Kkkkk Amen! Koma tiziwe kuti ophunzira a Yesu anaphedwa ndi anthu ena amene anayesa kufalisa uthenga. Elia naye munthu wa Mulungu anadandaula kuti aneneli anzake onse anaphedwa anasala yekha. Meaning YEHOVA akhoza kulola muphedwe ndi wa satanic but God alibenazo ntchito zophedwazo koma chimene amafuna ndi choti tikoze miyoyo kanthu basi. Ngati sakufuna kuti muphedwe amapulumusaso according Daniel ndi anzake