Тёмный

Malemu John Tembo; Tidzamukumbukira bwanji ngati amalawi 

Bakili Muluzi TV
Подписаться 113 тыс.
Просмотров 57 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

30 сен 2023

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 242   
@husseinmoffatt
@husseinmoffatt 10 месяцев назад
Muluzi TV ndi number One tchanelo of Malawi utube I like you man
@rosseshaibu1576
@rosseshaibu1576 10 месяцев назад
John tembo no rest in peace wakumoto basi
@staceycossam5933
@staceycossam5933 10 месяцев назад
Kkkkkkkkk
@daviemafunga
@daviemafunga 10 месяцев назад
Kkkkkkkkkkk
@TakosaGideon-ho6ng
@TakosaGideon-ho6ng 9 месяцев назад
Nobody knows it's only God who can judge...
@user-vu8si9eb6k
@user-vu8si9eb6k 10 месяцев назад
Akumudikila achina mr Dundudzu chisiza Mr chipembele ndi amalawi ochuluka omwe anawampa 😭😭😭😭😭😭😭💔💔💔💔💔
@elizamaster2168
@elizamaster2168 10 месяцев назад
Km brother inuyo mumayimad pachlungamo, ndpo simumawopa, mulungu apitilize kukutetezan🙏
@CHINDEBVU
@CHINDEBVU 10 месяцев назад
We will remember him like Malawian Yudas
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 10 месяцев назад
He always stood for evil. He supported one-party system during Kamuzu. During Bakili he supported 3rd term just to fight Gwanda Chakwamba.
@GwazaGomuzy
@GwazaGomuzy 10 месяцев назад
😂😂😂u are right 👍
@CHINDEBVU
@CHINDEBVU 10 месяцев назад
Mu history yathu tili ndi nthawi yokumbukira achina John chilembwe Ndi gulu lake Achina Sangala Gadama Ndi ena Otero Osati anthu amene sanapindulire amalawiwa Tilibe ubwino wawo ndithu Kwa munthu amene anasatapo kapena kumva za mcp bwino lomwe Palibe angaifunire Rest in peace gulu limeneli Asogoleri ambiri ankalimbana ndi Asamunda nkumaika anthu awo pasogolo koma anthu awa amazuza anthu awo osusna nawo nkumaphedwa Zooona mmalawi weni weni Rest in peace Kwa zigawengazi Osaisunga bwanji misoziyo tizalire pa chilembwe day either kumukumbukira Bingu better than this crimals
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 10 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 10 месяцев назад
@@CHINDEBVU You're very wise
@user-fl7br3dw4h
@user-fl7br3dw4h 10 месяцев назад
Timakonda kumvela khani zanu big course mumaikamo chilungamo chokha chokha. Big up broh
@prayphiri3184
@prayphiri3184 10 месяцев назад
Please give us history of Gwanda Chakwamba and why kamuzu choose him over John Tembo to be success of MCP
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 10 месяцев назад
Zainu aliyese akudziwa Big up Mr kma za RIP kwa chigawengachi ndepalibe
@umalikawiya9995
@umalikawiya9995 10 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 10 месяцев назад
Kip doin de good work bro God is and will protect u. Munthu ochita zabwno amalandila madaliso. Upitilize kusegula anthu maso.
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 10 месяцев назад
It's very complicated to remember this man his death when we remember our parents who died through him and Kamuzu Banda Cecilia Kazamila eish munthu amakoma akamwalira only God knows rest in peace
@gregchisuse830
@gregchisuse830 10 месяцев назад
Akazipedza ntchito zake zoipazo
@WashingtonMalunga-cw2pe
@WashingtonMalunga-cw2pe 10 месяцев назад
All in all we shallow remember Tembo but in a wrong way Mzimu wa Gadama on repeat
@josephphiri4185
@josephphiri4185 10 месяцев назад
The great historian. Man u r a good narrator ever, sending some from Lusaka Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲
@cheruartsofficial
@cheruartsofficial 10 месяцев назад
You are a powerful researcher. I like how you put pieces together. I have learnt a lot of historical facts for malawi. My father is zambian but mother is malawi. Great documentary.
