Тёмный

"Tikusakasaka mnyamata wa Bakili Muluzi TV." Watero Zikhale Ng'oma 

Bakili Muluzi TV
Подписаться 102 тыс.
Просмотров 44 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

24 сен 2023

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 588   
@stemango
@stemango 9 месяцев назад
Malawi is one of the peaceful country in Africa with lovely people who are loved worldwide, my advice to all the citizens safeguard this heritage and keep on loving one another. May the good Lord Keep on Blessing Malawi and Africa
@patsondamascus885
@patsondamascus885 9 месяцев назад
You say this is peaceful just because we don't have war ? The war we fight here in malawi it's worse than those gunshots
@user-ie7ut3qb8v
@user-ie7ut3qb8v 9 месяцев назад
Dziko mukachuluka umbanda ndiye kuti milibe chitetezo ndingomukonza zikhaleyu and atola khaninso akuchita matha kufunsa mafunso akuopa kuphedwa kkkkkkkk #malawiwavuta# akuwalemba mayina kuti akangofunsa funso lutsutsana nawo achite naye 😢 shame
@bayview4554
@bayview4554 9 месяцев назад
Koma wabakili mluzi yekhayo is true man
@victorbanda9039
@victorbanda9039 9 месяцев назад
Ndipo amaonjezadi kunyoza ati president ndiodwala kkk kwaiyeyu wabwino ndipitala basi was waonjeza agwidwe ameneyu
@SaidEfrem
@SaidEfrem 9 месяцев назад
bakili muluzi simbava ayi
@LikoMandowa
@LikoMandowa 9 месяцев назад
Mungovomeleza Kuti simukudxiwapo kuyendesa dziko ,sopano asilikali Ali kumenekoo ntchito yawo ndichani komawayitana akumaiko enaoo komano komanda was ame nayo kumangoonela ali aduuuu😂😂😂😂 dziko samayendesa munthu osavinidwa onani mulungu watikwilatu
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 9 месяцев назад
Zaziiiiiiii, ndiye bolansotu akanangokhala osapangitsa press briefing
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 9 месяцев назад
Chidzete ichi muyaluka
@user-td5zr7pd2u
@user-td5zr7pd2u 9 месяцев назад
Palibe chilipo et?
@kelvindickson
@kelvindickson 9 месяцев назад
Mabi okhaokha chosaphunzila chenicheni
@cassimmeleka40
@cassimmeleka40 8 месяцев назад
Awa a kayankhula amakhl pansi kunva zomwe adalankhulazo?
@georgesmart3791
@georgesmart3791 9 месяцев назад
Inu zoona so that truth is paining this government ndipo Awa adayamba kukusakani kale brother koma amalephera kukupezani.. Almighty God b with you always boss
@user-Grant260
@user-Grant260 9 месяцев назад
Arresting a person for speaking the truth is not allowed in the law, as the Minister of Homeland Security you should just follow what the Bakili muluzi channel is saying and not deny it like you are talking about. In short, you has failed to bring security to this country, so it is not good to scare people who are speaking justice
@nlbutoya.butoya
@nlbutoya.butoya 9 месяцев назад
For sure Truth 👍👍👍👍
@markoviskyhernandez9706
@markoviskyhernandez9706 9 месяцев назад
👍👍
@SameKaposa
@SameKaposa 9 месяцев назад
I'm agree with you brother
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 9 месяцев назад
Fact
@JohnMaonga2021
@JohnMaonga2021 9 месяцев назад
Fact
@Rafiki-pk7hw
@Rafiki-pk7hw 9 месяцев назад
galu wamuthu zikhale alibe chazeru,khope ngati nyani.komaso Miluzi Tv musaope,bweretsani chilungamo poyera.musaope muthu guys muope mulungu.Mulizi TV 🔥🔥🔥 🔥🔥🔥🔥
@davidkadyakapita8836
@davidkadyakapita8836 9 месяцев назад
Zikhale Ng'oma chitsiru kwambiri
@afritouch4660
@afritouch4660 9 месяцев назад
Mr. Bakiri Muluzi TV. Your life is in danger.! The fact that minister of home affairs calls you out that way, signals danger to your life.. The work that you’re doing is more than any other journalist ever rise in Malawi.. I would like to invite you to USA for your safety.. You will have your studio in my house until all settles.. We can’t manage to lose a nation asset like you.. Once you get here, We will help you to get an Asylum so you could do your work freely.. Get out of the country now before this Mbuzi eats you.. I’m seriously invite you to safe home here until all dust settles.. Come & do your work here.! Galuyu akukufunafuna kwambiri
@achinabonzoaise405
@achinabonzoaise405 9 месяцев назад
Muthandizeni MUNTHU
@MaxwellMustafa-ec8fc
@MaxwellMustafa-ec8fc 9 месяцев назад
Please 🙏 help him because MCP is after anthu akumenyera ufulu i respect him a lot.
