Тёмный

Wakatolika uyuyu Amutapa posachedwapa😂😂🤣😂😂 

Malawian Cameras
Подписаться 24 тыс.
Просмотров 69 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 июн 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 342   
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py Месяц назад
Ndipo abale chilima adalakwanji tikamaona ma pick Ake ngat Ali Moyo mwapheranji? Achakwera mudalakwisa inu ? Chilima waferanji? 😢 Talira AMALAWI mwapha dzuwa likuswa mtengo tikuona yehova akukususani Kuti bwanji sumudakhilukire ngat amalakwisa ? Anthu OIPA inu amcp amalakwa chiyani chilima? Mudzisuse achakwera ndi m,boma lanu pangani lizayini MWAONESAT nyasi kupha vice President wanu komat ndatiii inuyo Mufa mwachabet
@user-yz4mx7py3b
@user-yz4mx7py3b 26 дней назад
Powerful preaching may the Lord show us the way coz we are lost in wilderness this government eshh full of wicked leadership 😢😢
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e Месяц назад
God protect you in Jesus name because this speech is is very important to learn something and open eyes of Malawian
@nnmzakwachamzakwacha9405
@nnmzakwachamzakwacha9405 Месяц назад
Just say God protect you/us not in Jesus name... Jesus equally was protected, wasn't God but a messenger. +2773@440799
@user-vp5ez1dp6y
@user-vp5ez1dp6y 27 дней назад
Oo
@peterkampira7613
@peterkampira7613 25 дней назад
Amen Amen . You are preaching to us really. May the Lord my Father protect my father.
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Месяц назад
Apa Pali mau or satana wachita manyaz Be blessed papa
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 26 дней назад
Ndipo kwambiri tu mmm, atampachika pamtanda anagawana zovara zake esh
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 27 дней назад
Akatolika sangawapute dala azingomuyangana ameneyo 😂😂😂
@PreciousChiphwanya
@PreciousChiphwanya 27 дней назад
Amugunde aone ndindaletu imeneyi kut ayerekezi aona pompopompo, ndipo anthu awa ayabwa sanati uku nkuyamba chabe
@simeonkhamwaha8529
@simeonkhamwaha8529 26 дней назад
​@@PreciousChiphwanyakkK ndipo kwambiri sangayelekeze ayi mistake imeneyo
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 Месяц назад
Father Elizeo mtalika ndi wansembe opanda mantha and amalarika za uzimu komanso zochitika mu dziko lathu la Malawi,, Ngati Chakwera akufuna kuti apenge Misala ayelekeze kumugunda.
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 27 дней назад
M,busa opanda mantha eshhh ambuye MULUNGU akusamalireni ndipo muli uthenga umu ndi Ma ves ake
@jumagombeza486
@jumagombeza486 27 дней назад
Kkkkkkk koma ndipo 😅😅😅😅😅😅😅😅😅kkkkkk apalamule chitedze aone
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 27 дней назад
Ndipo sangayerekeze
@matildakaudzu5027
@matildakaudzu5027 27 дней назад
Ndipo ine ndinamudziwa thawi ya covid anauza a bishop kut ine ndimatumikira mulungu osati muthu ndipo adakana utseka church adat akatseka church matendawo atha bwanji pot tisiya upephera
@MaggieCement
@MaggieCement 26 дней назад
Amen kumwamba kumve kulira kwa ana ake
@DivineMercy-df2pu
@DivineMercy-df2pu Месяц назад
This is how God expose wicked people ndipo awa nde agwidwa ufiti ndithu.
@ulemujumbe8501
@ulemujumbe8501 Месяц назад
God 🙏 please protect this man at all cost
@ErnestAllex
@ErnestAllex Месяц назад
Ikakwana nthawi yoyaluka or ukamat ukukoza umayalukabe😂😂😂
@augustMag
@augustMag 26 дней назад
Si iye amene akuyankhula koma ndi mphamvu ya Mulungu imene ikuyankhula iye wangokhala chinkuza mau komanso sanatchure dzina la munthu ayi iye akungolalika ❤❤❤❤❤
@user-pr3xg9fg9y
@user-pr3xg9fg9y 24 дня назад
Nde aphunzitsi Aja ankati something is rotten in chani?
