Тёмный

BON KALINDO APA NDE WALANKHULA MOTO KUTI BUU | 

DZIWE TV
Подписаться 24 тыс.
Просмотров 22 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

8 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 135   
@VungaQueen
@VungaQueen 15 дней назад
Number Bon kalindo munthu osaopa kotse mulungu azikupatsani moyo wautali 👏👏🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 16 дней назад
The DC mwana oopsa kwambiri from Njedza vg😅😅 love you more
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj 16 дней назад
THE DC IS THE ONE WHO TELLING PEOPLE THE TRUTH TO ANDSTAND EFFECT ON THAT'S ALL THE WAY I'M IN THE SAUTH AFRICA ESTAN CAP THANK YOU MR BON KALINDO MY ALLAH BLESS YOU ALWAYS HAVE A GREAT DAY ORROWYESS
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj 15 дней назад
CONGRATULATIONS TO YOUR MY BROTHER FRIEND FROM MALAWI I'M OLOSO FROM MALAWI ASHANKWELA HIS MUST LEE SINE PEOPLES OF COUNTRY 👌
@AshleyPhiri-m7t
@AshleyPhiri-m7t 14 дней назад
The DC fire fire 🔥 your speak true papa don't be afraid, God i will protect you all the time
@FahadiFalaji
@FahadiFalaji 16 дней назад
Watching from pmb south Africa number 1 God first❤
@MahallaMinistries-fv1hw
@MahallaMinistries-fv1hw 16 дней назад
Thanks Bon. I deeply feel that any priest asking for citizens' silence on the Chikangawa plane accident must first silence him/herself in the Spirit. Any gracious priest must flee from the tricky temptation of deliberately misinterpreting related scriptire like Romans 13:1-7). O LORD, save the integrity of our priesthood for a godly Malawi.❤❤❤
@user-or7ng3fj8f
@user-or7ng3fj8f 15 дней назад
Bonnnnnnnn kalindooooooooo the DC 🔥fire
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 16 дней назад
Mangochi ndi district yodzuka yosagona sitimaopa ife Ayao amanyi mutimva a MCP ,ife nganganga! Pambuyo pa president wanthu the DC mwana oopsa kwambiri. Ndiponso simukwanitsa kumupha tadzuka , munantola Chilima kuchikangawa pano tonse tadzuka pa ifa ya Chilima ndipo tipanga za ku Kenya very soon.
@DissChikondi
@DissChikondi 16 дней назад
Fire fire
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 15 дней назад
We silute you the DC. May the almighty God continue protect you wherever uou will go♥️♥️♥️♥️
@annamazingashaibuh6276
@annamazingashaibuh6276 14 дней назад
😂😂😂😂😂😂your expensive mwana woopsa kwambiri eish koma Bon the DC!
@FlechaChipeta
@FlechaChipeta 16 дней назад
Warankhura bwino kwambili kalindo ❤
@aggogokina8992
@aggogokina8992 16 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂 azunguze anthu okubawa Boooon Kalindooo💪💪
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no 16 дней назад
Thanks so 🎉🎉🎉🎉🎉
@JosephLuna-o1d
@JosephLuna-o1d 16 дней назад
Thanks for all you doing Mr kalidoo
@MacreaChilingulo-ob9gb
@MacreaChilingulo-ob9gb 15 дней назад
The DC ! !!! MWANA WOOOOOOPSYA !!! Kwambiri , Nyama muzidya inde !; koma movutika kwambiri !
@MaureenMollen
@MaureenMollen 14 дней назад
The DC keep the fire burning.
