Тёмный

BON KALINDO PA 2 JULY 2024 | 

DZIWE TV
Подписаться 19 тыс.
Просмотров 18 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

1 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 52   
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 2 дня назад
Bonnnn! Kalindoooooo! The DC😅😅😅😅 mwana oopsya kwambiriiiiiiiiiii😅😅😅 We love you forever asanje atembenuke azilume kunsana😅 😅 more 🔥 🔥 Dr DC
@smartjohn4684
@smartjohn4684 2 дня назад
I like bon kalindo amatiimilira kwambiri zed
@mecanhelaseomundo915
@mecanhelaseomundo915 2 дня назад
The DC umakwana. From Mozambique.
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 День назад
Our own opposition the DC
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e 2 дня назад
Ndakulira konko ku police nthawi ya Kamuzu ,Ndipo M'sandikumbutse inu zokoma ndi nzabwino zomwe zinali nthawi imeneyo Sir❤❤❤
@AzaniaSibuqashe
@AzaniaSibuqashe 2 дня назад
Bon kalindo the dc sanama ❤❤❤❤
@user-eh6xz1vx8p
@user-eh6xz1vx8p 2 дня назад
chabwino born kalindo akupanga ndale komano fact zomwe akunena zikuchtika en ambiri tikuona koma mantha kuyakhula hahah salute to yuh the DC born kalindo
@dysonmasiye5736
@dysonmasiye5736 2 дня назад
Nkhani zonse zamveka ndipo Ambuye azikusungani ndi moyo wautali. Dzikoli likuonongeka ndi anthu ophunzira komanso opembedza osaiwala amaudindo. Anthu ochuluka ali mu umphawi wa nyoooo koma sangalankhule chifukwa alibenso ufulu wolankhulawo. This is why Christ is to come adzapereke makofi ndi mateche plus mambama kwa anthu tonse oipa, ozunza, ankhanza. Akubweratu ndipo si kale owowo
@chiletsobisweck5007
@chiletsobisweck5007 2 дня назад
Alindinkhaza chifukwa cha mkwiyo wamalipiro ochepa 😂😂😂 Kalumo kobunthwa🤸🤸🤸
@WiskMaulana-ky6nf
@WiskMaulana-ky6nf 2 дня назад
😂😂😂😂😂😂 ameneyo ndiye booni kalindo aka winiko
@FrederickFyson
@FrederickFyson 2 дня назад
Exactly ❤❤❤❤❤ Mr DC
@crosbeygondwe5403
@crosbeygondwe5403 2 дня назад
Bonnnn!!!!!! Kalindoooooo!!!!!
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 2 дня назад
I salute you 😅😅😅 muzibwera everyday,chilungamochoooo tizimva
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn День назад
TAPANGISANI MA DEMO UTHENGA UMVEKE IZI ZOMANGUYANKHULA SAAKUMVA ABOMAWA
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 2 дня назад
Mmatiuza zoona , izi ndi zeni- zeni maka za ku mapasipoti mukutiuza chilunga. Komatu Chakwela nda agulu anzakewo azafera kutulo , boma lankhaza ndi kuba, Chakwela must gooooo!
@user-se7wf4ei5b
@user-se7wf4ei5b 2 дня назад
Zovuta kwambiri kuma passport tikuguba ngati tikulonjelela ngongole koma amene anatikhalilayo anatikakwila kwambiri
@LeooTungama
@LeooTungama День назад
The Dc moto kuti buuuuuu🎉🎉🎉
@user-xc1gk6bw6m
@user-xc1gk6bw6m 2 дня назад
We are love you always fadah
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn День назад
Director wa Migration yo akugwira ntchito yanji??? ma passport sakupangidwa ..
@AngozoMalunga
@AngozoMalunga 2 дня назад
Keep it up Mr born kalindo
@PasadiKatole
@PasadiKatole 2 дня назад
Kuswa kuswa basi akunjoya ndi a mcp okhaokha mdziko muno ngakhale akufonyika alibe problem
@LovenessNdlovu-w1p
@LovenessNdlovu-w1p 2 дня назад
Born kalindo mr nyooooo !! Umatha❤
@user-yi2fg1lh8x
@user-yi2fg1lh8x 2 дня назад
Mpaka kusilila usilikali chifukwa cha Nido..
