Why is it that such leader are not given support? And why such advised are politicised insteady of taking them as it is and put into use. It won't Kapito getting appraisal rather those implement the advice.
A Kapito izi mukanakhala Kuti munayamba chonchi poyamba atakupatsani udindo Ku Cama, bwenzi nditakupangani salute Koma Ai udindo wanu ,mumangodya osaganizira the poor Malawian as poor consumers. SHAME, mukufuna udindo winanso? People have been criticizing you for not assisting them as per your responsibility to Malawians.
Eeeh ok hp u r saying the fact , kma ndie zosaenda , apa nkhani yakula anthu azindilambila pa chifukwa choti ine ndi wankulu than enawa zavuta. Vuto ndi lomweri nsogoleri wadyela osakonda ziko lake
Zaziiiiii Mesa malawi ankauzidwa kuti MCP dizinthu Koma okha Amafuna dala nde mukufuna DPP izitani? Asiyeni a DPP azipuma... Mesa mumati asogoleri aDPP samatha kulankhula nde mukufuna chani?,,, mpando wa u president anausiya mopanda kukangana ndi munthu kuutengaso azatenga mosakangana ndi munthu.... Zomwe mukukamba zikunveka zanzeru Koma musalimbane ndi DPP, am not a politician but,, vuto si DPP or MCP Koma tokha amalawi timafuna kusintha now kusintha takuona.. Then next choice we shall make it with real sense.
Panopa ndawamvesa a DPP chimene amakhalira chete President uyu ndi wamagazi ifeyo tikuziwonela kunja koma anzathuwa akuziwonela pafupi President uyu si munthu wabwino a DPP akhalebe chete mpaka campaign iyambe
Mr kapito inuyo ndi a bodza nthawi ya dpp mumapanga ma demo Koma pano zinthu zikulakwikwa mwangokhala chete chifukwa Mukudya nawo ndalama, chotsani kaye chisoso chili diso lanu musanayambwe mwawona chili mwa zanu