Тёмный

SITINANENE KUTI CHAKWERA WAMWALIRA - LIMPOPO FM komanso BAKILI MULUZI TV aikana nkhani ija. 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 63 тыс.
Просмотров 15 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

12 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 102   
@MosesDicostar
@MosesDicostar 13 часов назад
Limpopo fm and bakili muluzi tv number one in Malawi
@AbdullahAllie-k9l
@AbdullahAllie-k9l 13 часов назад
Amene akt limpo mpo inalengeza kt achakwera amwalira aponye umboni osat kumatukwana.
@AgnesMatola
@AgnesMatola 13 часов назад
Chimwendo ndiwa usilu akutiwonongela dziko lathu😢
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 9 часов назад
Ali Limpopo ndinu a boza
@AaliyaKalembo
@AaliyaKalembo 8 часов назад
Zoti chakwela wamwalira sanene Koma wadwala ali garden city. Ndipo apezeka ku bt Izi zomwe ananena.
@georgesmart3791
@georgesmart3791 3 часа назад
More fire Limpopo fm 🔥 🔥
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl 14 часов назад
Bvuto ndiloti onse a mcp mitu sikugwira aii president akudwala ndipo izi ndizoona that's why mnaona dzuro a Richard komanso nkukuyu analiko okha ku Rally ya dzuro ija, kodi amalawi enafe tikanagonabe mpaka lero dzukani sinthawi yogona inu amalawi
@jameschiwanga
@jameschiwanga 6 часов назад
@@DalitsoPhiri-sq5nl Ife tikudya nsimatu nde odya nsima NDI odya chiteze amene Mutu wake sukugwira ndiuti
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl 6 часов назад
@@jameschiwanga ndi chifukwa tikumati mitu sikugwira do you think anthuwo kudya chitedze ndi ntendere kuganidza mopelewelatu ankolo kumeneko
@MulowokaBlessings
@MulowokaBlessings 12 часов назад
Ndiwe opusa wa iwe Limpopo FM sukukwanilanso kugwira ntchito iyo komanso umangidwa kupusa bati
@isaaczuze
@isaaczuze 14 часов назад
Lipompo fm woyee iyi ndi radio imene timaikonda ife
@PhillipChisanu-k3r
@PhillipChisanu-k3r 11 часов назад
Uthenga udali oti akudwala osat wamwaliraai,paja enatu amamvera mphunotu,ngat ineyo sindingasiye kumvera B-tv komanso Limpopo Fm
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 10 часов назад
Dzikomo kwambiri Limpopo fm muchimve kuti timakunyadirani kwambiri Kubwera kwa inu pa Malawi palibe chisinsi kani akungozikola kola okha kusowa chogwirika choti angakambe kwa a Malawi Inu akuti a Kunkuyu komanso ati a Chimunthu Banda chitani manyanzi sitimakusowani ndi ma rally anu ongotukwana ndikunena anthu mm'alo mowanamiza kachikena aMalawi enanso otemberedwa kt azakuvitereni mfundo za chitukuko, mukhalike Ife Limpomp fm, Bakili Muluzi tv, the DC ndi onse amaimira a Malawi pa chilungamo tili nawo ngangangaaaaa bco akuulura nyatsi zobisika
@jameschiwanga
@jameschiwanga 6 часов назад
@@KingDavedNkhata muziti amayimila DPP osati amalawi osasokoneza pakati pa DPP NDI amalawi amalawi it's everyone pamene DPP it's a specific party nde anthuwo amayimila DPP as party not as a country.
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 10 часов назад
Sananenedi choncho anati sakupeza bwinooooo
@MastonWatson-g7g
@MastonWatson-g7g 14 часов назад
Chakwera ndi bwana? mwinatu wa ku nyumba kwako, mbava ngati ameneyo iwenso suganiza bwino.
@FrankMankhokwe
@FrankMankhokwe 12 часов назад
Wa Limpopo ndi gulung'ande akuyikana bwanji nkhaniyi Wadziwa kuti ndiwabodza
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 3 часа назад
Zoonadi Limpopo ifetimakunyadilani ulemu wanu
@DaudRashid-sp3sk
@DaudRashid-sp3sk 13 часов назад
Asiyeni agalu amenewa amene tinavela ife mau oti chakwera wamwalira sitinauve ai
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 3 часа назад
Inusananene kuti chakwera wamwaira ananena kuti chakwera akudwala kumavesesa A Richard
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 9 часов назад
Chakwera mpaka 2045 woooo ganyu afika kukutopesani
@MynessChirwa
@MynessChirwa 13 часов назад
@leahkasiwa5033
@leahkasiwa5033 4 часа назад
Ngakhale lipompo ndi bakili muluzi anati a pre amwalira inu mumati .Mesa anamwaliradi achita ku bwelera kwa akufa 😂😂😂😂
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f 7 часов назад
Agalu inu, mesa mumati ali ku garden city.