@martinkalaka2667
@martinkalaka2667 10 месяцев назад
Resting In Piece Mr Tembo we don't want unnesessary history please only God judges the problem
@eunicemoyo6024
@eunicemoyo6024 10 месяцев назад
Nanga osasiya kumveselako bwanji hiyaaa
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 10 месяцев назад
Chipepeso kwa mabanja omwe sawona chilungamo pamilanduyi. Apume mumtendere. Thank you for documenting our history.
@AshrafuBwanali-qi3my
@AshrafuBwanali-qi3my 10 месяцев назад
Ànzanu atulusatso mbili yake koma sitinamvele kudikla inu inu Mulungu anakupasan nyota yakayankhulidwe mukamayankula munthu amamva sekeseke
@JacksonDamiano-ko8ui
@JacksonDamiano-ko8ui 10 месяцев назад
Our own interpreter ❤️🔥🔥 Rest in peace Mr Tembo🙏🙏
@mataxsimon1737
@mataxsimon1737 10 месяцев назад
penatu I just like your voice, koma kanyimboko mopempha ndimayesera kukasewera pa keyboard, I wish simudzandipanga sue?
@ibrahimmeemzy9754
@ibrahimmeemzy9754 10 месяцев назад
Original bakili muluzi tv ❤❤❤
@dingiswayokatundu2696
@dingiswayokatundu2696 10 месяцев назад
May the blessings of anger fall upon him
@christophermkhize1991
@christophermkhize1991 10 месяцев назад
Ndimakhala ndikudikilila kuti no matter what muyiponya imeneyo big up bro mulungu adzikhala nanu nthawi zonse my brother
@staceycossam5933
@staceycossam5933 10 месяцев назад
Kkkkkkkk this guy yooo
@webstermbewe8395
@webstermbewe8395 10 месяцев назад
Thanks for the nice video continue providing wonderful data
@ChomeNgondolo-uh5mu
@ChomeNgondolo-uh5mu 10 месяцев назад
Mwanena mwanena basi chilungamo chimawawa but anyway ndimamukonda John tembo moti nkhata yanga ndiyo ili patsogoloyo ndukapeleka 🔥
@Sandi-xr6ug
@Sandi-xr6ug 10 месяцев назад
Akanyimbi ozola manyi ku maso
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 10 месяцев назад
Big up bro you need to be our president future
@JacksonDamiano-ko8ui
@JacksonDamiano-ko8ui 10 месяцев назад
Big up bro out own interpreter ❤️🔥🔥🔥🔥
@abisalomchunga6695
@abisalomchunga6695 10 месяцев назад
Thanks brother 🙏
@user-hs5xv6bk2f
@user-hs5xv6bk2f 10 месяцев назад
AAAA munthu woyipa uyu Joni unawona ngati uzakhala wamuyaya unapha azibale anthu iwe
@gracetjomane-jj3ib
@gracetjomane-jj3ib 10 месяцев назад
Mbamba bigger wanga❤❤❤❤❤🎉
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 10 месяцев назад
Imfayi osatengakoso amene akutizunza lerowa bwanji apite onsewa basi
@edsonndalama2334
@edsonndalama2334 10 месяцев назад
We can't remember him without remembering the death of Aaron Sangala, Gadama, Dick Matenje and some other people who were sent to their early graves because of politics.
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 10 месяцев назад
Tidzamukumbukira ngati mfiti. Kupha ndi chikhalidwe cha MCP. Pano ikupha a Malawi ndi njala.
