Ndi amozi , usi ndi wa mcp ameneyo munthu winaso oipa pa ziko pano. Ku utm Michael usi anangobisalirako ku utm chifukwa amaziwa kuti ilibe pic yabwino ku ntundu wa amalawi, tingoti ndi ochenjela kwambili.
A usi tsekani makutu anu muva zambiri kuchokela ku anthu osiyanasiyana paja bible Ku miyambo limati chitsiru chifunafuna zeru koma osayipeza koma milomo ya zeru impulumutsa iye. Chonde endetsani udindowo motsogozedwa ndi mulungu was zatheka bwanji
Ufune usafune using ndi vice president iwe Cadet ulongolola utopa chifukwa ukungonaniza chabe choona akudziwa ndi mulungu koma ngati uli ndi umboni oposa mulungu kalankhula koma ngati ulibe umboni okwanila Kuala chete ungachimwe pa maso pa mulungu
Dr usi ,welcome you have a lot to do at a short period,study Bingu politics before candidacy which led him to be elected to be president, people will watch your practices very carefully.And learn how good was Saulos.wish you good Long live.
Akuphipilitsa za imfa ya achilima kokhonza ma program okumupha chilim utsi yo analipo akuziwapo kanthu nagati amqfuna kusankua munthu ochokera ku UTM ndikumuyika ku MEC nanga sipamenepo mgwirizano ukanakhala ukupitilirabe
Brian ndi azinzakowo ndinu agalu nonse, muli pamenepo kuseka uku mukukambilana zanu zapamtumbozo, inu moti simukuona kut iyi ndi game plan kut imva ya Chilima mbali foul play kuti napamtumbo wako Manganya wapha nawo Chilima😭😭😭🤚🤚
Komanso malangizo kwa usi,,alembe asilikali achitetezo ambili owateteza otherwise sitifunanso kulira popano,ndege ukamakwela pls make sure pls ,n akakupasa ndege yoti uyendele paulendo make sure employee 5000 asilikali n also they mct gurd 5 days bfr ulendo
Inu mukamati president mukunena chakwela yo ife kuna tilibe president ayi tilindi galu chakwela ndi galu dzikoli lalowa ma masewela latha basi paka manganya inu koma mukuti ganidzila ku malawi kuno mulungu chonde tithandidzeni kuno kumalawi tili ndi ophudzila ambili ambili koma panopa dzikoli likuyendesedwa nimbuli chonde mulungu tikakhala kuti ife ananu mulungu
What did he do to try to help chilima as he was his vise when the search was obviously being handled poorly. Anakayesesa pa yekha to demand better response.not to be trusted, Njoka ya mitu iwiri.
Anangokhala chete osalunkhula kalikonse. Kodi kusangidwa kwa Michael ussi asangidwa kuchokera ku mcp or utm? Nanga mgwirizano udakalipobe? A kuti Dr ussi anachosedwa ku utm nanga asangidwa kuchipani chiti?