@CeciliaNkhoma-nz7uj
@CeciliaNkhoma-nz7uj 16 дней назад
Thank you very much the DC for your work on behalf of poor Malawian
@ElizaSemu
@ElizaSemu 15 дней назад
He feels pain of all poor Malawians Bon Kalindo mwana owopsa kwambiri the DC even angel akukuwombela mmanja good work reveals the truth while the evil hides inside the money
@user-mv8vy3ht3n
@user-mv8vy3ht3n 16 дней назад
Watching from zimbabwe DC
@StevenNyozan
@StevenNyozan 15 дней назад
😂😂😂😂amasulidwe basi Ana akubawa atikwanaaah
@user-lw9su5om5z
@user-lw9su5om5z 15 дней назад
😂😂😂😂 kma bon kalindo chipongwe eee kkkkkk the Dccccccccccc
@SilenceSanued
@SilenceSanued 16 дней назад
😂😂😂😂😂😂 Iputeni milandu inayo ife tiri ku msana kwanu😂😂😂😂😂 mantha njeee
@masmonmark84
@masmonmark84 15 дней назад
Ndimawona ngati alankhula zanzeru awa tinvomereze kuti mukufunika kubwerela ku uphuzitsi kuja mukapange upgrade chifukwa chomwe mumapanga ndikunyoza koma osabweretsa solution.aaaaah
@masmonmark84
@masmonmark84 15 дней назад
And Kodi mukufuna ife tizitengeka Nanu kenaka mudzatipusitse Pamawa mwayiwala kuti munanena nokhat zakuti Malawi siomufera? Ndiye musatikwanepo apa
@RichmondHavy
@RichmondHavy 16 дней назад
The DC 🔥🔥🔥
@ishmaelcassim806
@ishmaelcassim806 16 дней назад
The Dc mr bon kalindo you are talking true. M C P Must go Out we don't want m c p any more.Mr bon kalindo more
@user-ih7li3im4s
@user-ih7li3im4s 16 дней назад
God always protect you, Chilungamo chako Mulungu akuziwa kufunika kwako kwa ife
@joneskalitsilo6556
@joneskalitsilo6556 16 дней назад
Akuti osampha mwanako bwanji!😂😂😂😂 Koma kalindo.. kkkkkkkkk
@FranklinNdovi
@FranklinNdovi 16 дней назад
This nation needs causal factors that lead to the plane crash not autopsy reports.
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 16 дней назад
Ambuye mutetedzereni bon kalindo ndi munthu yemwe akutitthonza pa mavuto athu
@lucianosamissonejose2374
@lucianosamissonejose2374 16 дней назад
A Bon kalindo inuyo mulungu adzikudalitsani ndine Luciano kuchokera ku Mozambique
@UsenLashid
@UsenLashid 15 дней назад
DC woyeeeeeee katundu womanga ndi mawaya
@MacleanMkhalipi
@MacleanMkhalipi 16 дней назад
Stand to honest Mr kalindo
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 16 дней назад
Inu ndi 1 Bon Kalindo 😂❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@nessiemfunie
@nessiemfunie 16 дней назад
,,ngakhale tili Mayiko akhunja tizabwela tizaku votelan Mr bon karindo
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 16 дней назад
Kkkkkkkkkk if you try to catch my people I will catch you 😅😅😅😅😅😅😅
@user-mq5vs4hn6o
@user-mq5vs4hn6o 16 дней назад
Watching you from Zambia ❤❤❤❤❤❤❤
@PhillipLipenga
@PhillipLipenga 16 дней назад
😂😂😂 aidya nyama koma azidya akulila kkkkkkk
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 16 дней назад
You are becoming bakili muluzi TV 😂❤❤❤
@StanlyBeza
@StanlyBeza 15 дней назад
😂😂,😂😂the diiiisiiiiii
@GiftSaidimbewe
@GiftSaidimbewe 16 дней назад
Ndimakunyadilan the DC tilinanu
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 16 дней назад
Chilima anaphedwa ndi Chakwera. Aliyense akudziwa zimenezo ndipo ndikudikira mwachidwa kuti atiuze chomwe chinamupha Saulos Klaus Chilima
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 16 дней назад
Tifufuza mbuziyi ikatuluka mboma...ndipo chikaferatu kundende chimfiti chimenechi.......mbuzi😮😮😮😮😮
@MphatsoBanda-uv4nr
@MphatsoBanda-uv4nr 16 дней назад
Ati tikusendani😂😂😂😂