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 10 месяцев назад
God will continue to panish you where ever you are, Enjoy it John Tembo 👉🔥🔥 Kadzamila will join you very soon
@christopherbottoman9131
@christopherbottoman9131 10 месяцев назад
Congratulations bro everything else is good
@humairamalombe295
@humairamalombe295 10 месяцев назад
Tembo kungoka pulumuka ku ufumu wakumwamba dziwani kut anthu onse okupha alubino akapulumuka pamodzi ndi aliyense amene anaphako munthu, mwachudule dziko lonse lapansi likapulumuka
@Cr7bianca
@Cr7bianca 10 месяцев назад
I love you bro
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 10 месяцев назад
My king ❤
@user-tg8ye9yp8p
@user-tg8ye9yp8p 10 месяцев назад
Ndimupemphe mulungu kuti amukaniretu ameneyi pansi pompano asanamukwilire. Galu wa sankho ameneyi, anabalitsa umasiye ku mtundu wa amalawi, Nsaname ankhanza asamamveredwe chisoni. 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥Apserere ku gehena akupitako
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 10 месяцев назад
Thank you bg mn respectful
@YusufRahimu-be9hu
@YusufRahimu-be9hu 10 месяцев назад
Big man❤❤❤❤
@JohnesDishan
@JohnesDishan 10 месяцев назад
Ndizamkumbuka ngat chimuthu choipisisa pokupha a Malawi azake Rest in fire
@TakosaGideon-ho6ng
@TakosaGideon-ho6ng 9 месяцев назад
Nobody knows it's only God who can judge..
@LUCIUSCHARLES-ei5vu
@LUCIUSCHARLES-ei5vu 10 месяцев назад
Yeah salute big
@user-tp7ze7qy3s
@user-tp7ze7qy3s 10 месяцев назад
Ayende bwino ku gahenako ameneyo
@frankchavula3594
@frankchavula3594 10 месяцев назад
Next mai kazamila dai please
@robertchikaonda-mu1bg
@robertchikaonda-mu1bg 10 месяцев назад
I hope he is enjoying the 🔥
@ashikalam8616
@ashikalam8616 10 месяцев назад
We will remember John Tembo as a thug .
@ziwani3682
@ziwani3682 10 месяцев назад
BIG 👍
@rosseshaibu1576
@rosseshaibu1576 10 месяцев назад
John tembo ndimunthu wakumoto
@ishmaelmkuluma2013
@ishmaelmkuluma2013 10 месяцев назад
Azikhale ngoma ndale ndizosala tembo ndameneo wafayo uziyakhula bwino ngt uzafa wamva umuuzeso cakwelayo kut amwene tifa tiyen tizikhala bwino ndi anthu
@KanguwoGift
@KanguwoGift 10 месяцев назад
Nah I can't say rest in peace coz I know that he is not going to rest this guy did alot there rest for people who did murder
@TakosaGideon-ho6ng
@TakosaGideon-ho6ng 9 месяцев назад
Nobody knows it's only God who can judge.
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 10 месяцев назад
Exactly madder case Brah
@francispanyenyeramithi764
@francispanyenyeramithi764 6 месяцев назад
This man has a stinking legacy.
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 10 месяцев назад
Munthu wankhanza, wakupha, opanda chisoni
@user-qv6ey9ul9w
@user-qv6ey9ul9w 10 месяцев назад
Following 😊
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 10 месяцев назад
Go's round comes round palibe wamuyaya anayiwalazimenezo
@ririvilla1423
@ririvilla1423 10 месяцев назад
😂 You are funny ya interpreter yokhayo wakhwana
@WysonChinyangalala-qj6oo
@WysonChinyangalala-qj6oo 10 месяцев назад
❤❤❤
@user-qi8xe7qh1e
@user-qi8xe7qh1e 10 месяцев назад
Ndiyenso choti aziwe zikhale ng'oma pano sikuseli kwa 2000 kuti anthu abadwa nthawi ya bakili muluzi kuti zithu zonse zinali chonchi kuseli kwa 2000 kunalibe tv kunalibe ma Radios komanso ukangoyelekeza ku chula zina la kamuzu amakuuzakuti ankhwazi akukumvani ku sanjika kukhala ngati malawi yonse anayi microphone everywhere anthu amaletsedwa kupanga mabissines bottom line John tembo tizamukumbukila ngati munthu mmodzi oipa kwambiri kuno ku malawi John tembo kamuzu banda anali anthu oipa kwambiri Ndiye pano mmalo mwa john tembo akufuna akhale mulowammalo wake zikhale ng'oma munthu oipanso kwambiri
@shaik4123
@shaik4123 10 месяцев назад
Akuti Nyimbo ikhale Nzimu wa Agadama
@edwinrobert5346
@edwinrobert5346 10 месяцев назад
Rest in peace Mr Tembo
@BenissoneErnesto-kn9bd
@BenissoneErnesto-kn9bd 9 месяцев назад
Mai mulungu wanga ine Joni tembo nde panopo Ali kuti siwafaso mulungutu simunthu
@staceycossam5933
@staceycossam5933 10 месяцев назад
Yooo kkkkkkkkk great guy
@VioletChikopa-mx1ye
@VioletChikopa-mx1ye 9 месяцев назад
Jon tembe anayili munthu oyipisisa ngati chakwera nd zikhale Ng'oma
@user-px9jd9co3v
@user-px9jd9co3v 10 месяцев назад
Akawapeza komweko onse omwe anaphawa ..