@janelukundo8803
@janelukundo8803 9 месяцев назад
Chilongamo chawawa koma bakili tv ndi one help the guy if possible nchito agwilile ku abroad
@mustafapoison6546
@mustafapoison6546 9 месяцев назад
@@afritouch4660 I support you, this should be done in quick
@MALAWImovieslatest2024
@MALAWImovieslatest2024 9 месяцев назад
This man is the greatest man nde wina akufuna kumusowesa zachamba ay just leave him a a akufuna kuthesa history
@user-dm3bb4of9d
@user-dm3bb4of9d 9 месяцев назад
Speech yomwe alankhula andunawa.akudzilakwila Iwo akuyemela kudziwa kut kumangidwa or kugwidwa kwa mnyamata wa bakili muluzi. Kudzagwedeza Malawi yose.ndie pamenepo ofunika asachedwepo.coz awononga zinthu.eeehee
@markoviskyhernandez9706
@markoviskyhernandez9706 9 месяцев назад
😅😅😆😆😂😂!! Bakili Muluzi Tv ikusowesa mtendele zimbavazi!!
@user-px9jd9co3v
@user-px9jd9co3v 9 месяцев назад
Very true !
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 9 месяцев назад
😂😂😂😂😂 akutelo, zikhale ng, oma 😂😂😂😂
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e 9 месяцев назад
KkkkkkkkkkBakili tv ndi yonse .
@Eshumaelyussfu-fr9of
@Eshumaelyussfu-fr9of 9 месяцев назад
patumbo
@Fatima-li5rg
@Fatima-li5rg 9 месяцев назад
Machende Ako iwe zikhale mkamwa mopanda manomo😭😭
@abdulaziziislaj2416
@abdulaziziislaj2416 9 месяцев назад
Sangakupeze bro akunama love you bro.zikhale wasowa chokamba
@joemapiri4050
@joemapiri4050 9 месяцев назад
Wachamba ameneyo kusiya mbava zeni zeni kukalimban ndi mnyamata wa BM channel😮😮
@MartinJangaza
@MartinJangaza 9 месяцев назад
May the Good, Almighty and Loving God protect you bro. Continue exposing the dirty acts of these insane like ppo
@user-df1ct4bh7f
@user-df1ct4bh7f 9 месяцев назад
Bwanji enawo sakuwatchula ngat alipo.Inuyo brother mumanena zoona zen zen may Allah protect you brother 🙏 ❤
@joicemartin-ji5zu
@joicemartin-ji5zu 9 месяцев назад
Zikhale ng'oma ukumudziwamulungu Iwe okupha wakumidima
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 9 месяцев назад
Popanda inuyo a bakili muluzi TV, bwezi tili mumdima chifukwa cha akuba ngati amenewa. May God be with you always and protect you.
