Тёмный

USAUVER S07E08 ENJOYMENT 

Piksy TV
Подписаться 56 тыс.
Просмотров 48 тыс.
50% 1

Happy New Year!!!!

Приколы

Опубликовано:

 

30 дек 2022

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 230   
@enitterfretcher6567
@enitterfretcher6567 Год назад
Mpaka wapakira kale kkkk sopano Berita ukuithawiranji nkhan mpaka akakupakirire kkkkk kwanu ukufunadi kma iwe
@tazmeenmdals9904
@tazmeenmdals9904 Год назад
Ati ngati watopa nane ukandisiye kwathu.....😂😂😂 It's the response for me ati walongeza kale???
@jamesonvunikaphiri8300
@jamesonvunikaphiri8300 Год назад
This bartender he's also a good actor, koma Gani yo 🙌🏾😂
@watipatsamtepa953
@watipatsamtepa953 Год назад
A Eddoh ndi amuna ali ndi Data 🤣🤣🤣🤣🤣
@alinafemakandanje4687
@alinafemakandanje4687 Год назад
The "walongeza kale" part 😭😭 🔥🔥
@lyndandovie-jere2063
@lyndandovie-jere2063 Год назад
Ndipo. Mwano wake eee
@lusunguhkayira6924
@lusunguhkayira6924 Год назад
Inu mmabanjamu anthu akuyankhana🤣
@macjessierachel9776
@macjessierachel9776 Год назад
Koma Albert muli mwano kkkkkk ati imeneyoso ndi option ndithu😂
@ekarikalaje
@ekarikalaje Год назад
😂😂Ati tiye ukandilongozere aah aaah Berita
@lusunguhkayira6924
@lusunguhkayira6924 Год назад
I really love how you address real-life-current issues... Love that
@sothinchipeta6098
@sothinchipeta6098 Год назад
Albert banja lake nde lalowa competition sure kkkkkkkk
@troychikhwaza-Mw
@troychikhwaza-Mw Год назад
Kept up guys God bless you all I learned zinthu zambili kuzela ma movies anu
@tiyanjanethomo8560
@tiyanjanethomo8560 Год назад
Albert wakwiya,,, komaso tu ngozo and barman,, penapake ,, that was nice,,,,
@dominicmokowa9170
@dominicmokowa9170 Год назад
Ngat watopa nane ukandsiye kkkkkk wina kuzayakhaa kkk walongeza kale wamowa makan at sanaledzere kkkkkkkkk
@giftmatemba3194
@giftmatemba3194 Год назад
Super Guys continue and continue God bless your team guys and this coming yr mupitilize kuti sangalatsa ❤❤❤
@corneliusphiri5519
@corneliusphiri5519 Год назад
Ati Mwalongedza kale😂😂😂😂some options so simple to manage wena🤣
@quincyswart1884
@quincyswart1884 Год назад
Ndipo inu kkkk
@priskela1
@priskela1 10 месяцев назад
Not the abusa trying the mowa and kunyambitila😂😂😂😂
@hanifamussa3949
@hanifamussa3949 Год назад
🤣 🤣 Ati, tiseke aaah kma barman, ati walongeza kale 🤣🤣Albert kuyankha kwa Bwanj 😅😅😅😅Kmatu mai ngozo asowa eeh🙌
@glochilangwe936
@glochilangwe936 Год назад
Mmatha guys........thumbs up
@BebehRhymah
@BebehRhymah Год назад
Everytime am watching this series am overjoyed I wish to wait kut ma episode achuluke but I fail🔥😂
@Xris241
@Xris241 Год назад
Abusa satisunga awà....amva kale kuti ndi mutu wa kachaso koma kumwansooo😂😂😂