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 9 месяцев назад
Rest in the 🔥🔥🔥 John Tembo , Kadzamila will join you later 👉🔥🔥🔥
@juniortsegula3847
@juniortsegula3847 10 месяцев назад
Udasi😢
@TakosaGideon-ho6ng
@TakosaGideon-ho6ng 9 месяцев назад
Nobody knows it's only God who can judge.
@JumaMboneka
@JumaMboneka 10 месяцев назад
Mumakwana big ulemu wanu
@ChikumbutsoPumani
@ChikumbutsoPumani 10 месяцев назад
Rest well Mr murderer
@user-ge8lf8ii6g
@user-ge8lf8ii6g 10 месяцев назад
Good
@BrightonPhiri-ug3gk
@BrightonPhiri-ug3gk 10 месяцев назад
Let Malawians mourn Tembo peacefully than br br br
@MosesShaibu-ee8hn
@MosesShaibu-ee8hn Месяц назад
It good to remind people
@williamsmanda8592
@williamsmanda8592 10 месяцев назад
Ichi ndi chigawenga chomaliza Cha MCP kukaliwa ku gahena. Chakwera adzakhala chimtseka khomo ku gehenako
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 10 месяцев назад
😂😂😂😂
@giftevans2957
@giftevans2957 10 месяцев назад
Yes
@user-hm7wh6ol3m
@user-hm7wh6ol3m 10 месяцев назад
Alright
@user-iy8vi7nn8r
@user-iy8vi7nn8r 10 месяцев назад
Rest to he'll jonh
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 10 месяцев назад
MCP kupha ndikoyamwira, they're being led by Demons 😢😢😢
@ishmaelmkuluma2013
@ishmaelmkuluma2013 10 месяцев назад
Ndipo ngt galu ameneo sanalape ndithu mulungu amulange komwe aliko mfit yamunthu nde iweo zikhale ngoma uziwe kut chuma sutenga kumanda
@DitebogoMarutle-wy8qo
@DitebogoMarutle-wy8qo 10 месяцев назад
Tidzamukumbukila ngati munthu oyipa amene adapha wanthu osalakwa satana
@inkprokasungu9287
@inkprokasungu9287 10 месяцев назад
There's no need to remember him is only cruel people who support mcp like chilima joice banda lucius banda
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 10 месяцев назад
Kodi iweyo ukakhala nawo pa chiweluzo kuti udziti John Tembo sakalowa kumwamba? Do u know the the relationship he had with God at the time of his passing? Sitiyankhula chonchi pa nthawi ya maliro galu iwe opanda khalidwe ndi mwambo
@rickiez
@rickiez 10 месяцев назад
In time like this, sikwabwinodi. Any way pakuti ndi nthawi ya demon class
@eunicemoyo6024
@eunicemoyo6024 10 месяцев назад
Rest in peaces son of jazbel pano akukondwa ku helo ndi kamuzu wake rubbish
@MUSSAHMBILINGANO
@MUSSAHMBILINGANO 10 месяцев назад
Oweludza ndi mwini chilengedwe not us
@fedson2050
@fedson2050 10 месяцев назад
Mbuzi iz zonama aaaa a Galu awa
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f 10 месяцев назад
Zoopsatu zithu zake
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 10 месяцев назад
Eeeeee koma john tembo wagwira ntchito yopha anthu iiiii
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 10 месяцев назад
