Тёмный

MUFT CHIBEKETE _ AKABIBI BUNO MALIK 

Luis Adamo
Подписаться 988
Просмотров 32 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

3 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 48   
@MustafaHenderson
@MustafaHenderson Месяц назад
Respect our ulama Allah will grant us good life Inshallah, sheikh Chibekete was a good muft always striving in the path of God almighty may God almighty Allah grant him everlasting life n paradise
@MusaSanudi
@MusaSanudi 5 месяцев назад
Chisilamu ndi chipembezo Cha mulungu,ife ndi asilamu iwe ngati uli mu mpingo ndi zako .amene mukuwanena kuti mbuliwa ndi amene atisungila chisilamu lero mukuwatukwana mulungu akukhululukileni simukudziwa komwe mukuchokera ameen
@rashedzain6507
@rashedzain6507 2 месяца назад
May Allah grant you jannatuh filidausi & male your grave free from difficulties
@Zaza87-w
@Zaza87-w Месяц назад
❤❤❤❤❤ amezing
@AbgirlChinheya
@AbgirlChinheya 2 месяца назад
Ameen ❤
@MustafaHenderson
@MustafaHenderson Месяц назад
Ulemu kwa masheikh awa amatitsitsimusa ndi history ya aneneri abale tiziyamika
@attaufeeqmuhammad718
@attaufeeqmuhammad718 6 месяцев назад
Chibekete si muft ayi koma mbuli yopanga bidi'a asakudziwa
@alfredwasili4267
@alfredwasili4267 6 месяцев назад
Koma adali ndani ??
@SdreckLashid
@SdreckLashid 6 месяцев назад
Paja mukaphunzila mumanyoza makolo, ok zikomo
@rumicmalawiamovies
@rumicmalawiamovies 6 месяцев назад
Umbuli ndiumene mukupanga inuwo, coz mukadakhala mudaphunzira bwino simungayankhule chomcho. Allah akukhululukireni, komanso akuphunzitseni. Mukadakhala ndiinu ophunzira choyamba mukadakhala ndi adabu, ngatinso mumaidziwa
@IshmaelBamusi-u9k
@IshmaelBamusi-u9k 5 месяцев назад
Mweje ngawa silamu
@IshmaelBamusi-u9k
@IshmaelBamusi-u9k 5 месяцев назад
Chibekete one of them to keep Islam malawi to Mozambique
@HusseinWabu
@HusseinWabu 5 месяцев назад
Mashaallah allah grand him. Fridaus.
@issahsabitilawey2091
@issahsabitilawey2091 2 месяца назад
Please muziponya zambiri kapena muzangotigawila ku wap number bwanji
@OmarkanjezaKanjeza
@OmarkanjezaKanjeza 17 дней назад
Masha Allah all brothers allah brace you
@alfredwasili4267
@alfredwasili4267 3 месяца назад
Namu
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo Месяц назад
Masha Allah
@ThembaThemba-vy6un
@ThembaThemba-vy6un 3 месяца назад
Zili bwino allah akudalisen posiya ulaloki umenewu
@MosesNdebele-kc2cp
@MosesNdebele-kc2cp 4 месяца назад
Muziyamba kaye kukasesa Manda amakolo,a achibale,kenako mupite ku Hajj.kapena kukapanga zomwe ankapanga mtumiki wa Allah mtendere ndi madalitso apite Kwa iye,kapena kukasesa Manda Ake mtendere ndi madalitso apite Kwa iye❤❤❤❤❤
@issahsabitilawey2091
@issahsabitilawey2091 2 месяца назад
Achimwene Achimwene anthu timalakwitsa kwambiri manda amakolo omwe atiwonetsa dziko li pomwe anagona panaiwalika kalekale koma kupita kusaudi 😢😢😢
@MosesNdebele-kc2cp
@MosesNdebele-kc2cp 4 месяца назад