@HassanNopdhh-qc5ut
@HassanNopdhh-qc5ut 9 месяцев назад
Inu ndi athu oipha kwambili odana ndichilungamo agwilen inuso muzagwilidwa lino ndi ziko lilibe mwini sekilite ili bwino athu akufa si ugalu umeneo
@user-om7ol2mp6z
@user-om7ol2mp6z 9 месяцев назад
Koma galu uyu zikhale ng'oma ndye watikwana bwanji, komaso chitsilu chikulephela kuyankhula mbuzi yopanda mzeru. Koma sir osadandaula ife ndi ma support anu ndinu ndi amene mumatiuza zoona zikomo kwambiri sir
@user-nz8mq4ff3e
@user-nz8mq4ff3e 9 месяцев назад
Mukufuna kumpa ufulu wathu we have freedom to speak yes yes yes yes yes yes kulibe chitetezo kuno kumalawi ngati mukulowetsa asitikali aku Rwanda zonse tikudziwa Muthu oipa iwe zikhale Ng,oma chilichose chomwe mugatiuze mukufuna mutitseke cholinga tisadziwe zomwe mukuchita mukunama mwachepa we have freedom to speak
@BenardPeter-pd5mh
@BenardPeter-pd5mh 9 месяцев назад
Zikhale ng'oma machende ako forever with kagame and chakwela including Malawi army commander osaiwala wankulu wa police kulilongweko pamnyelo Panu tisiyileni malawi wathuyo muzipita Kwanu ku Rwanda musamale nane mukamapanga misonkhano yanuyo muphedwa nane, big bro pitilizan kutipasila nkhani mbulixi zikudana ndi chilungamo coz ayaluka
@francisiwalani4263
@francisiwalani4263 7 месяцев назад
Bakili Muluzi TV yatitsekura mmaso , more fire osaopa Bro
@samkazembe2393
@samkazembe2393 9 месяцев назад
😢 bro will make dua for you
@idris6597
@idris6597 9 месяцев назад
Iwe zikhale ng'oma mboli yamako wamva don't take Malawi for granted dzikoli si lako wamva udindowo wakukanikani ukulowesa zigawenga Za Ku Rwanda Mesa ndinu mu dziko muno pamsana pako
@user-bt5ud4bu9u
@user-bt5ud4bu9u 9 месяцев назад
Zikali ngoma thundu whanji wa mundu uyu eeeeee
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw 9 месяцев назад
Uuu even nkhuku kapena Galu ili nzelu ulula tiwaziwe mwina umawatuma ndiwe
@mayilosmunongwa
@mayilosmunongwa 9 месяцев назад
zoti anthu omwemwachula afadi ndiye ngati athu akamanena kuti chitetezo sichilibwino ndiye mukukana kufabwanji ziko muli chitetezo palibe zowopsezana tizinenabe khaya ndipanish tipase sitingasiye mukuyendesa ziko ngati akazi tikuvekani madiresi olomutayitana zigawenga muzangoti fera muzafa mosaziwika timakusiya dala inuso mukazangoti mwafa tizango pepani kwa able anu panyopanu azikhale Ng,oma mulibe zelu mwangokula chimbuno mumasekelela zopusa zomwe akupanga
@bkelly3053
@bkelly3053 9 месяцев назад
Ndiwopenga ameneyu akufunika zikwapu Zikhale ng'oma ndiopenga
@user-kv2vh8so3j
@user-kv2vh8so3j 9 месяцев назад
May good Lord protect you boss.