Yah its not fair
@BrownKCMarcDormand-rs3es
@BrownKCMarcDormand-rs3es 10 месяцев назад
Anali Muthu woyipa kwambili Tembo anazuza azake mu ndale
@user-zp6ge9vs9d
@user-zp6ge9vs9d 10 месяцев назад
Eeee kwachema apo 😢😢
@johnchavula3282
@johnchavula3282 10 месяцев назад
Ndimadabwatu😂 kuti zikuphonyani bwanj
@victorbanda9039
@victorbanda9039 10 месяцев назад
Ndiwe chitsiru wabodza iwe Tembo anabadwira kukhola ntcheu osati Dedza
@ShadrackMsitweni-sr2uo
@ShadrackMsitweni-sr2uo 10 месяцев назад
Ulemu upite kwainu big ulibwino big serious
@user-nz8mq4ff3e
@user-nz8mq4ff3e 10 месяцев назад
Wini adziti tikufuna timange wa Bakili muluzi TV koma padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta yes zomwe tikufuna ife ndizimezi wina adziti tikufuna timange wa Bakili muluzi tv zosatheka wina asayelekeze kumanga pa Bakili TVmuluzi asafe chifukwa akafa pavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta chifukwa timakonda kwambil chifukwa chilichose chomwe amanena zoonandi ife timafufuza zonse zomwe mukunena ndizoona ndithu ndiye wina aziti tikufuna timange wa Bakili muluzi TV Malawi mono padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta padzavuta
@BenissoneErnesto-kn9bd
@BenissoneErnesto-kn9bd 10 месяцев назад
Rest in peace Mr Jon tembo
@PeterSamson-ym4mk
@PeterSamson-ym4mk 4 месяца назад
infa yayandikira 😮😮😮😮😮
@DevidoJone
@DevidoJone 2 месяца назад
Machende ske
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 10 месяцев назад
Iiiii ai mulungu amamusunga ndi cholinga poti mulungu wathu ndikhulupilika
@ramseycrown483
@ramseycrown483 9 месяцев назад
Akalowa kuthako kwa make mbuzi imeneyi. Ndisaname I don't even want to hear the name of joni tembo. Munthu oyiiipa zedi.
@user-nr2bi5zm9f
@user-nr2bi5zm9f 2 месяца назад
Tzamukimbukira chifkwa cha kupha ma minister 4 cha mma 80's
@OwenNyangu-nv1yt
@OwenNyangu-nv1yt 10 месяцев назад
Munthu wamwalira mulimbananYe bwanji?
@user-md5uv2cg6i
@user-md5uv2cg6i 10 месяцев назад
Choka iwe mbuzi
@alfredbanda886
@alfredbanda886 10 месяцев назад
Ndipo Kaya Yehova amasunga Bwanji chimunthu choipa chonchi Ndimoyo zaka zonsezi???? Ena mwaagalu akutizunza Amalawi Achina Chakwela osawapha Bwanji Dziko Lamalawi lipeze Ntendele koma akufa ndiokhulipilika kwa inu Mulungu kusiya Afitiwa
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 10 месяцев назад
Ndipo😂😂
Далее
Schoolboy - Часть 2
00:12
Просмотров 3,1 млн
CRUISE 5 WITH JOHN ZENAS UNGAPAKE TEMBO
59:58
Просмотров 234 тыс.
Europe ndi America amabisa ma Dictator chifukwa chani.
13:59
Minyama yathu ngati amalawi ikuchokera pati?
16:31
Просмотров 61 тыс.
Dictatorship tinathana nayo 1994
14:50
Просмотров 55 тыс.