You are blind because you don't know how many millions this man given but not a single day you will hear that he has donated to the poor he claims to stand for. Hypocrisy at its best.
Amalawi tafatsa mopusa kwambiri tikungodandaulira kumbali waiting for someone to come and fight for us yet ife tangokhala koma bon kalindo wayesesa kumbali yake
Mzoonadi wamisala anaona nkhondo inu mumatiyimilira the DC booooon kalindooooooo mwana owopsyaaa kwambiri.Auzeni amve a opposition they have to open their eyes