@LameckDanken-tm4rt
@LameckDanken-tm4rt 16 дней назад
The DC more fire anthu admarc bwana akuvutika kooopsa bwana president wa osauka
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 16 дней назад
Asaaa koma winiko mpaka amako😂😂😂😂
@RASHIFORDHSK
@RASHIFORDHSK 15 дней назад
My vote
@chifukanyo9447
@chifukanyo9447 16 дней назад
😂😂😂😂 ati atamangidwe ndi amako😂😂
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m 15 дней назад
The DC ❤❤❤❤❤
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 16 дней назад
😂😂😂Akakumanga bail ilipo
@Zamwano
@Zamwano 16 дней назад
Kd nanga ma demo aja Mesa lero pa 10 tulukan munyumba am already outside
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 16 дней назад
The Dc good Messnge Mr bon kalindo ❤
@BensonChilundu
@BensonChilundu 16 дней назад
Tikufuna Chakwera adzayankhe milandu yonse,yosakaza chuma cha boma komanso imfa ya anthu asanu ndi atatu omwe anafa ku Chikangawa ndi ena onse ngati Zikhale Ngoma,Mkaka,Chimwendo Banda mkulu wa apolisi,mkulu wa nkhondo ndi ena onse mkazi wa Chakwera komansotu mwana wake Nick
@TalazanGamah
@TalazanGamah 16 дней назад
We follow
@LamieTiger
@LamieTiger 16 дней назад
Captain kalindo dolo kwambili
@user-gx3xc9lk8x
@user-gx3xc9lk8x 16 дней назад
The DC😂😂😂😂😂❤❤❤❤
@ThokozaniChadza
@ThokozaniChadza 16 дней назад
Moto booo Dc tililimozi ❤❤❤
@ChimwemweNgwende
@ChimwemweNgwende 16 дней назад
A keyala anakanika kuipeza ndege yawoyawo 24hrs ndiye pano ati akuti akufufuza chomwe chinagwesa ndege kodi achipeza? Kkkkkkkk 24hrs failed to trace ndege by using technology search ndiye achipeza chomwe chinagwesa ndege?
@aarongrey5620
@aarongrey5620 16 дней назад
Komaso Bon kalindo ndimangowona ngati tingopeza nafeso futi kujozi kuno timenyane ndiboma lachakwela ukuwona bwanji
@Dysonkhofi
@Dysonkhofi 16 дней назад
Inenso ndikuona choncho Tiwachotse agaluwa
@LinlyNakombe
@LinlyNakombe 16 дней назад
Keep fire burning
@williamdaka79
@williamdaka79 16 дней назад
Umakwana boma lautsiru kwabasi
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 16 дней назад
Kkkk boma laluza milandu
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 16 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Born kalindo 🙏🙏🙏🙏🙏
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 16 дней назад
D c wi love you 🎉
@Mohammed-sk1fy
@Mohammed-sk1fy 16 дней назад
The DC Born
@Momweekly
@Momweekly 16 дней назад
DC he is the voice of the voice less
@user-cg5ml7ym4v
@user-cg5ml7ym4v 15 дней назад
Uthenga wamphavu kwambiri ife tili pambuyo
@thokozanisukah6448
@thokozanisukah6448 16 дней назад
Mfana oophya kwambili
@jamesgama5489
@jamesgama5489 16 дней назад
Unasala wekha bon anzako onse anadyesedwa ma banzi pano ali chete
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 16 дней назад
Km ndodo iyandikile coz komwe tikupitak kulib kuchez
@LINELYBISANI
@LINELYBISANI 16 дней назад
Antongwetongwe olalikira hahaha
@PhysicChands
@PhysicChands 16 дней назад
Boni kalindo moto kuti buu umatiyimilila ❤❤
@FrancisDinala
@FrancisDinala 16 дней назад
Watching from israel pa boma
@ShupeZiwa-s4y
@ShupeZiwa-s4y 16 дней назад
Uyu ndi one😂
@fransiscopetro7491
@fransiscopetro7491 16 дней назад
The DC njedza Villege TA MABUKA
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 16 дней назад
Yomweyo DC😅
@user-rc4pf7hr9f
@user-rc4pf7hr9f 15 дней назад
👌👌👌👌👌👌👌
@AdamSamson-gb7qz
@AdamSamson-gb7qz 16 дней назад
Koma kumenekoo!!
