Amen pastor chifukwa cha uthenga uwu wabwino koma ulamuliro ndi Sunday ndizoonadi koma 666 ndi chilemba chimene chidayamba kuikidwa kudzera mu COVID-19. Mwa chinsinsi . Let us calculate : COVID-19 C=100 O= 70 V= 5 I=. 1 D=500 Total 685-19 Answer 666 imene idayamba kuikidwa kudzera mukatemera ambuye akudalitseni pastor potiuzanso za ulamuliro wa Sunday.