Тёмный
No video :(

BON KALINDO LERO PA 17 JULY 2024 | 

DZIWE TV
Подписаться 29 тыс.
Просмотров 27 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

29 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 124   
@johnmpatama1461
@johnmpatama1461 Месяц назад
Watching from Stellenbosch Capetown
@DanielKatengeza
@DanielKatengeza 11 дней назад
Watching from Spain
@SahilluYusuf-sk7es
@SahilluYusuf-sk7es Месяц назад
He us totally true to convince us ,anyera many I aMCp.Even UTM was there because of Chilima
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Месяц назад
Anthu safuna ku sogolera dziko ayi amafuna maudindo ndi ndalama palibe chazelu chomwe angachite
@AlickDaud
@AlickDaud Месяц назад
Watching from Botswana the Dcccccc
@JohnfosterNkusengwa
@JohnfosterNkusengwa 12 дней назад
Watching from cape Town pa boma the DC
@IssahAluba
@IssahAluba Месяц назад
Watching from S/A
@OsmanGift-f4p
@OsmanGift-f4p Месяц назад
Watching from SA cape town langa. Bon kalindo you the powerful do not just leave like that help Malawi from this creaminals
@KayRolly-l7n
@KayRolly-l7n Месяц назад
Watching frm Johannesburg. This man is wise.
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 12 дней назад
The DC'S mwana woooopsa kwambiri chilungamo chiyende ngat madzi umakwana Iweyo
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu Месяц назад
50+1 is here to stay.... munangoifuna kuti muthane ndi dpp inu mukuithawa zanu musova
@AngolanChinga
@AngolanChinga Месяц назад
I'm hear cape town khayelisha but i love bon kalindo always God bless you bro
@EllinaBitto
@EllinaBitto Месяц назад
Tell them,watching from Durban South Africa ❤❤❤❤
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w Месяц назад
Chilima anatisiya ,Koma UTM ,mupangisa Kuti chipanichi muwononge ,Kalindo ndizowona akunenazi
@VincentMagriva
@VincentMagriva Месяц назад
Ndipo they need money olo zot tsiku limene Dr saulosi chilima anakumana nalo mosayembekezela nawonso azakumana nawo anaiwala pa dziko lapansi palibe wamuyaya this is your time ndalamazo ibani koma musamale pot pot baibulo limat tsoka ntunde nd nyanja pot oipayoo wasikira komweko
@user-gn4mx2es3k
@user-gn4mx2es3k Месяц назад
Ine monga Vice DC ndikungogwedeza mutu pa zomwe bwana wangawa akulankhula
@CHRISSYBALALIKA
@CHRISSYBALALIKA Месяц назад
Kuyankhura chilungamo osaopa aliyense 🔥🔥 more fire DC
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Месяц назад
Akaliyati bingu anamwalira mmanja mwanu mnachitapo izi mnali anduna nthawi yimeneyo mlomwe mzanu mnachitapo izi nyifwa yikuwawa kufwa kwa kwachilima ambiri mwasangalala kuti mpeze mavoti koma ziwani kuti maw lanu simkuliziwa
@aubreykatembe3081
@aubreykatembe3081 Месяц назад
Takawabanduledi DC
@HamitonFrank
@HamitonFrank Месяц назад
Watching from Johannesburg the DC
@JibuzahDrag
@JibuzahDrag Месяц назад
Watching from Johannesburg South Africa
@EmmanuelMalata-r4j
@EmmanuelMalata-r4j Месяц назад
Mr Born kalindo more fire mumatiyiimlira❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-dp7bc7yy6s
@user-dp7bc7yy6s Месяц назад
Iwedi ndichilombo the DC ndimwana woopsa
@UlemuKwilambo-o3j
@UlemuKwilambo-o3j Месяц назад
Watching from SA, Bloemfontein free State
@OsimanIbnAkim
@OsimanIbnAkim Месяц назад
The DC munthu ooooopsa💪💪💪
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Месяц назад
kukamba mosabisa phuma LA mai kaliat ndi bambo njalawa liononga chipani anthu awiri awa ndamene akuchita zinthu mwa phuma kwambili
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq Месяц назад
AniBo umakhwana,tikuverani ndithu,kuchokera kuno ku Molere,masambanjati.