@AustiniHendersoni
@AustiniHendersoni Месяц назад
Poti tili mudziko lodana ndi chilungamo koma ichichi ndi chilungamo
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka Месяц назад
Sanga mange sine mkatolika km mkatolika mene ndimadziwa sangayerekeze kutalitali sangafikeko olo
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 27 дней назад
Ndipo kwambili vuto ndiloti anthu timadana ndichilungamo,komatu ndibwino kufa chifukwa choyamkhula chilungamo
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 27 дней назад
Iwe nde ukudziwa
@AustiniHendersoni
@AustiniHendersoni 27 дней назад
@@inessmsiyambiri8517 kod inuso mutichan apa
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 25 дней назад
Akatolika ndiye anthu oyenerera kapena opemohera zenizeni?
@patrickndojime1632
@patrickndojime1632 Месяц назад
Father munthalika mumakwana Mulungu ankhale Nanu nthawi zonse
@EmilyLipande
@EmilyLipande 20 дней назад
Go deeper Father Elizeo M'talika
@UwaisBakhas-hw7eb
@UwaisBakhas-hw7eb Месяц назад
Ameni powerful massage man of God.
@EvanceSungani-cv9jk
@EvanceSungani-cv9jk Месяц назад
I think Malawi was blessed with people of intelligent kuposa charakwe wen weniyo,,,, this is bravo Sir your good Lord protect you and okunva wanva osanva asanve your mwana mlomwe wakwathu wen wen😊
@SithembilePhiri
@SithembilePhiri 26 дней назад
Amen and amen ambuye avumbulise zochuluka kuzera mwayinu. Papah God bless you
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 27 дней назад
AMEN AMEN abusa awa ndawakonda ndipo mu dzinala YESU samangidwa chilimatu adali ofunika kwa anthufe koma kwambili akatolika amkomkondatu chilima
@petertaulo8014
@petertaulo8014 Месяц назад
😂😂😂 this is great message
@AnnastasiaChakwiya
@AnnastasiaChakwiya Месяц назад
Ntalika ndi one
@user-ve4zn2ne1k
@user-ve4zn2ne1k 29 дней назад
This is talented Bishop in love with Jesus ,you are really a man of God.
@owenmoses9434
@owenmoses9434 Месяц назад
Bravo bishop may God bless you and protect you wherever you are
@samsonyuda674
@samsonyuda674 Месяц назад
It's true something is ltt thank you man of God ❤🎉
@dumisanimoyo3152
@dumisanimoyo3152 27 дней назад
Something is rotten in the state of Denmark 😅😅😅😅😅 u r so creative mubusa keep it up mupaka manyazi awagwire anapanga zopepera kwambiri
@suprianomgalla5512
@suprianomgalla5512 26 дней назад
Something is rotten amwene 😅😅
@agnessjuttah7491
@agnessjuttah7491 25 дней назад
😂😂😂😂😂🙌🏻🙌🏻🙌🏻
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu Месяц назад
May God bless you sir kuyankhula kwa mzeru ndithu umunthu palibe
@bornface4786
@bornface4786 Месяц назад
Mulungu akudalitseni bambo anga kumalawi kukufunika anthu odziwa mau amulungu ngati inu
@BennieKanama-yr3sh
@BennieKanama-yr3sh 7 часов назад
Powerful message father
@DavidMtambo-zm8ne
@DavidMtambo-zm8ne 17 дней назад
Chakwera mpando womwewo kumphà mzako sure, wazelezekatu iwe, timve kwa mubusa uyu unyongedwa siiwe mulungu.