@husseinmoffatt
@husseinmoffatt 9 месяцев назад
Zaziiii kodingati mukupanga ZAuchitsilu tizingoyang'anila iwe ng'oma dzikolitu silamakoyi
@user-zd8cp9uo2e
@user-zd8cp9uo2e 9 месяцев назад
😂😂 Anachita kumulembera uyu amutuma km inu zinenan chilungamo bas zikhareyu n mbuz
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 9 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@parker2104
@parker2104 9 месяцев назад
I love you Mr Zikhale Kungoti athuwa amadana ndi Boma la mcp Koma fact is ma refugees amayenera kumakhara ku camp
@user-sk1wj9bw6l
@user-sk1wj9bw6l 9 месяцев назад
Ndiwe Galu naweso wava ndi mcp yakoyo stupid close your toilet mouth
@parker2104
@parker2104 9 месяцев назад
Inetu siwa mcp kapena DDP am just a fellow malawian amene amakonda dziko lake.
@parker2104
@parker2104 9 месяцев назад
Boma sina lirinso limakhala ndizoofoka zake. Chabwino inuyo akuzani then onetsani udolo wanu do something kuti musithe zithu not kumangopanga post ma video
@parker2104
@parker2104 9 месяцев назад
Kodi liliko dziko lomwe athu saphana
@user-sk1wj9bw6l
@user-sk1wj9bw6l 9 месяцев назад
@@parker2104 Ine samasapota wandale aliyese or chipani ayi kma kunena zoona Mcp ndi chipani cha magazi kuchokera kale lonse kmaso nkhanza lero zikuwachitira umboni. Ku Malawi utsogoleri unathera pa Bingu munthalika basi . After iye uja mpaka pano malawi sinapeze mtsogoleri ngati iye uja or bakili
@ElizabethChola
@ElizabethChola 9 месяцев назад
Asowa mutendele ndi bakili muluzi tv kkkkkkkkkk.
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 9 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂
@ImuraniChinyama-fq6np
@ImuraniChinyama-fq6np 9 месяцев назад
A1m proud to be third guy to my comments....our big mn don't be scared for this idiot dom chakwela n zkn we r behind u dawge lord protect u
@AbuMussah-wi7gb
@AbuMussah-wi7gb 9 месяцев назад
Don't worry my brother Allah is with you always. Let's go my brother and sister to make dua for him Allah can protect. Sikhale is crazy man
@muhamadshaibu9261
@muhamadshaibu9261 9 месяцев назад
Never give up mulungu akutetezan bro
@powercharios2087
@powercharios2087 9 месяцев назад
My the load be with you Bro and protecte you all the time Azikhale ngoma achitsilu inu mutu udangokula ulibe nzelu
@GoodluckPhiri-rc4sh
@GoodluckPhiri-rc4sh 8 месяцев назад
Aasaa ukupanga follow anthu pa socia media chifukwa chani????ndiwe ukupanga zimenezo God it's not u
@user-sk1wj9bw6l
@user-sk1wj9bw6l 9 месяцев назад
Zikhale ng'oma ndiwopusa kwambiri satana wa munthu
@hucklyrajabu7137
@hucklyrajabu7137 9 месяцев назад
Namachende ameneyu wamwa magazi chifukwa akuyankhura nyasi zimenezo
@benardmwenechanya7670
@benardmwenechanya7670 9 месяцев назад
Just continue we support you until the truth revealed government yoruba kwambiri kwasala kutigulitsa ndi Anthu tomwe
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 9 месяцев назад
Don't fear anything.wasala madzi amozi uyu Mulungu akuona .bakili Muluzi Tv ndi utumiki Heavenly sent. Mulungu akona everything yesaya 54:17 ipaseni moto zenzen kut adziwe kut malawi uno siwakale.
@khalifacalvinajass9998
@khalifacalvinajass9998 9 месяцев назад
Allah protecte you my brother don't worry
@user-dx4zu1wv4q
@user-dx4zu1wv4q 9 месяцев назад
Bless you brother where you u wamizala uyu zikare ngo,ma
@japhethjeremulimba
@japhethjeremulimba 9 месяцев назад
Being a minister dont think that youre mighty one, dont think that you can use your thoughts, power to interfere people or torture citizens. Siinu wamuyaya, and don't think kut people cant reach you there, let me repeat this DONT THINK THAT PEOPLE CAN'T REACH YOU THERE, bro zikhale ng'oma we can bring you down from there in a minute.
