Тёмный
No video :(

KUYANKHULA KWA MICHAEL USI LERO KU BLANTYRE PAKAMEZA | 

DZIWE TV
Подписаться 29 тыс.
Просмотров 9 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

29 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 156   
@SolokingChimzy-yt7dj
@SolokingChimzy-yt7dj Месяц назад
Ndaona ma comments ndikanakonda ngat Boma akhaleko ndi nthaw yowelenga ndipomwe adziwe kut Bomali Dziko lonse siliwafuna
@VungaQueen
@VungaQueen Месяц назад
Ndipo aziwawerengadi Pali olifuna bomali achoke basi
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад
Iwe oipa kwambili matako ako manganya mthira kuwili iwe palibe chomwe ungawauze amalawi palibe
@MosesKalenge
@MosesKalenge Месяц назад
Manganya Yuda amwenee
@user-fh7sd6gp3f
@user-fh7sd6gp3f Месяц назад
Bakili ananena zowona kuti a Malawi sitichedwa kuyiwala. Ndiye kuyimbira m'manja zitizoo
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 Месяц назад
Eti ndipo amalawi timagopita kulikose akudya ndi ena aaaa ine kma Malawi si womufera wallah aaaaaa
@HoseKatsekera
@HoseKatsekera Месяц назад
udzinamiza mbuzi zizakozo ife ay,pa malilo paja udatani kulankhula mbuz iwe?
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb Месяц назад
chilima mzimu wako uuse mmutende tima kuwawa ife
@user-ke4dk2io6q
@user-ke4dk2io6q Месяц назад
Amanganya ngati wakhuta kagoneni ndirande mumadziwa? Usamale ukafuse brown mpinganjira
@user-xo8ms5wh2s
@user-xo8ms5wh2s Месяц назад
Iwee ndiye satana weni weni mukungoona kubvutika mwakwera ypkuphwa mateyala lakhulani pano nthawi yoti mulakhule ndi tomweyino
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em Месяц назад
Tidzaiwala bwanji chilima, ife tikukanika kukuiwala chilima, mzimu wanu uziutsa mu mtendere SKC
@IanAllstal
@IanAllstal Месяц назад
Riooooo Rioooooh Nanga Za Ku chichikangawa Ati chani Akutumanio
@WilliamChanza
@WilliamChanza Месяц назад
Manganya sanandilankhulire bwino, akutanthauza kuti kupereka ngongoleko, chitukukocho amalepheretsa ndi a Chilima?
@MosesKalenge
@MosesKalenge Месяц назад
Eti et.. ndigalu kwabasi us
@user-zg9jv5ns1c
@user-zg9jv5ns1c Месяц назад
Sanalankhuleko zanzeru uyu
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Месяц назад
Anthu anjala kumaimbera mmanja. Landilani ndalamazo koma musazamuvotere mfitiyi chilombo munamupha mwankhaza nzanu
@HamiltonSinosi
@HamiltonSinosi Месяц назад
Inunso ndindani kuti mungasinthe zinthu kunali anzanu ankayankhula zimenezo akulowa m'boma pano anaiwala zonse zomwe amalonjedza ku ntundu wa a Malawi. Daily kwacha ikumangogwa tikufuna ndrama yathu ibwelere mchimake ngati muli ndi mzeru.
@imaculadaAndre-ns1py
@imaculadaAndre-ns1py Месяц назад
Zopusa ngongoleyo pano chifukwa zoko wafa chakwalayo anali Kuti galu iwe nonsenu mwapha chilima chifukwa chá udindo chitsilu
@mthawisakaunda
@mthawisakaunda Месяц назад
Amalaw amangoombera mmanja zlzonse.. ngongoleyo nthaw yonsey unalikut pathako panu nonse. Kod iwe manganya uli mbal iti makamaka???
