Тёмный

LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA 1 JULY 2024 

Club Junta
Подписаться 42 тыс.
Просмотров 50 тыс.
50% 1

Развлечения

Опубликовано:

 

30 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 274   
@Sammy-vb1ed
@Sammy-vb1ed 3 месяца назад
Mmmmm ay koma mcp yaonjeza nkhanza ndipo sitikuifuna.
@RuiJemusse-om7po
@RuiJemusse-om7po 3 месяца назад
Mulungu akhale Nanu amina Inu, wina asakutsekeni pakamaa, Mr Ntanyiwa and Mr Kalido go ahead
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 3 месяца назад
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you all the time.
@PreciousChlima
@PreciousChlima 3 месяца назад
I love limpopo fm with Comrade ntanyiwa
@memoryedwin
@memoryedwin 3 месяца назад
Mulungi azikudalitsani mr mtanyiwa
@HaliJana
@HaliJana 3 месяца назад
A MCP NDIKUUZENI SIMUNGAWAGWILI ANTHU AWA KUFIKILA MUTACHOKA MBOMA ,
@harrisonkalimbakatha5339
@harrisonkalimbakatha5339 3 месяца назад
Comrade ntanyiwa umatiyimirira MCP ndi chipani chakupha ndipo sichizasintha mpaka kalekale ndipo atikwana anthu amenewa tikuona kuchedwa 2025
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 3 месяца назад
Ndipo kwambiri tu mmm
@ImanRashidi-so4oo
@ImanRashidi-so4oo 3 месяца назад
Dziko lanthu la Malawi likamati lizilakhula chilungamo ngat Limpopo FM tikadalemela kwambiri koma eeeeeh
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 3 месяца назад
Dziko lija azaza ndi afiti adyera, magazi mmanja
@INNOCENTJANUARY-v5c
@INNOCENTJANUARY-v5c 3 месяца назад
Long live bwana Ntanyiwa
@GreysonChilongo
@GreysonChilongo 3 месяца назад
From Zambia I love bro with bon kalindo my wife came from chitipa MCP yampa athu anzelu,
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 3 месяца назад
Andale ndi athu oipa ndizoona ,,koma ndale za tonse alliance ulendo una akutionjeza,,,zinazi this current government akuyenera afufuze nkhope yamulungu,,,azidziwatu pena kuti izi ndizachabechabe Iwo eni adzafasotu!!!
@GeorgeChakuamba
@GeorgeChakuamba 3 месяца назад
kkkkkkk😂😂😂😂Ntanyiwa yemweyo auzeni aMalawi chilungamo
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 3 месяца назад
Mchewa watichitisa manyazi kwambiri zaonesa ngati achewa tonse ndi mbuli. Zandinyasa zedi.
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer 3 месяца назад
Sitikufuna mcp ife sitikuona tsogolo kwa chakwera shem on you a mcp nose
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 3 месяца назад
Ndipo tikuziwa zinthu ndi BAKILI MULUZI TV bg up brothers
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 3 месяца назад
Malawi army and police will side with the civilians on 10th July. You will see.
@EdithKachule
@EdithKachule 3 месяца назад
Hopefully 🤞
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 3 месяца назад
Nawoso amanganya ali kwangwalala njekate kuno olo ndimantha omwe alibe adzikale ng'oma mudzazafe mukale amuyaya ku MCP pamosi ndichimimba chanucho pamosi ndi chakwela chigawenga chakumpa chilombo chigawenga chakumpa
@BlessigsChabzola
@BlessigsChabzola 3 месяца назад
Nanga Iwo a Mcp sakulira nawo nanga bwanji 21days isanathe Iwo akupanga program ya convention. Ndizona zimezi,
@africahasani-gl2nq
@africahasani-gl2nq 3 месяца назад
Manganya kumupeleka chilima kwa pilato mmmmm wandikumudwitsa kwambili manganya
@ZionekaMember
@ZionekaMember 3 месяца назад
@@africahasani-gl2nq kamba ka udindo
@GeraldMustafa
@GeraldMustafa 3 месяца назад
Ndamuda manganya
@MphatsoMhoney-xn2ft
@MphatsoMhoney-xn2ft 3 месяца назад
MCP yonse ikupenga pano ?? Keep Resting well Klaus Chilima
@MisheckBandah
@MisheckBandah 3 месяца назад
I love and I'll ❤ chilima for ever
@CharlesPhiri-ds1rk
@CharlesPhiri-ds1rk 3 месяца назад
Km ndalama mukuonongaz mukudziwa kt eni ake aMalawi akuvutika?........bwanji ngat zachuluka tamapatsan ma company kt bread atsike ndi soap bwanji just mention a few..