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 16 дней назад
Zikuyenera kutero, DC ndiwe President. Ukuyenera chitetezo chochuluka ndithu. Komanso achitetezowo awonjezere, azikwana 3000
@kayceesamuels
@kayceesamuels 16 дней назад
Amve pain amenewo
@FreddieNkhoma
@FreddieNkhoma 16 дней назад
Boni kalindo keep it up
@JanaAmina-iw6bf
@JanaAmina-iw6bf 16 дней назад
👌
@TisopeChagala
@TisopeChagala 16 дней назад
Enafe nde tinasiya kale kale kuonera Mbc tv
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 16 дней назад
Thanks watching from Blantyre
@NeverBeforeMnesa
@NeverBeforeMnesa 16 дней назад
Kodi za ma demonstration pa 10 July zili Pati?
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n 15 дней назад
nane ndufuna kuziwa.. zilipati zakuyenda pa nseu lero?
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 16 дней назад
Chakwera sakumvesa za kulimba mtima kwako
@user-zm9sf2mj7u
@user-zm9sf2mj7u 15 дней назад
Thanks bon kalindo
@AnnieZiba
@AnnieZiba 16 дней назад
Moseliwa
@stevejizaremu3396
@stevejizaremu3396 16 дней назад
Osaopa
@MphatsoMhoney-xn2ft
@MphatsoMhoney-xn2ft 16 дней назад
Akalindo
@user-yk4by8iy8k
@user-yk4by8iy8k 16 дней назад
Zoona bon kalindo mulungu alinawe
@oskidooscar7468
@oskidooscar7468 16 дней назад
Koma sakuyamkhulapo za manganya ku mcp
@davidjames679
@davidjames679 16 дней назад
kod mesa mmat lelo tikathamange kod ??
@user-rc4pf7hr9f
@user-rc4pf7hr9f 15 дней назад
🎉🎉🎉🎉🎉
@texonkautera
@texonkautera 15 дней назад
😅😊😊😊😮
@PhysicChands
@PhysicChands 16 дней назад
❤❤❤
@MusaManati-ho4zf
@MusaManati-ho4zf 16 дней назад
The dc Moseliwa mapwiya......
@AngolanChinga
@AngolanChinga 16 дней назад
The DC ❤❤❤❤❤❤
@chipilirokalison1334
@chipilirokalison1334 16 дней назад
Mwana ooopsyaa kwambiri mulungu akudalitse
@Janatukaunda
@Janatukaunda 16 дней назад
The DC mwana owopsa kwambiri
@StanleyDama
@StanleyDama 15 дней назад
Lelo ? Wait for next
@JonathanChimwaza
@JonathanChimwaza 16 дней назад
Chilungamo chi ma wawa chikamayakhulidwa
Далее
BON   KALINDO LERO PA  26 JULY 2024 |
16:05
Просмотров 4 тыс.
Я читаю переписки сына
00:18
Просмотров 663 тыс.
Speech by Honourable Dr. Kondwani Nankhumwa
5:28
Просмотров 6 тыс.
KWACHEMA KUBWEZA MOTO CHAWEZI |
29:18
Просмотров 10 тыс.
Lwasa afunye sente bupya,aguze benz ne rangerover
30:52
MZUNGUYU APA MCHOTSENI |
27:24
Просмотров 18 тыс.
ZOMWE ZIDALI KU BALAKA 🙌🙌🙌🙌25 July 2024
27:52
Я читаю переписки сына
00:18
Просмотров 663 тыс.