@FrancisGama-qb7ze
@FrancisGama-qb7ze Месяц назад
Kukanika kuyakhura ku maliro a mzako uja lero ukufuna uwoneke wa dzelu aaaa zaziiii
@SteveKanongwa
@SteveKanongwa Месяц назад
Olo mupeleke ngongole ngt ndalamayo ilibe mpamvu ululu wa anthu sutha, osayamba kae kukonza economy bwanji ngt uli dolo kuti zinthu zisike mtengo anthu soap azigula 150 or 200 hundred kwacha.. Chifukwa olo mutapanda kugawa ngongole koma mutasisa ma basic needs ndekut basitu Malawi wamutha
@VungaQueen
@VungaQueen Месяц назад
Muudzeni chilungamo uyu Amati Bambi asikono😊
@SangwaniThika
@SangwaniThika Месяц назад
Zigawenga izo usiru wekha zachamba
@PatrickJemus-tx6ue
@PatrickJemus-tx6ue Месяц назад
Koma mukamalankhura ngani Za chakwera paribe chimene chingakunyendere asatana😢😢
@LawrenceBelson
@LawrenceBelson Месяц назад
Utipeze kuno ku ndilande tikulandira wamva kafula
@TonyMpate-by9gp
@TonyMpate-by9gp Месяц назад
Mapwalaaaaa ako palibe chomwe ungachite galu iwe ndidzomwe unkafuna dzimenedzo
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Nthawi zonsezi munali kuti anthu akungofa ndinjala fertilizer odula ngt uyo munthu wosauka wa kumudzi sangakwanise kugula, komanso ngongole yo simungapatse munthu aliyense mupatsa okhawo amene ali ndi ma business akulu, bola mukanatsitsa fertizer, mzipatala so mankhwala adzipezeka
@user-rz9rm4cb8x
@user-rz9rm4cb8x Месяц назад
U vice president wa chaka chimozi umenewo
@MosesKalenge
@MosesKalenge Месяц назад
Palibe chanzeru apa. Kumaliro SKC utsalankhulako asatana inu wasangalala tsopano😢😢😢
@UsenLashid
@UsenLashid Месяц назад
Uyu ndichontcho kufuna kipepeletsa athu Anthu akulankhula chplakwikacho komaso Usamati mulungu Ayi chosecho umaziwa chilicho pa chiwembu cha chilima kuti afe cholinga utenge u vice president wa chilima mulungu amene ukumutamandayo ndi amene ali ndi kathu kotsutsana nawe samali Kwambiri Michael usi ukapanda kulapa uchititsidwa manyazi ndi mulungu pamodzi ndi chigawenga chizakocho,
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Месяц назад
A kamatchula chakwera anthu zikuwanyasa ndipo mfundo Zina sakugwilizana nazo .
@user-hp9bn4rl3o
@user-hp9bn4rl3o Месяц назад
Zauchisilu basi nthawi yonseyi sumumapeleka ngongole yo bwanji... Iwe galu kwabasi
@GiftKananji
@GiftKananji Месяц назад
Sibwino kutchula za mubaibulo chifukwa si iwe oyenera kwa mulungu lapa m'bare
@RazackKabadwe
@RazackKabadwe Месяц назад
Akuziwa chimene akuchita galu ameneyo mmaso mwake
@user-nc4vi1jt5g
@user-nc4vi1jt5g Месяц назад
Zopusa zimenezo tifuna atiuze kuti atipatsa upresident kuchipani cha utm osati ngongole ndiwegalu
@PaulineKamwana
@PaulineKamwana Месяц назад
Zaziii chikangawa chakwera anali kt nthawi yonseyi 😂mukatero mwaiyamba compain mukhaula anthu okupha inu
@Stevekatiwa-tp3oq
@Stevekatiwa-tp3oq Месяц назад
Namapwala uyu asandithele bundle! Akuyesa ngat ali pa tikufelanj eee?? Zitsiluso nndizemene zikuombela manja zopusazo akukhalangat man ga ya saziwa bwanj bushitt!!!!!!!
@omarajibu860
@omarajibu860 Месяц назад
Ngongole yopeleka chifukwa choti campaign yayandikira?
@HopeLyson
@HopeLyson Месяц назад
Aaaa mfundo mulibe chifukwa anthu akufuna zinthu zikonzeke osati kumawawuza anthu mbwelera ngati izi
@francismungu7749
@francismungu7749 Месяц назад
Akufuna voti uyu ndi chakwela wakeyo. Idyani ndalamazo koma osawavotela anthu oipawa
@JamilahJuma-pp1hv
@JamilahJuma-pp1hv Месяц назад
Abhiyeni mwaphela dala dzikoli mukhalenalo😢
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q Месяц назад
Manganya ungozipepeletsa wekha palibe angakunvere iwe za ziiiiiiiiii
@PetroMatias
@PetroMatias Месяц назад
Koma amarawi chili chose kuimbira mmanja koma mukuliraso 😭😭😭😭😭😭😭😭 ndijara
@user-tx7xz9kf1w
@user-tx7xz9kf1w Месяц назад
😂😂😂😂 Waukape chilibeso fundoo
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb Месяц назад
Akunama ameneyo wadya bhanzi.