@jamiajafali6619
@jamiajafali6619 3 месяца назад
Ndizoona
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa 3 месяца назад
Kodi a zikhale ng'ona mvuto lawo ndi chani?
@sarahlukongolo4901
@sarahlukongolo4901 3 месяца назад
Tinaona kale ife a usi kuti aliku mcp mmene amkayankhira pa Times nawo akolola akuona ngati chilima anali opusa eti
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 3 месяца назад
Zoonadi penapake Chilima anali osamva komanso osakhwima pa ndale chifukwa Michael Usi ankaonekeratu kuti ndiwa MCP and why Chilima bravery told Usi kuti akufuna kuthetsa m'gwilidzano, that's why he's died
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki 3 месяца назад
M'busa wa ntundu wanji opanda chifundo,opanda chisoni,, kukanika ku khululukila Chilima ngati adawalakwira
@wittinessnkhokwe
@wittinessnkhokwe 3 месяца назад
Iwe Monica chakwela usatitukwanise ,mpaka tikutchule phunzo?khope yonyatsayo
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 3 месяца назад
Km anthu kusankha akazi kunawadutsa kumanzere ...nkhope yopyelera.
@aligrayjeo1071
@aligrayjeo1071 3 месяца назад
Kodi nzotheka kuti tikhale ndi silent special forces Ku Malawi kuno tingopanga za MCP iyi basi chifukwa campaign nde sapangatu akapangila ground yake iti yoti akhale ndi chikhulupiliro kuti a Malawi akawamvetsera nyasi zawo mapeto Ake akachoka ataphwanyidwa ndi miyala ngati sakudziwa savage people
@MercyNyachi
@MercyNyachi 3 месяца назад
Mulungu akulangeni achakwera mwadzuza amalawi ambiri ambuye ngati mukumva pemphelo lathu ife amalawi timenyeleni nkhondo ambuye amen
@ShareefDouglas
@ShareefDouglas 3 месяца назад
A boma ndi opepera chikondi pa anthu awo alibe ndalama zonse akuonongazo bola akanamangira zipatala olo kumanga miseu
@HaliJana
@HaliJana 3 месяца назад
Zakhali n'goma panyopako wava ukuwasakilanji azako galu iwe osongomadya ndalamazo bwanji mimbayo ngati nyini yamako zakhali n'goma
@MercyNyachi
@MercyNyachi 3 месяца назад
Anya nayodi😂😂😂
@jamesmulangalimatemba5351
@jamesmulangalimatemba5351 3 месяца назад
May God protect you my brother tikufuna anthu olimba mtima ngati inu
@GiftSoko-i3s
@GiftSoko-i3s 3 месяца назад
😂😂😂morning Mr Ntaaaaaaaaanyiwaaaaaaaa we love you
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 3 месяца назад
Apa palibe kusunga chilungamo chakwela wapha chilima ndiathu 8 opanga cholakwa dyela
@FelixKada
@FelixKada 3 месяца назад
Big up mr ntanyiwa, ndipo pitilidzani kuigwira ntcito to.🤝🤝🤝🤝🤝🤝🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@Yungjoe786
@Yungjoe786 3 месяца назад
142 million for what?they're very stupidity instead of helping the needy with that cash.....mitu ngati zidebe
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 3 месяца назад
Mumakwana ma Freedom fighters athu athu akumalawi, timakukondani guys❤, MULUNGU azikutetezani ndikukupasani zosowa za pa umoyo wanu, inudi ndima HEROES adziko lamalawi ❤❤❤😢
@NastonVickta
@NastonVickta 3 месяца назад
Tili ngaaaaaa pa Limpopo fm, mpaka agaru oyamwitsa Inu mawere auma
@HestingsZiba-d6k
@HestingsZiba-d6k 3 месяца назад
Manganya namuwonakale kuti ndikamuthila kuwili
@cynthiataulo5211
@cynthiataulo5211 3 месяца назад
Usi amaoneka maso mwa mwa mwa kuchenjelesa. Ka snake kenikeni. Blood in their hands, angobwelesa matemberero to their generations to come. Anawo zizukulu zawo mapemphero awo azakhala abomination before God. Peace will be their enemy.
