Тёмный
No video :(

KUZUKUTA NKHANI ZOMWE ZACHITIKA.UKU KWATENTHA 🔥🔥🔥🙌🙌 

HOT 265
Подписаться 76 тыс.
Просмотров 45 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

25 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 100   
@CHRISSYBALALIKA
@CHRISSYBALALIKA Месяц назад
Mukaona munthu akuti MCP my vote ameneyo ndi wa family ya chakwera mwina ndi ankolo ake kapena chakwera anakwatira pakwawo which means phindu la chakwera akuliwona ameneyo wachita zolozeka kwawoko
@macdonaldmunthali9895
@macdonaldmunthali9895 Месяц назад
Very wrong decision,the end of utm.chilima was the only leader with great vision and calmness, you can't make decision out of anger.
@user-nc4vi1jt5g
@user-nc4vi1jt5g Месяц назад
Kabambe afunampando ku utm koma autm samalanaeni mtsogoleli wanu autm sankhani kaliati ndiponso pamasankho adzawina anthu tilinae ndichikhupililo enawa tawaesa akanika
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l Месяц назад
Nkhani ndiyomweyo mwamva bwino zikomo kwambiri pamibawa.. God bless you two guys... Mamakutu wava koma wopanda makutu mawa wazakuwawani
@lifayohbenson1994
@lifayohbenson1994 Месяц назад
Ku utm kulibe mphungwe mpungwe Winayo chipani chake ndi odya zake alibe mulandu
@user-io2uw2me9f
@user-io2uw2me9f Месяц назад
Anapha dala chilima cholinga anthu abalalike koma mulungu ndiwadongosolo a utm osafooka osatopa osaopa
@SharifChibwana
@SharifChibwana Месяц назад
Bakili Muluzi tv ndi katundu
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Месяц назад
Uku nde kuyankhula kopanga umodzi that's y ndimakukondani amibawa chifukwa mumayankhula chilungamo
@DavieChiwale
@DavieChiwale Месяц назад
Apa a UTM Mukapanda kumva zanu izo
@PeterTembo-zj5jk
@PeterTembo-zj5jk Месяц назад
Dpp moto❤❤❤
@ManzyNgoleka
@ManzyNgoleka Месяц назад
vuto inu akulu mukukocha ndale mwachidule nanu mulikuseli kwa enaake
@user-gk6bf7xe9g
@user-gk6bf7xe9g Месяц назад
MCP my vote ❤❤❤❤❤❤
@user-px6kt8rx2p
@user-px6kt8rx2p Месяц назад
Also me my vote
@JazzdMonga-v6e
@JazzdMonga-v6e Месяц назад
Kumupeza wina akuti mcp my vote Amalawi ndichani
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Месяц назад
Ena si anthu....ndizinyalala tu.
@BlessingsNyirenda-ru7ss
@BlessingsNyirenda-ru7ss Месяц назад
Eti eti amwene mumune mcp yawonongera zinthu ndiye wina akut mcp my vote eeeesh
@nellybruhan5834
@nellybruhan5834 Месяц назад
Anthu ena alibe mzimu... Kuti mwaoneso akuyankhulawo ali mbuuu
@pemphokatembe443
@pemphokatembe443 Месяц назад
Kufuna kuzamva mkhwangwa ili mmutu
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn Месяц назад
Khondo Yochita kutiponyera Mcp kumupanga usi LET HIM BE THERE WILL MAKE CONVENTION SOON
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Месяц назад
Aaa manganya ngati mutu mwake dziyendamo bwino ayi musiyeni ku MCP koko afela nayo limodzi
@VincentMbeye
@VincentMbeye Месяц назад
Yalakwa UTM kuchoka msanga ....awonesa umbuli kwambili
@Aqiec09
@Aqiec09 Месяц назад
Ndipo usavage wa athu ophunzira umakhumudwisa
@daviskamonde4882
@daviskamonde4882 Месяц назад
Don't lie to us. You support MCP.