@user-yq1fl7ez1o
@user-yq1fl7ez1o 9 месяцев назад
Be safe big..... Allah akusogoleleni insha Allah
@samsonpadiwa9185
@samsonpadiwa9185 9 месяцев назад
uyu akunamatu we are all pray for you bro he can't do anything
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 9 месяцев назад
Chilungamo paja chinayandikana ndi mwano..... Big up bro
@AnordThomson-iw5ny
@AnordThomson-iw5ny 9 месяцев назад
Uyu amakhulupilila kagame kumapanga zanyasi mam'dziko lathu lamalawi, ndipo ife ndife eni nthaka Zikhale ng'oma ndi chakwera sumungatipusitse zonyasa zose mukupanga tikuzidziwa nthawi ya DPP kunalibe zimenezi kumakangana ndiwanthu obwela kumabela, dziko limachita bwino pachuma ngati muli anthu ochita ma business, mufufuze ka South Africa eni dziko za business alibenazo ntchito omwe amapanga ma business ndi ma foreigners obwela, nde inu mumalimbana ndi obwela ama business awo kodi dziko lamalawi lidzatukuka bwanji
@user-td5zr7pd2u
@user-td5zr7pd2u 9 месяцев назад
Auzenibwnobwno ndxodukamitu zkukamba andunawa
@MathiosJonas
@MathiosJonas 9 месяцев назад
Wakachaso uyu mburi kunthupi komaso muyuzim
@SamuelNandolo-nc2mo
@SamuelNandolo-nc2mo 9 месяцев назад
God bless bakili muluzi tv
@IsmailMadan-no7er
@IsmailMadan-no7er 9 месяцев назад
Nthawi ya ke si ino yoopa muthu naye azamwalira nd imfa yoopsa chisomali chizalowera ku chikamwa ko kuzatulukira ku Blantyre ndat asiye kuopseza mzika zanthu Allah is enough for me.
@nlbutoya.butoya
@nlbutoya.butoya 9 месяцев назад
Wait you will see where you are putting this country the tears of refugees always alive to god and god receive it 😭😭
@user-qm1ri6cr6w
@user-qm1ri6cr6w 9 месяцев назад
Zitetezeni big,timakusatani kwambiri
@user-zj2dr2rp1e
@user-zj2dr2rp1e 9 месяцев назад
Zikhale Ng'oma ndi ndunaaaaaa kapena bwampini! , akufuna funa munyamata wa Bakili tv chifukwa chiyani, chitsilu ichi, munthu akutsegula a Malawi kumaso uyu.
@sammalvitha
@sammalvitha 9 месяцев назад
May the God be with you bro,
@rickiez
@rickiez 9 месяцев назад
Uncle KZN ine sindikuonapo nkhani apa. Ndakhumudwa nanu kwambiri. Focus on developmental activities please. Otherwise timakufilani ✌️
@RichardSuman-cx3ls
@RichardSuman-cx3ls 9 месяцев назад
Zoti ndiwe wakulu wazachitetezo zaboza wabisaliramo ziwembu ndi Chakwera wakoyo
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 9 месяцев назад
Don't worry bro we are together with you
@swadickbasheer3665
@swadickbasheer3665 9 месяцев назад
Agaru awawa afikapo the is no need to theaters someone for speaking the truth kumati nkhani inakambidwayo ndiyaboza asilika akuruwandawo kulibe, anthu sakufa kumalawiko with terror attack useless leaders at tonse satana
@JonathanMkwamba-bz6du
@JonathanMkwamba-bz6du 9 месяцев назад
Chimutu chonyatsacho zikhale wamva
@alexiousmmwala
@alexiousmmwala 9 месяцев назад
This minister his head is not working properly and I'm sure he has problem in his head Don't worry brother man we're be with you always God will punish zikhale
@omarrasheed5568
@omarrasheed5568 9 месяцев назад
Zinkhale ng'oma u look like from Rwanda
@LUCIUSCHARLES-ei5vu
