Тёмный

Mary Chilima akuimira President wa UTM kulowa malo mwa Malemu Amunanu awo 

Jay Kawere Mw
Подписаться 13 тыс.
Просмотров 37 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

8 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 148   
@Royhauya-uw2kr
@Royhauya-uw2kr 16 дней назад
It's not a good idea to make Mai Chilima leader of UTM. There's time. Meanwhile let her follow her career to the top.
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 16 дней назад
Ndinaganidza izi tsiku limene Achilima anatisiya kuti Marry ngati amamukonda mwamuna wake kuchokera pansi pa mtima akuyenera kuimira u President now am so happy to hear that Osatopa osatopa Mary Ambuye akutsogolerani mu zonse chifukwa chipanichi mukapatsa munthu wina ndithu kutha kukhala komweko chikadzawina azatsintha zina Ndiye Ife sitikufuna kutichipani Cha UTM chinthe chonse Mah musafooke maso patsogolo❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 16 дней назад
🙏Zoona zake ife tikufuna chipani chisathe compaign anapanga kale chilima timangiodkira tsku
@SamJalie
@SamJalie 16 дней назад
This woman is gonna rise
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z 16 дней назад
It's not good idea at all because we all know that there is vise president of UTM, that person he is the one who suppose to be incharge despite everything.
@WisdomMaseko-fi5sv
@WisdomMaseko-fi5sv 16 дней назад
Mai Mary mukane. Anthu asakuikeni Mau mkamwa
@AminahMussah
@AminahMussah 16 дней назад
ndipo bola asamale ana awo asaluzenso Mai wawo ayii
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 16 дней назад
Mary has got a capacity to govern but only if she is willing. Azibambo ena akupangaso dyera heavy atha kuphetsa chipanichitu oooooh....
@Namphuno
@Namphuno 14 дней назад
Malangizo aulele,, mai chilima osayelekeza kulowa ndale,,ndale zimapha pitilizani zina zomwe mumapanga and live longer,,anthu akukukopani lerowa mawa atayiwala zonse azakutembunukilani kuti simunachitepo ndale muzaononga dzina lanu ndikuchosa ulemu onse wa inu komanso malemu,, osayesa.
@paulinekayuni1621
@paulinekayuni1621 14 дней назад
Munthu analowa kale ndale nde mukuti asayerekeze kulowa bwanjiso.😅 Komaso mukati ndale zimapha kodi ose atati aziopa chonchco zingakhale bwa. Aliyese azafa even amene amapha anzawo. Ndipo zimenezo ndizomwe mwina atha kulimba nazo mtima kuti ngati mamuna wake anafa iye aoperanji
@DrolieDongowa
@DrolieDongowa 16 дней назад
Musiyeni marry alire mamuna wake
@user-to5of3ks3g
@user-to5of3ks3g 16 дней назад
P
@hudycorex1893
@hudycorex1893 16 дней назад
P
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 16 дней назад
Koma anthu mumakonda kusokoneza zinthu,Marry Chilima watani? Tamusiyeni munthu musamuike maganizo opotoka, musaiwaleso Chilima munamupopaso ndinu nomwe kumuuza kuti ayambitse chipani chake
@PemphoKatembe
@PemphoKatembe 16 дней назад
Mawu
@mayamikothomson
@mayamikothomson 16 дней назад
Mayi Chilima I believe she's not a politician,Kalindo bwanji?
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn 16 дней назад
Tiyeni uko ndi Kalindo We need chilima legacy And Mai Mary chilima She was closest to skc she is only one can take utm
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 16 дней назад
Live from SA cape town muzen kaliyati Mary akurila plz
@chrisboyce2
@chrisboyce2 16 дней назад
Fredokiss president wa UTM ndipo SKC Forever in Our Hearts ❤
@MathewsNyate-y9g
@MathewsNyate-y9g 16 дней назад
Kuwafusa kaye ali ready kutero,bcz kupanga run chipani ndi ndalama
@nathannbanda3345
@nathannbanda3345 16 дней назад
Alowepo Akweni
@SildaKatundu
@SildaKatundu 16 дней назад
Kufuna kumuphetsanso eti,mulibe chisoni guys ee
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn 16 дней назад
Kufa tose tizafa we need her now to take this party
@samchibenene4458
@samchibenene4458 16 дней назад
Maganizo anga ndikuona kuti asankhe wina osati Mary ndare zotani zimenedzi munthu akayambisa chipani basi akamwarila or retirement chizikhara cha family aaaa amalawi this is another generation let's change gyz
@mosesnyirenda5010
@mosesnyirenda5010 10 дней назад
This a great idea
@LiamTennessee
@LiamTennessee 16 дней назад
A kalindo ndi amene angatsogolele bwino UTM,, Ali ndi masomphenya ,munthu okonda dziko ndi anthu ake,,
@SamJalie
@SamJalie 16 дней назад
Kalindo is illiterate
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 16 дней назад
Kalindo anasiya ndale
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 16 дней назад
Kalindo azitani ku UTM mumasowa zoyankhula eti??
