Тёмный

Gogo Rodgers Zuze (74) battles inflammation of the manhood 

Rodwell Lumbe
Подписаться 16 тыс.
Просмотров 11 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

19 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 54   
@HawaMamo-q2v
@HawaMamo-q2v Месяц назад
Koma nkhani ndiyakuti bolani kwathandiza apite akakhale ndi abale awo .koma ambuye apamene mukuchilitsa onse odwala osayiwale abambo amenewa🙏🙏
@ChifundoJeffrey
@ChifundoJeffrey Месяц назад
Ambuye mene mukuchilitsa ena gogo Rodgers Zuze musawapitilire 🙏😢
@ScillaMau
@ScillaMau Месяц назад
Monga mmene anachilitsira Yobu, Ambuye awachilitsanso a Lupiya Amen 🙌
@Rhoda-g1y
@Rhoda-g1y Месяц назад
yehova mulungu ndiwachikondi wachifundo mopepha awachosele ululu kwa lupiya🙏🏻🙏🏻🙏🏻
@Mavitoabdulla
@Mavitoabdulla Месяц назад
Mr lumbe please yingo kwathandiza transport yokafikira kwawo ku mulanje is best way
@lastondaniel6697
@lastondaniel6697 Месяц назад
Akamutafunako bola apite ku hospital
@DrolieDongowa
@DrolieDongowa 9 дней назад
Ambuye achilitseni bambowa "komaso achibale ndi ana chonde komwe muliko athandizeni bambowa
@bernarddaniel4413
@bernarddaniel4413 Месяц назад
Eish zosayendatu,,, ambuye akuoneni mukhale bwino
@yaokingdailess
@yaokingdailess Месяц назад
Ambuye muchitilen chifundo mwana wanu
@Lloyd-gd6pu
@Lloyd-gd6pu 10 дней назад
Eeeeiiish ambuye achitireni chifundo bambowa
@BenjaminMtima
@BenjaminMtima Месяц назад
Mmmm gogo ali mmavuto uyu ambuye awakhuze
@mimizammimba7506
@mimizammimba7506 Месяц назад
Abale may God see him through 🙏🏾
@BlessingsMalunga-d8o
@BlessingsMalunga-d8o 3 дня назад
Iiii koma pepani agogo anga
@SankpA-t9
@SankpA-t9 Месяц назад
Zokhudza😢
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Месяц назад
So sad😢
@tambalahaggebunaya
@tambalahaggebunaya Месяц назад
oooh Allah make easy for him heal him give him good health😢😢😢 u know everythings 🤲🤲🤲🤲
@PriscillaKamkuzi
@PriscillaKamkuzi Месяц назад
Eeeeee koma ana amenewo amati bamboo awo Ali kut😭😭😭
@JaydreamDream
@JaydreamDream Месяц назад
Lord have mercy 😭😭🙏🙏
@BakaliJustice
@BakaliJustice 22 дня назад
Mulungu aikepo zanja
@isaacfesani2357
@isaacfesani2357 Месяц назад
Ambuye tipempha nkono wanu wamachilitso🙏🙏
@ManuelMalunga-j3l
@ManuelMalunga-j3l Месяц назад
Mulungu adalitse bambo Rhodgers ndidzanja lamachilitso
@BazlioDenja
@BazlioDenja Месяц назад
Pamene kumwamba mukukambilana zoyendela ena awaso muwayendele Ambuye
@BridgetKasira-bi2js
@BridgetKasira-bi2js Месяц назад
Ambuyee😢😢😢
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb Месяц назад
Mulungu wachisoni mukhala bwino agogo inshallah
@vatineseduwin
@vatineseduwin Месяц назад
nkhani zi zimandivesa chison ,muyendelekoso ku nkhatabay kwa TA malenga mzoma village lichenga Cheyeka kuli mayi loyina Ali ndi ana olumala ndi azibale akeso ngolumala ,mayuka, Jojo chutuwep osewo ngolumana ayendelen ndithu
@MadalitsoBokosi-j3u
@MadalitsoBokosi-j3u Месяц назад
Old age azibambo ambiri amagwidwa ndi matenda amenewa koma kuchipatala amangchila koma nkhani ndi chisamaliro alibe owasamala ..... Ambuye awakhuze
@lastondaniel6697
@lastondaniel6697 Месяц назад
Kuchila imakhala mwai chabe
@LekeThomson
@LekeThomson Месяц назад