❤ timamukonda chifukwa zonse zimene ankanena zikuoneka tsiku ndi tsiku zikuchitika.Allah amukhululukire ndikukamulowenza Jannatu fridous.chifukwa pano dzikoli lasokonekera aliyense kungodziwa kuwerenga Qru'aan pang'ono akuti ndine mufti ndikumabwerenza zachilendo tsiku ndi tsiku.yemwe atasiye chipembedzo cha chisilam ndi yemwe atakanile zomwe amkatilalikira ameneyo ndiwa BIDIA'A.chifukwa sitingasiye kusesa kumanda,Kuyimba lailaha illahllah,ndi Zina zambiri.koma mukumbukire chisilam chizafika magulu 73.
@rumicmalawiamovies
@rumicmalawiamovies 6 месяцев назад
May Allah grant him aljannatu firidausi.
@YersnKaifa
@YersnKaifa 4 месяца назад
Emen
@BalakasiMalunga
@BalakasiMalunga 5 месяцев назад
Manshalla zoona zake shehk takabilu
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 6 месяцев назад
Wayamba khale kuweruza amnzanu you be careful with Allah
@abdullahassani4557
@abdullahassani4557 6 месяцев назад
Yes I know you 16 22😢,but I don't know 9 1 ly🎉😊😅
@Lashidilashidi-y5u
@Lashidilashidi-y5u 6 месяцев назад
Q¹​@@abdullahassani4557
@MkalongaChaibu
@MkalongaChaibu 5 месяцев назад
MashaAllha 🙏 🙏 🙏
@MosesNdebele-kc2cp
@MosesNdebele-kc2cp 4 месяца назад
Muziyamba kaye kukasesa Manda amakolo,a achibale,kenako mupite ku Hajj.kapena kukapanga zomwe ankapanga mtumiki wa Allah mtendere ndi madalitso apite Kwa iye,kapena kukasesa Manda Ake mtendere ndi madalitso apite Kwa iye❤❤❤❤❤
@AbudurazaqChikande
@AbudurazaqChikande 2 месяца назад
kod ku hajj anthu omwe amapitawa amakasesa kumanda? tidziwitsen tiphunzire nawo
@IshmaelBamusi-u9k
@IshmaelBamusi-u9k 5 месяцев назад
Mbambande
@IshmaelBamusi-u9k
@IshmaelBamusi-u9k 5 месяцев назад
Allah akupasen Jaana muft chebekete😢😢😢😢
@AbdurashidAhmad
@AbdurashidAhmad 6 месяцев назад
Ambuye mulungu akhululukileni makolo athu amene anasamala chipembezo chathu chachisilamu
@luisadamo4114
@luisadamo4114 6 месяцев назад
Amém
@IshmaelBamusi-u9k
@IshmaelBamusi-u9k 5 месяцев назад
Ameen
@augustoluave3601
@augustoluave3601 Месяц назад
Que a Paz de Allah esteja com Muft Chibekete
@bashirimwewamusa1074
@bashirimwewamusa1074 5 месяцев назад
Masha Allah
@Xolani-jd7fo
@Xolani-jd7fo 5 месяцев назад
Hi 💯🙏💪
@ShariefGama
@ShariefGama 3 месяца назад
Ameen
@YahayaSaeed-bw3mp
@YahayaSaeed-bw3mp 6 месяцев назад
Comments
@JamesMufuti
@JamesMufuti 6 месяцев назад
Naam sheikh yakuwona ❤
@daviekachambo
@daviekachambo 6 месяцев назад
@NoahKalima
@NoahKalima 6 месяцев назад
Chisilam chipembezo chamafano
@yusufjonas5088
@yusufjonas5088 6 месяцев назад
what do you mean?
@LungaMvambi-zk3mv
@LungaMvambi-zk3mv 6 месяцев назад
Chibekete ya Allah give him janatu firidauth
@ShabanNicks
@ShabanNicks 6 месяцев назад
Aameen
@luisadamo4114
@luisadamo4114 6 месяцев назад
Amém
Далее
MUFTI CHIBEKETE _ AYUBU
1:02:14
Просмотров 17 тыс.
mufuti chibekete achikalakasa
55:34
Просмотров 18 тыс.
Китайка нашла Метиорит😂😆
00:21
anganga  afik pat 2  ndakudandaula
25:12
Просмотров 12 тыс.
SURAT AL BAQARA JUZZU 01 IN CHICHEWA
1:34:07
Просмотров 64 тыс.
KUSANTHULA QUR'AN NDI BIBLE
25:55
Просмотров 4,1 тыс.
Bimu chibekete
28:37
Просмотров 85 тыс.
Chibekete,     Achikalakasa
55:35
Просмотров 1,9 тыс.
anganga afiki malangizo pat 1
27:47
Просмотров 10 тыс.
mufuti chibekete n Nabi mussah full
1:05:25
Просмотров 7 тыс.