Тёмный

IWE RICHARD CHIMWENDO BANDA CHISALE SI SIZE YAKO - KWANUNKHA MWAZI KU LILONGWE DPP YAGWEDEKA 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 63 тыс.
Просмотров 8 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

12 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 75   
@PhillipChisanu-k3r
@PhillipChisanu-k3r 2 часа назад
The Blues! The Sky! The Colour of the Colours! 👊💪✊👆👆👆
@AugustineChimaliro-e5i
@AugustineChimaliro-e5i 3 часа назад
Ndipo no ndalama amangopita wonkha kuribeso woyimba ❤❤❤❤❤❤
@isaaczuze
@isaaczuze 3 часа назад
Anthu amenewa sakupasidwatu ndalama ....inuyo anthu amabwela ku misonkhano yanu chifukwa chogawa ndalama
@Pangolinimw
@Pangolinimw Час назад
Inde😂😂😂
@RebeccaChikalenda
@RebeccaChikalenda 2 часа назад
Boma lrooo ❤❤❤❤
@LennieNyirenda-w6p
@LennieNyirenda-w6p 2 часа назад
My vote
@emmanuelchikowi8786
@emmanuelchikowi8786 2 часа назад
Chisale siogulitsa Malala ndimveleni Richard is far far behind with chisale
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 часа назад
Iwe namachende chimwendo uzathawa ziko lino 2025
@uzaleuzale8603
@uzaleuzale8603 2 часа назад
Ine chimwemwe chokha chokha😅
@JosephChingombe-o3i
@JosephChingombe-o3i 2 часа назад
Apm my vote
@PhilimonThegha
@PhilimonThegha 4 часа назад
Chiyembekezo Cha amalawi llove this DPP🎉🎉
@HawahMussah
@HawahMussah 3 часа назад
Zana amuna osachita kuwauza anthu kuti kwenzani manja mwamba okha kufuna kwawo
@isaaczuze
@isaaczuze 4 часа назад
Koditu chimwendo ndi chisilu cha munthu
@MikeSymon-si8dw
@MikeSymon-si8dw 2 часа назад
Boma ili lipweteka anthu 😅😅😅😅😅😅😅😅 anthu onga ngumbi.. . Ntchito zamanja kuchitira umbonii🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥👞👞
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 4 часа назад
Eeeh KOMA Mgona sigawa ma sweets ndi DPP
@PreciousChisale
@PreciousChisale Час назад
Ndipo anthu awa akumabwera okha osati kuwanyamula mmagalimoto ayi DPP ,my vote,2025
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 3 часа назад
Boma ilo 🔥🔥 chikangawa azipsa mtima
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 3 часа назад
Yeé koma zilikotu,, DPP WOYEEEE
@MosesTangwe
@MosesTangwe 3 часа назад
Koma chikhwimbi chawanthu chanyooo😂😂😅 DPP 2025 Boma iloo DPP 🔵💙💙💙🔵💙💙💙🔵
@BettyByson-t4z
@BettyByson-t4z 53 минуты назад
Akamuna wawa apm my vote
@NiccoGama
@NiccoGama 3 часа назад
Boma ilo my vote 🗳 ❤️
@ChisomocaxstonStima
@ChisomocaxstonStima 3 часа назад
Boma koma ili.Dpp woooyeeeee
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 3 часа назад
Ya Allah imvani kulira kwa ana anu tipaseni tsogoleri okomera aliyense maka osaukane Ya Allah🤲🤲
@cjaylucky
@cjaylucky 2 часа назад
AMEEN INSHA ALLAH
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o 4 часа назад
Achimwendo akuziona kukula chimimba chija nde akuziona kukura mwauze my dpp
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 3 часа назад
Chimwendo sakudziwa ndale uja angfuna Amalize Malawi kwasalaku Inshaa Allah Allah afewese
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 3 часа назад
Palibe a kulandila ndalama tu apa mongokumbutsana. Ngona sigawa ma sweet dpp nde kuchimake kumeneku
@TachikoMwanamanga
@TachikoMwanamanga 2 часа назад
Boma ilooooooooooooo❤
@NdaonaSandifolo
@NdaonaSandifolo 2 часа назад
Chokayiwe ngongole amapeleka ndiwolamula osati wotsutsa a dpp adasawuka alibe kanthu
@ElisyIweni
@ElisyIweni 3 часа назад
Chimwendo milomo ngati khumba
@HassanOmar-v2e
@HassanOmar-v2e 3 часа назад
Dpp my vote ❤
@FrankMakulumiza
@FrankMakulumiza 3 часа назад
Akuti ndikuchipinda cha mcp anthu atopa. Awa sanapasidwe ndalama koma okha kubwera osagulidwa ayi.