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Amen powerful Zowona ndithu zachisoni ndithu
@sulleahmnyimbili1362
@sulleahmnyimbili1362 26 дней назад
Ndipo sitingayiwale akunama amenewo, Amen Bishop powerful teaching
@FelixJackson-qg7nw
@FelixJackson-qg7nw 14 дней назад
Powerful
@user-wv5hz8ce3i
@user-wv5hz8ce3i 27 дней назад
Nkhani iyi ndiyoona ndithu wakwiya ndi mfiti amen man of God ❤
@ThokoMsonkho-hy4uc
@ThokoMsonkho-hy4uc Месяц назад
Akuti akulemekeza malamulo a dziko koma anthu omwewo akupwanya malamulo daily
@ZakawiroNkhoma-qs7nq
@ZakawiroNkhoma-qs7nq 12 дней назад
Amen,,let's God protect you....man of God
@isabelmartin7567
@isabelmartin7567 27 дней назад
Tidakali mu chikangawa 😭😭😭adalakwanji achilima mpaka kuchita chozinga 😭😭
@user-kc7sh2ey4r
@user-kc7sh2ey4r Месяц назад
Powerful messages mn of God
@hopesato
@hopesato 27 дней назад
History is the best teacher... True should be spoken
@EnelessLundu-sn8om
@EnelessLundu-sn8om 27 дней назад
Manganya wakangaza kutenga mpando😂
@PaulMdezah
@PaulMdezah Месяц назад
Mawu a bishop mwatiyakhulila zakukhosii🤗
@CATHERINE-rk5rk
@CATHERINE-rk5rk 25 дней назад
Mwainu timakondwera bambo mthalika god bless you all the time 🙏🙏
@user-ji3in4cp3m
@user-ji3in4cp3m Месяц назад
Ambuye akhale nanu munthaw zomse
@AlifeChiwanda
@AlifeChiwanda 27 дней назад
Amen wakuvayo wava may God protect you
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka Месяц назад
Ameeeeeeeeeen powerful abusa ndye anthu asakayikile kuti apha chilima ndiwowo m'busa oyipa
@mphatsophiri8882
@mphatsophiri8882 11 дней назад
Amen father Elizeyo m'nthalika,
@ivychithyoka1551
@ivychithyoka1551 Месяц назад
Our Father in Catholic ....Amen
@WezzieChimuzi-ek7bk
@WezzieChimuzi-ek7bk 29 дней назад
Mmmmm kulila kwakukulu uku Munthu wa Mulungu....Ambuye akutetezereni ndi mwanzi wawo mwalila kwachikulu Papa
@frankjolijo
@frankjolijo 25 дней назад
Tifela mbendela imeneyi🙏👊💪🔥
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju Месяц назад
Zinsinsi ndi zanu baba zobvumbuluka ndiza ife anthu akudxiko lapabsi....bi blessed bishop
@peternashyo9850
@peternashyo9850 Месяц назад
Ulemu ndi matamando zipite kwaiye mwini moyo. ❤ Long live Fr.
@ivychithyoka1551
@ivychithyoka1551 Месяц назад
Man of God!!!!!!!!
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 27 дней назад
ALLAH is the greatest
@HenryLaidon-pl9ly
@HenryLaidon-pl9ly Месяц назад
Munthu ndi THUPI NDI MZIMU paodzi, tsopano thupi takwikila yatsala Ndi MIZIMU ndipo MIZIMU IMENEYI IZUNZA KOOPSA kwa iwo opanga NTCHIMOLO, MTENDERE SADZAUPEZA UFULU SI NDALAMA ndipo CHIKUMBUMTIMA ndiyo nthenda yoopsa kwambiri komanso CHIKONDI NDILO LAMULO LOPAMBANA MALAMULO ENA ONSE
@ireenbottoman8120
@ireenbottoman8120 3 дня назад
Our own fearless and courageous Father
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 27 дней назад
Malawi need brave priest like you and don't be scared for God is greater than everything
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 27 дней назад
Amen Father ndipo osaopa potumikira Ambuye satana achite manyazi
@user-hk1kj9bk7b
@user-hk1kj9bk7b Месяц назад
Murungu akudaritseni abunsa ,chirungamo ndithu ma drama alowa
@aaliyah3109
@aaliyah3109 25 дней назад
Mulungu not murungu Akudalitseni not akudaritseni
@maggielothisonkosi3671
@maggielothisonkosi3671 23 дня назад
Amen and amen powerful message and very true fear not God is with you and is above all things
@SteveChirwa-ne9nt
@SteveChirwa-ne9nt Месяц назад
Zoona apa ayaluka achakwera amasileni anon kalindo ndi a Mr kamlepo kalua mukumva mau amulaliki mnzanu Koma inu basi kutengera mphamvu mukugwilitsa.apolice kukhala chida chanu phepani
@janemvubu7750
@janemvubu7750 Месяц назад
Mawu achilungamo ndipo zoona zenizeni Amen
@HarrisMathew-ve5ib
@HarrisMathew-ve5ib 25 дней назад
Powerful message 🙏 alindi makutu wamva basi
@manualrapheal6048
@manualrapheal6048 Месяц назад
Amutapa bwanji popeza iye akungowerenga za 1.8 billion yrs ago?
