Тёмный

NDIKUKUPATSANI 30DAYS KUBOMAKO MUKHALE MUTAYAMBA KUGAWA CHIMANGA APO AI MUONA - ELIZABETH KALONGA 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 62 тыс.
Просмотров 3,5 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 24   
@HarryKandani
@HarryKandani 4 часа назад
Mwazipentatu amai eeish
@issahmaloto9141
@issahmaloto9141 3 часа назад
Ndale kusiya uko plz thandizani kugawa chimanga anthu akufa mamva bwanji koma 😢😢😢 keep up mama potiyankhulira
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 6 часов назад
Anthu ayakhula azeru koma bomali silikuva ndizizake za anthu atsogoleri wose ndi ana zalowa kunkhongo . Siwuyu mwamuona akuti anadwala koma ndikukasewera pamusewu ndi zipukupu asilikali kumangodya ma alawasi kuonenera wina akugona pamusewu ngati njoka cholinga anthu ayakhule ndikuwakola ndi mawubyolo
@FionaKhoma
@FionaKhoma 6 часов назад
Ameneyu agawe chimanga kumene angoyenda yenda
@Daniel-cf4tu
@Daniel-cf4tu 4 часа назад
Ndiye ukumutuma ndani pamenepo? Osanena wekha bwanji?
@petrokagona1708
@petrokagona1708 8 минут назад
Ndiye zalowa zibwanatu. The whole 30 days kupereka kupanda kutero kutokota? Anthu adya kutokotako?
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Час назад
Ss ndnu wa MCP full stop koma nkhani yogawa chimanga President wanuyo aliku BT aku pusha kae ndye akamalizam mwina mukambran
@DaudBonomali
@DaudBonomali 7 часов назад
Nanga akakuonetsani ma video akalekale ndiye mudzatani kapena achitenga chimangacho ndikumangoyenda nacho koma osagawa nanso mudzikhala ngati boma lanu la mcp mumaliziwa bwino bwino simwanena kale kuti makolo anu ndi a mcp
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 7 часов назад
Anayamba kale kugawa chakudya ku mulanje iwe
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p 7 часов назад
Mwina inu akuvelani koma ife atikanika chomwe akudziwa ndikugawa ndalama ndikugulira oyimba
@billykhonje1433
@billykhonje1433 3 часа назад
Ukunena Kuti ulibe chipani tagonena Kuti ndiwe wa chikangawa bwanji
@MosesDicostar
@MosesDicostar 7 часов назад
Kuyakhula athu ndy achita kutopa Nako tabwerani muzangopanga action bas
@MrMagombo
@MrMagombo 7 часов назад
Pitani ku embassy ya malawi mukapange ma Demo ayaluke a Ndale.
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 6 часов назад
Ndemukayakhula chitasinthe ndchan ?
@petrokagona1708
@petrokagona1708 6 минут назад
Zachibwana basi. Anthu sitikusowa kutokotako. Ngati muli dolo just act kuti anthu apeze chakudya basi. Osati zachambazo
@StewartGoma
@StewartGoma 4 часа назад
What happening in malawi is not good The best way is to change president who can change the life of Malawian to a better life Chakwela is surrounded with stupidly advisers Let's change leadership new president like Burkina Faso president who care more about his people
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr 4 часа назад
Ndi mcp ndi tambara yamweuja zichimanga timachiziwa chija ndiye tingodwa nkhuku zokhazokha opanda ufa 😂😂😂😂😂😂
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 5 часов назад
Iwe 😂😂😂😂iwe iwe mphuvu ya hule
@Janekapats
@Janekapats Час назад
Yambanipo inunso kuthandizako basi enafe tidzibwera pambuyopotu
@fiskanichiumia7733
@fiskanichiumia7733 3 часа назад
kugawana ndi osowa siudindo wa boma lokha ayi inuso zochepa mulinazo gawilaniko osowa kuthandizana ndi boma
@WilsonFelix-j9n
@WilsonFelix-j9n 5 часов назад
Zoonadi chemwali
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p 7 часов назад
Ena kumati boma ndi la chakwela kusaganizira moyo umene uli kunza chifukwa tikamuvotela chakwela ndithu kuli Mavuto kutsogoloku lero zili bwino si mukulandila ti 2000 sindikudana ndi chakwela ayi koma zintchito zake iiiiiiiiii Amalawi chonde tikavote mwanzeru anthu chomwe akudziwa ndi kuba
@MoosaSame
@MoosaSame 6 часов назад
Kod hule iwe ulikut galu
@HarryChindiwo
@HarryChindiwo Час назад
Kwanu kulibe ma hulewo
Далее
Nancy vs Che Nkope - Apatseni moyo wautali
11:05
Evance Meleka _Yashuta
5:10
Просмотров 10 тыс.
ENIGMA...NEW PASTORS REVEALED, WHO SOLD THEIR SOUL
25:36