Apapa ndiye mfumukazi ndi mdyangu akuyisokoneza , potenga nkhani ya uko kubweretsa mbali ina . Otherwise izizi ananyoniwo amayenera kuwapeza ku mdyangu komweko osati ku fumukazi
Msatisokoneze abale za mndyango zikhale za mndyango za mfumukazi zikhale za mfumu kazi osati mpange mpange mix anthu omwewo kwa mndyangu omwewo kwa mfumukazi
Joshua Agabu as much as I love the link as well but I think somehow it will be confusing as some characters appear on both shows under different names i.e. Sasoka on Mdyangu while Gututu on Mfumukazi. Imagine Nanyoni appearing on Mdyangu and being welcomed by Sasoka how was just hitting on her few weeks ago on Mfumukazi under Gututu.. kikikikiki
Pajatu Nanyoni aka Mfumukazi amapanga za traditional Dr mu tikuferanji, and if you remember a couple of episodes ago in Mdyangu Queen anagwilizana ndi ashokoshoko kuti akapeze sing'anga to help Mrs Shokoshoko...
Queen wayatsa moto on a mission to settle her bill ya ku chipinda plus kukonza mental health challenge za Cecilia Ananyoni sing'anga. Queen ndi maulendo Mr ShopRite wayang'ana mopherela
Kusonyeza kut Msing, anga yemwe akufunikira mwa mdyangu pa misala ya Mayi shokoshoko ndi mfumukaziwa eeti kkkkk ndikuzitsatira bhobhoo ndpo tili limodz ndthu
off course mwapanga cross over from mdzyangu to mfumukadzi bwino apapa koma munayiwala za mercy, kodi munthu modzi azipezeka ku mudzi yomweyenso ku town? but anyway keep it