@Mervic-vm8eo
@Mervic-vm8eo 27 дней назад
Wakwiya ndi fiti,,chakwera unatilakwira ife amalawi😭😭😭
@user-dt8nr1zx6e
@user-dt8nr1zx6e Месяц назад
Amen mawu osaopa munthu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Месяц назад
Mtalika auze zenizeni a atonse alliance wa😂😂😂😂
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 26 дней назад
Kkk
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 26 дней назад
@@user-ky4ce9gb6j 😃😃😃😃😃😃
@PatrickLloyd-qm2dq
@PatrickLloyd-qm2dq Месяц назад
Chilungamotu ichi .... awa agwidwatu ufiti
@emmanuelmoffatmkaleya4105
@emmanuelmoffatmkaleya4105 26 дней назад
Ife akatolika sitiwopa chilungamo, ayelekeze zimenezo awonanso , zinamukanika Kamuzu awa ndindaniso 😂😂😂😂
@user-vq5qm1sg1e
@user-vq5qm1sg1e 27 дней назад
Amen 🙏 mulungu munthu wamba ,amayankha mnthawi yake ,amamva ndithu kulira kwathu
@user-xh1ve5ym3l
@user-xh1ve5ym3l Месяц назад
Pangafupe, or pangatalike chowonadi chidzaziwika.
@user-nt6qr8vs6e
@user-nt6qr8vs6e 26 дней назад
Powerful words father..
@powercharios2087
@powercharios2087 27 дней назад
May the Lord be with you Father and protecting you kwadani amene amadana ndikuunika
@user-yz5ic6ky7z
@user-yz5ic6ky7z 29 дней назад
Shaaaaa Koma anthu ena anyamula ma tsoka ndithu
@johnkayira8188
@johnkayira8188 19 дней назад
GOD bless you for the truth preached
@ThandiBinali
@ThandiBinali 26 дней назад
AMEN AMEN Father Mulungu akufungatileni
@louismagongwa
@louismagongwa 29 дней назад
kuyakhulatu uku 😅😅😅😅 wakuv wava apa
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani Месяц назад
Amen 🙏🙏🙏 Bishop
@sukiemapemba4094
@sukiemapemba4094 29 дней назад
Eeeeeee ulaliki okoma Kwambiri Amen bishop
@fjtkusamba5948
@fjtkusamba5948 24 дня назад
Alemekezeke chauta chifukwa cha uthenga wakuya ngati umenewu ndipo ulemelero ukhale Kwa mulungu Ku nthawi zosatha, amen.
@GeraldHaltonJnr-vs9wc
@GeraldHaltonJnr-vs9wc 18 дней назад
Fr Elizio Mthalika this is a true definition of calling and photo yiii siyakenso try
@MalawianCamera
@MalawianCamera 18 дней назад
@@GeraldHaltonJnr-vs9wc true
@jonathanmasebo1591
@jonathanmasebo1591 Месяц назад
Powerful speech Amen
@DoreemSemu-ho3lt
@DoreemSemu-ho3lt 26 дней назад
Eeee ulaliki obaya ,ulaliki wastraight long live father nthalika dzikoli likufunika anthu ngati inu
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 27 дней назад
Wow!!! wa nsembe wolimba mtima zedi Ambuye amutetezere Madera onse amoyo wake
@user-dd8ds6wk5q
@user-dd8ds6wk5q 26 дней назад
More fire Bishop
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 Месяц назад
Uthenga wamphamvu kwambiri chauta yekha akudziwa chisisi chili pamenepa, amen munthu wamulungu.
