Chapter chimenechi mwalembedwa zoti Yesu ndi Ambuye komanso mwalembedwaso kt Yesu ndi mwana wa Mulungu zomwe inu mumazikana mumati Yesu simwana wa Mulungu komaso Yesu si Ambuye, koma zili m,buku lomwe mukuwerengalo. Brother ndinu achiphamaso ongotsata zomwe zikupanga suit mchiphunzitso chanu
Agnes Katwela ndipezeni panambala iyi +27715528411 (Whatsapp) kapena muyimbe pa +27786868209 or ndilembereni pa facebook mungopanga search Elias M.Pemba,kapena email pa epemba3@gmail.com
Anakuuzani kuti yesu ndi mulungu ndani ????? Ife a Christu we don't say Jesus is God ..but he is the only loved son by God sent ...the Messiah ....the rest are just bogus