Тёмный

BON KALINDO LERO PA 16 JULY 2024 | 

DZIWE TV
Подписаться 28 тыс.
Просмотров 38 тыс.
0% 0

Опубликовано:

 

22 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 150   
@user-lz4kc5ob1t
@user-lz4kc5ob1t Месяц назад
Ife tamupasa kale mai kaliyati president of utm
@user-ig9ip8jq7v
@user-ig9ip8jq7v Месяц назад
Watching from S A port Elizabeth timakunyadilani bwana pitilizani kuti imilira Mr Bon kalindo l Salute u bwana
@EnittaDavison
@EnittaDavison Месяц назад
Umatiymilra iweyo ulemu wako bon 🔥🔥🔥🔥👏👏👏👏👏👏
@justinmakiyi4189
@justinmakiyi4189 Месяц назад
As UTM and Malawi as whole country we are luck having this guy as somehow a prophet or advisor to the difference parties. The choice is in our hands to take the advise or leave them. But one day we shall remember Him. That's the free advise indeed. Regards
@GreyJecky
@GreyJecky Месяц назад
True
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f Месяц назад
😅😅 zapana ndithu ndipo sanati and who is Manganya??? U don't know Bonnnnnn Kalindooooo mwana oopsa kwambiri ndiponso mumumva, the DC mwana woyankhulira pa mchombo pa Malawi, alibe mantha ndipo saopa Unyolo kaya mfuti😅😅😅
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl Месяц назад
President wathu wathu amangoyima pachilungamo🎉
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Месяц назад
@@Lazarus-qo1sl president wa zitsilu zokhazokha ndi mbuli zophumzila koma makolo awo fees anagowononga ngati mmene DPP inawonongera dzikoli
@VungaQueen
@VungaQueen Месяц назад
Mmmmmmmm inu Bon Kalindo musiye nde zitsilu tili ambili inu anthu abwino Kharani km siwani kt choyipa chitsata Mwini nadutsa sindinyoza ine
@christopherphiri8476
@christopherphiri8476 Месяц назад
Born kalindo will help UTM if anything engenge him to assist he is a man of action Christopher phiri from Zambia
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer Месяц назад
DC born kalindo more fire 🎉
@SteveSamson-t9d
@SteveSamson-t9d Месяц назад
following kalindo Diiiiiìiiiiiiii siìiiiiiiiiiiii
@user-dp7bc7yy6s
@user-dp7bc7yy6s Месяц назад
Awa ndiye amkamuna a UTM zili ndiinu kunyozera km Bon ndiye walangiza.
@MisheckAselo
@MisheckAselo Месяц назад
The DC, Mr booooooon kalindo 🎉🎉🎉
@TooNajahInsideKoshah
@TooNajahInsideKoshah Месяц назад
Iwe ndiye president wathu wathu
@DalitsoTwalick
@DalitsoTwalick Месяц назад
Thanks my president for ur information
@user-yk5qd6sk8e
@user-yk5qd6sk8e Месяц назад
the dc 🎉🎉 mwana ooopsa kwambili
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i Месяц назад
Kodi a UTM mukuitana athu kwana chifukwa ninji Kodi menemo mulibeathu oti angayendese chipani ?bwinonazotu ndalama inampha mwanawamuthu zayekha ananyika sima m'mazi
@vincentkhunsanama584
@vincentkhunsanama584 Месяц назад
Yeah, the DC is not making mistake to advice the utm fam big up the DC
@JosephLemani-qq1is
@JosephLemani-qq1is Месяц назад
Mwayankhula bwino bon kalindo ena akufuna kugwetsa chipani cha UTM koma bola abwelele komwe anachokela
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Месяц назад
Inetu ndimaganiza Kuti boni kalindo ndi mamuna koma ayi eti ndi wamkazi or kuganiza kwake ndimadabwa nako aaah lero ndamumvetsetsa ndi mkazi paja amavalaso ma browsers amamangaso tsitsi 😅😅😅😅😅 koma MCP yamulela bwinji because popanda MCP sibwenzi ali miss kalindo lero ayi akuyenera ponyoza MCP uku ndlama zikulowa kuchokera kwa anthu a ndale opposition 😅😅😅😅😅 uyithokoze MCP ukuchita bwino kwambili keep it up moto kuti buuu Satana akugwila ntchito yowatsogolela anthu ku moto ndi pakamwa kulankhula sosakondweretsa ambuye work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die
