA ALOMWE KUTI LAMULILA KAWILI IWALANI ZIMENEZO NGATI MUNAZOLOWELA KUDYA ZA MUCHIPANI MWAWUPONDA THAWI YAKWANA YOTI MUNYAMULE KHASU WAKUMUNDA MUZIKALIMA MADIMBA,,, PETER MUTHALIKA OLO AFUNE KAYA ASAFUNE MCP YILAMULILASO KAYA MUYAKHULE CHILIMA MUNGOONA KUTHA MAU ANU MCP NDI BOMMMMA KALE,,ALOMWE TENGANI MAKHASU PITANI KUMUNDA MUDZIKALIMA VUTO LANU SUKULU MUNAKANA NDENO TCHITO YOTI MUGWILE INUYO NDIYAKUMUNDA BASI.
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 месяца назад
KODI PETER MUTHALIKA SANAMANGILE MADEMO AKOMA PATI PETER MUTHALIKA,,NGATI MUDZA VOTA NDINU NOKHA MWAINA MUDZAYITCHOTSA MCP KOMA NGATI ADZAVOTA NDI A MALAWI SANGANVELE FUNDO ZOOLAZO,,,,KODI IWE PETER MUTHALIKA AKUPASANI NDALAMA ZINGATI????MUTHU ALI NDI ZAKA 85 YEARS MUKUFUNAKO CHANI KWA KHALAMBA NGATI YIMENEYO
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 2 месяца назад
iwe ukufuna ndani
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 месяца назад
Naweso ndwe chisilu ine si mulomwe ndne nchewa km mcp sitikuifuna ife ngat iweyo umadya nao ndalama ndalama boma lakupha ili manja mwao mwazaza magazi chipan chakupha kuba agalu amenewo
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 месяца назад
Zakuwawa basi zakuwawa ticosa cisoso kapena minga inalasa chilima
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 2 месяца назад
Akulu ganizani before you think simumalikonda dziko lanu or muli mu gulu lasatana nanu
@JessicaManda-zm1ug
@JessicaManda-zm1ug 2 месяца назад
Azikayenda ku midzi azikawona anthu mene akuvutikira agugawana onkhaonkha ndi ufiti wawo
Далее
DACHA Webinar Series: Lunchtime Webinar 2
1:30:48
Просмотров 13 тыс.