@LUCIUSCHARLES-ei5vu 9 месяцев назад
Sopano inu azikhale Ng,OMA mukuiwala Kuti muno muli democracy nthawi yotutumusana idatha chimenecho muchiziwe komaso wa bakili muluzi mukumunenayotu sadayambe lero kulankhulapo Za anthu amene amachita zachinyengo Ngati inuyo zikhale Ng,OMA ,ndiye musamuopsese ayi
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 9 месяцев назад
Ndimaona ngati muyamba mwapepesatu kumabanja oferedwawo Kaye,komano zikuoneka kuti mulibe umunthu
@falayichitsotso5371
@falayichitsotso5371 9 месяцев назад
Zikhale Ng'oma pls utalking nosense ngati watopa ndindala zowabera amalawi bwezi utangogona nkhaza zomwe mukupangila amalawi ndindani yemwe sakuziwa mipando yoikidwa ndi amalawi pano amalawi omwewo asanduka agalu anu omwe mukungowapha
@ThomasTrein
@ThomasTrein 9 месяцев назад
Machende osadulawo zikhale Ng,oma munthu akuuzani chilungamu dziko ufunaso kumangaso waku ulila chisisi chako shitsilu iwe
@user-qk1zg5ec5h
@user-qk1zg5ec5h 9 месяцев назад
Ameneyo atetezedwa ndi mulungu ndipo timamukonda kwambili ❤amakamba zoona
@WakuMalawi
@WakuMalawi 9 месяцев назад
Facts..!!!
@user-hd1dz5ni4x
@user-hd1dz5ni4x 9 месяцев назад
Ngat timadalila muthu kumalawi ndinuyo tikhala tikukupepherelani pachimenechi osaopa ndipo mupitilize kuti tsekula maso
@fraserbereck2269
@fraserbereck2269 9 месяцев назад
Just look at his face changonyasa zonsetu 😮😮 don't be scared bro always stand for truth
@user-zh9kb2sj2i
@user-zh9kb2sj2i 9 месяцев назад
Dzikomenelawolelamu simukuwona komaso za bakili muluzi tv usalankhulepo tangoyambaniina
@user-mc8gk4xv3f
@user-mc8gk4xv3f 9 месяцев назад
Tiyeni tonse tipemphere masalimo 35 kwa masiku 7. Ziwabwelere okha amene akuwafunira zoyipa anthu awa. Bakili muluzi channel bon kalindo mutholo mphepo pungulani longwe munlo Billy Banda ndi ena onse amene akusakidwa.
@sadickhassanie7486
@sadickhassanie7486 9 месяцев назад
Akuti pali wina umaika ka nyimbo ka sports tiliiii tiliii😂😂😂😂😂
@kachingweshareef2302
@kachingweshareef2302 9 месяцев назад
Osapa bro Alla will protect u
@staubioxygensensor559
@staubioxygensensor559 9 месяцев назад
Aaaaaaaaaah iyi ndimbuzi pakut I'm far from yu bro koma osadanda sapanga kanthu uyu
@user-ui4ux5kc8d
@user-ui4ux5kc8d 9 месяцев назад
Motiii zotii akufadi iweyo sukudziwa bwana tangoyesa kuika chitetezo cholongosoka osati zomwe mukuophyezazo ayii dziko lino linali lamkaka ndi uchi nanga ziripati?? Zikhale Ng'oma tetezani anthu osati chiwembucho ndipo mukufunanso ena chonsecho aku Rwanda alikomkono eeee Malawi watha basi
@user-lh9ue5np8o
@user-lh9ue5np8o 9 месяцев назад
Uyu zikhale ng'oma ndichisiru kwabasi usowa ndiwe ,mmalo mosaka mbava ulibize kulimbana ndi anthu opanda zolakwika
@amabhohlela.3492
@amabhohlela.3492 9 месяцев назад
Mmm koma press conference yake mmmmm,yaziiiiii!!! Kulankhula kumeneko n'kumati ndi Minister of Security and Homeland ???🤔🤔🤔,
@wonganinyirongo1887
@wonganinyirongo1887 8 месяцев назад
I'm with my beloved country and government, osati ma bulutu oti u don't even do thorough research but kupanga ma post without research, akunjatani!
