Тёмный
No video :(

Sizachilendo Nduna Kuona Nduna Ikupeleka Ndalama Kwa Delegate Kuti Awine Convention - Billy Malata 

Nyasa VoiceBox
Подписаться 26 тыс.
Просмотров 4,6 тыс.
50% 1

On Nyasa VoiceBox Billy Malata says it is perfectly ok for a Cabinet minister to spend money on party delegates in order to win a seat at the party's convention. Being a minister and competing in a party convention is not a reason to subject the individual to smear campaign.
Pa Nyasa VoiceBox Billy Malata wati sizachilendo kuti nduna ya boma iwononge ndalama kukopa nthumwi za chipanichi kuti apexe mpando kumsonkhano wa chipanichi. Kukhala nudna ndikupikisana nawo pa msonkhano wa chipani si chifukwa chomuyipitsira munthu mbiri pa kampeni.
#malawi

Опубликовано:

 

29 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 33   
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo Месяц назад
Amalata simungakambe za MCP zokha osanenako za dpp chifukwa mukuoneka kuti mukulimbananaotu dpp chifukwa khani imene mukunenazo ndi za MCP koma inu mukukamba za dpp zikuoneka kuti mukuiopa dpp
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 Месяц назад
Muphana sumunati nzimu wa chilima wakwiya
@SurprisedDrumKit-ql7rj
@SurprisedDrumKit-ql7rj Месяц назад
Abilly malata meafunsidwa za mcp osati za dop ndie zoyankha mopepelazi achitsilu inu pa
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx Месяц назад
Amenewotu akuwululana ifeyo amalawi tikusangalala kuti akuwululana
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Месяц назад
Komatu nkhani ndi komwe akutenga ndalama.chifukwa ngt kuli chimbava choipa kut mcp nde ndie chithyola...ngt anafika pogula magalimoto 30 amwana wake yekha,nanga akazake ,nanga iye mwini...nde izi nzopusa
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 Месяц назад
This how you politicians play with taxes??? You are backing each other then by taking it as normal? Why not also rebuking misusing that money??
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Месяц назад
Billy malata is a motherless dog..unreasonable fool
@LuciusKazembe
@LuciusKazembe Месяц назад
Akupasa dzingat pano wasiya yogulisa masache
@simonpaul6567
@simonpaul6567 Месяц назад
Mr malata anapengapo kodi?
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy Месяц назад
Komano ndalamazo sanamugwire nazo 😂😂😂
@user-dp7bc7yy6s
@user-dp7bc7yy6s Месяц назад
Iwe ndimbudz kwambiri kdmata ndindan?
@ChristopherMatemba-m4g
@ChristopherMatemba-m4g Месяц назад
Atamungwila ndimatumba andalam pa airport..
@AdmoreSingini
@AdmoreSingini Месяц назад
Koma kugawa ndalama for campaign ndi mulandu azanthu a ACB akuti bwanji,.?
@SamuelMthengo
@SamuelMthengo Месяц назад
Onongoni ndalamazo pakuti nthawi yanu yatha.
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 Месяц назад
Wasowa zokamba iwe osangonena zaku mcp zakozo bwanji a DPP chikuwakhuza ndi chiyani mbwaaaa iwe
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Mwasowa chokamba inu, inu nde zithumwazo mulibe? Musalimbane ndi Dpp siyinayambepo yagawa ndlama zimenezi tikuwonera kwa mcp
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i Месяц назад
Amalata mukatelo mwadyapo zoyakhulula achitchola koma zilipo koma osalimbana ndi DPP akupanga zawo Nanu pangani zanu tangoyamika kuti mukuwululana nokhanokha komande mphanatu munadya olakwika SKC
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy Месяц назад
Try to do your own things dont mention Dpp kuulurana mukuulurana nokha a MCP ife tilibeko
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo Месяц назад
Iwe uzikamba za mcp osati DPP ayi iwe ndi ngalu kwambiri et
@user-cv3zw9ic6d
@user-cv3zw9ic6d Месяц назад
Akugula iwe galu bweletsa masache kuno tisesere kuchimbudzi
@user-iw6cz5ft2l
@user-iw6cz5ft2l Месяц назад
Amalata mwatani kd?
@MaxwellMbesa
@MaxwellMbesa Месяц назад
Nthawi yanu dyeranitu
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Месяц назад
Galu wa MCP utu munawonapo nduna ya dzachuma kele kaja ikumwadza ma milion ngati mene mukupangila inu a MCP nde muwone KWACHA INATHA KALE KALE PANO CHIDZUDE CHA NDALAMA CHIFUKWA CHA UCHISILU WA CHAKWELA NDI MCP YAKOYO INU AGALU KWABASI
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Месяц назад
Machende ako iwe wagwa nayo
@user-bk4sm4jn9y
@user-bk4sm4jn9y Месяц назад
Ken panyapako galu wachabe chabe
@OswinDzama
@OswinDzama Месяц назад
Ifemusatisokosereinu muona kutsogoloku
@WillamLawson-gk1lw
@WillamLawson-gk1lw Месяц назад
Choka iweee zaziiiiiiiiiiii
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa Месяц назад
Chitsiru iwe mbuzi ya munthu maphwala ako wakudyesa ndalama simplex chithyola Banda
@user-lr5bz7qk2d
@user-lr5bz7qk2d Месяц назад
Malata mbuzi
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Месяц назад
Mbuzi iwe malata
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc Месяц назад
Galu wachabe chabe
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu Месяц назад
A Richard chimwendo Banda akuphatu aise
Далее
Ndikuopsyezedwa Chifukwa Cha Ma VN - Pastor Shumba
16:55
Chakwera V Mutharika: 2025 Kuli Gule - Redson Munlo
23:01
A Bakili Muluzi TV Tiwonana 2025  - Charles Ben Longwe
22:21