Тёмный

LIMPOPO FM - AKULU AKULU ENA A MCP ANAPITA KUNYUMBA KWA BAKILI MULUZI 

MPUNGWE-PUNGWE MW
Подписаться 65 тыс.
Просмотров 15 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

20 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 51   
@dyba-x9w
@dyba-x9w 16 часов назад
ubwino wake ife tingowasiyira udf yaowo ku mcp ko apita banja lawo lokha ife bola kujoina dpp kapena utm or aford
@KhadijaMbwana-eu8qk
@KhadijaMbwana-eu8qk 16 часов назад
Ubwino wake voti ndimutima apm my vote udf tinayituluka kale akale
@ernestphiri5507
@ernestphiri5507 5 часов назад
Ufitiii chani
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 18 часов назад
Zoonadi brother Don't trust timakunyadilani ndipo UDF anthu anaituluka kale kale sangawine achepa Ana amenewa pano Deal ndi APM UTM Alford basi
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 9 часов назад
Ngati zili chochi abale tituluke udf because ifa ya chilima ilipoela kuti chilima anapedwa ndi udf
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 9 часов назад
Sorry ndi mcp , ndee mcp mukaloweso kokho aaaaa tingokutulukani bwanji
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 14 часов назад
UDF sitilola kukhala munkhwapa mwa MCP or DPP sitikuifuna tipita tokha kumasakho win or lose period
@AbdulrazaqHussain
@AbdulrazaqHussain 17 часов назад
Ndizoona kuti ndichisankho chawo, koma what does a leader lead? can you take that kind of money n forgetting your pipo, is it worth it?akulakwa, we expect those pipo put pipo 1st, but what l see, is disgusting leadership, with no desire to make pips life better, but for themselves, zanselu
@HusseinMofatt
@HusseinMofatt 17 часов назад
Ndimakunyadilani inu Limpopo fm
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 9 часов назад
A MCP muchipheso chinkhalamba chopanda zelu amuluzi mwayiwara dzomwe munamuchita kamuzu 😂😂😂 mufa Ngati galu
@AbdulrazaqHussain
@AbdulrazaqHussain 17 часов назад
Akakhala Elasoniyo, DNA yake ndi mcp,(Malawi chakwela party)we are not surprised, kaulemu tanatsala nkati mwathuka, kupanga expire, utsogoleli ndi anthu, popanda anthu utsogoleli palibe, wandu akulaga wawo che bakili, akatutapisya
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 17 часов назад
MCP kuwononga ndalama kupasa mafumu palibe amene akumvera mafumu. Poti mafumu ena NDI adyera kwambiri
@JibraanSharief-ol1yn
@JibraanSharief-ol1yn 21 час назад
Yhoo leave them is there's choice
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 14 часов назад
Lipopo FM mumakwana
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 16 часов назад
Kulandira ma 5 milkion kwacha kwa mafumu whilst amalawi mmdziko muno.akudya chitedze ndi kumalephera kugula cĥmanga mmisika a chakwera atapanga devalue kwacha kuti amalawi onse afe ndi njala ndi umphawi .!!@ kodi kukhala amatero inu mafumu abodza ndi afiti nonse inu ?
@ehinsupport3217
@ehinsupport3217 3 часа назад
Nde kupita Kwa anthuwo Kwa Bakili Muluzi, inuyo chakukhuzani ndi chani anthu opanda manyazi inu
@MwinkhulanaLulu
@MwinkhulanaLulu День назад
Mafumu aku Machinga anthu anu akudya chiteze inu muli busy kumakumana ndi anthu okupha omwewo tikwiya nanutu mukufuna mutigulinse
@tingamasi106
@tingamasi106 13 часов назад
komatu Regional Governor wa UDF ku mwera ndiwamkazi nde akhalanso pa chibwenzi ndi mzimai mzake?
@YOUNGKIDS-k5d
@YOUNGKIDS-k5d 11 часов назад
Kkkkkkkkkk 😂😂😂 boza ili apasidwa ndalama ndi aja akanika kutsutsa boma aja ife tanva kale
@sanudiasikemu2672
@sanudiasikemu2672 6 часов назад
UDF inaikidwa m'manda 2009 ndipo apapa ndimwambo owaka manda ake basi. Ine pheee! kuweza nsomba ndi adad ku Page house.
@hassanmpate7538
@hassanmpate7538 День назад
Freedom of assembly komanso choice sasankhilana
@YusufKazembe-po6qo
@YusufKazembe-po6qo 16 часов назад