@ForsterThawan
@ForsterThawan 2 дня назад
Sukunama aise iweyo umatha kuyankhula Bon kalindo
@JonathanTambwali
@JonathanTambwali День назад
DC tsopano 🎉🎉🎉🎉
@RamseyWasi
@RamseyWasi 2 дня назад
Apempheni apuulewo kuti Mulamuliileko inuyo miez isanu.tione kenakake kamene kangasiinthe. Please abeg
@user-so7wg6ii5m
@user-so7wg6ii5m 2 дня назад
The DC mwana ooooooopsa kwambili ❤
@wisdomchilanga723
@wisdomchilanga723 2 дня назад
Tiyeni tonse tikavote mwanzeru 2025 awa akapume chifukwa ndiye sasiya kukhesa mwazi mmalawi
@smartjohn4684
@smartjohn4684 2 дня назад
Km a malawi tilibe gwirizano tiyen tizuke malawi
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 2 дня назад
Inu aboni yambisani chipani tizakuvotereni ndipo mzawina
@user-ph6yr3fh8w
@user-ph6yr3fh8w 2 дня назад
The DC mwana ovuta kwambiri
@JamesMwayi-ct3wv
@JamesMwayi-ct3wv 2 дня назад
Nde maganizo amneoo mudachedwa nawo coz pakatipa pa dutsa anthu awiri peter nd ndi mzake nde mukalakhula lero chifukwa Cha chakwera aaaaa muzikhla nd umunthu osangoti kukhla nd Kwa ulere ai
@franklameck5700
@franklameck5700 2 дня назад
Inu munali kuti osayankhula ??? Mzanu wadzuka mkuyankhula walakwa ? Inu osayambitsa zanu bwanji, mukudikila wina ayankhule inu mkumampanga let down ?
@John-v7p
@John-v7p День назад
Keep on fire
@user-vw4vc9xd5z
@user-vw4vc9xd5z 2 дня назад
malawi Pena tiziganiza asamangoyika anthu pampando anthu opanda dzelu alipoyi Bola kazizi amaganiza koma uyu aaaaa ayi
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 2 дня назад
Zoonadi tikuvutika kuno chifukwa kumalawi ntchito kulibe
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m 2 дня назад
The DC ❤❤❤❤❤
@Catheymtimuni
@Catheymtimuni 2 дня назад
Mavuto aonjezadi
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 2 дня назад
Bon Kalindo number one
@andrewmtendere3167
@andrewmtendere3167 2 дня назад
The dc❤
@ImraanKaletso
@ImraanKaletso 2 дня назад
Zoona the DC that's true
@getbusy7173
@getbusy7173 2 дня назад
mwaaaaaaaaaaaaana oooooooooooooopsaaaaaaaaaaaaaaa kwambiriiiiiiiiiiii
@JamesMwayi-ct3wv
@JamesMwayi-ct3wv 2 дня назад
Km ngati ku Malawi kuno kuili chitsilu kwbri nde nd iweo kd umafuna kutchuka kpn udindo aaaaa machende ako bwji umandipsetsa mtim kwbri
@user-qn9vc8em6z
@user-qn9vc8em6z 2 дня назад
Inu ingokhalan chete ....monga mmene akuendela malawiyu zikukukomeran ......
@mwayimmbanga4011
@mwayimmbanga4011 2 дня назад
Machine
@chrisgremu740
@chrisgremu740 2 дня назад
Mukunya inuuu
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 2 дня назад
I trust you mr DC
@JhdaLifi-vu9sd
@JhdaLifi-vu9sd 2 дня назад
Ddddddddddddddddccccccccccccccccccccc
@SellahBanda-cg9kh
@SellahBanda-cg9kh 2 дня назад
The Dccccccccccccc
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer 2 дня назад
Tili pambuyo panu DC born kalindo more fire 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Далее
It was like a real simulation👩🏻‍💻
00:15
Просмотров 3,6 млн
LIMPOPO FM 04 JULY 2024 NDI COMRADE NTANYIWA,
29:32
Просмотров 18 тыс.
BON KALINDO LERO PA  4 JULY 2024 |
18:15
Просмотров 24 тыс.
ZOCHITIKA KU DPP🙌🙌🙌🙌
23:16
Просмотров 26 тыс.
Kodi Malawi Adzasintha Liti - Bon Kalindo
21:07
Просмотров 13 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 110
29:32
Просмотров 13 тыс.