@JusticeNyirenda
@JusticeNyirenda Месяц назад
Thanks for the information about Jesus, but the rest is senseless
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Месяц назад
@@JusticeNyirenda so it's better not to take part to these people we can die in sins we are in the last days all things must come to pass like economy James 5 the whole chapter famine, wars, disease all these they contribute financial crises all over the world Mathew 24 vs 5 to 8 then you will here about the national Sunday Law to combat all the crisses mentioned above by force in the name climate change and the pope will rule the world for 3 and half years but he will be overflow by all nations when they will see that no change but hypocrisy leading people to destruction and people will be against him work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die follow Jesus not politicians ndi abodza Ngati omwe akuchulikitsa machimo awo pa social media
@ElizaJames-by8ef
@ElizaJames-by8ef Месяц назад
African man ❤❤❤
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi Месяц назад
Muzibwereza mau aoooooopsya kwambiri 😅😅😅 ndi iiiiiii
@KondwaniBilliat-t4g
@KondwaniBilliat-t4g Месяц назад
A DC tikupempha Mulungu wa kumwamba akupaseni moyo wautali ndi ntchito zanu zabwino pitilizani tilipambuyo panu nga!nga!nga!!!!!!!
@EdwinMabviko
@EdwinMabviko Месяц назад
Unayankhula zimenezo ,galu iwe!!!
@user-zr7wk4oq2x
@user-zr7wk4oq2x Месяц назад
Very sensible message bwana #DC♥️🔥🔥🔥
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx Месяц назад
Good advice Mr President
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Месяц назад
The DC we are with you Mr president wa anthu osawuka ❤❤
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f Месяц назад
Wolimbana ndi Boooo Kalindo oooo the DC atembenuke ndipo azilume kunsana more 🔥🔥🔥 Kalindooooo the DC 😅😅
@LuckyMhlanga-m1u
@LuckyMhlanga-m1u Месяц назад
Kalindo you are true
@HajjiSufiyani
@HajjiSufiyani Месяц назад
Pitilizani. Kutisogolela. Ndithu kuyakhula koveka bwana
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x Месяц назад
Ndizona osangotenga zili zonse km a Malawi asanhhe
@user-wu8kp7ui5j
@user-wu8kp7ui5j Месяц назад
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥
@AliajoeAliajoe-vv1wo
@AliajoeAliajoe-vv1wo Месяц назад
Great man
@violetpotani
@violetpotani Месяц назад
Eeeish koma information mumayipeza 😅😅😅anthuwa bwenzi atangokhala coz akunyozeka
@Judah-zb6sl
@Judah-zb6sl Месяц назад
The DC ❤🎉🎉🎉🎉🎉
@ErickMambelera
@ErickMambelera Месяц назад
Umakwana kalindo
@WanangwaVwalika
@WanangwaVwalika Месяц назад
More fire!!
@eliaschinoko2086
@eliaschinoko2086 Месяц назад
The Dc Booooooooooooooooooooooooooooooooooon Kalindo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@OmrahGeraldOmrahGerald
@OmrahGeraldOmrahGerald Месяц назад
❤❤❤❤ The DC kungalula
@davidmzee2205
@davidmzee2205 Месяц назад
Nde mwati Pepe Kale ?😂😂
@annamazingashaibuh6276
@annamazingashaibuh6276 Месяц назад
The DC kkkkkkkkk🔥🔥🔥🔥
@KingLunda-u1t
@KingLunda-u1t Месяц назад
Big man hooooooo
@Lemankais
@Lemankais Месяц назад
Bon ndi kampani simunthu wamba
@SteveZimba-e8s
@SteveZimba-e8s Месяц назад
Gwiritsani ntchito malangizo amene wakupatsani DC osazitaya muononga chipani chanu chabwino bwino
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb Месяц назад
Ng''alula m'bale.