@leahkasiwa5033
@leahkasiwa5033 16 дней назад
Kaliat ukhale iweyo bwanji osogolera UTM mary akadali kulira mwamuna wake please napapata
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn 16 дней назад
We need Mai Mary Chilima must take over
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 16 дней назад
Marry saphedwa mu dzina la Yesu ndipo satana achita manyanzi No matter kuti ndi banja koma tikupanga izi chifukwa mwamuna wake wamfa imfa yowawa zinakhala ali moyo Saulosi Chilima zinali zosatheka kusiilira mkazi wake mpandowu anthu inu kumaganidza pena MCP ikufuna chipanichi chithe kungoikapo munthu chisawawa akachifulitsa ku MCP aime Marry kuti chakwera achite manyanzi kuti ndinachitanji pompha Chilima uja?
@HellenNyambose
@HellenNyambose 16 дней назад
Let's people choose their leader freely
@andrewchiusiwa3487
@andrewchiusiwa3487 16 дней назад
❤❤❤
@user-es4jt6ds8m
@user-es4jt6ds8m 16 дней назад
Zoona mary aimepo ena achigulitsapo Chipani pliz osagulitsa
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 16 дней назад
❤❤❤❤😊
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 16 дней назад
Maganizo anga ndamenewo since day one SKC atatisiya, mmene nduonera mu UTM atsogoleri omwe angapitise UTM patsogolo ndi Mayi Chilima kapena Che Kaliati apo ayi atenga wakunja ngati achina Dalitso Mpinganjira or Kabambe ndekuti chikhara cha mphamvu nkuzawinaso
@user-gg9hw4oj2v
@user-gg9hw4oj2v 16 дней назад
❤❤
@KondwanKafuratira
@KondwanKafuratira 13 дней назад
Shaa!!
@TiyanjaneMkwate-we8gu
@TiyanjaneMkwate-we8gu 16 дней назад
Bola Mayi Kaliat.
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 16 дней назад
Bwanji osayika mayi kaliyati
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 13 дней назад
Mmmmh musiyeni Mary pls,sakhani ena
@williamsalexmbonga
@williamsalexmbonga 12 дней назад
Osaikapo Uncle ake a Chilima yo bwanji kuti zimveke bwino
@TaweniChavulaKamwendo
@TaweniChavulaKamwendo 16 дней назад
Eeee 😳
@MalawiRiddles
@MalawiRiddles 16 дней назад
Mom Patricia kaliyati can do that
@LimbikaniKadzongwe
@LimbikaniKadzongwe 15 дней назад
It's possible to do that ,is a right person to fill the position let her to be....
@user-xo8ms5wh2s
@user-xo8ms5wh2s 14 дней назад
Amai chonde zisakuchedwetseni izi tapangani zosamala ana anu osati iziii mama chonde ndizopanda phindu iziii
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 16 дней назад
😢 😢😢 guy's give madam chilima chance she can make it dont choose manganya his Judah's
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 16 дней назад
😢😢😢😢😢😢😢😢😢 ndalira size pangani choncho guy's sankhani mai chilima osati manganya please
@BlessingsKalonga
@BlessingsKalonga 14 дней назад
Nde Mary president adzawina chabwino ndikhare Burundi pa zandale poti sindipanga zandale
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 16 дней назад
Ndiokwanila kuima ndipo azawina
@imraanJafal
@imraanJafal 16 дней назад
Kkkk Kom ziona izi
@blessbless6929
@blessbless6929 14 дней назад
Nyimbo yake ikhale yomwe ija ya Joseph Nkasa amati mng'ono wanga
@greymitomoni4047
@greymitomoni4047 12 дней назад
ukatswiri uli pati pamenepa🤧🤧🤧
@BennieMdezA
@BennieMdezA 14 дней назад
Afuna amalize chuma chimene adasiya chilima timming ya azibambo adyera.