Kudya mkhumba nthawi yothaitha
@InnocentNitamanMilanzi
@InnocentNitamanMilanzi 8 часов назад
Atupere timakudalira koma panopa takutuluka uzazivotera wekha chomwe ungadziwe ife monga ayawo sitingavotere chitsiru cha munthu chosamva chisoni ndi amalawi mmene akuvutikiramu
@DamsonMcdonald
@DamsonMcdonald 9 часов назад
Ndie vuto ndchani kodi? Zaziii😅😅😅😅
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 12 часов назад
Nde kwa chair ko amapereka ndalamazo ndi ndani?
@ImraanKananji
@ImraanKananji 15 часов назад
UDF bolaso afford iri ndi phavu tinachituluka ichi
@YOUNGKIDS-k5d
@YOUNGKIDS-k5d 11 часов назад
😂😂😂 mr f don't trust tava kale galu iwe ukumunamiza ndani cadet wa dpp iwe ivani izi amalawi ma activists ose apasidwa ndalama ndi dpp kut asokoneze chipani cha UDF zindikirani izi o.wewa ndi omwe ativulalitsa
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl День назад
Mafumu alibe ntchito vote ndi mumtima ko voter munthu amakhala yekha
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 7 часов назад
A mcp ngati awatenga ma supporter a udf agwa nayo atenga dzina la udf not with people
@BensonGama
@BensonGama 12 часов назад
Koma mcp amaganiza anamupha mkazi bakili muluzi ndiye akufuna m'gwilizano udf ngati mcp payokha ikuzidalira azaime paokha
@BerthaChasweka
@BerthaChasweka День назад
@LuckyBiziweck
@LuckyBiziweck День назад
Ichi ndichabodza nanga akunena kuti amfumu kapoloma anapita nawo mmmmmmm amfumu kapoloma anamwalira now is 5manths ago ndipo ufumu siwunalongedwe tsono ukoko awa asamatipusitseko ayi aaaaaaaa amapita ndaninso
@DeMu-t2v
@DeMu-t2v 9 часов назад
Kukomera kwake mfumu singandikakamize kuvotera chipani chomwe chikuzuza moyo wanna.ndalama imene akupatsa mafumuyo Bola akanagawa mamidzi olo munthu atalandila 100 pin atha kuthokoza,MCP akuti chidzawina nanga chomagula anthu zikukhala bwanji?komatu ndalama zikusakazidwa bomamu
@Daniel-cf4tu
@Daniel-cf4tu 14 часов назад
Mpaka khani ya zibwezi zijugwilizana bwanji ndi mavuto athu😊
@BenedictoJoseph-dh7gi
@BenedictoJoseph-dh7gi 13 часов назад
Ife tipindulapo chiyani ndi zibwezizo😂
@ChristmasChapeta
@ChristmasChapeta 10 часов назад
Kuthere mcp gonero wake ndi udf
@Ggg-q5h2e
@Ggg-q5h2e 18 часов назад
Chisankho chawo asiyen😂😂
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 10 часов назад
Alemba mmadzi
@StevenFombe
@StevenFombe 20 часов назад
Paja nsana uja wachira
@EvelineGalion-vw9bc
@EvelineGalion-vw9bc 18 часов назад
Aliyense atha kupita nanunxo pitan akakulandiran zonyasisa anthu ai hyaa@@@ mwaswa zokamb kambn inah ńot zopusazi,muluzi sapanga nawo ndale
@TimothyNkhutembaChirwa
@TimothyNkhutembaChirwa 16 часов назад
Mafumu adyela
@awettesfamichool5009
@awettesfamichool5009 17 часов назад
Panopa UDF suyili mufasho inatha basapita omwewabasi
@ThomsonShunga
@ThomsonShunga День назад
Following
@JibraanSharief-ol1yn
@JibraanSharief-ol1yn 21 час назад
Mafumu alibe tchito
@frankmanda639
@frankmanda639 16 часов назад
That's very bad
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo День назад
Koma chonde chonde asheya timakudalilani koma zoti muzigwilizana pandale ndi chipani cha mcp sizimakhala bwino kumbaliyako ya athu omwe amakukondani komaso omwe timakonda udf mukutilakwila ndipo chipani hi chitha ine akumangochi makanjila lugola inuyo mutawona mwana wanu akucheza ndikangofuna mungakondwele
@EvelineGalion-vw9bc
@EvelineGalion-vw9bc 18 часов назад
Inuh atcheya sapanga ndale plz ndie atha kulandra munthu wna aliyense
@EvelineGalion-vw9bc
@EvelineGalion-vw9bc 18 часов назад
Kmanxo he iz founder of democracy
@MarthaNkosi-c6i
@MarthaNkosi-c6i 16 часов назад
😅​@@EvelineGalion-vw9bc
Далее
Fake Referee Whistle Moments 😅
00:38
Просмотров 4,2 млн
Ребенок по калькуляции 😂
00:32
BON KALINDO - MA DEMOSTRATIONS ALIPO NDITHU
16:26
Просмотров 8 тыс.