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 3 месяца назад
Mmmmmm koma ndalamazi zimenrzi zokumachokera kuti? Chifukwa nde zikumadabwitsatu
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 3 месяца назад
Mumuwuze Cilil Ramaphosa President wa South Africa kuti chakwela and his useless government ndi zigawenga
@ZioneMkwanda-y6i
@ZioneMkwanda-y6i 3 месяца назад
Who are you Pepe Kally Zikhale Ng'oma?? Useless man, Tsk! 😂😂😂
@MemoryBanda-yf8jw
@MemoryBanda-yf8jw 3 месяца назад
😊
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw 3 месяца назад
We Love you our junior pangolin no matter what they can't find you chifukwa inuyo Muli mumapapiko a mwini moyo wanu Chauta, Namalenga chisumphi. Ndeno angotaya nthawi azingodya basi
@hannahchimz
@hannahchimz 3 месяца назад
Dumela
@GiftPhiri-tt7nn
@GiftPhiri-tt7nn 3 месяца назад
Usi or akanapanda kuwauza a mcp zoti akuthetsa chibale koma Chilima akanafabe chifukwa chipani cha mcp sichimafuna chilima kut adzaimile pa president so osaloza chala usi ayi mcp ndiyakupha basi tiyeni pa ten tichotse pampando chakwela basi , Chakwera ananena yekha kut adzaimaso kusonyeza kut mpando amkaufuna and anakapezabe njira yophela Chilima
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu 3 месяца назад
Manganya fiti yudasi chakwera pilato mwampha chilima wanthu tsogoro lathu tikulira lfe chakwera please usogoreri amatero manganya galu wanthu
@MerryWayson
@MerryWayson 3 месяца назад
Mr Mtanyiwa End Mr Kalindo , mulungu sakutayani tikukuikizani m,mmanja mwa mulungu azikutetezani nthawi ndinthawi mukutiimilira ambuye akusungeni maka kukutetezani Kwa adani a MSP
@MadalitsoTamayenda-ez5pj
@MadalitsoTamayenda-ez5pj 3 месяца назад
Stay safe doctor ntayiwa ,, God protect yu whereever yu go kept up💯🔥💥
@frankdiyele7467
@frankdiyele7467 3 месяца назад
Truth shall prevail we have suffered enough abale
@LYDIANYAKATU
@LYDIANYAKATU 3 месяца назад
Ambuye azikutetezerani a ntanyiwa ,amene akulimbana ndi Inu akulimbana ndi Mulungu kumene amene akulimbana ndi a rwara akulimbana ndi Mulungu kumene anthu a Mcp opanda nzeru mmalo mopangira chitukuko ndarama akupangira kuti achotse mutiti ya anthu heeedee tawaonani eti anthu opanda manyazi ngati awo timakhnyadirani a ntanyiwa may God bless you all the time
@patrickndojime1632
@patrickndojime1632 3 месяца назад
Sizayiwalika ifa ya Chilima mpakana kale kale tizakhala tikukumbukira misozi yosantha
@YohaneChibweya
@YohaneChibweya 3 месяца назад
Mwadzuka bwanji Ntanyiwa musaope mulungu amapanga njira popanda njira masalimo 35 komanso masalimo 91 Pali mmawu a chilimbikitso
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 3 месяца назад
Limpopo ndiyakatundu
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 3 месяца назад
Iwe Zikhale ng'oma udzathera mmanja tsiku lina😂😂😂😂😅😅😅😅mimba yako
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 3 месяца назад
Nanga uthawa chani iwe kudafa abale ambilimbili chitsilu iwe kukamwa kowolako
@MadalitsoTamayenda-ez5pj
@MadalitsoTamayenda-ez5pj 3 месяца назад
Safe your self
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 3 месяца назад
Manyazi mulibe inu
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki 3 месяца назад
Ndani amene Ali ndi pakamwa powola
@HassanWasili-jg9nr
@HassanWasili-jg9nr 3 месяца назад
Pamtumbo pako napanyelo iwe pankholo pako
@BlessDoor-jk6ni
@BlessDoor-jk6ni 3 месяца назад
Malawi people we tired for stupid president
@hudycorex1893
@hudycorex1893 3 месяца назад
More moto Ntanyiwa!!!