@SteynMaduka
@SteynMaduka 7 часов назад
Akulepheratu kuishura ladio yomwe imanenayo koma chifukwa limpopo ndi bakili muluzi TV samapuma nayo bwino that's why mmmm ndale za ku Malawi zotukwanana
@mollymasangano473
@mollymasangano473 9 часов назад
My Radio Limpopo .FM my TELEVISION Bakili Muluzi TV 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅 simunanene zomwe akunenazo A MCP iiiiiii tatopananu .😢
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 7 часов назад
ukudwala ndiwe ndipo ukunama iwe aliku garden city kuti 😂😂😂😂😂😂
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 6 часов назад
Sizachilendo ngakhale Peter munthalika anafunsapo pa nsonkhano kuti mukuwona mtembo pano? Mesa nayenso anatchukitsidwa kuti wamwalira? Zikuwawa pati lero?
@RajabShahida
@RajabShahida 11 часов назад
Limpopo fm bakili muluzi tv number 1
@jameschiwanga
@jameschiwanga 6 часов назад
@@RajabShahida awo si ma TV inu ma Facebook and RU-vid channels osasokoneza
@muhammadjuma3317
@muhammadjuma3317 9 часов назад
Nokha nokha mukungodzikola kola kola . Anthu asiya kukukhulupilirani inu
@RuthUnderson
@RuthUnderson 7 часов назад
Amene akuti limpompo idanena kuti chakwela wamwalira ameneyo ndiye kuti amamvera kunyelo kusukulunso nkalasi samakhoza limpopo idati akudwala zoti wamwalila adati umboni umenewo alibe anthu omvera kunyeloinu ngati achina kunkuyu pofunika achakwela akutumizeni kuchipatala mukalandile chithandizo chavuto lankhutu
@jameschiwanga
@jameschiwanga 6 часов назад
@@RuthUnderson nde or zoti akudwalazo ndizaboza zokha zokha zo Mesa alimpopo or what ever you call it amanena Kut chakwera akudwala ndipo mwakaya Kaya Moti Ali Ku chipatala cha garden city Ku south Africa chonsecho zaboza inu or mtanyiwayo he is there just to let chakwera down but let me mind you come September 2025 chakwera will still be president mark my words.
@RuthUnderson
@RuthUnderson 6 часов назад
@@jameschiwanga no one knows about chakwera peter or udf cames back 2025 all of theme are stupit
@PatriciaAlomwe-oz8wc
@PatriciaAlomwe-oz8wc 14 часов назад
MCP ndi abuluzi okhaokha akapolo magaz anthu anawapha aja akuwayenda maganizo muthawa ziko lokhala lanu muziona
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 9 часов назад
Zangokuvutani chabe mesa mumati apita naye ku garden city Ali mwakayakaya
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 9 часов назад
A Limpopo manyaz akugwilani ndipo mwayaluka anthu ambiri sakukhulupililaniso maboza thooo
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 14 часов назад
❤❤❤❤❤❤
@gladyschisomo4324
@gladyschisomo4324 10 часов назад
Ngakhale kubwezela kuli keamwini Yehova koma achakwela adwale ndithu mpaka alape mizimu yaanthu 9 it's not easy magazi awo akumuzunguza mutu chaona nzako chapita mawa chili kwa iwe imfa imapita palipose
@ChiwaloWilliams
@ChiwaloWilliams 13 часов назад
Kani Limpopo FM ndi Bakili TV amamvera aliyense ndi ku Boma komwe zilibwino tadziwa
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi 11 часов назад
Mcp yatikwana osalimbana ndi Limpopo koma yavuta ndi mizimu ya anthu 9
@MagretBula
@MagretBula 4 часа назад
Aguness replies to u❤
@AndrewjemesJemes
@AndrewjemesJemes 11 часов назад
Inuyo alipopo FM ni bakili muluzi tv ni mbambande ndinu chiphinjo ku boma
@StanelyPhiri-kg1ix
@StanelyPhiri-kg1ix 13 часов назад
Limpopo Fm ndiyamakape okhaokha
@thomaswyson-e2q
@thomaswyson-e2q 12 часов назад
Kape ameneyi samamvela limpopo ngat amamvela amamvela mwamantha
@ZephMbeleswa
@ZephMbeleswa 13 часов назад
Ngati mumaima ndi ovutika inuyo bwanji osamapita kumakawathandiza bwanji 😂😂😂😂
@KnaanSiyan
@KnaanSiyan 10 часов назад
Limpopo fm is devil slayer
@captainmdima1102
@captainmdima1102 7 часов назад
Aaaa mukana chani ndinu a boza kwambir mwayamba kukana nde ku south Africa anapita lit?