@collennyadile8179
@collennyadile8179 Месяц назад
koma chilungamo ndiye chimenechi zovala agawana kale chakwera alibe chisoni ndi infa ya chilima koma aziwe infa yilibe kuti ndine president dziko lilibe mwiniwache
@HenryLaidon-pl9ly
@HenryLaidon-pl9ly Месяц назад
KHALIDWE NDI CHUMA osati CHUMA NDI KHALIDWE ndati osati CHUMA NDI KHALIDWE, tiyeni nazoni ndipo kumva CHIDZUDZULO NDI MBALI INANSO YA MUNTHU
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Месяц назад
Azitumiki omwe akufunika ku Malawi kuno ndi amenewa oyima pa chilungamo osaopa ife kuno ku Ntcheu Central BAWI near Nsipe tikuti AMEN 🙏
@user-oe6hy4fy5v
@user-oe6hy4fy5v 23 дня назад
Munthu WA Mulungu samaopa go deeper man of God with no fear
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 13 дней назад
Manganya ndi yudas yemwe.anapereka yesu sidzikusiyana lero iye wapereka chilima mmanja mwa cakwera kuti amuphe ambuye akuyendere manganya ndipo mzimu wa cakwera ukukathe
@ChimwemweMaganga-pg8nr
@ChimwemweMaganga-pg8nr 24 дня назад
🎉go deeper
@EagerChicken-qj6xu
@EagerChicken-qj6xu Месяц назад
Zoonadi abambo mumakwana.
@FrancoKaunga-rq2ki
@FrancoKaunga-rq2ki 27 дней назад
Amen God is faithful one day truth shall set us free!
@user-qs2tx7wt6g
@user-qs2tx7wt6g 27 дней назад
Malamulo amati bwanjiii kapena uzilowesa ndalaaa
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Месяц назад
Amen!!! Kwezani volume anvesese aghothiwa!!!!!
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r Месяц назад
Tell them the truth man of god baibo rimati muzaziwa ndi zipaso zawo paziko rapansi pano pari ana amurungu nde parinso anthu amurungu osama sokoneza apapa
@user-gg9hw4oj2v
@user-gg9hw4oj2v 19 дней назад
😂😂😂 good
@user-on9qy6is4z
@user-on9qy6is4z 29 дней назад
Amen and i hope all this drama will end somedays in Malawi
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 27 дней назад
Ambuye akhale nanu amen 🙏💖💖
@norabanda3891
@norabanda3891 14 дней назад
Kuthamanga kusankha Vice President ku ndikufuna kuti tiiwale mwachangu indeeee.....look at how social media is plastered with the Vice President dramas...hmmmmmmm
@EsnartMbalale
@EsnartMbalale Месяц назад
Abuye akutetezeleni muthawiyanu yose chifukwa chotulusa chilungamo
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 26 дней назад
Ndipo kwambiri tu mmm
@SherifaG.Mlelemba
@SherifaG.Mlelemba 21 день назад
Ulaliki..... SOMETHING IS ROTTEN......INDEED....😂😂😂 REALITY KILLS....When you stand in justice,you'll have been enemies.....
@ShadreckKusani-vi5ki
@ShadreckKusani-vi5ki 29 дней назад
Man of God amen,,
@TaweniChavulaKamwendo
@TaweniChavulaKamwendo 27 дней назад
Eeeee 🙄.nkhopa 😂😂😂
Далее
BISHOP MTUMBUKA'S HOMILY ON LIFE AFTER DEATH
6:39
Просмотров 3,7 тыс.
Rev. Alexander Kambiri preaching at Chibanzi, Dowa.
20:56
How to Measure ANY Cliffs Height with a Rock
00:46
Просмотров 12 млн
Born Kalindo Watulukira wafikira Kung'alula
15:31
Просмотров 4,8 тыс.
SILIKALI KUWULULA ZA IFA YA ACHILIMA 😭😭🙏
9:06
How to Measure ANY Cliffs Height with a Rock
00:46
Просмотров 12 млн