@ChifundoNinje
@ChifundoNinje Месяц назад
Watching from cape town
@MariamChipoka
@MariamChipoka Месяц назад
Your a hero❤❤
@ellensambo6323
@ellensambo6323 Месяц назад
Watching from midland south Africa
@SahilluYusuf-sk7es
@SahilluYusuf-sk7es Месяц назад
Watching from SA pretoria
@AgnessMzengo
@AgnessMzengo Месяц назад
😢😢koma zoona a UTM😢koma mzimu wake utikanthe.... A malawi ndife anthu osachedwa kuiwala..... Evance Meleka anaimba kale # Adzakuiwala, uzasanduka nyasi😢chikondi cha pa dziko lapansi
@VincentMagriva
@VincentMagriva Месяц назад
Ndipo they need money olo zot tsiku limene Dr saulosi chilima anakumana nalo mosayembekezela nawonso azakumana nawo anaiwala pa dziko lapansi palibe wamuyaya this is your time ndalamazo ibani koma musamale pot pot baibulo limat tsoka ntunde nd nyanja pot oipayoo wasikira komweko
@JeanChirwa
@JeanChirwa Месяц назад
Zoona D C Walankhula Zoona. Keep it Up. God Be With You Always.
@PaulMwachande
@PaulMwachande Месяц назад
Mwiniwake oziwa ku ng'alula umakwana THE DC
@CharityKangulero
@CharityKangulero Месяц назад
Watching from Belleville copetown
@KaisiAbdullah
@KaisiAbdullah Месяц назад
Watching from Durban the DCEEEEEEEEE my precedent wathu
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Месяц назад
Dc we love you ❤
@AmosMkandawire-re9pw
@AmosMkandawire-re9pw Месяц назад
The DC mwana wowopyaaaaaaa kwambiri tell them the truth. From South Africa
@james-zd2nz
@james-zd2nz Месяц назад
Watching from jhb
@YusufChipojola
@YusufChipojola Месяц назад
From tete Mozambique
@AliKaukutu-bo7cx
@AliKaukutu-bo7cx Месяц назад
Watching from cape town Mitchell's plan all the from malawi balak
@joanaKachiwaya
@joanaKachiwaya Месяц назад
Ubwino wake wovota ndifeyo tikufuna Mary chilima atuluke aphulitse bomba
@masterkachingwe7448
@masterkachingwe7448 Месяц назад
Mai Kaliyati atsongolere UTM kukhala bata and morale
@MargaretMillion
@MargaretMillion Месяц назад
Well said brother
@JunaKananji
@JunaKananji 12 дней назад
Karido Dc❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@violetpotani
@violetpotani Месяц назад
Anthuwa ngamadyera chabe palibe chanzeru chomwe akuchita iwo bola ndalama
@LindaChikwawa
@LindaChikwawa Месяц назад
Mumakwana mr DC uremu wanu
@JascoUluma
@JascoUluma Месяц назад
Koma umanena chilungamo chokhachokha umakwana l proud of you
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk Месяц назад
Ndalila ine chomwe akuchita sakuchiziwa zoona chilima azimupanga chonchi chifukwa chandalama
@STEPHENBJNKUMBIRA
@STEPHENBJNKUMBIRA Месяц назад
Koma munthu uyu zimagovuta amalangiza vuto ndi ife anthu 50+1 iwewo akuti akufuna kuyichosa analowa boma ndi chani ngati zili zimenezo ndiye kuti anthu aja sakuyenera kukhala pamene paja
@petertaulo8014
@petertaulo8014 Месяц назад
We will stand as UTM forever
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw Месяц назад
I'm hearing live from khayelitcha Barracks ( Capetown)
@BettyByson-t4z
@BettyByson-t4z 12 дней назад
Flom phalombe mbambande bon,
@MarvinChilombo.flourish
@MarvinChilombo.flourish Месяц назад
Kalindo akundisokoneza, akuti a UTM akanadekha kaye. Aaaa nthawi ndimene yatha. akufunika apange strategize za 2025 race. After all, divisions are inevitable in politics coz even Kalindo himself can not name Chilima's successor who will be liked by everyone in the party. UTM is running out of time. Rest well SKC