@jameschiwanga
@jameschiwanga 6 часов назад
@@captainmdima1102 eti eti anthu adpp awa Mitu yawo ndiyobalalika
@WilsonImedi
@WilsonImedi 13 часов назад
Tiyeni tsatukwanizane a MALAWI tizi ngomvera izi tisavutike m"maganizo taonanani panopa munthu wamoyo .Timve ziti
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 10 часов назад
Ndipo zoonadi simunanene kut chikangawa wamwalila
@jameschiwanga
@jameschiwanga 13 часов назад
Izi NDI mbuzidi izi mwaona akuti Ali Ku chipatala Ku garden city Koma munthu akumenya golf uko or Ku south Africa sanapiteko
@thomaswyson-e2q
@thomaswyson-e2q 12 часов назад
Iwe mbuz ndiamako machendeako
@jameschiwanga
@jameschiwanga 12 часов назад
@@thomaswyson-e2q zikomo 👍
@gomezthera535
@gomezthera535 9 часов назад
Akuyesa anthu amadya boza anthu sangazakhulupilileso limpopo fm ndi mbuzi za anthu
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o 13 часов назад
Chakwera amwaliredi mkazi wake uja sakumusamala😂😂😂😂
@muhammadjuma3317
@muhammadjuma3317 9 часов назад
Sitidzakhulupiliranso wa Limpopo komanso wa Bakili muluzi. Budzi Inu musamatinamize ife mwamva .
@LaylaPhiriMuhammad
@LaylaPhiriMuhammad 8 часов назад
Mmmmmh bro anangonena za matenda osati maliro
@FrankMankhokwe
@FrankMankhokwe 12 часов назад
Iwe wa Limpopo poti unaona ndi diso lako lapamphumi kuti anali serious ya kayakaya tumiza video yaku garden city clinic ko Ukalephera ndiye kuti ndiwe satana
@AlickjoiceMatchipisa
@AlickjoiceMatchipisa 13 часов назад
Mcp inali plan kuti wa limpompo akalakhulapo amuyipise kuti amanena bodza cholinga akamalakhula zochitika aziti ndi bodza
@JosephChiccoNkhulande
@JosephChiccoNkhulande 11 часов назад
Munanena kuti Ali. Ku Garden City komanso munati wafa ziwalo anthu aboza inu nanga anapitapo ku Garden City anthu opanda manyazi inu
@gladyschisomo4324
@gladyschisomo4324 10 часов назад
Limpopo imakhala ndi information yose zitha kutheka Kuti anafadi ziwalo zina
@DoricaGoweka
@DoricaGoweka 3 часа назад
Game on 😅😅😅😅
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 12 часов назад
ZAWAKULIRA ANA A CHIKANGAWA MITU YAO SIKUGWIRA AMWALIRABE CHIKANGAWAYO AFUNE ASAFUNE MIZIMU YA ANTHU AMBIRI IKUFUULA KUNSI KWA NTHAKA
@DixonChimanya
@DixonChimanya 13 часов назад
Mcp yokupha Adapha chilima pifuna kuti adzaimiletso 2025 kunyoza gwirizano Chifukwa adali chiphijo cha chakwera ndi mcp
@thomasphiri-o3p
@thomasphiri-o3p 6 часов назад
minyelo yanu inu ndinu aboza chakwela sakuchoka
@ernestsanjira7859
@ernestsanjira7859 14 часов назад
🥰🥰🥰🥰🥰🥰🥰🥰🥰
@LacksonPhiri-z2t
@LacksonPhiri-z2t 14 часов назад
Yy uli cha bodza.