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l Месяц назад
Njawala number one, kaluati number two be careful ndi anthu awiriwa ndi anthu oyipa mutima kwambiri We love utm kwambiri koma isakhale ya munthu
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 Месяц назад
Zoona zake anganidze mofasa sure ❤❤❤❤❤
@JaphetSakala-pq4fl
@JaphetSakala-pq4fl Месяц назад
UTM motomoto osadandaula
@MosesNanchinga
@MosesNanchinga Месяц назад
Ma comment onsewa bwanji simukukamba za ndalama ai kma UTM sinalakwitse kuchoka ku alliance coz sanalandire ulemu uku ku MCP atizuza ndlmazo mukukanika kugulira mankhwala zipatala bwnj
@TonykalicheloKalichelo
@TonykalicheloKalichelo Месяц назад
Inu ngat mwin wake amafuna kusazika ndiye mukufuna omusatila atan
@lyiemax
@lyiemax Месяц назад
Proper narration, big up guys ❤❤❤
@RegistermoseskashonKashon
@RegistermoseskashonKashon Месяц назад
Inu nde munabwela kudzauza amalawi tchutchutchu osat akapilikon enawa ongokamba zinthu zopanda kumutu
@user-rf4br1fv2z
@user-rf4br1fv2z Месяц назад
Mwawathandiza ulemu
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl Месяц назад
Skc ankafuna kutchoka after kusalemekdza mgwirizano omwe unalipo ndiyeno kutchoka it's a good move komano to agree with ndikutenga mnthu kunja that's wrong indeed
@EdsonNjonjo
@EdsonNjonjo Месяц назад
Munthu uyu akunena zoona
@AlliSaiti
@AlliSaiti Месяц назад
Athu akuda ndife opanda nzeru
@MervinKandoje
@MervinKandoje Месяц назад
You to be specific
@OsmanMasamba-ck4mo
@OsmanMasamba-ck4mo Месяц назад
Manganya iwetu wagulidwa ndichisilu chinzako
@FloraBanda-w7t
@FloraBanda-w7t Месяц назад
Koma selina 😂😂😂akut kod akabambe akulowela kut 😂😂😂😂
@user-ux9ik4zr5x
@user-ux9ik4zr5x Месяц назад
Probably the best program
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi Месяц назад
Ndibwino kt atengane okhaokah
@StevieTaiza-r9j
@StevieTaiza-r9j Месяц назад
Mulungu azikutete bro
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Месяц назад
Akumatibera zathu zomwezi zamisokho
@EstherManda-ex3bc
@EstherManda-ex3bc Месяц назад
🤣🤣🤣🤣 nkhani zake
@Aqiec09
@Aqiec09 Месяц назад
Yea that's very true and I see it ku utm utsogoleri unali wa chilima ena onsewa mavuto bola ku MCP komweko mudziwa bwanji mwina the death of chilima was planned with those who are on top blaming MCP for the death yets amafuna mpando wachilimawo why so early kutuluka mugwilizana without solid proof that is MCP guilty , ine unless pa social media muzabwerese real proof how you saw the killing happen that's when I will find them guilty
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw Месяц назад
Njawala ndi kaliati mutiwonongera chipani chathu ndakwiya Nanu heavy kuno kuntheu mutisamale awirinu
@Ishriss1999
@Ishriss1999 Месяц назад
Ma prophet watu koma atilankhilitsa pambali mxiiiiew
@mzeewandembonyirongo2972
@mzeewandembonyirongo2972 Месяц назад
Gwende u have fairly advised
@user-lg6ym4hz3w
@user-lg6ym4hz3w Месяц назад
Kkk😂😂😂😂😂😂😂😂 anzanga afumu owuka
@SabinaNkhoma-sf7kz
@SabinaNkhoma-sf7kz Месяц назад
Mmmmm km mcp yaonjeza,zot amalawi akuvutika sakuganizako
@user-rx7cc7tc6b
@user-rx7cc7tc6b Месяц назад
MCP 💥💥💥❣
@GiftKaunda-f8j
@GiftKaunda-f8j Месяц назад
Analysis yanzeru zozama koma imeneyo?
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga Месяц назад
anthu atamalankhura ngati mmene ukuyankhulira lweyo anthu akhoza kumachitazinthu mwanzelu
@ChrispinKashosha
@ChrispinKashosha Месяц назад
Mcp ya wina kale
@user-he5ol5or7f
@user-he5ol5or7f Месяц назад
Gwede is the best
@dysonmasiye5736
@dysonmasiye5736 Месяц назад
Nduna zomwe zikugawa ndalamazo akumatibera misonkho yathu yomweyi...ifetu maso athu tikuona ndipo tilankhula chaka cha m'ma chino....40million plus just for one meeting business yanji imene akupanga? Apapa zaonekeratu kuti andale amatibera pomwe anthu akufa ndi njala. Ambuye akukuonani ndithu
@innocentissah2636
@innocentissah2636 Месяц назад
Pamaliro wandale athamangitsidwe
@JasonMailos
@JasonMailos Месяц назад
😢😢😢😂 ozuka kumandao Eeeeee kusokonezatu kkkkkkk
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Месяц назад
First to comment
@MasaukoNyirongo
@MasaukoNyirongo Месяц назад
😂😂😂😂😂😂😂 koma zinaz abale kkkkkkk kuthamangitsa masiket mudzi kkkk
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Месяц назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Koma abale
@AdenaGuest-g4b
@AdenaGuest-g4b Месяц назад
Kuwechetamwangajimbilambali
@AdenaGuest-g4b
@AdenaGuest-g4b Месяц назад
Aaaaa Malawi
@ZioneMkangadzula
@ZioneMkangadzula Месяц назад
utm igawana zida zafikapa angonamizana
@chrisgremu740
@chrisgremu740 Месяц назад
MCP 🔥🔥🔥🔥
@IshmaelIbrahim-s8c
@IshmaelIbrahim-s8c Месяц назад
Pathako pako 😂
@ThomasShuga
@ThomasShuga Месяц назад
Wabaya ase kkkkkk​@@IshmaelIbrahim-s8c
@ThomasShuga
@ThomasShuga Месяц назад
Iwe fisi eti 😢😮
@user-he4jv1sb1m
@user-he4jv1sb1m Месяц назад
Mapazi ako nd mcp yomweyo
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh Месяц назад
Njoka iwe fiti
@AdenaGuest-g4b
@AdenaGuest-g4b Месяц назад
Umakwana
@PociahMack
@PociahMack Месяц назад
Kma nkhani ya a pro andiseketsa bwanj😂😂
@PhiriChitani
@PhiriChitani Месяц назад
Ndinu a Mcp chokani apa mukuyiwala kuti UTM idayamba yokha without mcp
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l Месяц назад
Usi ndi munthu yimodzi yomwe mwini wa UTM
@SprianoJeke
@SprianoJeke Месяц назад
Kugawa ndalama Koma ma servants ndee ka salary ka mmanja
@SprianoJeke
@SprianoJeke Месяц назад
As government I think abalalika ndithu
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga Месяц назад
vuto amalawi timasapota vitsilu kali ndi ........
