Watching from Capetown,we are together brethren.chilim is one of the best freedom fighter ever in the history of our country.he will be remembered in the country history.
Mwaonatu ngati ndi munthu obadwa mwa munthu yemwe unachita zimenezi,uchite manyazi ndipo usiku wa lero tulo sutinunkha 😅😅 unapha thupi,koma nzimu is still alive rest well SKC
Pemphero ndi chida choopsa kwambiri. Kuteroko kuletsa mapempheroko ndi mantha komanso kusautsika. Ichi ndichizindikiro choti anthu omwe adakhersa mwazi umenewu sakugona tulo, akusowa mtendere. The good thing is that the spirit of SKC is still with us, and he will not rest until justice for his death and the other 9 shall prevail. Rest in peace all the departed souls of 10th june 2024.