Тёмный
No video :(

Kumangidwa Kwa Monika Chakwera Ndi Mwana wawo Nick ''MPHEKESERA'' 

Hanifa Mw
Подписаться 70 тыс.
Просмотров 34 тыс.
50% 1

MPHEKESERA ZOWAMANGA A MONIKA CHAKWERA ZICHOSETSA NTCHITO A CHIZUMA
Mkulu wa nthambi ya Anti-Corruption Bureau (ACB) a Martha Chizuma asanachotsedwe ntchito, mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera anali atamva mphekesera zomwe zimanena kuti nthambi ya ACB ikufuna kumanga akazi awo, a Monika Chakwera ndipo izi zinawatutumusa. A Chakwera anamva nkhani imeneyi kuchokera kwa munthu wina wamkulu wogwira ntchito m’boma ndipo mphekeserazi zimanenanso kuti mwana wamkulu wa a Chakwera, Nick amangidwanso limodzi ndi mayi ake pomuganizira kuti akuchita zinthu za katangale komanso ziphuphu. Izi zinadza pamene zikumnvekanso kuti nthambi ya ACB inali ikumaliza kafukufuku wake wokhudza kuphwanya malamulo pa ntchito kwa mlembi wa mtsogoleri ndi nduna a Colleen Zamba komanso mkulu wakale woyimira boma pa milandu a Steve Kayuni.

Опубликовано:

 

7 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 34   
@jimmyzgambo9928
@jimmyzgambo9928 Год назад
He don't think , mbuzi
@chitimbethegreat8560
@chitimbethegreat8560 Год назад
Kodi akulu mutu wa nkhani mwaikawo zikugwirizana bwanji ndi zomwe mukunenazo nkhani zanu zimabowa chifukwa mumasephanisa simukamba zogwirizana ndi head line ya nkhani komanso simumatiwerengera bwino
@jimmyzgambo9928
@jimmyzgambo9928 Год назад
Chakwera ndi mbuzi ndipo ndi galu weniweni
@isaacmussa2942
@isaacmussa2942 Год назад
Chakwera akubisa mbava zizakezi
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 5 месяцев назад
Ayambe ndi chakwerayo
@gregorykandinda5546
@gregorykandinda5546 Год назад
amangeni awo onse ndi mbamva koopya
@moyowrobert3331
@moyowrobert3331 Год назад
Kkkkkkk chakwera akuziwa Kuti amumanga ndiokumba
@collinsassenga3711
@collinsassenga3711 Год назад
Ndewu ya aniwake savulira malaya, ziyakhulo 16 koma kumadana, zikanakhala 100 ngat mayiko ena kudakakhala chipwilikiti. Malawi imodzi dziko limodzi, tilemekezane tikondane.
@elizamaster2168
@elizamaster2168 Год назад
Mumaika mutu wakhan km mumafotokoza zosemphana nd mutu wakhan zinenan chlungamo Cha mutu wanu wakhan womwe mwatika
@jescarjimmy7537
@jescarjimmy7537 Год назад
Mitu ya nkhani imene umabweretsa iwe ndi yotsempha ndi nkhani ili nkati mwa program yako ndiwe galu yamunthu wamva iwe
@hamdanmasuku4800
@hamdanmasuku4800 Год назад
Inets ndnanena kale kkk
@mandamandamanda2208
@mandamandamanda2208 Год назад
Ndicho chifukwa chake Martha chizuma akuvutika chifukwa cha umbava WA president ndi banja lake apitirize kulifufuza banja LA president Linakhala PA mpando kuti azitibera misonkho yathu a Malawi wake up malawi
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 5 месяцев назад
Nthawi yawo iyi koma boma lawo likadzatula pansi udindo olamula onse adzamangidwa ndikuwalanda chuma chawo chonse. Mkazi wa president kusamangidwa iyeyo mndani? Mufune ,musafune koma banja la chakwela lonse lidzayankha milandu yosiyanasiyana.
@nkhwalamkwala6483
@nkhwalamkwala6483 Год назад
Tambwali iwe
@Mary-hx9fc
@Mary-hx9fc Год назад
Zoosiyana nkhanizi cholima tisegule
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Год назад
Za ziiii zeni zeni
@REDSKELETON1
@REDSKELETON1 Год назад
😂
@jahiemmusa8796
@jahiemmusa8796 Год назад
wasiyeni kuti agwile ntchito yayo bwino
@cadohjabu5565
@cadohjabu5565 Год назад
zoona koma Za chilima Osati zimenezi Anthu inu Muziopa Mulungu
@collinsassenga3711
@collinsassenga3711 Год назад
Zoona
@joycegondwe9560
@joycegondwe9560 Год назад
Tamanenani zoona Bodza
@chawanangwamkandawire5850
@chawanangwamkandawire5850 Год назад
MABODZA
@cadohjabu5565
@cadohjabu5565 Год назад
Akupatsani Ndalama
@chawanangwamkandawire5850
@chawanangwamkandawire5850 Год назад
@@cadohjabu5565 funsani apanga video clip wo, energy + time + resources spent pa ncito imeneyo nkumati phindu lake nchani ?
@robsontyg3928
@robsontyg3928 Год назад
Machende abambo ako wanva mbuzi iwe eti
@abduljafari7387
@abduljafari7387 Год назад
Akulu chakunyasani ndi Chiyani pamenepa
@hanifamw
@hanifamw Год назад
@@abduljafari7387 lol et et ndalakwaso chani
@eunicemoyo6024
@eunicemoyo6024 Год назад
@@hanifamw eshhiii kom zinazi zomwe zi mpakana ku madzitu kwanaso wekha, Munthu ngt sizinakusangalase umangolambalala ku mbali 🙄🙄🙄 ishall
@jumbradoone4164
@jumbradoone4164 Год назад
Koma muli ndi umunthu? Ndiyekuti nkhaniyi itha kukhala yowona nanga amuchotselanji ntchito mwa phuma.
@robsontyg3928
@robsontyg3928 Год назад
@@jumbradoone4164 nkhani yowona wakuza ndani kuti ndiyowona usamakhala ndi mtima wa nsanje inu anthu akumwela chimene ndi umfiti ndi nsanje, mudzikalimba ndi Peter munthalika nda zake amene wakubelani ma billions kwacha kumaso kukuphelani ma albino 48 in 5 years ya ulamulilo wake
Далее
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Просмотров 50 тыс.
Китайка Шрек поймал Зайца😂😆
00:20
Ching'aning'ani comedy, ft Ngiringande
6:53
Просмотров 309 тыс.
Oimba omwe ananyozapo Bushiri
13:06
Просмотров 483 тыс.
CRUISE 5 WITH MOSE WA PA PHIRI LA BUNDA
1:14:37
Просмотров 109 тыс.
Mkangano Wa Azikazi Asidik Mia Fatra Ndi Abida Mia
10:07
LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
56:54
Просмотров 142 тыс.