Тёмный

Inu chonde tamuletseni Chapondayu alivulazatu bomali ndi zimene akupangazi mapeto ake 

Malawi Trends TV
Подписаться 47 тыс.
Просмотров 6 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 28   
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 4 месяца назад
More fire Mr chaponda anthu amene akudana nanu zomwe mwayankhula akudya nawo ndalama chilungamo chimapweteka
@jamesgama5489
@jamesgama5489 4 месяца назад
Rev chakwera adazolowera misonkhano ya church ⛪️ musadabwe kuyendayendaku, wayiwala zoti ali mboma.
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 4 месяца назад
Umakwana chaponda all the best
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 4 месяца назад
Katundu ndiameneyu, osati mbuzi nankhumwa ankangoyang'ana zauchitstiru zikuchitika
@jamesgama5489
@jamesgama5489 4 месяца назад
Amene aja tsiku lina adzayitanisa chopereka pa msonkhano kuyiwala kuti ndi msonkhano wa chipani
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 4 месяца назад
😂😂😂😂
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 4 месяца назад
Good Message Mr Chaponda
@DanielHolla-c5y
@DanielHolla-c5y 4 месяца назад
Nice ❤❤❤
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 4 месяца назад
Zakwerayo akhsla mu office azitanimo ngati Pali chomwe akuonamp, kwamteleyo, ndilibudziwayi, koma kivala nyolonyo basi
@FunnyKatchenga
@FunnyKatchenga 4 месяца назад
Kodi iwe mwana wa hule, sindikutchula dzina koma udziziwa wekha. Umangoti ahlomwe ahlomwe, Kodi anakulakwira chani? Umbuli eti? Ngati ulibe cholemba kulibwino kukhala mudzalizedwa nazotu zimenezo be careful.
@MoosaSame
@MoosaSame 4 месяца назад
More fire
@SteveChirwa-ne9nt
@SteveChirwa-ne9nt 4 месяца назад
Zoona Lilongwe to Blantyre pandege/ Lilongwe Mzuzu nde be basi Mangochi chochita kusowa .
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 4 месяца назад
That is what we were lucking the opposition group,,, chaponda 1000000% muuzeni uyu mumutu mwake mwadzaza ukhutukumve what such a president is that one? We are tired of what he is doing,, or even udindowo kodi amayenda choncho? He is misusing our taxes.
@christophergibson72
@christophergibson72 4 месяца назад
Chaponda utibwezele ndalama za chimanga unaba zija sitdaiwale
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 4 месяца назад
Mavuto ali ku Malawi zoona kumangowononga ndalama ndi kuyenda yenda! Mmmmmm President wopanda manyazi uyu.
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 4 месяца назад
Koma ndiye ndi zoona, President ku.angoyenda yenda ngati kuti alibe ntchito mu office, sakuyendetsa boma, koma wayamba campaign chakwera.
@Kenmoney-xp7tz
@Kenmoney-xp7tz 3 месяца назад
Aziyenda timugende bwino
@JabesiLaphion
@JabesiLaphion 4 месяца назад
😢😮😮mbava izi aaaaaa
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 4 месяца назад
Chakwera koma amakhara mu office. Monday to Sunday up and down.Sika wa tomatoes amvekere ndikasegulira .sika wamakaka ndikasegulira
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 4 месяца назад
😂😂😂
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 4 месяца назад
Inde azakhale president ndi iyeyu azabetso,chimanga kukagulitsa kunja.munthu, osaziwa chichewa,ngati ameneyi.azathandidza, amalawi poba, chimanga amalawi tili pa mabvuto kwambili
@MolosonMisitala
@MolosonMisitala 4 месяца назад
Ndiyetu qdzitsekulila ndi mvula yomwe
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 4 месяца назад
😂😂😂😂😂😂
@TchumaKanyemba
@TchumaKanyemba 4 месяца назад
Khaaaaaa
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 4 месяца назад
Mbuzi Za DPP achipondanso akhala bwana chakwera ai zoti chiponda akudyabwino chifukwa cha abwana achakwera sakuona size yake timupatsa ochezanaye msonda katswiri pa ndale angofuna kuchimwitsa munthu pitala ayamukile zaziiiiiii
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 4 месяца назад
Kachimanga uyu bwanji chitsiru chenicheni mbava yeniyeni maizegate man za zii
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 4 месяца назад
Timafuna zimenezo ife pitilizani ntchito yabwino
@rashidadan2533
@rashidadan2533 4 месяца назад
Inshort , Chakwela is coward , as Malawians we want serious president , a president who can care about poor people , A president of vision , President without corruption , Not like this manyaka
Далее
Osamwa Juwisi wa Enjoy!
15:30
Просмотров 61 тыс.
Tisawononge Dziko Chifukwa Cha Mavuto   Bon Kalindo
15:38
BON KALINDO 12 OCTOBER 2024 KUNG’ALURA PA SATURDAY
16:15
Top 9 Ya  Anthu Olemela Kwambiri Kumalawi
8:17
Просмотров 115 тыс.