@StainlyMunthali
@StainlyMunthali 16 дней назад
UTM give yourself enough time to work out this gigsaw puzzle otherwise enafe mutipangitsa kuti chala changa chamukomba phala chizakhale pa holiday !
@josephinemisomali6840
@josephinemisomali6840 16 дней назад
Inendikuona ngati mai chilima apatsidwe mpata bwino bwino olira amunawo Chifukwa imfa Yangozi akulu akulu ndi imfa imene imakhala yomvuta kuimvetsa zimasiyana ndi munthu oti anadwala pena anthu mumavomereza kuti munthu anamvutika ndithu Chomwe chingachitike mwina mai Chilimawo nfikungowachita support anthu omwe angayendetse Chipanicho pakadalipano kutsogolo Kuno ngati atafuna athakudzaima ngati ndalezo zilimwaiwo masiku sachedwa
@priscaleofranknakari3117
@priscaleofranknakari3117 15 дней назад
ndiponso chifukwa chani iwonso ndiye kuti avomeleza aaa sikaganizidwe kwabwino ayi mix ndiye kuti akuyenera akwatiwenso mmm akalora samawakonda amuna awo ndithu mmmm maliro angozi ayi kuvuta kuiwala 😢😢
@MsondaBanda
@MsondaBanda 16 дней назад
Kkkkkk
@NDIZOTHEKABANDA
@NDIZOTHEKABANDA 16 дней назад
Sangakwanise
@user-yx6oo2pc3r
@user-yx6oo2pc3r 16 дней назад
Wachiwili wa malemu a Chilima ku chipani cha UTM amene ali Manganya anatuluka kalekale mu chipani cha UTM analowa malawi congress party. ndiye nkhani ya maudindo a ku UTM Manganya zisamukhudze ai chifukwa iyeyu ndi mpeni wa nsengwa wakuthwa konse konse. Madam Mary Chilima go ahead. inuyo a UTM musanvele maganizo a wanthu amene ali kunja kwa chipani chanu
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z 16 дней назад
Momwemo marry chilima uyimile kumene afitiwa awone manyi
@TheLeezo
@TheLeezo 16 дней назад
Noooo,leave her alone and let her grieve her husband bwino bwino. N I don't think politics is her thing. Akweni bwanji? That woman is a firecracker,she can make it.
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn 16 дней назад
Pakabwera wina azachigulisa chipani Ichi so mama Mary can't allow her husband legacy to be sold so she is worthy
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 16 дней назад
mmmm sakuyima msaname
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 15 дней назад
Abale a chilima ngati angavomere ayime basi mery,koma asadzipangile mwa yekha popanda akuchimuna coz pakhoza mwina kudzabwera udani Ali wapangilanji zimenezi
@tracybennie7783
@tracybennie7783 16 дней назад
Yomweyo atenge chipani basi
@JonesSiliya
@JonesSiliya 16 дней назад
Zoputsa zimenezo
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 16 дней назад
Mmmmm apapa nde ayitu koma mukwafunila za bwino mayi Chilima wo? Ganizani bwino pamenepo
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 15 дней назад
Ndiitaneni mama tidzapange surpot pamosonkhano tidzasangalatse anthu mmisonkhano yanu pliz
@user-fs5gr8iv5s
@user-fs5gr8iv5s 16 дней назад
Please osapanga zinthu mwachipwera mtima Mary chilima sangakwanitse komaso chipani chotere chikala ngati chabanja chonde ganizani modeka
@AnnoyedFallingLeaves-zp8dy
@AnnoyedFallingLeaves-zp8dy 16 дней назад
Radio yanji iyi
@masakaunga4099
@masakaunga4099 16 дней назад
Mary akudwala
@PriscahChikaonda
@PriscahChikaonda 13 дней назад
Ulendodi wa chipan ndumenewu,kuganiza kwabwanji uku.?
