Тёмный

OYENDA NDI LUPANGA/CHOIPA CHITSATA MWINI - NZWANYA CHARLEY PATACHE 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 62 тыс.
Просмотров 13 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 33   
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani День назад
Alimoyo Chakwera koma yekha ngt alindi nzeru adziwe kuti anthu atopa nae chfukwa munthu akamwalira anthu amalira osati amaseka ndikunyadra
@WysonChilonga
@WysonChilonga День назад
Mwatikumbutsa kale kkkk,tafufuzaninso 'nawonso akana' album yomweyi
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani День назад
Alimoyo sangafe kwacha agwesa ndani akafamo ngongole ija abweza ndani sakuthawatu ameneyo alimoyo ndthu Chakwera alipo
@CosterMustafa-m6h
@CosterMustafa-m6h День назад
Koma ndy kulli kalelangatu nyimbo izii zilipo kom ndy yomweyo dj 🎉🎉🎉😂😂😂😂😂
@WilliamNyirenda-xq4km
@WilliamNyirenda-xq4km День назад
Mixerxo ya akupita awo abwana ndi ulendo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani День назад
Chakwera yamba kukhal bwino ndi Amalawi nawo ndi anthu amafuna zabwino ichi chikhale chisadzo ngt uli ndi umunthu sintha khalidwe pliz pliz
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 День назад
Choipa chitsata mwini Ulemu Wanu mwatikumbutsa kale 💃💃💃💃💃💃❤️❤️❤️❤️❤️
@JamesMalango-h4y
@JamesMalango-h4y День назад
Mwatikumbutsa kale abale
@JOHNKANYALA
@JOHNKANYALA День назад
Yomweyo dj😂😂😂
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k День назад
Mwambo wowona nkhope tikachitira mchikangawa guys yomweyo garu iwe
@HandissoneMaquina
@HandissoneMaquina День назад
Mzimu WA chilima ndi anthu ema aja ine pheee
@WilliamNyirenda-xq4km
@WilliamNyirenda-xq4km День назад
Tiguliseniko zikuti bwanji Kodi 😂😂😂😂😂😂
@ElizaJoseph-q9w
@ElizaJoseph-q9w День назад
Malawi wavuta lelo anthu amwa wa mkaka ngati zili zoona zomwe ndikunganiza
@gizzykondwani865
@gizzykondwani865 День назад
😂😅😅😅😅😅 mr patache inu mumakwana
@HoseKatsekera
@HoseKatsekera День назад
yomweyo, malawi ali boh, tiwuchape bas 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza День назад
Aaaaaa ine nditenga mpando ndiwandikire basi zikuti bwanji?
@HandissoneMaquina
@HandissoneMaquina День назад
Chilima kupezeka wopanda nsapato nkumati inali Ngozi ààààa
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb День назад
Tiuchape tiutafune mahule mahule omwa fanta abwele pano.awuse muntendele bwanawo
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l День назад
R.I.P. DR
@Paul-q2p
@Paul-q2p День назад
Mungoyika zofanana lelo ngati mukuziwapo nenani mutsatithele nthawi
@HarryKandani
@HarryKandani День назад
Kkkkk koma timva nyimbo
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl День назад
Chakwela ukabwela uli ndi moyo chonde mukhale pansi kuwelenga makomeyi onse mmachanel mose ansala muyipedza nokha kuti anthu dziko la malawi akundifuna kapena sandifuna answer muyipedza muti akamadwala anthu amalira koma matenda ayinu 😂😂😂😂😂😂 zachisoni chonde sithani bwana 😂😂😂😂😂
@atanazimvuyekure955
@atanazimvuyekure955 День назад
Bola asazafe wa pandege ndiopa kuwonongetsa ndege yina
@JohnWalekana-z2f
@JohnWalekana-z2f День назад
Yashuta
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms День назад
Nice song
@LinlyMatheweKufakwina
@LinlyMatheweKufakwina День назад
Hmmm koma people aaa pliz polani moto
@LafickDickson
@LafickDickson День назад
Mcp achakwela alikuti
@ahmedmsume1489
@ahmedmsume1489 День назад
Koma sound imeneyi 😢😢😢😢
@PatriciaAlomwe-oz8wc
@PatriciaAlomwe-oz8wc День назад
Yomweyo galu iwe
@JOHNSANGWALI-r2m
@JOHNSANGWALI-r2m День назад
Iiiii zikuti bwanji Kodi Okay Dili Ku mastand kuvesera
@babranzima8120
@babranzima8120 День назад
Khasu lali fupi limudikirira nayyo😂
@PaulFrank-tj2mc
@PaulFrank-tj2mc День назад
Anakonza
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 День назад
Chakwera ngati uli moyo change please dziwa kukhala bwino ndi anthu, waona momwe ena akusangalalira za maliro? Please Apure sinthani
Далее
Mene Ali Achakwera basi MCP yatha ndithu
7:36
Просмотров 37 тыс.
Zeni Zeni zake Zokhuza Chakwera
12:31
Просмотров 118 тыс.
G CONDES   WAKUBA OKUMVA CHISONI  OFFICIAL HD VIDEO
8:11
Просмотров 331 тыс.
Phungu Joseph Nkasa - Ndani yemwe sakundiziwa
6:21
Просмотров 893 тыс.
Saulos Klaus Chilima zomwe ananena asanamwalire
2:31
Mlaka Maliro_Chilungamo
5:57
Просмотров 1,5 тыс.