Chakwela zoona tikufuna kuti atchokepo akuononga dziko,,tsono futso langa ndilakuti,,,,kodi pa udindo wa president akhalapo ndani,,????? Kuwikapo Peter Mutharika pa mpando wa president kumeneko kukutsonyedza kuti ife a Malawi ndife olephela,, chifukwa a Peter Mutharika kuwa tchotsa kwao,,,,anawatchotsa chifukwa cholephela tsono tidyetso dzolavula zija kodi????? sindine wa MCP koma kubwedzelapo Peter Mutharika ndikulephela kothelathu.
Would it not be possible to send delegates from religious and traditional leaders to discuss with the HE DR.CHAKWERA other than demonstrations that will cost lives of innocent Malawians and their properties looted.
Amalawi simukwanisa ,mantha ali pwiiiiiiiiii......inu mungawilikise 4dys osaima?onani anzanu ku Kenya apapa mawanso akuymbilanso akuti Pure aturuke ku state house izipit,inuyo mungakwanitsa?kumva bullet gun nkutawa😂😂😂😂.
Popita Aliyense kumeneko tiza pita ndizi kwangwe,akazango bwera wosokoneza Kaya ndiwa polisi,enafe siti maombereka tayembekezani muzaone zaku Kenya zija zachepa Aliyense popita ofunika chigubu cha madzi pamene apólice aku ponya ma tear gas ife tonse tizi za samba m'maso ngati Chigawo Chaku m'mwera azitenge Bwino tikhonza Ku za bweza Ndi Mabullet,ou posso dizer que podemos usar Armas com muito mais bara,wait we are getting ready for any attacks