I am completely convinced with this leader how I feel the majority should see the same as some of us are seeing in him...May the good Lord direct him more to build this nation
This guy wasemphana ndi Chilima anakavana hvy ndipo dziko lino tinakaliva kukoma.....komabe Mulungu salakwitsa APA nduu wabweretsaso Chilima wina,, ndag WA naye mchikondi Munthu amenei
As good citizens this is our chance to change our Malawi. Once we support this GUY and his team technically we have joined the GAME CHANGERS TO THE WINNING TEAM. BRAVOOOO!!!
Zinakati maphunzilo athu amakhala mchilankhulo chathu bwenzi dzikoli liri la chuma ndi kulemera koopsa. Phunzilo ili ndilovuta kwambiri mchingelezi koma apa olo nkhalamba ya zaka 80 itha kunvetsetsa.😢😢
Osamangoti skc chilichonse ngati kuti inuyo you were genuinely loving him.This guy has got good ideas which is needed to be taken seriously koma aMalawi gullibility imatipweteka ,kutengeka ngati kuti brain zanu munagulitsa, stop kumangotengeka ndale will never help single you kutukuka work hard atati alowe m'boma he will be advised and will forget everything he's saying now I tell you, Our late professor ngwazi Bingu Wam'thalika was a man koma lots of you simnamuonetu ,he was man I was telling my fellas akumavomeleza panopa chikufunika NB: n'kuzasintha government system everything will change thus all .. I like this guy but I already lost hope in policians, maybe tingapeze ozamuvotela next yr amenye campaign...tizamuone next yr..✊
Anthu ngati awawa ndi chiombolo cha dziko, (akundikumbusa ndi Bingu nkuluyu) chifukwa amayendesa dziko ndi mutu wawo monga akuonera pa ground osati kumangosatila ndondomeko zoti zinapangidwa kale ndi azungu. Koma kuti ayamba zandalezi payekha sizingatheke ndipo sangazakhale president mpaka kalekale.koma angochita kutengedwa ndi chipani chomwe chili chothekera kuwina mosavuta ngati DPP ija monga anachitila Bakili 2004 kungomutenga Bingu ku convention kuti ndi amene azaime ngati president wa chipanicho basi.
Vuto ndi lakuti anthu Ngati awa satengedwa serious,, anthu amakonda ndalama, ma t shirt ndi munthu wamolaro not nzeru,, Koma if party's like DPP, or UTM atamutenga zingathandize Kuti akalowe mu parliament
Uyuu katundu tiyeni timulange sponsor muwone agwetse yekha chakwera😂😂😂😂😂😂 I will I will be minister of finance in his government kungotero ma youth ntchito 5 million azipeza 😂😂😂😂 tiyeni timisapote nfanayu❤❤❤❤
Derete ua comment..mesiah ndi Mulungu in humana flesh don't compare Him with anybody else..mind you tinabadwa through brood shareling while the Messiah was born through the Word power of God@@fleshar-j6i
Akuluwa alibwino kwambiri,...Nzeru zomveka bwino ngakhale ma system azungu ndi amphamvu,....Pamodzi ndi achina Julius Malema,Bobi Wine,Ibrahim Traore nzotheka. Nkhani ndi zakazo chisankho chikubwelachi sangakwanitse kuima.. Ndulingalira ataenda ndi Martha Chidzuma ngati president,..zitithandiza. Bravo DMNk,... Mitu
I just like the guy's MFUNDO. Ndiwachichepere, koma wamva maitanidwe muutsogoleri wa dziko lino. Sikukulamulani aMalawi amnzanga makamaka inu achinyamata, let's give a guy much support. Timupatse sapoti yambiri, kuti Mulungu apitirize kumutsegula maso, komanso akhale nawo omuthandiza kukwaniritsa komanso kufikira masomphenya, for the betterment of ifeyo aeni ake aMalawi....
I was skipping this post but I took a few moment to listen to this video,there is wisdom in the guy,i thought tinathera pa Chilima but the guy is a genius.
He must talk and enlight the youth about pacts and treaties also signed by our government officials behind doors without consult the pple... IMF AND WORLD BANK
I had a dream last of last week chilima atauka nkumayankhula kut tinali mndende now this is the right time we have to work up tikapange campaign sono..
This guy is brave man ,genius ,I second this brilliant idea, I even read a quote from the bible ,"come let us reason together and make one thing" indeed just like Ibrahim Traore 35yrs he is leading BUKINA FASO ,young man 33yrs leading SENEGAL , why not Malawi ? Lets change our Nation with Servant leadership