@user-oy6dl1pv9e
@user-oy6dl1pv9e Месяц назад
Following kwa Diiiiiiiiiiiisiiiiiiiiiiiiiiiiii
@SanidaChirwa
@SanidaChirwa Месяц назад
Ing'alilen fada ,osaopa ay Malawi ndiwathu uyu
@FelixKazembe-wi5zb
@FelixKazembe-wi5zb Месяц назад
Ndizosantheka kutuluka anthu onse chipani" choti mudziwe chipani cha UTM chamwazikana! Pepho langa ndiloti osalawo asachuluke zomwe zitapangise chipani kuchepa mphavu...manganizo anga.😢
@sulleahmnyimbili1362
@sulleahmnyimbili1362 Месяц назад
Thanks for the advice Mr kalindo
@FionaKhoma
@FionaKhoma Месяц назад
Akunamizana kwambili athu amenewa mcp ikutula udindo pasi
@Raph-kayRaph-kay-g5v
@Raph-kayRaph-kay-g5v Месяц назад
Utm samalani ndi kabambe ndi brocko yati musabwerere Ku DPP matchera chenjerani mafana
@Pangolinimw
@Pangolinimw Месяц назад
The DC 🎉🎉🎉🎉🎉
@BrightNkhoma-xz4bg
@BrightNkhoma-xz4bg Месяц назад
❤❤❤❤ ukupangila sogolo lowala DC
@CHEWATCHMAIDAH
@CHEWATCHMAIDAH Месяц назад
It's true
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Месяц назад
Ur right the DC akapusa kulowa mikangano
@user-sk3ld2ss7s
@user-sk3ld2ss7s Месяц назад
Boni kalindo ndi chilata chopanda kanthu, chomangosokosera...
@Maliko-bp1xn
@Maliko-bp1xn Месяц назад
Mukulankhula zooonadi
@PetroMatias
@PetroMatias Месяц назад
Ndinzoonadi asangotora munthu
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i Месяц назад
The DC mwana wowopsya kwambiri Bon kalindo
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 Месяц назад
The DC mnyamata oopya kwambiri 😅😅
@EmmanuelMalata-r4j
@EmmanuelMalata-r4j Месяц назад
Mumatiyimilira bwana❤
@YolliyajeerasYeeras
@YolliyajeerasYeeras Месяц назад
Mwana ooooooooooopsa kwambili
@RuthMoto
@RuthMoto Месяц назад
Mukhalise comrade Bon kalindo
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Месяц назад
Amp alibe nawe nthito kambwe iwe chisilu
@AwetuAmidu-u2j
@AwetuAmidu-u2j Месяц назад
Wayankhula bwino bon
@user-pb6wb3iz7z
@user-pb6wb3iz7z Месяц назад
Well narrated
@BrightNkhoma-xz4bg
@BrightNkhoma-xz4bg Месяц назад
Athu opusa kwambiiri akuona ngat tikugona......... Our president Bon Kalindo 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 😂😂😂😂 pepekale
@user-mk4ju6iw7c
@user-mk4ju6iw7c Месяц назад
Mwathandidxa akafunakunyodxela anyodxele okha
@SHABBASELEMANI-o8d
@SHABBASELEMANI-o8d Месяц назад
Ati PEPE KALE... koma DC
@FionaKhoma
@FionaKhoma Месяц назад
We folow
@jacksonmaster2288
@jacksonmaster2288 Месяц назад
Kalindo UTM amaikonda kwambili
@EstherBailoni
@EstherBailoni Месяц назад
DC , tiye Nazo usaope
@DICODIDICODI
@DICODIDICODI Месяц назад
No☝️THE DC
@richardjumah198
@richardjumah198 Месяц назад
UTM malangizo a ulele awa please
@user-rr7je1zi8t
@user-rr7je1zi8t Месяц назад
Kuti nkhaaaa wabwela bon kalindo
@KondwaniBilliat-t4g
@KondwaniBilliat-t4g Месяц назад
Backward never forward ever ❤
@PeterNamphwanya
@PeterNamphwanya Месяц назад
Chi booooon kalindooooooo🎉🎉🎉🎉🎉
@HusseinAdamLidezo
@HusseinAdamLidezo Месяц назад
The DC
@user-ck7eb7tb7v
@user-ck7eb7tb7v Месяц назад
Sakumudziwa Boooon Kaliindo
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Bola mwachenjez ali ndi khutu ambve
@Momweekly
@Momweekly Месяц назад
Well spoken
@MecyMalothi
@MecyMalothi Месяц назад
The D C our pangolin
@jumahgeorge
@jumahgeorge Месяц назад
Following
@OwamiSimeon
@OwamiSimeon Месяц назад
Born kalindo the deceeee
@user-rr5nq2uo6i
@user-rr5nq2uo6i Месяц назад
Big up the DC
@AnyumbaJulias
@AnyumbaJulias Месяц назад
Ulemu wako iweyo bon kalindo
@user-zl5wv8ix8u
@user-zl5wv8ix8u Месяц назад
Kalindoo akunena dzoona
@jumahgeorge
@jumahgeorge Месяц назад
The DC more 🔥
@JohnWindford-jv8ls
@JohnWindford-jv8ls Месяц назад
Kma azipumako Tizimvako zina.
