Тёмный

Atupele wasokoloka komwe anali ndipo akufuna achemetse 2025 moto kuti buuu 

Malawi Trends TV
Подписаться 33 тыс.
Просмотров 11 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

9 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 41   
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 16 дней назад
Tupele thawi yanu timakuvuna mulungu akudalisene boma 2025
@JohnAsendi
@JohnAsendi 16 дней назад
Takukwela koma muzikhala serious kumayenda Madera onse osamango yang;ana bulantaya. Mangochi. Machinga basi no mudzizayenda Madera onse osamaopa ziko ilibe mwini ili or nso Ana alimmimba akudikira upulezdent osati za Boma LA Chakwera ndi kamasuti tilamulira 100 years kuyendesa Kwa uku dziko lidzakha opanda anthu kumangosamukira kumozambiki 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 16 дней назад
Atupele 🤜🤛
@user-kk4uj8ko8k
@user-kk4uj8ko8k 15 дней назад
Osaderakhawa ife tikufuna Ada d afa pita wamuthalika dpp🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤bas
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 дней назад
APM ❤❤❤❤❤❤
@amoschataika7440
@amoschataika7440 16 дней назад
Atupere samakhala serious
@user-pe7wg2js2z
@user-pe7wg2js2z 16 дней назад
Nthawi ya kwana president ndinu
@jamiajafali6619
@jamiajafali6619 16 дней назад
UDF❤
@arabisaidi4768
@arabisaidi4768 16 дней назад
Yah apano nde tanyadila vote yanga Atupele muluz 2025 ❤❤❤❤❤
@MagretMphalika-c5v
@MagretMphalika-c5v 16 дней назад
atupele emweyo moto kuti buuuuuuuu!!!!!!!@ vote for Atupele basi
@MagretMphalika-c5v
@MagretMphalika-c5v 16 дней назад
mmakwana akalindo apule aanthu osauka timakudalirani ife
@ThokozaniMaulana-oi5hz
@ThokozaniMaulana-oi5hz 16 дней назад
Be a president please atupele muluzi
@malickjeofly7843
@malickjeofly7843 16 дней назад
ipatse moto atupele ife pambuyo pako
@AlasonPaulo-ht7zb
@AlasonPaulo-ht7zb 16 дней назад
Sunalakwise chipan cha athu ichi ulem wanu bg
@user-rw8tb8pj8i
@user-rw8tb8pj8i 15 дней назад
Atupele ndi chiyembekezo cha Amalawi
@YaqoobStandwell
@YaqoobStandwell 16 дней назад
Atupele osamusiyila ziko chakwela akulamulila ngat akulamulila nyumba mwake
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 16 дней назад
Ndimweyu President tifuna mnyamata
@MustapherLino
@MustapherLino 16 дней назад
Atupere plz be serious for 2025
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 16 дней назад
Plz muzitipatsirako zomwe ayankhura eni akewo
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh 16 дней назад
Awa ndiye anthu oononga dziko,nanga mantha Ali umu angakhale mtsogoleri wa dziko?
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 16 дней назад
Ndi ofoila uyu
@AubreyChiyaya-ty8ge
@AubreyChiyaya-ty8ge 14 дней назад
Wadzuka uyu chifukwa CHOTI chilima watisiya
@MerryWayson
@MerryWayson 16 дней назад
Takulandilani Mr Muludzi
@JaneMapingo
@JaneMapingo 16 дней назад
Ipase Moto tili pa mbuyopo
@LiamTennessee
@LiamTennessee 16 дней назад
Iwensotu iwe wa Malaei trends bwanji subwela ndi ma actual audio kapena video , nthawizonse umangoti zakhalabwanji kuti???
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 16 дней назад
Ipase moto 🔥
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 16 дней назад
Dpp woye ApM ❤❤
@CatherineMbela
@CatherineMbela 15 дней назад
More fire 🔥🔥🔥🔥
@FelixPhiri-w1z
@FelixPhiri-w1z 16 дней назад
Boma ilooooo!!!!!!!!
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 16 дней назад
Asavutike tikavotela marry chilima
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb 16 дней назад
Atupele ndi munthu okhudwisa anthu.atupele akadali mwana angomusiya mayi akuyendesa yemweyo basi
@CatherineMbela
@CatherineMbela 15 дней назад
Eeee zoona samakhala serious Koma ndi wachinyamata wabwno
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 16 дней назад
Aaaaa sakhala serouus uyu
@CatherineMbela
@CatherineMbela 15 дней назад
Eeeeeeee zoona Komatu ndi wachinyamata wabwno kaya vto ndi chani akuluwa
@masakaunga4099
@masakaunga4099 16 дней назад
Its not a dynasty
@zondanitzulumusicfly.5202
@zondanitzulumusicfly.5202 16 дней назад
Amaopa chilima
@user-rl5zq1qr4d
@user-rl5zq1qr4d 16 дней назад
Nkhani yake YOMWEYO yapita kwa Chilima? Pali mitu Ina imakayisa kuti achimwenewa sanayambe apengapi?
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 дней назад
​@@user-rl5zq1qr4dNdipo brother mmmm chilima alipo mesa anaimiliranso? Anthu ndiovuta zed
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 16 дней назад
@@user-rl5zq1qr4dChakwera anapha Chilima
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 16 дней назад
Kikkkkkki ​@@user-rl5zq1qr4d
Далее
УРА! Я КУПИЛ МЕЧТУ 😃
00:11
Просмотров 509 тыс.
Получилось у Миланы?😂
00:13
Просмотров 789 тыс.
BON KALINDO 26 JULY 2024 KUGAZAGAZA KWA PA FRIDAY
14:46
BON   KALINDO LERO PA  26 JULY 2024 |
16:05
Просмотров 11 тыс.
ZOMWE ZIDALI KU BALAKA 🙌🙌🙌🙌25 July 2024
27:52
МУХОЧИРО КОР НАКОВЕН
16:58
Просмотров 47 тыс.
Nancy vs Che Nkope - Zikhale Ngoma Kapena Drums?
10:46
Mkangano wa Lucius Banda ndi Bingu
13:20
Просмотров 144 тыс.