@Uncle_B265
@Uncle_B265 3 месяца назад
Ndalama mmalao mothandiza a malawi Ali buzy kupanga hayala kuti azipha anthu osalakwa why koma
@Stuartkachali45
@Stuartkachali45 3 месяца назад
Usi ndamuda bas tilire bwanji ifa ya chilima😢😢😢😢
@BeatrizUlanda-ht2th
@BeatrizUlanda-ht2th 3 месяца назад
Asirikari aja ayamba kuurura kuti anapasidwa ndarama zokwana 14mirioni
@VirginiaPaulino-xc8ph
@VirginiaPaulino-xc8ph 3 месяца назад
What either like or not ife nganganga pa Limpopo aziona agalu amenewa
@lottiempata2487
@lottiempata2487 3 месяца назад
Don't be afraid 😨 for anyone else
@jafalimussa5146
@jafalimussa5146 3 месяца назад
Wawa ma boss muwuze avesese azazolowela
@EllahEllah-hu7hi
@EllahEllah-hu7hi 3 месяца назад
God have mercy
@OweniMalokooweni-es9qx
@OweniMalokooweni-es9qx 3 месяца назад
Kwacha bwenji if kuno ku khonjeni kwa bhobho 🎉🎉🎉🎉
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 3 месяца назад
God fights the battles
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e 3 месяца назад
Oyimba anayimba kuti amene udyanaye ndiamene azakupeleke. Manganya unapangilanji zimezi ndalama sizitha koma moyo wamuthu ukatayika kulibe kwina kokautenga muzivele chisoni ambuye achitenanu ndiye tikuwonelali 2025 ngati muzapitilize nawo azanuwo kuyendesa boma kupepela kwake kwantunduwanji munampeleka zanu chifukwa cha udindo kapena kungongola kwake poti anabadwa ndizose zomuyenela zelu chifundo kukongola komaso kuzichepesa nfikusasakha ntundu mulungu simuthu amatulusa zobisika lino ndiziko
@EmmieMlothaMbewe
@EmmieMlothaMbewe 3 месяца назад
,ooooooo
@SalmonMhone-zq7tb
@SalmonMhone-zq7tb 3 месяца назад
Murungu azikutetezan bwana mupaka chirungamu chiwone tizikupephereran
@samuelazumah1050
@samuelazumah1050 3 месяца назад
Umakwana iwe
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 3 месяца назад
Basi nkhani ndi pa 10 sitikuopa police tikaponda zimenezo pa 10 sikale tasala ndi 8 days so soon
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 3 месяца назад
Ndipo kwambiri tu
@FrancisDominic-w1s
@FrancisDominic-w1s 3 месяца назад
Mumakwana musapase ndimpasa
@JoyceChingamba
@JoyceChingamba 3 месяца назад
Am
@GreysonChilongo
@GreysonChilongo 3 месяца назад
God bless you
@ThialingsonChiphwanya
@ThialingsonChiphwanya 3 месяца назад
Mmmm koma zinazo mmmmm ma bodza sadzatha
@AlinafeChimoto-pp7wp
@AlinafeChimoto-pp7wp 3 месяца назад
Power message
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 3 месяца назад
Mungoti pheeee muone !!!! 🎉🎉
@MadaloZelela-m4n
@MadaloZelela-m4n 3 месяца назад
Musadandaule mulungu ali painu
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi 3 месяца назад
comrad mungulu akuonjezele moyo
@ventonngwira
@ventonngwira 3 месяца назад
BV
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 3 месяца назад
Amenewo tikumana pa 10 pano
@happykingsley
@happykingsley 2 месяца назад
More fireeeeee
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 месяца назад
58million nyini dzamao
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 3 месяца назад
Wachedwa nayo mai yolamu, ukanapanga zimenezo chilima asanafe.