@user-gk4nu4xr8r
@user-gk4nu4xr8r Месяц назад
Of course
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Месяц назад
akuononga chipani cha utm ndi mai kaliati ndi azao filex njawala anthu awawa ndithu amaliza chipani cha utm samalani
@RhodaBandah-sh1ir
@RhodaBandah-sh1ir Месяц назад
Tafotokozani mmene akuwonongela ....
@MsondaBanda
@MsondaBanda Месяц назад
Ntchindi mulije mu utm
@user-kj7hr2jf1l
@user-kj7hr2jf1l Месяц назад
Zowona utm yisatenge munthu wakunja
@atupelemposa4786
@atupelemposa4786 Месяц назад
😂😂😂
@MayesoKulea-sh8xd
@MayesoKulea-sh8xd Месяц назад
MCP ☑️
@YohaneMotison
@YohaneMotison Месяц назад
😂😂😂😂😂😂
@PulayaKalaka
@PulayaKalaka Месяц назад
Mcp mooootooooooooo
@user-cb5gh9md4i
@user-cb5gh9md4i Месяц назад
Kodi ntchentche zikutanipo pamibawapo
@officemoyenda-rj2hz
@officemoyenda-rj2hz Месяц назад
Si ntchentche
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Месяц назад
😂😂😂😂😂
@FloraBanda-w7t
@FloraBanda-w7t Месяц назад
😂😂😂😂esh I think ndi lens
@YamikanAbubakary-my4ie
@YamikanAbubakary-my4ie Месяц назад
Ambuye mulungu daritsani chipani cha mcp 🇲🇼❤️ 🙏🙏
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Месяц назад
Ndiwe opembedza mafano Mulungu wa Abraham sangadalitse MCP...siwachisokonezo ngat Chakwera wakoyo...usamutchule Mulungu pachabe...ungaone tsoka
@user-px6kt8rx2p
@user-px6kt8rx2p Месяц назад
Ukunama ukadakhumudwa mcp chiyembekezo cha Malawi ambiri
@robertkalima874
@robertkalima874 Месяц назад
@@user-px6kt8rx2p MCP chipani chafuko
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Месяц назад
Usatchule dzina lamulungu wako pachabe chome iwe
@MosesNanchinga
@MosesNanchinga Месяц назад
Ma comment onsewa bwanji simukukamba za ndalama ai kma UTM sinalakwitse kuchoka ku alliance coz sanalandire ulemu uku ku MCP atizuza ndlmazo mukukanika kugulira mankhwala zipatala bwnj
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Месяц назад
Abwenza ndalamazi...eni ake akutuwa kusowa sopo...akuoneka a fumbi lokha lokha km ena akuononga mosaopa Mulungu...ayi tiona posachedwapa....nafe tikudikira
@AdenaGuest-g4b
@AdenaGuest-g4b Месяц назад
Aaaaa Malawi
Далее
Whoa
01:00
Просмотров 10 млн
HOT CURRENT YA LERO 🔥🔥🔥🔥🔥
59:36
Просмотров 29 тыс.
A RICHARD CHIMWENDO BANDA KUNG'ALULA DPP
25:45
Просмотров 20 тыс.
AZIMAI A UTM KU AIRPORT KOWALANDILA ACHAKWERA
17:16
Просмотров 10 тыс.
ZOMWE AYANKHULA A CHAKWELA LERO
14:19
Просмотров 3,5 тыс.