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq Месяц назад
Agalu a mcp maka makaka pepe kale ndi ndi Chalakwe,aluga kwasiba
@DOMINICSOKOSO
@DOMINICSOKOSO Месяц назад
Ubwino wake Ife tikuyang'ana inu konko make the utm party walks accurate there u r our trust
@JonathanChimwaza
@JonathanChimwaza Месяц назад
Live from south Africa cape Town
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx Месяц назад
Akhaula amenewo. 50+1 mmesa anayiyambisa ndiiwowo kodi, ndiye lero akuyiopatu powona kuti sangamake. Mulingo omwe munamuyezera nawo Peter Mutharika 2025 walunjika pa inu achakwera ndi uhule wanuwo
@TemwaKabisa
@TemwaKabisa Месяц назад
Ulemu wanu Mr DC ❤❤❤❤
@user-xv5pr3ji6w
@user-xv5pr3ji6w Месяц назад
Tiri pano kumvera ine pat wa patrick, from Pretoria SA
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl Месяц назад
The DC kunena chilungamo
@MoosaChirwa
@MoosaChirwa Месяц назад
Keep fire burning mr
@PempheroMoleni
@PempheroMoleni Месяц назад
Live the DC wa ine umakwana
@lonnexjeke6840
@lonnexjeke6840 Месяц назад
Ulemu wanu Mr DC❤
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад
Number one ❤❤❤❤
@UlemuNewton
@UlemuNewton Месяц назад
Zeeeeeeeeee Dccccccccccccccc ❤❤❤❤❤❤❤❤❤kuti khazuuuuuu
@mrcool531
@mrcool531 Месяц назад
Akhale phee ali ndi nthawi? Next year elections
@StanleyDama
@StanleyDama Месяц назад
Choka iwe nesa unawauza ndiwe
@lastchipwere4481
@lastchipwere4481 Месяц назад
Ngati pali munthu mmodzi yemwe bon kalindo sangamuzuzule ndi Michael usi,,now i beleive
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i Месяц назад
The DC mwana wowopsya kwambiri Bon kalindo kuyankhula mosaopa
@Kareemah-y4p
@Kareemah-y4p Месяц назад
Koma umanena chilungamo chokha chokha bro mumatiyimilila
@MarcRero
@MarcRero Месяц назад
❤❤❤❤❤
@patrickjaenda8288
@patrickjaenda8288 Месяц назад
Katundu waboma
@jacksonmaster2288
@jacksonmaster2288 Месяц назад
The D C, mwana oopsa kwambili. Koma kalindo UTM amayikonda kwambili. I will keep saying this now and again
@yassinn5634
@yassinn5634 Месяц назад
Kodi inu a Kalindo siinu nomwe mumalimbikitsa kuti UTM choke ku MCP ndipo abwelere ku mene anachokera ku DPP. Ndiye lero mwapeza choyankhula chifukwa zomwe mumayembekezera sizinachitike
@user-mf7hf7we2u
@user-mf7hf7we2u Месяц назад
Iwe umafuna zimenezi
@freedahjere2164
@freedahjere2164 13 дней назад
Zamveka ndithu
@OwamiSimeon
@OwamiSimeon Месяц назад
Born kalindo the deceeee
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f Месяц назад
Zosatheka kupha iweo, iweyo ndi mwana oopsa kwambiri ,
@cictechnologies1091
@cictechnologies1091 Месяц назад
Munthu uyu ndi wamisara ndareka kumuvera
@Charlesnsiri
@Charlesnsiri Месяц назад
😢Amakuza ndan kt uzmunvela
@user-mx5cx3gl4h
@user-mx5cx3gl4h Месяц назад
🤣🤣🤣the DC moto
@pemphero-fo9en
@pemphero-fo9en Месяц назад
Mwalankhulako zazelutu lero akalindo
@JustinLoka-ed4bx
@JustinLoka-ed4bx Месяц назад
😂😂 katundu uyoo
@sheila5812
@sheila5812 Месяц назад
UTM yama kandulo 😂😂
@GeorgeWhite-f1p
@GeorgeWhite-f1p Месяц назад
👍💪💪💪
@iqrahzaheed8633
@iqrahzaheed8633 Месяц назад
Kubandura kubandula
@mensuremegrem8330
@mensuremegrem8330 Месяц назад
50+1 ilipo ndipo ndilamulo sitilola nanu mulione
