Тёмный

Zina mumatiyamba dala kuti muzitimanga. Uthenga opita kwa Chakwera. 

Jay Kawere Mw
Подписаться 13 тыс.
Просмотров 12 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

9 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 67   
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 17 дней назад
Keep it up my brother for standing and show the Nation that Tonse Alliance is usiless Government and let me warn Kumkuyu for playing with the Malawians.
@dominicmphepo-jk8lk
@dominicmphepo-jk8lk Час назад
Chitukuko chomwe abwelesa a chakwela kumpoto ndi kumanga kamulepo kaluwa basi osati zinazo bro palibe chomwe angapange let's wait will judge them better pa 2025. Osawopa, osafooka, osatopa.. Big up bro
@JuvenileDebwe-bv8ow
@JuvenileDebwe-bv8ow 17 дней назад
Broz kulibe komwe zikuyenda ata! konse kuno mavuto man anthuwa ngakuba mukadzamva wina akuyamikira ameneyo ngo jiya
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 17 дней назад
MCP ndi chakwera akuchoka kale osadandaula, no vote.
@michealchaomba9761
@michealchaomba9761 16 дней назад
Mcp = kuba, kupha ndi kuononga amanga malawi yonse
@patrickkadzeya3020
@patrickkadzeya3020 17 дней назад
Mulungu akwaona zonse zoyipa zonse akupanga ku mbuba ya Malawi, ku chokera ku mpoto, pakati ndi ku m'mwera tonse ndi a modzi .😊
@user-lr5bz7qk2d
@user-lr5bz7qk2d 17 дней назад
Mabugwe kunja amapeleka ndalama koma zonse zimabedwa ndi chakwela ndi chifukwa chache anapha zake cholinga azibabe galu amenei zakoma ndalama mbava ndalama anavomeledzana Kale ku parliament zili kuti galu chakwela
@samchibenene4458
@samchibenene4458 17 дней назад
Chakwera Na commit yako yose vimavi vinu Mose masende inu
@coastersRob
@coastersRob 17 дней назад
Inu mukuganiza kuti zinyawu zingamange nsewu malo moti azikazola manyi kudambwe ndiye eeeee
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 17 дней назад
Boma iri ndi manyaka kukanakhala ku Lilongwe bwezi atamanga kale
@SELLASella-bb1mr
@SELLASella-bb1mr 17 дней назад
No voting for chakwela
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Yes we don't need to vote for him
@user-nd9cm3yl7e
@user-nd9cm3yl7e 16 дней назад
Beautiful Bg km utopa mcp ilibe organaisa oionela zachitukuko kulibeko athu azelu iweyo asiye thawiyatha kale ingodikila apm muthalika ndikatundu azakoza zimenezo mosamvuta mcp palibeso chimene amadziwa Akubwela ma drive adpp azaendetsa zonsezo
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 17 дней назад
Shame Bagamoyo chikangawa💔💔💔🙌🙌🙌
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v 16 дней назад
Palibe chomwe akuziwa ngakhale reshafu cabinet sakuyiziwa mungobwerera Ku Church basi
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 17 дней назад
Asiyeni amenewo Achakwera ndi Achisiru sangapange chitukuko kumpoto. Boma lawakanika basi
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo 17 дней назад
Kulibe komwe akuyamikila Boma la MCP ,ndipo pamenepo ndipang,ono madala Ife kuno ndiye kulibe chimanga
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 17 дней назад
Minister of transport Jacob hara akulephera kwawo kumzimba kulibetuu mseu, kumzimba kuliseu unayamba nthawi ya bingu mpaka pano amapangilapo kampeni bas alipheee. Mseu wa mzimba eswatini mzalangwe kudutsa kafukule kufika ekwendeni thakhala tikunamizidwa mpaka pano ma contractor anochoka kalekale. Komaso mavuto onsewa ndi mafumu athu sakutithandiza ai, Pepa mubale wanga zativuta bas miseu ikupangidwa komwe ku Lilongwe northern region zero pa 10
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk 17 дней назад
Osawopa osatopa osafooka
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b 17 дней назад
Koditu ngat kumangako akumanga ku Lilongwe kokhako kwawo amanama za msewu wa mangochi makanjira km ndi boza proper gander ikumaveka pa MBC ija kulibeko makanjira road sakumanga
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Chakwerayi Eeeeee Ndi nthakati
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 17 дней назад
Nduna ndi ma MP akumamupusisa president kumamunamiza kuti zimthu zimuyenda pomwe palibe chikuyenda nduna zones sizimamufunila zabwino president wawo akumunamiza
