Without Bakili Muluzi TV and the great journalist we are nothing why this is the only TV channel that reveals the hidden story. I❤ the guy coz he exposes the secret of the useless government under Chakwela to let us know. May Allah the almighty protect him as he did with Moses pamene falao amkafuna kumupha.kunkuyu avule dzina la Moses coz Moses amene tikumudziwa ife adali ooa Yehova ndibwino atamatchedwa Yudas ndikupha kwakeko
Anthu anasiya kalekale kuvera chiwayalesi Cha radio1 ndizinanzi sopano anthu angoveza Bakili muluzi tv bon kalindo ndi Limpopo FM mosogozedwa ndi mtanyiwa 😂😂😂
Boma la mcp kuyambila kale silipanga chitukuko km kusaka athu tiyeni tipephe mwini moyo atilanditse kuzoopswazi but God is not human body atimenyela khondo yawe bless yours and you me love getting blessed with God amen
That's why we love our only bakili muluzi channel TV every explation it's their own witnesses no matter how u hate it mr promise president with ur ministers mcp evil government of Malawi
This guy is number one,,,and he is not alone 😂😂😂muli finger mkatimu,alipo akumuuza zinsisi from state house, chakwera galu iwe uyaluka,,,pantumbo pako pamozi ndi gulu lako
bakili muluzi tv iweyo ndi number one ndipo iweyo ndi womphuzila kuposa achakwela enafe mwatitsakula maso ndi chilungamo chanu ndipo musasiye ayii ndipo mulungu ayenjezele mzeru zina
Best of the best journalist, eyes of the country, we know kuti chakwela ndi gulu lake la zigawenga spent sleepless night planning to silence you. But you're in our prayers, God is gonna fight for you.
That's why l like this chanel chifukwa Akayankhula amationesa umboni kp it up Bakili muluzi tv.mbuzizi zayamba kuyaluka ndipo ziyalukadi sazayiona voti yathu agalu awa tinawabitera kamba ka manifesto achilima za MCP tinazitaya kalekale iya
Koma anyaniwa tikazawachotsa m'boma chaka cha mmawachi dziko likuna likuziwen big man not now because we know anthu akukusakan but next year amalaw tikufuna tizakuziwen akulu 💪
Chakwera sanakhalepo mbusa ndichigawenga kuyambila pachiyambi pamozi ndi nkazi wake zigawenga koma satitha. Akulu ndinu patali tisaname mukuvesa kukoma ndithu