@calvinkawisa824
@calvinkawisa824 Год назад
A Edoo ayiopera ,,, 😂😂 aaaah sinanga phone yo ndiyosweka
@florencechaps1518
@florencechaps1518 Год назад
Koma Guys ai ndinthu mumaitha. Mumatiiwalitsa mavuto m'makomomu. U ar talented indeed
@MsSerahMw
@MsSerahMw Год назад
Albert ndi obowa🤣🤣🤣🤣🤣utseka bwanji buyer alipompo
@gracekachali4505
@gracekachali4505 Год назад
Ndiponso asanamalize kumwa😂😂😂😂
@LaughMalawi
@LaughMalawi Год назад
Big up ma guy🔥🔥🔥
@godsgirl480
@godsgirl480 Год назад
Team barman.. happy new year 🥂 to you all 🙏❤️
@mwaikopolande1446
@mwaikopolande1446 Год назад
Abusa mpaka kulawa mutu wa kachaso,,very kiritiko
@mimiwrld202
@mimiwrld202 Год назад
😂 😂 Barman ndi Ngozo muleke zomampanga confuse Albert 😂😭
@tgf2240
@tgf2240 Год назад
Zoona Barman angakanike kuyizindikila pic ya Belita chifukwa choti phone ya Albrert ndiyosweka?😂
@ReubenGoliath-dl9zp
@ReubenGoliath-dl9zp Год назад
Koma azibambo anakonza😂😂 uncle HYPHEN ulemu wanu
@josephydeves5589
@josephydeves5589 Год назад
Big up gyz km mukumachedwa kutulutsa2 mpaka pano ya week ino kulibe2 ay😂
@tasneemkuipa5761
@tasneemkuipa5761 Год назад
Big up guys🔥 nyccccccc keep bringing the heat!! Happy new year to y'all 🎉
@janenkhoma6447
@janenkhoma6447 Год назад
Kkkkkkk maboza amuna kwathu Tema tiyole ngozo
@kingllie2433
@kingllie2433 Год назад
Gani🔥🔥sinalezele ine...I should die and decompose😂😂😂😂abudulatu ndiwo zagulu uyu😂😂😂😂
@williamskaudzu3523
@williamskaudzu3523 Год назад
You guys are good. Keep it up
@brandylikoswe1898
@brandylikoswe1898 Год назад
Bar man sanaone nkhope screen ndiyosweka😂😂😂😂😂😂😂😂🙌
@gracekachali4505
@gracekachali4505 Год назад
Ndiponso aona bwaj nkhope phone iliyosweka😂😂😂😂😂
@ulemuvinmcentkaliwata9604
@ulemuvinmcentkaliwata9604 Год назад
Kkkk,ati ndiseke,mukamwa umenewo
@ogrinhomkandawire4907
@ogrinhomkandawire4907 Год назад
Mbusa mpaka kudziwa mutu wa kachasu😂😂😂
@gertrudechipojola
@gertrudechipojola Год назад
Koma abale, ati walongeza kale 🤣🤣🤣🤣
@khadijailiyasa5315
@khadijailiyasa5315 Год назад
Big up guys keep the fire burning 🔥 🔥🔥😉
@dylessmwanguku5958
@dylessmwanguku5958 Год назад
Komatu kwachitika chipwilikiti kumalo komwela 😂😂😂😂😂
@faindanbanda3840
@faindanbanda3840 Год назад
Eeeh barman ndi moto😂😂👏💥
@faithbanda6493
@faithbanda6493 Год назад
Ndiye mwati Mtebe ali pa banja
@Aaron-MW
@Aaron-MW Год назад
😂😂😂Nkhani ya Mtebe mpaka yapangisa barman kutseka bar
@raymondlaisi2095
@raymondlaisi2095 Год назад
Abusaaa kudzalawa mutu wakachasu 😂😂
@lindiwemisomali178
@lindiwemisomali178 Год назад
Bar man, kuyipatsa moto 🔥🔥🔥
@dicksonbanda5731
@dicksonbanda5731 Год назад
Koma kwavuta eeeee, man Gani ndi fireeeeee
@lusunguhkayira6924
@lusunguhkayira6924 Год назад