@jagudanicolas5436
@jagudanicolas5436 9 месяцев назад
Never give up asatana awa akunama titsekula ina
@user-hz9gw6mm4z
@user-hz9gw6mm4z 9 месяцев назад
Asakuopsezeni Sir Go ahead
@davidkadyakapita8836
@davidkadyakapita8836 9 месяцев назад
Zaziii Zikhale kape
@ZONKEMASEKO-rm5fn
@ZONKEMASEKO-rm5fn 9 месяцев назад
Never give up
@nyararaishumba9288
@nyararaishumba9288 9 месяцев назад
Iwe zikhale usamale dzikoli silako wamva. Chimutu chotupacho osaopa bro
@SACHAMAGIC
@SACHAMAGIC 9 месяцев назад
Press briefing yake yopanda fundo . Ndima points omawelenga amenewo 😂😂😂 ayalutsa ndani poti tadziwa ma secrets ake
@robertbanda765
@robertbanda765 9 месяцев назад
Nyasi zimene zimachitika ku malawi, aliyense kukhala mtola nkhani? Aliyense akufuna upulesident pa nthawi imodzi, ichi nchifukwa chake kuli 5 years taem yoti munthu mmodzi akhale mtsogoleri wa dziko mukakondwera naye mumamusankhaso, boma lilipoli linachita kusankhidwa ndi anthu ambiri ndichifukwa ali mboma kwatsala 2 years yokha adzasankhidwaso ena olo omwewa koma not zimene mukuchitazo ayi zikutanthauza chani kuwanthu zikubweretsa mgwirizano olo kusankhana ndi chipwirikiti, mavuto aliponseponse tikukhumbila kuno kwa anzathu kuli mavuto kudula kwa zinthu kuposaso uko koma kuli bata anthu amalemekeza mtsogoleri sungamuvere munthu kuyankhula zomanyozana kapena kunyoza mtsogoleri wa dziko kulibe umangiwa ncifukwa chake kuli mtendere kuno, mukumapha anthu ndinu kuti muzipeza zoyankhulayankhula pofuna kumanyoza mtsogoreri sorry Malawi pariament iunikepo pa za social media anthu akupusa kwambili.
@fredgabrielnyangulu
@fredgabrielnyangulu 9 месяцев назад
Ndipo awa ndi a chitsiru kobasi mfundo alibe akungokamba nkhani zaziiiiiiiiii ndie press briefing yake iti kapena akufotokoza nkhani kwa Ana ndi mkazi wake . Zoti anthu ambiri akumvera alibe nazo ntchito ai
@jayzerfficial4417
@jayzerfficial4417 9 месяцев назад
May the almighty living GOD protect you brother❤️
@user-dx4zu1wv4q
@user-dx4zu1wv4q 9 месяцев назад
Zikare ngo,ma ndi wasatanic chimutu choipacho akadafa komaso ndi wakatangere😂😂chibwana eti muri tendere wanji wayiweyo anthu akupedwa never trust you
@raytavares2256
@raytavares2256 9 месяцев назад
Its called photoshop and promoting hate speech and representing misinformation on Internet is crime you are right honourable minister. What you are saying the truth.
@ShuaubuBanda-yh1er
@ShuaubuBanda-yh1er 9 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂
@raytavares2256
@raytavares2256 9 месяцев назад
What is laughable about this? Its the truth misinformation and promoting hate speech is crime like those ISIS terrorist were doing earlier days.