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo Месяц назад
Umaufuna u Vp eti? Zaziiiiii
@Kenmoney-xp7tz
@Kenmoney-xp7tz Месяц назад
Amalawi ndi zitsiru mukuimbila manja chani mfiyi khati imeneyi
@PaxKinley
@PaxKinley Месяц назад
I would wish this Stupid VP to see these Comments and he must regurgitate mbwerera zomwe wayankhulazo
@pempheronawani4627
@pempheronawani4627 Месяц назад
Kodi wayamba campaign wa Mcp eti okay bhobho
@EagerChicken-qj6xu
@EagerChicken-qj6xu Месяц назад
Kulankhula kwina ndikodzigwirisa ufiti.
@MuhajirinaSaid
@MuhajirinaSaid Месяц назад
Za iwe bakili muludzi TV inatiwuza kare panya pako galu iwe
@NabeelAlie
@NabeelAlie Месяц назад
Kampen imeneyo ,kale loseli zinali kut,mzeru mulibe mukanakhala amzeru bwezi mutatchipisa zinthu zimene munakwezazo
@brightkaunda920
@brightkaunda920 Месяц назад
Koma ma comment ali apa😂😂ndawerenga ma comment onse ofuna achakwera ndi usi tilipo atatu okha muno mhuuu😢
@MphatsoMhoney-xn2ft
@MphatsoMhoney-xn2ft Месяц назад
Kulowa N,boma basi kuthamangira kugawa ngongole basi mwanva Kuti anthu akufuna ngongole kapena akufuna zinthu sizike mitengo mukanfuse Bakili Kuti azatani Kuti zinthu zitsike
@MosesKalenge
@MosesKalenge Месяц назад
R.i.p SKC 😭 😭😭
@user-xg5dg7jj4d
@user-xg5dg7jj4d Месяц назад
Ife sitikufuna ngongole kapena chimanga koma kkma tikufuna kukomza dzjko lamalawi kuti likhale lokomela tonse
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 Месяц назад
Kumagochi kuno usabwele tizakuonesa iwe kape
@EsnartMalewa
@EsnartMalewa Месяц назад
UTM ilibe tsogoleri padakali pano
@HanifuIshmael
@HanifuIshmael Месяц назад
Chakwera manganya machende awo osapita kujando mwava
@AbdulShafi-n1k
@AbdulShafi-n1k Месяц назад
Tachoka iwe apa mbuzi ya munthu. palibe cha nzeru chimene ukulankhula apa
@SALADIC410
@SALADIC410 Месяц назад
Aaa ndiye alipo wamuona iwe akudya katatu?
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 Месяц назад
Kod iwe wa mcp kapena wa utmost zachamba et tatompa nanu inu
@asahelmachila3026
@asahelmachila3026 Месяц назад
Uyu Manganya wanu shit yamunthu. Chakwera amupasa chibhanzi chilibe butter. Shame
@Martha-m6e
@Martha-m6e Месяц назад
Tikuferanji weni weni ndithu.
@user-ki8hm1xp4p
@user-ki8hm1xp4p Месяц назад
Ziphikani nsimayo ife tizayipakura
@ShantKalinda-oq2iy
@ShantKalinda-oq2iy Месяц назад
Phwala lako manganya
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Месяц назад
Mbudzi ya vice president
@hugoorthodontics4486
@hugoorthodontics4486 Месяц назад
Mwazi ulipamutu pako ukhaula iwe
@OmegaMussa
@OmegaMussa Месяц назад
Oyipa iweyo
@CathrineBizza
@CathrineBizza Месяц назад
Aaaaa Komanso awa aaaa zaziiiii
@user-ke4dk2io6q
@user-ke4dk2io6q Месяц назад
Iwe upusa kwambiri usamale usatinamize
@anicakandiado
@anicakandiado Месяц назад
Nthawi yonseyi unali kuti? Usatikwanepo apa kwatsala miyezi yochepa kukavota. Munthu wachabe udzititchulira Chakwera mmene mavuto atikwanilamo zinthu kudula palibe chikuyenda zachabe ukunenazi. Kuusangalala ndi udindo wa u vice wapatsidwawo? Palibe mfundo wanenpo apa za ziii zenizeni
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 Месяц назад
Koma manganya abale kuthatu ukuu
@IssahAluba
@IssahAluba Месяц назад
kachigawenga kachabe chabe
@AndrewChazika
@AndrewChazika Месяц назад
Tamayankhulani zot tiziva
@OsmanPatrick
@OsmanPatrick Месяц назад
Kd aMalawi Di simuchedwa kuyiwala et uyu munamuonapo akuyamikira chilima liti nde inu muli busy kumuombera manja zimu wachilima ukuzuze agalu inu