@JosephyKambalame-g4g
@JosephyKambalame-g4g 3 месяца назад
😅
@jesusminded3033
@jesusminded3033 3 месяца назад
Osafooka,osaopa osatopa.
@FrancisDominic-w1s
@FrancisDominic-w1s 3 месяца назад
Atanyiwa ife timafuna pamenepo musamachoke
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula 3 месяца назад
Ine ntanyiwa tikungodikila 10 July kuti zalire bwino marilo achilima from kalonga
@AminAbbasi-xc4qk
@AminAbbasi-xc4qk 3 месяца назад
🎉🎉🎉🎉🎉
@tingamasi106
@tingamasi106 3 месяца назад
How can I talk to Mtanyiwa? I want his number
@giftsululu4274
@giftsululu4274 3 месяца назад
Ali ku maximum ku zomba
@tingamasi106
@tingamasi106 3 месяца назад
Ndiwe opusa😊
@Nelliekaiya
@Nelliekaiya 3 месяца назад
Ingoing'alulani azidzakugwilani atayaluka kale
@AliAli.aliheassim
@AliAli.aliheassim 3 месяца назад
💪💪💪💪❤❤❤
@FiskanPhiri
@FiskanPhiri 3 месяца назад
Pitilizani kutipatsila kuti tinzivako chilungamo Cha vemvemve osaopa munthu pamene palichilungamo tiuzeni basi tidziwe
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 месяца назад
Mr Ntanyiwa aphaso Lucius Banda a MCP 😢😢😢
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 3 месяца назад
For sure amphaso lusiyasi agalu
@AndrewSimakweli
@AndrewSimakweli 3 месяца назад
Takunyadilani
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 3 месяца назад
I trust Limpopo FM because of the first to announce the plane crash while the Government of MCP was hiding this.
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 3 месяца назад
For sure
@ZionekaMember
@ZionekaMember 3 месяца назад
Ndipo ine siku limenelija ndilomwe ndinakhulupilila ada amenewa
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 3 месяца назад
For sure he was the first to announce about the plane crush. I mean Limpopo FM along with comrade Ntanyiwa. From Mozambique.
@wezzieneba9238
@wezzieneba9238 3 месяца назад
This is very sad. Chili kwa nzako chigwile nyanga zoona? This is evil at its highest peak. Wafa wafa! zoona....the real photocopy of the devil himself. Ambuye atikhululukile. Komanso mu Bible mulibe this Quote or the phrase “to err is human, to forgive is divine” is not a biblical quote, but some Bible verses support the idea: Colossians 1:14: Says that in Christ, people have redemption and forgiveness of sins Ephesians 4:32: Says that people should be kind, compassionate, and forgiving to one another, just as God has forgiven them in Christ
@AgnesMatola
@AgnesMatola 3 месяца назад
Likai Ntate
@JummahNelson
@JummahNelson 3 месяца назад
❤ lipopo
@SymonZemben-gd3ne
@SymonZemben-gd3ne 3 месяца назад
Much love to you Limpopo FM with your team,Mr Born kalindo and Bakili TV we love you all keep it up leave long with 🐐🐐🐐
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 3 месяца назад
People are sleeping literally without food yet they can spend all this huge amounts of monies just to protect themselves.May God honestly judge them.God bless you in and may he always protect you
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 3 месяца назад
Michael Usi wanted that position of vice president of Malawi than Chilima who helped MCP to come back to power after a lot of years
Далее
pumpkins #shorts
00:39
Просмотров 30 млн
EVANCE MELEKA - ZONSE TAONA - KWAYAKA MOTO
6:07
Просмотров 1,1 тыс.
The History of University of Limpopo
6:51
Просмотров 2,6 тыс.
Это просто волшебная рыбка...
0:21
ТВОЙ БАТЯ И ТИКТОК😂#shorts
0:59
Просмотров 4,8 млн