Тёмный

COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM - AKAIPUTA NGONGOLE INA 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 62 тыс.
Просмотров 18 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

10 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 47   
@RuthTimothyChirwa
@RuthTimothyChirwa День назад
My sweet brother keep it up ❤❤
@StoniaMoyo
@StoniaMoyo День назад
Ng'alura mr ntanyiwa more fire 🔥
@Felie-p7l
@Felie-p7l 16 часов назад
Love u comrade mtanyiwa
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza День назад
Ankhadza wonse safika 2025 Mulungu akuwona zonse zikuchitikazi Mcp yayamba kupenga misala ntchito kuzunza anthu ndi kugula anthu koma fertilizer kulibe shame Mulungu akulangani ndithu mudziwona ntanyiwa woyeeee long live❤❤
@EsmeMpewe
@EsmeMpewe День назад
Ntanyiwa woyeeeeee
@DalitsoKaunda
@DalitsoKaunda День назад
Mulungu wathu ndiwamoyo sagona saiwala
@GodfreyKamphiripiri
@GodfreyKamphiripiri День назад
❤❤❤❤❤Fireeeeeeeeee Fireeeeeeeeee Fireeeeeeeeee Fireeeeeeeeee
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 2 дня назад
Tadswera bwino ifeso❤
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 дня назад
More fire comrade osaopa osatopa osafooka Allah atiombore mukaporo tili nawo pano
@VeronicaMatiki
@VeronicaMatiki День назад
Paja Ntanyiwa unakana kuti suziwapephelela nawo, koma nawonso aziwone zomwe anapanga nzawo, Mulungu Wathu ndi wa mayakho, sanati wangoyambapo😂😂😂
@JudithMajawa
@JudithMajawa День назад
Ayende bwino aaa watikwana
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 дня назад
More fire comrade ntanyita osaopa osatopa osafooka Allah alipo mpaka tituluke mukaporo tilinawo pano ndi boma ra crocodile
@IbrahimUseni-p8f
@IbrahimUseni-p8f 2 дня назад
Amwene Ntanyiwa kuno Ku machinga tikuvutika ndi njala komanso kulandidwa katundu ndi neef
@Maxwellmsowoya-i4x
@Maxwellmsowoya-i4x 4 часа назад
Mmmmmm zosayenda
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 2 дня назад
Limpopo fm woyeeeeee
@ConnexKhomba
@ConnexKhomba День назад
Kod kulapa sangakwanise 😮😮😮
@JessicaManda-zm1ug
@JessicaManda-zm1ug День назад
Koma nde ngongolezo azavutika kubweza azawo bambo awa koma mmmmm
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 дня назад
Timpephe Allah atisogorere tonse a Malawi amene tikuvutika komaso Allah amuteteze comrade ntanyiwa mpaka mcp ituluke basi
@MikeLodzi
@MikeLodzi 2 дня назад
katundu waboma uyu
@AusimanKassim
@AusimanKassim 2 дня назад
Ayende bwino
@RosinaPatel
@RosinaPatel 2 дня назад
Mulungu wa moyo akuona zonse
@FredKanyerere
@FredKanyerere 2 дня назад
Zovetsa chisoni, fertilizer nkhani.. Tsiku ngati boma libe 😢😢😢😢
@McshonWilliam
@McshonWilliam 2 дня назад
Wina atupa mutu kkkkk 2025 dpp kut buuuuuuu whether they like or not kkkkk God already.......... Writen
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w День назад
Anause msanga kuti wamkulu uja wasami la dzanja
@sabinaphili
@sabinaphili День назад
koma tizimva choncho
@MariaLevi-e7y
@MariaLevi-e7y 2 дня назад
Osaopa bg man
@AmosScott-z9x
@AmosScott-z9x 2 дня назад
Kd chakwera akumusungiranji Sam kawale nde bolaso Lowe yemweujasotu
@RosinaPatel
@RosinaPatel 2 дня назад
Ndalama zawachulukira MCP..mafumu landilani ndalamazo Ku voter umakavota wekha
@HarryChindiwo
@HarryChindiwo 2 дня назад
Katundu weni weni
@WilliamChi-c6p
@WilliamChi-c6p День назад
Eeeeeesh koma yaaah kunja kuno kuli atolakhani
@ReginaMaxwell-sv8kl
@ReginaMaxwell-sv8kl 2 дня назад
❤❤❤
@ChrissWtness-e1z
@ChrissWtness-e1z 2 дня назад
Mwabwera madala
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx День назад
Timayesa samwalira ndi aambeu iwowo afa bwanji iwowo aPita wonse atsogozanatu
@LovemoreCathy
@LovemoreCathy 2 дня назад
Kkkk zokayikitsa kuti tifikadi ku 2025 coz tayamba kale kufa ziwalo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 дня назад
Paja kuli maliro Ai rest in piecessss koma imfayo ili bwino koma wamwalirayo alibwino bwino bokosimo koma wafadi zatheka bwanji unyolo unali kutiko
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 2 дня назад
Kaya unali kuti unyolo kaya 😂😂😂😂😂😂 apita ambiri angoyambapo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 дня назад
Anthufe timalakwirana koma anthu awawa ai dziko lonse mkumadandaula iwo
@MaryMputi
@MaryMputi День назад
God is Love always Amen 🙏
@JerseyAlfred
@JerseyAlfred 2 дня назад
Umakwana ntanyiwa 😂😂😂
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 дня назад
Mcp yazazana ndi mbuli zokha Zokha basi onse a mcp ndi manganya crocodile team
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 2 дня назад
Kkkkkkkkkk
@MariaLevi-e7y
@MariaLevi-e7y 2 дня назад
Adadiomwewobasi
@AdamMakala
@AdamMakala 2 дня назад
Kkkkkki
@ReginaMaxwell-sv8kl
@ReginaMaxwell-sv8kl 2 дня назад
😂😂😂😂😂 ntanyiwa
@MateusPhiri-d2f
@MateusPhiri-d2f 2 дня назад
Ziliko 😂😂😂😂😂
@BrijlallDularie-d8o
@BrijlallDularie-d8o 2 дня назад
😂
Далее
Обыкновенное чудо
00:48
Просмотров 760 тыс.
NKHANI YADZIDZIDZI - COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM
19:11