@DysonTummiesSajiwa
@DysonTummiesSajiwa 12 часов назад
Mukadakhala ma dolo simukamadabisala makape inu dolo amayima pa mbalambanda osat kumakhala kuphanga zitsilu za anthu
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh 11 часов назад
Zoonadi simudanene kut wamwalira kma mudat adwala,onama ndio a mcp wo
@RebeccaChikalenda
@RebeccaChikalenda 12 часов назад
Bwanji anwariredi ameneyu
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 8 часов назад
Kodi lero zawawa olo anakafa alibe ntchito munthu oyipa mtima
@SandraBanda-hd1li
@SandraBanda-hd1li 14 часов назад
Pankonzo. Pako. Iweyo,.. back. bwanji... ukudzitenga ....... ngati.. iweyo.... chitsilu . eti
@andiwochishadreck3753
@andiwochishadreck3753 14 часов назад
Iweso panyopako
@JoeBanda-gk4ss
@JoeBanda-gk4ss 13 часов назад
Beat tv❤
@FrankMankhokwe
@FrankMankhokwe 12 часов назад
Uzakhumudwa 2025 utagwa chagada
@AchimkokoChigonambango
@AchimkokoChigonambango 13 часов назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣AKumva kuwawa yekha Ena akusewelesana mmalisani
@RichardWilliam-t7w
@RichardWilliam-t7w 14 часов назад
Ndinu madolo mesa ndy bwerani poyera kaa osamabisala kaaa
@YaqoobStandwell
@YaqoobStandwell 13 часов назад
Chimwendo ndiye saziwa kuyankhula mbuli kwambuli ndiye chimwendo omangochemelela mcp akuziwa kut palibe chimene akuchita akut kufuna akuwoneka wabwino tamangokudya ndalamazo koma azizindikila kut one is one day mulungu ndiamene akakulangen inuyo a mcp nose
@James-v8v8d
@James-v8v8d 14 часов назад
Ufiti
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o 13 часов назад
Bwanawakoyo pachinyero pake
@KnaanSiyan
@KnaanSiyan 10 часов назад
Oyipa amavutika yekha
@James-v8v8d
@James-v8v8d 14 часов назад
Bodza lakolo
@YaqoobStandwell
@YaqoobStandwell 13 часов назад
Aaaaaaaaaa mcp palibe amene akuifuna or muone mmene anasangalila amalawi no one need mcp and kungomwalila kuzakhala ma patty akuziwa a mcp kut amalawi sakwafuna that's why akulimbana ndi limpopo
@LawrencePhiri-sf6nl
@LawrencePhiri-sf6nl 14 часов назад
Pankholo panu a limpopo fm mesa mmati bwana amwalira lero mukukana pankodzo panu ndithu a limpopo fm ndi ntanyowa wanuyu
@stevovosalimu5443
@stevovosalimu5443 14 часов назад
Kod iwe wamva ndindan kape iwe
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 14 часов назад
Wachamba ingobani ndaramaso limozi nichikangawa
@JudithKatungwe
@JudithKatungwe 14 часов назад
Unamvera kuti zimenezo??? Sanakambe zokufa
@AaliyaKalembo
@AaliyaKalembo 8 часов назад
Ndipo sanakambe kuti wafa koma wadwala
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 13 часов назад
Aaaa OTHANDIZA SALEGEZA NDIWEWADZODZA INU MWAYAMBASO KUKANASO AAAAAAA
@FuxyMwale
@FuxyMwale 13 часов назад
Mbuzi inu ndibodza
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 12 часов назад
Auze amvetse a Mcp
@ChisomoSaiti
@ChisomoSaiti 13 часов назад
Tonse Kwa mgona tikakumanae
@FlorenceKamtambo
@FlorenceKamtambo 11 часов назад
Chitani manyazi
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 7 часов назад
achitsilu inu
@andiwochishadreck3753
@andiwochishadreck3753 14 часов назад
Apenga
@GibsonBankha
@GibsonBankha 14 часов назад
Citsilu iwe akudwala ndimako
@EmmanuelMphande-f4l
@EmmanuelMphande-f4l 13 часов назад
Ukuyankhula bwanji mwana wahule iwe ana amutchile inu musativutise bambo anu simukuwaziwa mwina ninali ine poti mayi ako ndihule weniweni
@EmmanuelMphande-f4l
@EmmanuelMphande-f4l 13 часов назад
Chimwendo pambina pake
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx 10 часов назад
Vitsilu
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi 9 часов назад
❤❤❤❤❤
Далее
ЧТО ВЫРОСЛО ОТ КОКА КОЛЫ😱#shorts
00:26