Thanks for this
@farmproducetraders5463
@farmproducetraders5463 2 месяца назад
Akuti imeneyoso ndi option ndithu 😂😂😂😂 Albert
@modiseusi4412
@modiseusi4412 Год назад
Happy New year GANIZANI 😃😃😃😃😃
@collinsdickson983
@collinsdickson983 Год назад
Fire kut bhùu🌋🌋🌋🌋🌋
@moniccamlima1418
@moniccamlima1418 Год назад
Edo for me😂😂... Edo 2023 uyambe kunenetsa chilungamo osamathawa nkhani
@brightonnanyanga3
@brightonnanyanga3 Год назад
Kodi anthu inu mwasiya ...now two weeks Ife tikudikira aaaaaa plzi we are following with interest
@keithwellzande1199
@keithwellzande1199 Год назад
kasowatu ka USAUVER KOMA 😉
@harrisonyambukani4468
@harrisonyambukani4468 Год назад
koma kuchema mzanu akufuna aweluke inu mukuti 4 shots
@mpido-mpido9250
@mpido-mpido9250 Год назад
Wow! This is nice...keep it up guys....
@jameslenardmasamba794
@jameslenardmasamba794 Год назад
bola Albert wadziwa zoona zinazo athana nazo konko bola asazimangilire chifukwa ndiye malawi walusa
@Stoker_Austin.
@Stoker_Austin. Год назад
Big up to Ganizani 😂😂
@isaacnkhadze135
@isaacnkhadze135 Год назад
Mutu wakachasu abusa kudzalawaso hahahahaha
@teyshachiwenda
@teyshachiwenda Год назад
Gani🔥🔥🔥mumakwana ma guy big up
@quincyswart1884
@quincyswart1884 Год назад
Atseke shop kkkk
@ellanchirwa1957
@ellanchirwa1957 Год назад
Yalakwa
@abackmtambo9947
@abackmtambo9947 Год назад
😂😂😂ayed mkaz yo amudziwa angokana kutay customer 🔥🔥🔥🙌
@fredrickjrmanjandima6508
@fredrickjrmanjandima6508 Год назад
ati imeneyoxo ndi option🤣🤣🤣🤣
@chikaikogolowa6303
@chikaikogolowa6303 Год назад
Amwene nditseke
@watipatsamtepa953
@watipatsamtepa953 Год назад
Ndayamba ndine apa
@mussaabdul6142
@mussaabdul6142 Год назад
😂
@imamwali2693
@imamwali2693 Год назад
Gani🤣nde abusa akulawaso mutu
@owenthewenbub4439
@owenthewenbub4439 Год назад
Can't wait ooooo 😁
@laustkay5245
@laustkay5245 Год назад
Eeeh 🔥🔥🔥🔥.... Zili bhooo
@andrewchiusiwa3487
@andrewchiusiwa3487 29 дней назад
Mmakwana ma biggy
@ImmzyP
@ImmzyP Год назад
Poledzelapa Gani 🙌🙌
@steveal-banda2517
@steveal-banda2517 Год назад
Abusa alawa mowa kkkk
@blessingsmunthali9202
@blessingsmunthali9202 Год назад
Basitu nde nkhani zake
@hamzarhanniff
@hamzarhanniff Год назад
aaaaaa mpaka 3weeks bwanj
@chisisbongani5664
@chisisbongani5664 Год назад
Ndipo inuyo Ndi mayo mayo🥳🥳🥳🥳
@lusunguhkayira6924
@lusunguhkayira6924 Год назад
Bartender mpaka akutseka nthawi isanakwane...
@osbornleman2500
@osbornleman2500 Год назад
edo bar amatseka masana kkkkkkkkkkkkkkkkkkk after mutaishosha eti kkkkkkkkkkkkk
@dysonart6003
@dysonart6003 Год назад
Koma barman!!!alibho
@beatricechanache4864
@beatricechanache4864 Год назад
Bartender pora fire 🔥 kkkkkk ati phone ndiyosweka sindikuona kkkkkkkkk
