Тёмный
No video :(

ATUPERE MULUZI KWAGWANJI? 

HOT 265
Подписаться 76 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

25 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 21   
@KenHaji-z3q
@KenHaji-z3q Месяц назад
Anthu ena saziwa zabwino amangoona zoipa zokhazokha,, atupele analosela zikuchitika lelozi koma amalawi sananve,, m'malawi amanva nkhwangwa ili mutu
@MustapherLino
@MustapherLino Месяц назад
Atupere my vote
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l Месяц назад
Atupele mbava ngati abambo ake 😂😂😂
@VailetnyirendaShamah
@VailetnyirendaShamah Месяц назад
😂😂😂😂😂😂
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu Месяц назад
Inu mwasowa chonena atupere alibe mbiri yoipa ndpo sapanga ndale zonyoza munthu
@shotsfired588
@shotsfired588 Месяц назад
Atupele ansbadwa kolemera sangaone kuvutika kwa mwana ogona ndi njala, vuto amaziona ngati anabadwa kukhala president wadziko, he wants desperately to be a president of Malawi
@user-uv5rf4zt5q
@user-uv5rf4zt5q Месяц назад
we can change leaders many times but the only way to go is federal system of government
@user-wr1km2gh4g
@user-wr1km2gh4g Месяц назад
Atuele ali ndi vuto loti samapereka ndalama kwa omusatira komanso kwa amphawi muja amachitira bambo ake,Atupele ndi oumira kwambiri ndichifukwa chake anthu sakonda chipani cha UDF
@Freedomchennl47
@Freedomchennl47 Месяц назад
Amalawi tintekhela serious kumene inu mumafuna tintenge serious ndan ife ndli nd Atupele ❤❤❤❤ 2025
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 Месяц назад
Mr president is Atuphere muluzi vp president fredo Malawi 📷 ukuona bwa anthu awawa apange alc Malawi wathu maybe is gonna change
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Месяц назад
Zoduka mutu zimenezo Bola President APM runningmate Mary Chilima or Fredo
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Месяц назад
Aaa sitikuanga nawo za agogo zo ife musova
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili Месяц назад
Palibe chipani chingajoinane ndi mcp muno mumalawi
@OretarbadrBwanali
@OretarbadrBwanali Месяц назад
Wabwino Ku Malaw simuzmupeza limban mtima vuto mumasankha atsogoleri kamba ka mitundu nd sankho
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Месяц назад
Atupele boma
@EdwardSimfukwe-d2q
@EdwardSimfukwe-d2q Месяц назад
Poyikila vn ndipati kod kut ndifotokoze bwino
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q Месяц назад
Zaziii zachamba mukungolimbana ndiazanu
@user-cv8wb6im1c
@user-cv8wb6im1c Месяц назад
Hot election 2025
@polesanamakwenda6932
@polesanamakwenda6932 Месяц назад
mmmmhhhh
@user-ml2vw1dc9c
@user-ml2vw1dc9c Месяц назад
Zipani zakubanja
@BreezyRoben
@BreezyRoben Месяц назад
Iyi ndikwagonanji not kwagwanji 😂😂
Далее
HOW DID SHE DECIDE TO DO THIS?!
00:27
Просмотров 6 млн
Wife habit 😂 #shorts
00:16
Просмотров 49 млн
拉了好大一坨#斗罗大陆#唐三小舞#小丑
00:11
NDUNA ZAMASUKA KU PARLIAMENT
23:05
Просмотров 802
AZIMAI A UTM KU AIRPORT KOWALANDILA ACHAKWERA
17:16
Просмотров 11 тыс.
When A Gang Leader Confronted Muhammad Ali
11:43
Просмотров 7 млн
A RICHARD CHIMWENDO BANDA KUNG'ALULA DPP
25:45
Просмотров 21 тыс.
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Просмотров 123 тыс.
HOW DID SHE DECIDE TO DO THIS?!
00:27
Просмотров 6 млн