Тёмный

SIMUNGAIME NDI CHAKWERA MWACHEPA - SYMON AND KENDALL kwaipilatu Ku mw. 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 62 тыс.
Просмотров 6 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 86   
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem 18 часов назад
amene zikumunyasa amwe nchape🥂 😂 achira!!!!
@christophergibson72
@christophergibson72 4 часа назад
Komaso aka bibe
@aaronziyeretsa6420
@aaronziyeretsa6420 12 часов назад
More fire MCP Chipani cha dziko lonse la malawi
@unclepaulmw1506
@unclepaulmw1506 День назад
Chonchi cyclone athe ku Malawi, ka dziko kongozaza ndi anthu adyela opanda Chikondi Chilungamo mukuchiziwa kuti zinthu sizilibwino ku Malawi koma chifukwa choti akugawilani ndalama zakubazo basi Shame😭😭😭
@IbrahimMatias-te1kc
@IbrahimMatias-te1kc День назад
Kkkkkk cyclone sangathe chifukwa choti kwa chulukana adyela
@pemphokatembe443
@pemphokatembe443 22 часа назад
Chilungamo akuchidziwa kumene koma ndalama zaphimba zonse
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 20 часов назад
Inu osaimba yanu nyimbo mulandileso bwa😂😂😂😂😂😂 Hypocrites people in Malawi mwachuluka... Even muzintchito mwanu mazoba inu mukuba imagine mutakhala nduna basitu mumaliza dzikoli.... Muzifufuze man ngati iweyo pawenkha you are a saint... Zoba
@TamaraSeleman-cl2fc
@TamaraSeleman-cl2fc 19 часов назад
munyabe zanu izo ife sitikusintha boma ndilomweri
@unclepaulmw1506
@unclepaulmw1506 18 часов назад
@@wisdom20mkango49 achitsilu inu vuto simukuvesesa kuti ifeyo tikulira chiyani Palibe boma limene siliba koma a kanyimbi awa awonjeza anthu akuvutika mu dziko basi busy kumawalipila anthu oyimba ndalama zambilimbili cholinga anthu azawavotele, akanakhala kuti zinthu zilibwino bwezi akupanga Zimenezi? Ntchito kuphana basi, chindalama kugwa daily koma ma salaries aanthu osawaganizila zinthu zikukwela mtengo daily koma ma salaries ndi omwe aja do you think kuti makolo ovutika akwanisa kuwalipilira school feez ana awo Ma promises onse aja alikuti? Fertilizer osika mtengo alikuti? Kumangonamizila kuti Malawi dziko lowopa mulungu mulungu wake uti?? , dziko la azitsogoleri adyela okhaokha ozikundikila. Mulungu ndi Chikondi Malo amene anthu sakukondana mulungu sapezekapo ndi chifukwa chake mavuto sazatha ku Malawi. Mulungu watiyanganila kumbali sakuvaso kulira kwathu
@Godabless12
@Godabless12 День назад
Sikut tayiwala zomwe munayankhula mukucheza ndi chakhaza
@GloriaChiwanda-l6g
@GloriaChiwanda-l6g День назад
Za let's gather here zikhalaposo pa nyimboyi?
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 День назад
Ovitadi ndi ife osati oyimba mukuononga nsogolo ranu nyimva zanuzo timagura ndi ife ndiye basi palibeso kuvuta nyimbo. Ungosiya kuyimba
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 20 часов назад
😂😂😂😂😂 Kuteloku once you view basitu mwagula... Stop complaining mbuzi iwe
@elishangalu5852
@elishangalu5852 День назад
Basi ndawatsika
@ThandiShandu-l6w
@ThandiShandu-l6w 18 часов назад
Tsika sudalipile cadets wakwera yolakwika nyembanyemba boys ikutsotsomora sicheza
@blessingsmtawanga
@blessingsmtawanga День назад
Nditukwana kwinako
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k День назад
😂😂😂 muyenera kutero cz ili paminga koma chilungamo chili muntima😂😂😂
@AugustineChimaliro-e5i
@AugustineChimaliro-e5i День назад
Eeeeeee😂😂 Koma ndalama anakoza awaso ayambapo tiziwona wokavota ndife
@TakondwaChirwa-f6d
@TakondwaChirwa-f6d 6 часов назад
Opposition ndi chinthu chowawa kma😂😂😂😂😂😂eeeeh
@FladielMwase
@FladielMwase День назад
Kendall kamwendo & symon 😂😂😂😂😂😂😂😂 unenesko mkuwumanya kale mwekha or imwe voti yinu yikuluta ku MSP yai mkuyimba waka pot ni business 😂😂😂😂😂
@omarajibu860
@omarajibu860 День назад
Songs of appeasement, you survive through this
@IsaacGingersonManda
@IsaacGingersonManda 14 часов назад
Just survive on what you do nawenso.