Ndipo inu ,bambo anga nthenda yomwe anamwalilira ndiyomweyi ndendende
@dorothymanda9106
@dorothymanda9106 Месяц назад
God have mercy 😢
@ericchilinjala481
@ericchilinjala481 Месяц назад
Atengereni kuchipatala inkhonza kunkhala prostate cancer..komanso apite kwao.
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm Месяц назад
Ambuye khuzani mwana wanu amene akuvutika ndi matenda ambuye dzanja lanu silalifupi kut simungakhudze chitan nawo abambo awo amene akumva ululu wa siku ndi siku ndkuziwa ine mbuye wanga mukayamba ntchito mumayimaliza
@PatienceMaere
@PatienceMaere Месяц назад
eish💔koma makolo osamafika powataya chonchi ana awowo akunva bwanji💔😭ndiakumudzi kwathu kumulanje mmh
@RuthMatimba-l1d
@RuthMatimba-l1d Месяц назад
Ambuye awachitile chifundo
@McdonaldMpeketula
@McdonaldMpeketula Месяц назад
Amen
@FrankLeckson
@FrankLeckson Месяц назад
Ambuye tumizani machiriso chilichonse munathana nacho pa mtanda paja ndinu yemweyo zulo lero ndi kunthawi zonse
@NaomiMoyo-x2r
@NaomiMoyo-x2r Месяц назад
Akuyenela chisamaliro athandizidwe kut azipita kwawo penanso koma limatha kukhala Vuto lamtima akaunikidwe moyenela😢😢😢
@LazarousKasambala
@LazarousKasambala Месяц назад
Too bad koma mulungu ndiwadongosolo amen.
@WenaniMwenda
@WenaniMwenda Месяц назад
Anthu akuvutikatu 😢😢😢
@ChisambaChidzungu
@ChisambaChidzungu Месяц назад
Ambuye akumbukireni bambowa ndi machiritso anu
@GraceLobart
@GraceLobart Месяц назад
Ambuye ndiwabwiño😢😢😢
@ShakiraBiton
@ShakiraBiton Месяц назад
Ambuye oziwa kuchilitsa mkhuzeni mwana wanu ndimkono wamachilitso paikha sangathe🙏🙏
@Oliver-2019
@Oliver-2019 Месяц назад
God help this man to recover from the disease he is suffering from 🙏
@AlinafeMoses
@AlinafeMoses Месяц назад
Chachikulu angopta kwawo ndithu mmm
@austenmalawi
@austenmalawi Месяц назад
EISH Koma mulungu achitileni chifundo
@CatherineMustafa-dq4qm
@CatherineMustafa-dq4qm Месяц назад
Ambuye awakhuze chonde😥
@RhodneyBwa3
@RhodneyBwa3 Месяц назад
Eeeeee zokhuza kwambiri
@Wyson-bo3sp
@Wyson-bo3sp Месяц назад
May the Almighty God heal you in Jesus' name amen.
@MaliamuSikawa
@MaliamuSikawa Месяц назад
Murungu aikirepo dzanja
@NaduMbewe-zz6iw
@NaduMbewe-zz6iw Месяц назад
Penatu umakhala vuto la mtima bambo anganso ankadwala choncho
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Месяц назад
Achibale akutipo chani alipo or ayi Mulungu achitapo kathu
@GiftChimtedza
@GiftChimtedza Месяц назад
eish
@HawaMamo-q2v
@HawaMamo-q2v Месяц назад
Boni kalindo bwa
@edgarmax-pi1bx
@edgarmax-pi1bx Месяц назад
Mukhara bwn madala
@BrightLuciano
@BrightLuciano Месяц назад
So sad
Далее
PHWEDO Plays TRUTH OR DRINK |MADNESS
1:19:01
Просмотров 104 тыс.
MFUMUKAZI COMEDY  SERIES 21/12/2022
27:04
Просмотров 154 тыс.
БЕЛКА РОЖАЕТ? #cat
00:29
Просмотров 308 тыс.
Usauver S09E02   AKAZANU ASOWA
16:28
Просмотров 214 тыс.
The Story of Chrissy Luhanga (41)
31:56
Просмотров 76 тыс.
Raped by my Sister's Husband
19:50
Просмотров 30 тыс.
Grace & Siblings
15:42
Просмотров 5 тыс.
BRENDA KOSAMU, LOST & FEARED DEAD
19:12
Просмотров 33 тыс.
THE COURT..(Malawi )🤔
20:45
Просмотров 235 тыс.
Mayi Nyumwa John akungotupa mutu kosalekeza
23:44
Просмотров 17 тыс.
BELITA, MOTHER AT 13
16:06
Просмотров 22 тыс.