@blessingsphiri7905
@blessingsphiri7905 Год назад
Hahaha komatu ganizani😂😂
@twarichissah4222
@twarichissah4222 Год назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Walongeza kale ameneyo ✌️😂😂😂
@jasonkamanga658
@jasonkamanga658 Год назад
Tiseke 😂😂😂😂 situation very tough
@thokozanimuyawa9365
@thokozanimuyawa9365 Год назад
Gani my guy😂😂😂😂🔥🔥🔥🔥
@lawrechi2364
@lawrechi2364 Год назад
Mumachedwetsa kutulutsa ma episode bwanji. Mpaka 2wks episode isanatuluke
@robertgbanda3825
@robertgbanda3825 Год назад
Mubusa wachinyengo kwambiri wadyaso
@thokozanimuyawa9365
@thokozanimuyawa9365 Год назад
Ati eeeeeh nditseke😂😂😂😂😂
@isaacnkhadze135
@isaacnkhadze135 Год назад
Bar man 😄😄😄 ndiweluke
@harrymagalasi9585
@harrymagalasi9585 Год назад
Ina ibwele koma😂😂
@pemphochingamba1548
@pemphochingamba1548 Год назад
Aise umatisiya malele....uzipangako ka 30 minutes
@eluffymthawanji8803
@eluffymthawanji8803 Год назад
Bartender uzapunthidwa za eni
@mathewsngosi2084
@mathewsngosi2084 Год назад
Mumakwana guys I can't wait the other part
@mayesotanangale2112
@mayesotanangale2112 Год назад
Abusa alawa mutu wakachasu kkkkkk
@lloykings3391
@lloykings3391 Год назад
za matope, even me i don't understand. Koma Gani palibeso😂😂😂😂😂
@daviekasusu9015
@daviekasusu9015 Год назад
Hahahaha barma nayeso aledzera😁😁😁
@khairamsiska5203
@khairamsiska5203 Год назад
Ase Gani🤣🤣
@francisc.nkhata3070
@francisc.nkhata3070 Год назад
Koma man Edo kukhala ngati kawabayaso nawo bwanji? Second thing, kodi m'busa nsapato samasintha ?
@isajames4501
@isajames4501 Год назад
Nyc gyz
@chikondikaliati8037
@chikondikaliati8037 Год назад
Aponde amapanga record kut akamadzamuza ntembe zidzamveke ndende
@priscachisi4345
@priscachisi4345 Год назад
Koma zinthu zake eish
@eluffymthawanji8803
@eluffymthawanji8803 Год назад
Komatu Ganiiiii
@isaacfesani2357
@isaacfesani2357 Год назад
Kkkkk, mpaka abusa kulawa mutu wakachasu
@eurekamulli3853
@eurekamulli3853 Год назад
A Edo😂😂😂😂
@genechanga5083
@genechanga5083 Год назад
Nasankha mowa pali love...
@MindsetChange144
@MindsetChange144 Год назад
Ganizaniiii 🔥🔥🔥
@pemphojimu
@pemphojimu Год назад
Ma videos mudapanga improve akumaoneka bwino. Happy New Year.
Далее
USAUVER S07E09   NDIKUFULUMIRA
16:13
Просмотров 64 тыс.
USAUVER S09E07 - GRADUATE
26:37
Просмотров 11 тыс.
Kunte - Chuma
10:24
Просмотров 32 тыс.
USAUVER S04E08 - NDALAMA ZANGA
14:34
Просмотров 33 тыс.
Kunte Komedy - Lata
5:19
Просмотров 14 тыс.
Tikuferanji 25 May 2024
26:23
Просмотров 52 тыс.
USAUVER S08E01  CHPS AND EGGS
18:54
Просмотров 63 тыс.
Mr Jokes/Kuopsa kwa Bausa.
1:00:16
Просмотров 62 тыс.
няня привела в дом чужого
0:59
СРОЧНО ДОМОЙ! Эта НЕ КОНФЕТА!
0:21