@MaryNgola
@MaryNgola День назад
Ndrqma ndi satanadi zinampeleka yesu
@EsChinombo
@EsChinombo 9 часов назад
Boma ndi lomweli 🔥
@MickyChikwana
@MickyChikwana День назад
Amalawi analozedwa ndithu, amadyela momo agalu amenewa afunika nthawi yakampeni sopano
@AlfredManjawira
@AlfredManjawira День назад
Yomweyooooooooo 😂😂😂😂😂😂 😂😂😂
@ThembaShandu-m9m
@ThembaShandu-m9m День назад
Akendo ngati matenda anawapeza eti? Kkkkkkkk azikamwa pompano atisiya mutuwo mwauona
@MosesDicostar
@MosesDicostar 22 часа назад
Zisilu kumalawi zikuchulukirabe
@riccodeeforces8097
@riccodeeforces8097 День назад
Awa akuyenera adya zambiri 😂😂😂
@CarolyneGunda
@CarolyneGunda День назад
Makape poyamba ndimakuonaningati madolo
@Godabless12
@Godabless12 День назад
Zitsilu zawanthu simumachita manyadzi inu nomwe kunena zoipa zamunthu imweyo then mukapatsidwa ndalama kuyamba kumuyamikira
@GustinoKamanga
@GustinoKamanga 15 часов назад
Tamangodyani zaulelezoo agalu inuu ngt mukudya inuu yamikan amxanu akufa ndinjala
@Alexkalonga-t9s
@Alexkalonga-t9s День назад
Koma ku opposition ku ndiye mukakhala ndi nyimbo zambiri zomvera komabe mupangiretu sinakha ndalama mukusiyana nazo bas😂😂😂😂
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 20 часов назад
The funny part is that 90% ikulubwa pa social media simuzavota... So mulimbe mtima Cox till 2030 muzilembabe za oppose 😂😂😂😂 munya mphwanga
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef 6 часов назад
Boma ndilomwelidi lophanali😂😂😂😂😂
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n День назад
Ovota ndi ife, mcp ichoke
@SamuelLiwonde
@SamuelLiwonde 21 час назад
Ndakusikani mulibenso umunthu mbewa inuu
@JamesMalango-h4y
@JamesMalango-h4y День назад
Malawi dziko lomvesa chisoni zedi
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o 17 часов назад
Mboroyanu akalamulira kumanda
@PaulFrank-tj2mc
@PaulFrank-tj2mc День назад
Anawapasa ndalama anthuwa zochuluka
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 23 часа назад
Nyimbo yosabeba
@AlicksonMakata
@AlicksonMakata 7 часов назад
Boma la mcp bomaaaaaaaaaaaaa ❤❤❤❤❤❤❤
@GrecianWyson
@GrecianWyson 11 часов назад
Zaziii kachakwera mkachaniso kudari akamuzu Amati wamuyaya, bigu,bakili ,joisi, Peter Mutharika. Nde aka mkachanukhaka mkachaniso
@thomasphiri7799
@thomasphiri7799 День назад
koma Zoopya kwabasi 😢
@DeborahGeorge-g3i
@DeborahGeorge-g3i День назад
Mukatero zalowatu 😅😅😅😅
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 12 часов назад
😂😂😂😂😂😂😂 Muzadilita 2025 nyimbo zimenezo bolo zanu
@TakondwaChirwa-f6d
@TakondwaChirwa-f6d 6 часов назад
Boma ndi lomweli ndipo sitikusintha😂😂otsutsa kwawo nkuti paja?
@InnocentMlowoka-ew4lo
@InnocentMlowoka-ew4lo День назад
Money stop Rubish, Komatu tikamaliza kuyimbako tiziwe kuti malawi tili nding’ongole ya 16 tililion, basitu zikoli 😢😢😢
@DixonChimanya
@DixonChimanya День назад
Machende anu week yatha ija mumati akuiwalani kuti mudamunyera limodzi khondo kuti alamule Basi mwadya bole zanu
@ChapwetekaChauluka
@ChapwetekaChauluka День назад
Koma ndiye machende awodi ndithu
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 21 час назад
Zadziiii ubwino wake simuzavota nokha
@TamaraSeleman-cl2fc
@TamaraSeleman-cl2fc 19 часов назад
zako izo tili pa mbuyo pa chakwera ndinthu boma ndilomweri basi😊
@sthoramexjrsa902
@sthoramexjrsa902 День назад
Kom tionadi zoopswaa chaka chino chakwerayo kd mmulungu wanu
@EnerstManess
@EnerstManess День назад
Inu mesa mumalila popano zalowano
@YusufAlidi
@YusufAlidi 16 часов назад
Paja amalilatu kuti sakwagaila ndalama apa zokuoneka kuti awagaila
@ConnexKhomba
@ConnexKhomba 19 часов назад
Zakumachende srs mukupangaz ziko mmene likuwawilamu
@mcnelsonmwanza4725
@mcnelsonmwanza4725 16 часов назад
Boma ndi lomweli 😂😂
@hazelmataya8537
@hazelmataya8537 15 часов назад
Yomweyo🔥🔥🔥
@JonaSato-j8e
@JonaSato-j8e 18 часов назад
Gwape
@chipiechizumba
@chipiechizumba 14 часов назад
A chakwera aja ndimadala
@MauriceMukona
@MauriceMukona День назад
Inu nde mwalandilapo zingati? Mwamuposa Dan Lu 70 mita or inu muli m,ma 200 million kapena?
