Tachipheni chi Yudas Chakwera cho, chitsiruu chikupangapo chani? wamupha si ndi iyeyo Chifukwa cha nsanje fisi ameneyo nkhope yake ngati mzukwa,muchithamangitse ku Malawiko
pali mau oti palibe ochita choipa azakhale moyo wake osalangidwa onse apanga izi i decrear kut Juses azuke and pay punshiment to those who take hand accordingly I pray to Jeaus to bring another person who will fullfi ma plan a Yesu pa ana ake death to the life opresser
Ndakhumudwa ine dzulo ndimayankhula ndi anthu kumudzi akundyankha ali musamanene ZA chilima akumangani ine eshhh akuti ndipoakuti ku Malawi kwavuta chakwera must go
Ndi zinthu zopweteka kwambiri, koma chofunika ndi kuvomeleza komanso kuzisiya zonse mmanja mwa mulungu. Chifukwa tisaiwale kt mulungu amakondwera ndi imfa ya munthu olungama. Koma tsoka Kwa iye emwe akakamila machimo nadzafa ali chichimwileni. Chifukwa mulungu sakondwera ndi imfa ya munthu ochimwa. Tsoka Kwa iye adzetsa imfa Kwa munthu osalakwa , komanso nalora kufa asadalape tchimolo. Mizimu ya anthu onse omwe adafa pangoziyi yiuse mu mtendere osatha. Ndipo mulungu apukute misonzi ya abale komanso amalawi tonse omwe tikulira pa imfa imeneyi. Mulungu ndiwachikondi nthawi zonse
I think we should be objective here. Have we considered the role that the pilots contributed? According to the UDF commander, he said the lady had 700 flying hours. That is not a lot and she may have been fatigued with the back and forth. Don't discount pilot error especially when the weather is not good. Let's wait for the inquiry
Ndipo satana chakwera akadakhala wina momwe anthu akulirira akanatula pansi udindo ndi nduna zake zonse lusifar kunamizira ubusa, saulos may your soul rest in peace, we shall remember you, koma Mulungu odziwa kuyankha ayankheni a malawi, pa kulira kwao LORD you are consumin fire please Lord consume every evil in Malawi's government
Hiloma tizimulirabe PA nkhani yamatumizidwe a ndalama kuno ku South Africa Airtel money ndiyachangu kwa Ife anthu tili ku South Africa adatikodzera tsogolo lowala lija 😢😢😢