@essaumatipwiri4370
@essaumatipwiri4370 9 месяцев назад
Zukhala ngati sitinakonzekere press briefing bwanji
@user-pt1fy3qg4u
@user-pt1fy3qg4u 9 месяцев назад
Never give up bro ❤
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 9 месяцев назад
Walephera kutetedza mzika iwee, ukungotionongela ndlama zathu zamisonkho. Chilungamo ukuchidziwa usanamize amalawi apaa. Ingotulani pansi udindowo uzikalela zizukulu ukoo after all wakula
@blessingschibaya6061
@blessingschibaya6061 9 месяцев назад
analiko Albert muwalo iwe zikhale batcha nthawi yanu ikutha tiwonana 2025
@ulemubanda3934
@ulemubanda3934 9 месяцев назад
BM TV ndi yabwinobwino only that amaonetsera mbali kuti ndi wa DPP komabe it's my favourite RU-vid channel
@ShavielSiment
@ShavielSiment 9 месяцев назад
Kuteroko akudalira asilikali a kagame. Munthu akunama bro ife timakonda bakili muluzi TV tilipambuyo pako
@paulthulama
@paulthulama 9 месяцев назад
Be safe bro
@sammyree8843
@sammyree8843 9 месяцев назад
I know Zikhale he was one a friend of my uncle but to be honest he is dumb. Why is he he'll bent to arrest people and punish them himself who is he? My brother keep doing your nobble work but we can't risk to loose you i am extending my invite to come here in RSA will stay with me till the dust settles these guys are hyenas we need to protect you at all cost
@josejoaolamissone4195
@josejoaolamissone4195 9 месяцев назад
Don't worry everything will be better
@user-mf4jv3tk7x
@user-mf4jv3tk7x 9 месяцев назад
Analephera za Satar apange prove kaye zimenezo komaso anene iyeyo Zikhale Ng'omayo ngati chakwera sananame kuti anthu azizagula fertilizer Mk4095 komaso iyeyo ayakheso zamabrundi kodi iyeyo mulungu ndiye samamuona
@sultancheyaoking1389
@sultancheyaoking1389 9 месяцев назад
Akuti tikugwirani tikuyaluseni 😂
@user-qi8xe7qh1e
@user-qi8xe7qh1e 9 месяцев назад
Osapanga ubale ndi Mozambique bwanji kuja ananyelanyelako kamuzu wanuwuja bwanji ngati mukufuna chitandizo chasilikali akunja osapita ku zambia kapena ku Tanzania bwanji ndi pafupi mukufuna chani ndi asilikali ku Ruwanda zauchitsilu ayi
@lastonkandiyado4526
@lastonkandiyado4526 9 месяцев назад
Panya pake zikhale ng'oma yo mbuzi yamuthu akulembela kukhazikisa chitetezo mudziko akufuna kulimbana ndi muthu osalakwa pantombo pa agogo ake
@liki-likiladies---lilongwe6963
@liki-likiladies---lilongwe6963 9 месяцев назад
Wamisala ameneyu he thinks tili under dictatorship leadership
@austinchimpakati8299
@austinchimpakati8299 9 месяцев назад
Azikhale ng'oma kumeneko nde kukanika bwanji ngati muli anthu ozindilira osawasaka nokha bwanji muitana anthu akunja Nde mukamakozeka kuitana akunjawo mukhala inu mutapindidwa pindidwa kale komaso okuthandizaniwo Led c ili ready
Далее
BON KALINDO PA 2 JULY 2024 |
15:55
Просмотров 15 тыс.
Lord Rothschild Claims His Family Created Israel
19:41
Dictatorship tinathana nayo 1994
14:50
Просмотров 44 тыс.
BAKILI MULUZI KUCHEZA NDI BRIAN BANDA 11/05/2024.
58:38