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 16 дней назад
Koma vice wake akhale Denice thandwe mufana wa nzeru ku mzuzu
@LottiAffati
@LottiAffati 16 дней назад
angozosiya zimenezo mamuna wake uja anali katundu olemera, mapeto ake Mary amuphanso and poti ndiwamkazi nde azamupezerera heavy
@user-jl6tr9wv3h
@user-jl6tr9wv3h 16 дней назад
It's too early give her time to mourn her husband
@christophermtonga8535
@christophermtonga8535 16 дней назад
Take note that UTM is not a family party like Dpp, Udf and Aford
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 16 дней назад
Who are you yourself talking this nonsense
@christophermtonga8535
@christophermtonga8535 16 дней назад
@@Eric-gb9ms I am a proud Malawian citizen exercising my right to share my views on the political landscape of my country, and you?.
@Shadreckdingiswayo
@Shadreckdingiswayo 16 дней назад
Kodi Mayiwa atawina koma akuziwa zoti president sayenda opanda mamuna nde mufuna kunena kuti akwatira popano palibe chikondi akaimira alire bwino bwino mamuna wake apo bii anali kale ndi chibwedzi cha nseli
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 16 дней назад
Komatu ofunika amaiwa asamale.
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 16 дней назад
Mukapanda kuzatenga bwino utm itha
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn 16 дней назад
Never and never Mai Mary will carry her husband legacy
@user-co6sc8om5n
@user-co6sc8om5n 16 дней назад
Bola kaliati osati marry Mmmm
@BrightonKamwendo-db1ci
@BrightonKamwendo-db1ci 16 дней назад
Maganizo anga ndimaona ku UTM kulibe munthu yemwe Ali ndichuma chomasuka ngati momwe analiri chilima ambili manja awo ndiouma paichi chipani sichinga ime Sono ngati Pali maganizo amarry chilima kuti asogolere tiyeni tipenphere kuti akhare iwoo pachifukwa ndipo UTM sizatha ngati zitatelo koma mukasankha mosaganiza UTM yantha basi chipanitu ndi dalama ndiye muone bwino anatisokoneza pamene paja ine ngati sapota wa UTM ndatelo
@HaroonMaundala-lg5lg
@HaroonMaundala-lg5lg 16 дней назад
Excellent mwalankhula bwino komaso moveka kwabasi. Ine ndine wa DPP koma fundo yanuyi ndagwilizana nayo. Uku nde kuphunzisana muchowonadi. Chipanichi akachitengela mosalongosoka chatha. Chifukwa chaka adatiphela chilima cholinga chake ndikupha chipanichiso.
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 16 дней назад
Amen amen Dear
@joanaKachiwaya
@joanaKachiwaya 16 дней назад
Musatibalalitse Mary yo ndiokwanira
@MaryMlomba
@MaryMlomba 16 дней назад
Izi ndiye za ziii malawi mwayamba kuitenga ngati dziko lotseweletsa
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 16 дней назад
Inu Inu VC wake uti Manganya asakupusitseni si wa UTM uyu anakakhala ndi wa UTM sanakora kukhala Vice chifukwa Chilima wafa imfa yowawa inu uyu ndi MCP mkuthekanso plan yopha Chilima inachokera kwa Maiko usi cholinga akhalepo Iyeyo musamale nae maiko Usi
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 16 дней назад
Mary alire mamuna wake bwanji sankhani wina
@user-pn6py6rf6k
@user-pn6py6rf6k 7 дней назад
Za family Kodi?
@SolokingChimzy-yt7dj
@SolokingChimzy-yt7dj 16 дней назад
Kkkkkkkkk Koma mau a Mulungu ndiowona sure..Dziko linachita khungu anthu lelo sakudziwa chomwe akupanga
@EmmyYafete
@EmmyYafete 16 дней назад
Musiyeni zimai alire maliro amuna ake,anthu mulibe chisoni mukufuna amupheso? izitu sizamwanatu
@MustapherLino
@MustapherLino 16 дней назад
Chipani cha utm chatha basi😂😂😂😂
@janssenmoyo7588
@janssenmoyo7588 16 дней назад
Terrible move.UTM constitution says what?
@sangwasa
@sangwasa 16 дней назад
I hope not
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 16 дней назад
Zipani za mabanja kkkkkkk koma Ku Malawi anaza tiye nazoni
@petertaulo8014
@petertaulo8014 16 дней назад
Kuima kwa Madam Chilima ndifundo yabwino, pali anthu ena ali ndi ma plan ogulitsa Chipani kwa Ng'ona za mabango!