@hugoorthodontics4486
@hugoorthodontics4486 Месяц назад
Komaso chakwera akuphaso nawe
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад
Ayi zidyani ndalamazo simulumphamo😂😂😂 ayi tikuonani 2025 chipande chilipo
@ChrispinLaxion
@ChrispinLaxion Месяц назад
😂😂😂😂 akufuna kunena kt chani kod ameneyi mbuzi yachabe
@SphiweSendaluzi
@SphiweSendaluzi Месяц назад
We don't want ngongole and maize We are tired osamangotipasa zakudya zasiku limozi ife Malemu sakusangalala naye uyu mbamba😢
@HopeLyson
@HopeLyson Месяц назад
Eti aaaa simfundo yoti azitiwuza ife so chimangacho ndi 10kg ungadye chaka chonse? Even ndalama zikunenedwazo ulandire 100pin upanga nayo chani ndimomwe Malawi wavutiramu
@LorraineSimwaka
@LorraineSimwaka Месяц назад
Mfundoless asaaah
@annamazingashaibuh6276
@annamazingashaibuh6276 Месяц назад
Bora musamangoyakhuraaa apa aaaa inuu ngone kumphee sali kutaliiii
@lyiemax
@lyiemax Месяц назад
We don't want to hear anything about MCP, zidyelelani ino ndi nthawi yanu
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Месяц назад
Mukunamisa ana ashokapa fusek
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Месяц назад
Adpp mumwa temiki ngati mmawona ngati mwalanda chipani chachilima mwauponda
@stelladolizyi
@stelladolizyi Месяц назад
Amanganya Mulungu achite nanu
@TimbaTv001
@TimbaTv001 Месяц назад
Panda panu big
@MisheckNtanbalika
@MisheckNtanbalika Месяц назад
Uyu atichimwinasa
@user-co2cz2ht8j
@user-co2cz2ht8j Месяц назад
Akagwele kumpanyila ameneyo 🖕🖕
@user-hq6dq7zr1e
@user-hq6dq7zr1e Месяц назад
Aaaaaa data ija
@DeborahGeorge-g3i
@DeborahGeorge-g3i Месяц назад
Pasanapako
@ZAGAHDADIE
@ZAGAHDADIE Месяц назад
Machende ako manganya
@Fatima-f5c
@Fatima-f5c Месяц назад
Ngongole yaamakoo patumbo pakooo
@braveglorymwanzagolah4899
@braveglorymwanzagolah4899 Месяц назад
Musamvele mthira kuwiri uyu
@DimisonMbewe
@DimisonMbewe Месяц назад
Mbuzi za mcp zinavala ma t shirt a utm nthawi yonse ija anali kuti
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu Месяц назад
Osamuponyapo bwanji ndi miyala
@WilliamChanza
@WilliamChanza Месяц назад
Ineso kudabwa nazo, ameneyu akakumana ndi miyala mazalamphuno akeo akanathera pomwepo
@omarajibu860
@omarajibu860 Месяц назад
Lo!
@ZAGAHDADIE
@ZAGAHDADIE Месяц назад
Anthu Ali apo mwagula. Ndi 5000 kwacha muyaluma palibe Cha nzeru apo
@SueWahna
@SueWahna Месяц назад
Inee nditukwana kwinako 😅😅
@user-ei5kv4fr2g
@user-ei5kv4fr2g Месяц назад
Zaziiiii
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Месяц назад
Mfiti iwe unya paja wapha nawo chilima, unamupheranji mzako chilombo iwe
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад
Usatipusitse iwe tikopeke chifukwa chachimanga Manganya dziwa ichi nzako uja wafa osalakwa iweyo ulimba ukuganiza
@jabulanstephano-sy1uo
@jabulanstephano-sy1uo Месяц назад
Wakupha iwe choka
@KennethDzama
@KennethDzama Месяц назад
Panyapako
@user-qi8xe7qh1e
@user-qi8xe7qh1e Месяц назад
Manganya usaname chifukwa tatopa ndikunamako mukuti mukwanilitsa malonjezo anu aja mukudziwa kuti mwasala mwizi ingati kuti muchoke munthu oipa iwe pofunika ubwerere ku adra
Далее
Malema addresses Gauteng EFF members
1:25:51
Просмотров 270 тыс.
Woman = best friend🤣
00:31
Просмотров 3,7 млн
🛑самое грустное видео
00:10
Просмотров 169 тыс.
НЕ ИГРАЙ В ЭТУ ИГРУ! 😂 #Shorts
00:28
Просмотров 303 тыс.
Singer Rema visit to Oba of Benin Palace
10:34
Просмотров 7 тыс.