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 17 дней назад
Kubwele a anyamata ndi atsikana'aku Kenya ngati muli ndi mantha kumeneko.apo,bi.kusa, anyamata ndi atsikana'kumangotibula, aliyese ngati uli pafupi ndi ma office.
@Mervic-vm8eo
@Mervic-vm8eo 17 дней назад
Chakwera no campain kupoto kulibe vote Yako
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z 16 дней назад
Amangileni msewu where is the money goes
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Chakwera kwake kunatha kale kale yekhanso akudziwa
@user-lr5bz7qk2d
@user-lr5bz7qk2d 17 дней назад
Ndalama anadya chakwela aboma awa AKUBA ndalama nanga zili kuti
@marryphili5419
@marryphili5419 17 дней назад
Ndalama anagulira magalimoto
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 17 дней назад
Koma vote nde yinapita mmatope basi kuvotela anthu akubawa
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Ndipo ndipo brother mmm
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 16 дней назад
munthu wa mulungu akugula ma Bible tiziwelenga
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v 16 дней назад
Chakwerayo ndi mbuzi yamunthu palibe chomwe akupanga
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Koma Chakwera guys mmmmmm inu munthuyi amatamba ndithu eeeeeeeeeee ndi mfiti yotheratu Chakwera 😢😢😢
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 16 дней назад
Akumanga kwawo ku lilongwe
@lucymuhala2176
@lucymuhala2176 17 дней назад
Kuyankhula mu chizungu tomato vindele ivi Vili m'boma vambula mahara
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Lucy tanditanthauzire pls
@innocentkandulu2825
@innocentkandulu2825 17 дней назад
mawu abwino kwambili MCP boma lawuchitsiru
@FinasonSmart-j9d
@FinasonSmart-j9d 17 дней назад
That's true
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Mu campaign tikuzapha ndi mwala Chakwerayo sure
@victormwamadi2725
@victormwamadi2725 16 дней назад
Keep it up brother good job
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 15 дней назад
Chakwela satana wohipa
@user-bb5iy7ry5h
@user-bb5iy7ry5h 17 дней назад
😂😂😂😂😂awuzeni inuyo
@user-dg5pc6rz1b
@user-dg5pc6rz1b 17 дней назад
Mmmmmm mcp
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 17 дней назад
Zoona wayitha
@jonathanmbewe4246
@jonathanmbewe4246 13 дней назад
Iiii komatu so sad
@saramoyo8019
@saramoyo8019 17 дней назад
Rumphi Rumphi work up
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 16 дней назад
Okuba amenewa
@user-gd2kl1fx1q
@user-gd2kl1fx1q 17 дней назад
Ndipo ku mpoto asazabwereso
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 17 дней назад
Achakwera akuba ndalama
@user-lr5bz7qk2d
@user-lr5bz7qk2d 17 дней назад
Chakwela uzikhala konko ku mpoto ndi ku mwela ilibe chako galu tizakuonesa pa kampeni Galu bwako ubele tu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Ndipo koopsa zedi azadziwanso
@dalitson3558
@dalitson3558 17 дней назад
Namachende chakwera akudya ndalama zamisewu pamozi ndi nyau
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d 17 дней назад
Apo pofunika ku matcha basi atule udindo
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Ndipo zoonad bro
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 17 дней назад
Zazii
@user-rm2xv8ys1i
@user-rm2xv8ys1i 17 дней назад
Useless boma
@MussaHassani-zg1hm
@MussaHassani-zg1hm 17 дней назад
😂😂😂
@robsontyg3928
@robsontyg3928 17 дней назад
Nywanamawo
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 16 дней назад
Inuyo mumatamba akulu ndinu mfiti pali zotukwanira munthu apa kungobadwa mokuda mtima basi olo unditukwane sindikusamala km ndinu achitsilu mani.
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 17 дней назад
I think ndalama anadya chatsika
@mathewsmbaluko8522
@mathewsmbaluko8522 17 дней назад
Koma boma ili🤔
@user-cs6zy3ix8d
@user-cs6zy3ix8d 17 дней назад
A chisilu inu
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d 17 дней назад
Chisilu Ndiwe
@user-wl4nd7ic1s
@user-wl4nd7ic1s 17 дней назад
Mbuziii ya Mano kusi ndiweooohh
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc 17 дней назад
Useless government
Далее
TRAFFIC VIOLATORS CAUGHT RED HANDED BY DMP POLICE
12:40