@marcelolemos1484
@marcelolemos1484 Месяц назад
THE DC
@ClementJosephy
@ClementJosephy Месяц назад
Inuyo munavaya patali ana achepa,... Eeeeee
@BrightonKamwendo-db1ci
@BrightonKamwendo-db1ci Месяц назад
Mau onveka zeeed mbuyanga
@GiftJulius-ro9ev
@GiftJulius-ro9ev Месяц назад
Kabambe simunthu ..
@MaxwellKananji-r5d
@MaxwellKananji-r5d Месяц назад
Makamaka pamene wanena kut pakufunika mery chilima amutenge kut agwile naye ntchito pamenepo Mr DC mwanena zoona ndipo mzimu wa SKC utha kuusa mumtendele
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Месяц назад
Chifukwa chamkazi wakeyo? Mukunama ....za Mulungu amaweruza yekha ndipo sapanga pangano ndimunthu...Za dziko lapansi musaphatikize Mulungu
@FelixKazembe-wi5zb
@FelixKazembe-wi5zb Месяц назад
Ndichaka amalawi dale zimativuta chifukwa mumafuna anthu omwewo azipanga dale. banja lonse abambo akakhala president mwanaso akufunaso wu president omweyo ayi😂😂😂😂 dale sichoncho.
@user-hq6dq7zr1e
@user-hq6dq7zr1e Месяц назад
Auzeni a utm azinyozela wokha
@TalazanGamah
@TalazanGamah Месяц назад
We follow
@lydiagadama4887
@lydiagadama4887 Месяц назад
The Dc
@YusufIbrahim-w1g
@YusufIbrahim-w1g Месяц назад
Boooon kalindo is not sepro man is big man chizulo chat ambawi Allah bless him
@RhodaNombo
@RhodaNombo Месяц назад
Mmatiimilila the dç
@oskidooscar7468
@oskidooscar7468 Месяц назад
Aaaaaaaaaa awa amaopa manganya ndamzawo
@Raph-kayRaph-kay-g5v
@Raph-kayRaph-kay-g5v Месяц назад
Manganya nkanyama kanji? Phwala lako wamva
@oskidooscar7468
@oskidooscar7468 Месяц назад
@@Raph-kayRaph-kay-g5v manganya olo nda bambo ako angafanane iwenso chisilu et Manganya is a vp of malawi You like it or not
@TemwaKabisa
@TemwaKabisa Месяц назад
The DC 🎉🎉🎉🎉🎉❤❤
@MosesShaibu-ee8hn
@MosesShaibu-ee8hn Месяц назад
Pepekale ameneyo wakumalawi?kapenawaku ithiopia
@JosephyMagombo-t7d
@JosephyMagombo-t7d Месяц назад
The DC ✊️
@stormchatepa134
@stormchatepa134 Месяц назад
bwana nyo
@ellensambo6323
@ellensambo6323 Месяц назад
❤❤❤
Далее
WANG'ALURA UKU AKUPHUNZITSA SAKUOPA ALIYENSE  |
29:10
Times Exclusive featuring Bon Kalindo - 6 January 2024
1:03:20
BON KALINDO LERO PA  21 AUGUST  2024 |
16:53
Просмотров 29 тыс.
BON KALINDO LERO PA 22 AUGUST 2024 |
17:14
Просмотров 20 тыс.
MICHAEL USI  KUDYA PA CHIYIMILIRE ONELANI  |
16:00
Просмотров 9 тыс.