@IshuBillalli
@IshuBillalli 21 час назад
Tafunseni nafe timve nawo amaoneka ngati ndi anthu anzeru koma zili mbuzi zawanthu basi ,,,,,,,, yashuta uku ya Evace meleka
@MangaDamiano
@MangaDamiano 22 часа назад
Mukatelo mwakudyapo ziko lathu ili silizatukuka ndithu anyamata tazilimbikani ntchito kusiya zotamanda satanazi please
@tingo3155
@tingo3155 16 часов назад
ADALIPO ENA ANKAYIMBA KUMANYOZA BINGU lero akuvutika
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o День назад
❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉
@MercyNkhoma-b6h
@MercyNkhoma-b6h День назад
Awanso zatheka kkkkk
@christophergibson72
@christophergibson72 4 часа назад
Koma kumeneko!!
@GustinoKamanga
@GustinoKamanga 15 часов назад
Gulu logulidwa ndi boma ili dzitsiluu muchita manyaza 2025
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 17 часов назад
😂😂😂 Koma Ku Malawi kukunvesa chisoni.. Koma mwati oyimba simulodzana Ku mcp ko ? Dyera Lanutu lafika povesa chison
@samchibenene4458
@samchibenene4458 16 часов назад
Boma ndi lomweri
@mkhokholasamuzonda5094
@mkhokholasamuzonda5094 13 часов назад
Manyi nde amenewo, ife anzeru tikudziwa kuti mungofuna kuwadyera ndalama zawozi nanga angosakaza okha njira zabwino zowadyera zimenezi, lo nyimbo zake zopekera nchimbuzi chokumba mukunyera, kkkkkk
@GreyMwanyimbo
@GreyMwanyimbo 12 часов назад
Kuopposition nkumanda
@chrischiwere7279
@chrischiwere7279 5 часов назад
😢money is evil
@aliedausi9733
@aliedausi9733 День назад
🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@ChancyMakondetsa-c2c
@ChancyMakondetsa-c2c 16 часов назад
Zalowa akatero
@alexsumani6823
@alexsumani6823 20 часов назад
Zitsilu
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 День назад
😅😅mor fire❤
@MbalakahAmini
@MbalakahAmini 8 часов назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@ChapwetekaChauluka
@ChapwetekaChauluka День назад
Zitsiru izi kwambiri
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 13 часов назад
Izi nazo ndimasase okilinira mu toilet yokumba oyimba akumalawi ambiri vyamba vikuwapweteka kwabasi kungoyamikira gehena yomwe amalawi alimo mmmm pumbwa amgayimbe zazeru osachula kunu kwathu kumupoto sitikumufuma chikangawa wamuyo or Orton chirwa wakuno kwathu sakafuna ng"ona zanu zo ndichifukwa munamusowesa. Zisapotani nkhandwe zanu zakwanuko osanena zalumupoto mwativulaza kokwana osayimba kuti kumupoto ndikufuma chikangawa akuwuzani ndani akape inu
@peterkakhome6976
@peterkakhome6976 День назад
Mwalandilatu mukatelo,😢😢😢😢😢😢😢😢
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 День назад
Simon ndi kendo ndima ca Kape zasatanic izo mbuzi zawathu nyimbo zanuzo muzigulisa ku lilongwe kwanu komweko ndi kukasiya basi
Далее
Kendall and Symon - Gwenembe
6:10
Просмотров 19 тыс.
Zeni Zeni zake Zokhuza Chakwera
12:31
Просмотров 118 тыс.
prophesy about 2025 presidential election
26:15
Просмотров 102 тыс.
Namadingo RM5 Lucius Banda part 2
15:29
Просмотров 4,1 млн
Milefa - Ndinu yaweh - malawian gospel music
7:06
Просмотров 722 тыс.