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l Час назад
Alikoti wa MCP machende Ali juuuuuuu,kaye chimwendo,ndi Azinzakewo,anyera m'pwererendithu
@RAJABSTYLESTYLE-yi1el
@RAJABSTYLESTYLE-yi1el 3 часа назад
Kkkkk chikangawa kuliliko akulila
@EllenChimera
@EllenChimera 3 часа назад
Wa mutu ngati Obama chimwendo waona koma😂😂😂
@SHAIBUSALIMU-l1o
@SHAIBUSALIMU-l1o 3 часа назад
Boma ilo❤
@ChisaleHedgens
@ChisaleHedgens 3 часа назад
Chimwendo machende ako wava mutu wawukuluwo
@PraiseKawerama
@PraiseKawerama 3 часа назад
Chipani ndy ici❤❤😊
@MussaZimba
@MussaZimba Час назад
Kulibetu anyamata woyimba uku ❤❤
@lacksonsiyadi943
@lacksonsiyadi943 3 часа назад
Dpp yabetcha lawyer
@juniortsegula3847
@juniortsegula3847 2 часа назад
Kulibe kugawa ndlamatu uku koma eeee hh kuli nchito chaka chino
@HamzahTwaib
@HamzahTwaib 2 часа назад
Dpp woyeee,, my vote
@isaaczuze
@isaaczuze 3 часа назад
Chimwendo mimba yaikuluyo unali ndani iwe .....umakonza ma radio lelo ukuona ngati wafikapo koma ukunamatu chisilu iwe
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 4 часа назад
WAMUTU NGAT FUWA LAPAUKWATI CHIMWENDO AKANGOONA MUMUONA AKUTHAMANGA ULENDO KU STATE HOUSE KUKANAMIZA CHAKWERA AMVEKERE ADPP KUTSOKHANO WAWO KUDALIBEKO ANTHU, KU LILONGWE PA HOME PANU BWANA , NDIY PAHOME PANUPO MUKUBESAPO DPP IKUSEZA KUMAKUSESANI MAPADZI PA HOME PANU
@Fanzo-h2l
@Fanzo-h2l 57 минут назад
Mcp boma logwa khunyu ngati apule ayamba kugwa khunyu kulibwanji chipañi charha basi DPP MY VOTE
@PhillipLucky
@PhillipLucky 3 часа назад
Mumakwana boma koma limeneli osati zinazija
@MphatsoGeorge
@MphatsoGeorge 4 часа назад
Dpp woyeeeee
@georgesmart3791
@georgesmart3791 Час назад
Koma Anthu atopadi ..Apm +Dpp 2025 boma 🔥
@LuciusScott-h7b
@LuciusScott-h7b 2 часа назад
Kunali munthu kowopsa
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 3 часа назад
😂😂😂😂😂 mpasen madzi chakwera amwe BP isayambiletso
@SolomonBewula
@SolomonBewula Час назад
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 3 часа назад
❤❤❤❤ boma iloo 💙💙💙💙✊
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 2 часа назад
DPP motooooo!🔥
@EdenNgulube
@EdenNgulube Час назад
Apm my vote 💙💙
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika Час назад
❤❤❤❤❤❤❤❤
@AnusaChiwale
@AnusaChiwale Час назад
Dpp my vote
@WatsonMalanga
@WatsonMalanga 2 часа назад
Koma dpp mulungu wakumwamba amaona ndithu nde kuli khwimba la anthu
@chcmzuzudiocese5916
@chcmzuzudiocese5916 26 минут назад
Not that I like dpp ,but its the color for me
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 4 часа назад
Ndizomwe tikufuna ife
@KingsleyJamison
@KingsleyJamison Час назад
Akupepha ngongole kwaomwe alikunja kwa boma
@FladielMwase
@FladielMwase 51 минуту назад
Ndili pambuyo panu dpp
@EstherMalunga-b9j
@EstherMalunga-b9j 3 часа назад
Boma ilo
@BlessingsTchapo
@BlessingsTchapo 2 часа назад
Anthu ngambwingambwi kwao komko
@MathewsMandutu-q9l
@MathewsMandutu-q9l 45 минут назад
Dpp ikukondedwa mmmmm taonani anthu inu
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 25 минут назад
DPP MY vote
@RyanDerSpartan
@RyanDerSpartan 2 часа назад
Umbuli wativuta ku Malawi,,,kufuna kutinamizanso,,,bwanji munachoka m'boma,Malawi wayenera kuyang'ana chisogolo
@SolomonBewula
@SolomonBewula Час назад
Mbuzi
@BrightZionga
@BrightZionga Час назад
Bwanji MCP idabweleranso mmboma italuza 1994
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 23 минуты назад
Chimwendo walimumazi
@MichaelBefore
@MichaelBefore 2 часа назад
Eeeeee km DPP oo yes
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 3 часа назад
Mcp yatha
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy Час назад
Ndipo no more kulamulilanso kumalawi chipani chakhadza ichi
@ChimwemweZgambo
@ChimwemweZgambo 3 часа назад
MCP my vote
Далее
这到底是怎么做到的 #路飞#海贼王
00:10
Просмотров 3,9 млн
RICHARD CHIMWENDO BANDA KUFIKA KU LUNZU LERO
1:58
Просмотров 2,4 тыс.
这到底是怎么做到的 #路飞#海贼王
00:10
Просмотров 3,9 млн