There's sense in thus speech This is what we call repentance It's up to yuo to accept but to him as far as this speech is concern a pule athu alapa Let's accept him 🙏🙏🙏
Everything is suspicious with chikangawa death. We strongly wonder why govt is shutting away people from speaking about death. What ever you speak is different from what you do, we are mostly intimidated and scared of death every moment but we have courage because we shall surely die by any means.
Ok nanga bwanji ngat tikulila shonshi Ena asamalire nawosso munkuwaresa bwanji pot tose ndi amalawi nkumanga andu nkuwasanka andu nkomwe ankulilla bwanj km tose ndi amalawi ndege yinangwa bwanji nanga 5haws munali kt ashankwela ankueononga Malawi live in the sauth Africa estan cap what's up number I will dor so I promise ✌️🤛✌️🤛🤟👌
Mukadati mupangitse nsonkhanowu musadaphe a Chilima ndi anthu 10 ena aja kuchikangawa kuja Mulungu akadakondwa nanu kobasi, koma apa mukumutola mulungu kobasi,, nde muwonatu exposure yakeyo,,mudayiwala president kuwadziwitsa a malawi kuti mwagula mifiti 4000 yoti mugawe kwa zifwAmba zanu zomwe zikgale zikupha anthu mmalawi before 2025 general elections,komanso mudayiwala kudzitsa a Malawi kuti zifwanba 8 zomwe mudazituma kuti zikafunefune ndi kupha a comrade Ntanyiwa a Limpopo fm komaso host wa bakili muuluzi tv ku South Africa zagwidwa pa beit bridge 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 koma zimene amachita Mulungu😅😅😅😅😅😅😅 zifwamba zotumidwa ndi Malawi Chikangawa party zagwidwa,,God has just started to expose you period
Sir His Excllence die for all malawians .as your sacrifice against the Europeans who order you to devaluation the Malawi kwacha so that your people inalawi die cos of fear and troubles of the mind and heart. The deceivers but don't say that "@ Mufera mbendera .? Mbendera yo ndi anthu.? Mbenderayo imadandaula inuyo mukamadulutsa katundu?
Mwaiwala za cyber crime ,anthu akungomangidwa apa poyankhula maganizo awo without kupwanya katundu wamunthu,, auzitseni a police anuwo ndi nduna zanu zozinva more Malawian than ena