Za ziii aaaaaaa ife si ana tikuziwa mukutipusitsa waziwa liti ndipo mutuluse ma lipoti a ife ya chilima atuluka munachita kunpha 2025 zikuntha zimenezo feti ameneyo
Musatitukwanisepo apa ..sitinakhalepo ndi a vp aafupi choncho... Awa. Pompano abwerera ku ntchito yawo ku Tikuferanji.. Kutiphera muthu yemwe anabadwa ndi utsogoleri even maonekedwe ake amamuchitira umboni ...
Michael usi siwa UTM koma wa MCP ndipo sakudziwa ntchito yake because akugwila ntchito ya minister Lero ngati iye ndi minister,,,,,,,,,ali pa u minister samkagwila bwanji,,,,,,,,,,wayamba mwaphuma ndipo akusewela ndi mkango mcp,,,,,,,,aziona because Malo akusewelawo siake ndi a bushiri
Koma sindingagwemo chifukwa Cha izi unless ndikuone usi uli limodzi ndi kaliati ndi ena onse omwe kaliyat akugwila nawo ntchito falling which sindiwe wa utm .ndanena ndanena sindikukhuluoilila ine ndipo zakozo sindinganve koma utagwilana manja ndi kaliati ndi ena mmmm ulemu wanga ukupezani ndithu koma mukupangazi mmmm mwavala Makaka a utm kunja nkati muli mcp
Usi ndimukonda ndipo ankandiwaza even malemu Chilima pomusankha anamukhulupilira koma anasintha atayamba kugwira ntchito ndi boma ndipo anadya bazi and akungoyankhula zambali yaboma not zolimbikitsa chipani cha Utm. Ndipo ukoko samagwira ntchito zaboma ndebwanji sanavale makaka achipani? Akunamatu Usi ndiwachabe l dont trust him
Manganya si wa UTM uyu, nanu mungowombera mmanja zilizonse mxiew! Tamusiyeni azipanga za MCP zakezo tatuwache Sikono wanuyo, SKC continue rest in peace, your still our president even in heaven will vote for you 😢