@VincentNyabanga-dw9uj
@VincentNyabanga-dw9uj 4 дня назад
Marry chikuni hi
@VincentNyabanga-dw9uj
@VincentNyabanga-dw9uj 4 дня назад
Marry chilima hy
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 16 дней назад
Zama banja izi asiyeni.
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 16 дней назад
Koma koposa akhale wina mayi chilima ayi kuganiza kwanga chifukwa panopa Ali ndimaganizo ambili
@PeterThomas-o9k
@PeterThomas-o9k 10 дней назад
Yoooohh Haybo she still crying his Husband she can't be leader that is people talking lie things
@SeanMatora
@SeanMatora 16 дней назад
Izizi ndi zomwe zikufunika Mary atenge mpando bas....❤
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z 16 дней назад
It's not good idea to be honest
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 16 дней назад
Even Patricia must not contest..Civil service suffered too much when Madam Joyce Banda was rolling Malawi .she hated civil servants and she grossly stole Malawi funds in her cash gate. So Malawi don't need women to be rulers OK notre women them are become so proud and pompous.. mpaka ife ma civil servants tinawapangirq mademo. Nkuwaika mbokosi ngqti amwalira.kkkk
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 16 дней назад
Ruling. Noy roling
@Lee-lee-w1r
@Lee-lee-w1r 16 дней назад
Exactly. As a female I agree
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 16 дней назад
Pambuyo panu madam
@user-lc3sw8iz2g
@user-lc3sw8iz2g 16 дней назад
Kwesi Msusa ndiye okuti atenge chipani cha Nzake Saulosi.
@Charlesnamalaka-uw6ug
@Charlesnamalaka-uw6ug 16 дней назад
Yakhwesi ndaivotera,maiyu amusiye kaye
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 16 дней назад
Vice azakhale Denice mahata
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 16 дней назад
😂😂😂😂 komatu ma guys mpaka UTM mukufuna apatse WINIKO Za drama eti
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 15 дней назад
Mery alibwino Kwa omwe timakonda chipanichi,komano atati wawina zizamupanga force kukwatila mwina asakufuna pomwe akulilabe mamuna wake coz sitikudziwa kuti inye mwini anayika nthawi yayitalibwanji kuti adzakhale pabanja.
@davidbulla5128
@davidbulla5128 16 дней назад
💯 correct
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 16 дней назад
Incorrect
@GiftMwaungulu
@GiftMwaungulu 15 дней назад
mufuna akwatiwexo pompano
@giftedmshan6779
@giftedmshan6779 16 дней назад
Mary tikufuna azawine 2025 azatifufuzile malilo a chilima
@SamJalie
@SamJalie 16 дней назад
Manganya kagwere uko
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v 16 дней назад
Iwe zibambo wandemvu zako ukuti chipani Cha banja ndekuyakhula kwabwanji kumeneko tazikhalani ndi zeru poyakhula ngati zibambo siyeni mery ayime
@HaroonMaundala-lg5lg
@HaroonMaundala-lg5lg 16 дней назад
Aaaaaaa brother ndikuyankhani ponkhapo. Kumankhala ndikuganiza komaso muliganizile banjali. Palibe cha zelu mayi chilima kutenga mpando wa amuna awo. Mkaziyu adakali pa ululu kulila kulilila amunache. Ife athu akwathu ndikungosonkhezela. Ngati akwanisa kumupha chilima uja awawa nde chizimu. Asiyileni chuma chomwe awasiyila amuna awochi kuti chisasokonekeleyi. Samalilani moyo wa mayiwa.
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu 16 дней назад
Mai Chilima musiyeni alire maliro amuna so,enanu kuthamanila kulakhula zosaveka,ngati Ali ndichuma maiwa asiyeni athandize ana ao osati muwasokonekeze mdzina loti aimilre muzidzawadyera bwino,sibwino siyeni alire Kaye maliro.
@KhatweebDickson
@KhatweebDickson 16 дней назад
kwathu kuonelera
Далее
FERNANDO DIAS NO PROGRAMA CAUSA E EFEITO
12:40
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Просмотров 190 тыс.
TRIBUTE DOCUMENTARY TO LATE DR SAULOS KLAUS CHILIMA
16:04