Тёмный

Mpungwepungwe pa kudwala kwa Mary Chilima ''zowona mpaka 312 million'' 

Hanifa Mw
Подписаться 70 тыс.
Просмотров 45 тыс.
50% 1

The K311 million doesn't include medical bills, folks. It's just pocket money.

Опубликовано:

 

19 сен 2022

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 36   
@ahamadulmbishana6629
@ahamadulmbishana6629 Год назад
Komad ndilamayo yachuluka osangowasiya afe bwanji ndilamazo akagulile Fertiliser wadulayu
@bobkenneth2947
@bobkenneth2947 Год назад
Eish komatu Malawi ndiye wafikadi pa worse But i curse the coming of Lazarus Chakwera God is Watching you guys 😫😫
@brendadumisan2526
@brendadumisan2526 Год назад
Mmmmmm koma nde mwatiseweresa ife amalawi zafikapa mukutiuza kuti muzipataramo odwara ndi nkazi chilima yekha kuti muziseweresa ndarama chonchi mmalo mokonza mavuto koma mwatizunza ife amalawi Mulungu akakulangani inu
@overcomers909
@overcomers909 Год назад
If thats what his condition of service since he is vice president of Malawi and if your currency is devalued badly K312m malawi currency
@blandinabonaventure5474
@blandinabonaventure5474 Год назад
Iwowo salary zawo ntchito yake ndichani mmmmmm kma misokho yathu mmmmm mavuto kwambiri
@blandinabonaventure5474
@blandinabonaventure5474 Год назад
Zitsiru zimenezi misokho yathu kma aliyese Ali ndi ufulu zikomo kwambiri mbuzi a utm nonse, +mcp tonse zipani 9 zero
@JohnMatope49
@JohnMatope49 Год назад
Anthuwatu ali pa pikisanu and zawathu sakuwelengaso ayi
@emmanuelweja9606
@emmanuelweja9606 Год назад
Kodi alibe medical aid?sagwada zomwe amuthyolazo apite ku mwai wathu hospital or Adventist ,osati zowatengera amalawi kuntoso ai
@charlesmuyaya8839
@charlesmuyaya8839 Год назад
Iwe voice yako si yabwino, ma videos akonso umawapanga mopusa. No interesting at all
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 Год назад
Zikuchita kuwoneka kuti anthuwa ndi akumazidi wotumidwa ndi satana, munthu wamzelu sungawononge ndalama yoseyi pamene athu akulila za njala, mankhwala muzipatala, kukwela kwa zinthu, feteleza, koma ndiye yah asiyeni gahena linayasama kale kudikilila anthu ankhazawa,
@alickhassan181
@alickhassan181 Год назад
Kalanga ine malawi ine chete🇬🇹
@jimmyzgambo9928
@jimmyzgambo9928 Год назад
Akupanga zopusa kwambiri
@hanafi4766
@hanafi4766 Год назад
Chilima hemust youz money from in his pocket this politicals the don't think for athars there Sany Of davors
@FrankKambwani
Amalawi ochuluka akungodzifera mudzipatalamu kamba kosowa mankhwala pamene boma likukhuthula ndalama dzankhaninkhani pa munthu mmodzi😢😢😢
@stevinmuhone877
@stevinmuhone877 Год назад
Akwanilitse zimene akufuna
@OjesYahaya-zl4rx
Athu akumwalila zimpatalamu kamba kosowa Panado ndiye Muthu mozi ndalama zosezo kusonyeza kuti miyo yanuyo ndiye yofunikila mumwalilabe mutisiya aphawife mulungu sowona chuma
@robenallie6985
@robenallie6985 Год назад
312milion thats tonse alliance
@emmakamwendo1370
@emmakamwendo1370 14 дней назад
Awesome
@dijayusuf2918
@dijayusuf2918 Год назад
This is not fair
@chifundonkhoma3642
@chifundonkhoma3642 Год назад
But these are their entitlements, don't compare the amount of money to the living standards of a commoner.... Guys we need to think, asagwiritse ntchito ma entertainments awo chifukwa wina aganiza kuti a kuwononga ndalama, izi ndi chimodzi modzi kuti musawalipire ogwira ntchito m'boma chifukwa a Malawi ena omwe Sali pa ntchito akuvutika ku mudziku... Ayi it's high time we need to change thinking like idiots....
Далее
Saulos Chilima on the Elections in Malawi - Part 1
9:55
Schoolboy - Часть 2
00:12
Просмотров 5 млн
ZODIAKTV CRUISE 5 WITH MRS MARY CHILIMA
41:54
Просмотров 95 тыс.
@DriemoMw's Performance at Waliko + Kuleza's Wedding
8:39
KUKHALA CHETE KWA A CHILIMA PA A CHAKWERA
10:02
Просмотров 24 тыс.
CRUISE 5 WITH BYSON KAULA - DEATH ROW SURVIVOR
50:51
Просмотров 93 тыс.
KWAPHULIKA AUDIO YACHILIMA MU NDEGE ISANAGWE. TAMVANI
10:45