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Месяц назад
Mbuli iwe thokoza MCP ndi akatundu pa nkhani za chitukuko komaso ukudya bwino chifukwa cha Boma limeneli ukulinyoza koma ndlama ukulandila from opposition 😅😅😅😅 Munda wako umenewu keep it up mpakana MCP iwina the more ukunyoza the more God's grace and popular MCP will gaining more popular 😅😅😅😅😅
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl Месяц назад
Kupusa ndikulankhula mopanda umunthu apa kagwere uko apa
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Месяц назад
@@Creslevison-vj2sl bola wamva ndithu pajatu anthu amakonda Balaba kusiya yesu wina ndinu bola zamveka mukadakhala mukumvetsera uthenga oti ukupulimutsani bola koma za ndale aaah sorry mzeru mulibemo koma opposition ilipoyi or atawona kuti ichi ndi chabwino sangayamikile because alingati satana amatsutsa chilichonse or pasimenti akuuzani kuti mukutithila fumbi nkhani ndi maudindo adziko la pansi kungowavotera mudzanenaso kuti bola yemweuja pa social media sipobweretsera nkhani za kunyumba kwanu ayi kapena kuphunzililapo kutukwana ayiso ndiye sankha wekha panopa ndi chakwera timusapote basi akabweranso wina timusapotenso kuti dziko litikuke koma Izi aaa tikhala pamodzimodzi momwemu
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Месяц назад
Inetu sindinyengerera pochita zinthu because mbuli zophunzila zachuluka koma zosathandiza dziko koma kumasula dziko ndi kuligawanitsa
@HanunKelekesa
@HanunKelekesa Месяц назад
Umakwana
@amosbula1249
@amosbula1249 Месяц назад
Bon Kalindo akunena zoona
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Месяц назад
Ndalama yimapangisa munthu kupanda nzelu akaliyati mawwona ngati alindi nzelu koma ayi awagula adpp ndi iweyo kalindo mwagulisidwa simukulira chilima ayi nkhani yake ndikugulisa utm
@oskidooscar7468
@oskidooscar7468 Месяц назад
Mau
@TessMjuma
@TessMjuma Месяц назад
I wont be a chakwela 😂
@ephraimnogwe6430
@ephraimnogwe6430 Месяц назад
50+1 idabwera kuzakhala imene inja
@DesireLuka-nf5is
@DesireLuka-nf5is Месяц назад
❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Месяц назад
Amai chilimawo sakuziwa kuti anzawo ali pachingalalo kugulisa chipanicha amuna awo sakulira chilima koma kuti akusangalala kulira ife timakuziwa
@NoelBurton-x1z
@NoelBurton-x1z Месяц назад
The DC
@RamadanShafisha
@RamadanShafisha Месяц назад
Inu pezani ntchito yoti muzigwila
@MoosaChirwa
@MoosaChirwa Месяц назад
Chilimalism😂😂😂😂😂
@EliasKawuwa
@EliasKawuwa Месяц назад
Is that activism,or politics? Osangoqasiwa bwanji,Mesa ndi chipani chawo,Mesa iwe unachokamo? Aaaaa asiyeni ndi chipani chawo, ndani safuna kudya?
@oskidooscar7468
@oskidooscar7468 Месяц назад
Kkkkkkk Iyeyi amamuopa manganyanso
@sheila5812
@sheila5812 Месяц назад
Paja amapangira ma drama limodzi 😂​@@oskidooscar7468
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t Месяц назад
Dc kuyankhula mopanda mantha 😅
@NovassTambala
@NovassTambala Месяц назад
Your the best, washing you form cape town graders
@user-rt6rd1em8y
@user-rt6rd1em8y Месяц назад
😂😂😂😂😂😂
Далее
KUFA NDI NJALA UTAPHODA // DENIS MAHATA
29:56
Просмотров 11 тыс.
버블티로 체감되는 요즘 물가2
00:15
Просмотров 2 млн
BON KALINDO LERO PA 30 AUGUST 2024 |
14:46
Просмотров 8 тыс.
버블티로 체감되는 요즘 물가2
00:15
Просмотров 2 млн